Psalms 86 (BOGWICC)
undefined Pemphero la Davide. 1 Ndimvereni Yehova ndipo mundiyankhe,pakuti ndine wosauka ndi wosowa. 2 Yangʼanirani moyo wanga, pakuti ndine wodzipereka kwa Inu.Inu ndinu Mulungu wanga;pulumutsani mtumiki wanu amene amadalira Inu.Inu ndinu Mulungu wanga. 3 Mundichitire chifundo, Inu Ambuye,pakuti ndikuyitana Inu tsiku lonse. 4 Bweretsani chimwemwe kwa mtumiki wanu, Ambuye,pakuti ndimadalira Inu. 5 Inu Ambuye, ndinu wokhululuka ndi wabwino,wodzaza ndi chikondi kwa onse amene amayitana Inu. 6 Yehova imvani pemphero langa;mvetserani kulira kwanga kofuna chifundo. 7 Pa tsiku la mavuto anga ndidzayitana Inu,pakuti Inu mudzandiyankha. 8 Pakati pa milungu palibe wina wofanana nanu Ambuye;palibe ntchito zolingana ndi ntchito zanu. 9 Mitundu yonse ya anthu imene munayipangaidzabwera ndi kudzalambira pamaso panu Ambuye;iwo adzabweretsa ulemerero pa dzina lanu. 10 Pakuti ndinu wamkulu ndipo mumachita zodabwitsa;Inu nokha ndiye Mulungu. 11 Ndiphunzitseni njira yanu Yehova,ndipo ndidzayenda mʼchoonadi chanu;patseni mtima wosagawikanakuti ndilemekeze dzina lanu. 12 Ndidzakutamandani Ambuye Mulungu wanga, ndi mtima wanga wonse;ndidzalemekeza dzina lanu kwamuyaya. 13 Pakuti chikondi chanu nʼchachikulu kwa ine;mwandipulumutsa ku malo ozama a manda. 14 Inu Mulungu wanga, anthu odzikuza akundithira nkhondo;anthu ankhanza akufuna kundipha,amene salabadira za Inu. 15 Koma Ambuye ndinu Mulungu wachifundo ndi wokoma mtima,wosakwiya msanga, wodzaza ndi chikondi ndi wokhulupirika. 16 Tembenukirani kwa ine ndipo ndichitireni chifundo;perekani mphamvu zanu kwa mtumiki wanundipo pulumutsani mwana wa mdzakazi wanu. 17 Mundionetse chizindikiro cha ubwino wanukuti adani achione ndi kuchititsidwa manyazi,pakuti Yehova mwandithandiza ndi kunditonthoza.
In Other Versions
Psalms 86 in the ANGEFD
Psalms 86 in the ANTPNG2D
Psalms 86 in the AS21
Psalms 86 in the BAGH
Psalms 86 in the BBPNG
Psalms 86 in the BBT1E
Psalms 86 in the BDS
Psalms 86 in the BEV
Psalms 86 in the BHAD
Psalms 86 in the BIB
Psalms 86 in the BLPT
Psalms 86 in the BNT
Psalms 86 in the BNTABOOT
Psalms 86 in the BNTLV
Psalms 86 in the BOATCB
Psalms 86 in the BOATCB2
Psalms 86 in the BOBCV
Psalms 86 in the BOCNT
Psalms 86 in the BOECS
Psalms 86 in the BOHCB
Psalms 86 in the BOHCV
Psalms 86 in the BOHLNT
Psalms 86 in the BOHNTLTAL
Psalms 86 in the BOICB
Psalms 86 in the BOILNTAP
Psalms 86 in the BOITCV
Psalms 86 in the BOKCV
Psalms 86 in the BOKCV2
Psalms 86 in the BOKHWOG
Psalms 86 in the BOKSSV
Psalms 86 in the BOLCB
Psalms 86 in the BOLCB2
Psalms 86 in the BOMCV
Psalms 86 in the BONAV
Psalms 86 in the BONCB
Psalms 86 in the BONLT
Psalms 86 in the BONUT2
Psalms 86 in the BOPLNT
Psalms 86 in the BOSCB
Psalms 86 in the BOSNC
