Psalms 38 (BOGWICC)

undefined Salimo la Davide. Kupempha. 1 Yehova musandidzudzule mutapsa mtimakapena kundilanga muli ndi ukali. 2 Pakuti mivi yanu yandilasa,ndipo dzanja lanu latsika ndipo landifikira. 3 Chifukwa cha ukali wanu mulibe thanzi mʼthupi langa;mafupa anga alibe mphamvu chifukwa cha tchimo langa. 4 Kulakwa kwanga kwandipsinjangati katundu wolemera kwambiri kuposa mphamvu zanga. 5 Mabala anga akuwola ndipo akununkhachifukwa cha uchitsiru wa moyo wanga wauchimo. 6 Ine ndapindika msana ndipo ndawerama