Psalms 86 in the BOTLNT
Psalms 86 in the BOVCB
Psalms 86 in the BOYCB
Psalms 86 in the BPBB
Psalms 86 in the BPH
Psalms 86 in the BSB
Psalms 86 in the CCB
Psalms 86 in the CUV
Psalms 86 in the CUVS
Psalms 86 in the DBT
Psalms 86 in the DGDNT
Psalms 86 in the DHNT
Psalms 86 in the DNT
Psalms 86 in the ELBE
Psalms 86 in the EMTV
Psalms 86 in the ESV
Psalms 86 in the FBV
Psalms 86 in the FEB
Psalms 86 in the GGMNT
Psalms 86 in the GNT
Psalms 86 in the HARY
Psalms 86 in the HNT
Psalms 86 in the IRVA
Psalms 86 in the IRVB
Psalms 86 in the IRVG
Psalms 86 in the IRVH
Psalms 86 in the IRVK
Psalms 86 in the IRVM
Psalms 86 in the IRVM2
Psalms 86 in the IRVO
Psalms 86 in the IRVP
Psalms 86 in the IRVT
Psalms 86 in the IRVT2
Psalms 86 in the IRVU
Psalms 86 in the ISVN
Psalms 86 in the JSNT
Psalms 86 in the KAPI
Psalms 86 in the KBT1ETNIK
Psalms 86 in the KBV
Psalms 86 in the KJV
Psalms 86 in the KNFD
Psalms 86 in the LBA
Psalms 86 in the LBLA
Psalms 86 in the LNT
Psalms 86 in the LSV
Psalms 86 in the MAAL
Psalms 86 in the MBV
Psalms 86 in the MBV2
Psalms 86 in the MHNT
Psalms 86 in the MKNFD
Psalms 86 in the MNG
Psalms 86 in the MNT
Psalms 86 in the MNT2
Psalms 86 in the MRS1T
Psalms 86 in the NAA
Psalms 86 in the NASB
Psalms 86 in the NBLA
Psalms 86 in the NBS
Psalms 86 in the NBVTP
Psalms 86 in the NET2
Psalms 86 in the NIV11
Psalms 86 in the NNT
Psalms 86 in the NNT2
Psalms 86 in the NNT3
Psalms 86 in the PDDPT
Psalms 86 in the PFNT
Psalms 86 in the RMNT
Psalms 86 in the SBIAS
Psalms 86 in the SBIBS
Psalms 86 in the SBIBS2
Psalms 86 in the SBICS
Psalms 86 in the SBIDS
Psalms 86 in the SBIGS
Psalms 86 in the SBIHS
Psalms 86 in the SBIIS
Psalms 86 in the SBIIS2
Psalms 86 in the SBIIS3
Psalms 86 in the SBIKS
Psalms 86 in the SBIKS2
Psalms 86 in the SBIMS
Psalms 86 in the SBIOS
Psalms 86 in the SBIPS
Psalms 86 in the SBISS
Psalms 86 in the SBITS
Psalms 86 in the SBITS2
Psalms 86 in the SBITS3
Psalms 86 in the SBITS4
Psalms 86 in the SBIUS
Psalms 86 in the SBIVS
Psalms 86 in the SBT
Psalms 86 in the SBT1E
Psalms 86 in the SCHL
Psalms 86 in the SNT
Psalms 86 in the SUSU
Psalms 86 in the SUSU2
Psalms 86 in the SYNO
Psalms 86 in the TBIAOTANT
Psalms 86 in the TBT1E
Psalms 86 in the TBT1E2
Psalms 86 in the TFTIP
Psalms 86 in the TFTU
Psalms 86 in the TGNTATF3T
Psalms 86 in the THAI
Psalms 86 in the TNFD
Psalms 86 in the TNT
Psalms 86 in the TNTIK
Psalms 86 in the TNTIL
Psalms 86 in the TNTIN
Psalms 86 in the TNTIP
Psalms 86 in the TNTIZ
Psalms 86 in the TOMA
Psalms 86 in the TTENT
Psalms 86 in the UBG
Psalms 86 in the UGV
Psalms 86 in the UGV2
Psalms 86 in the UGV3
Psalms 86 in the VBL
Psalms 86 in the VDCC
Psalms 86 in the YALU
Psalms 86 in the YAPE
Psalms 86 in the YBVTP
Psalms 86 in the ZBP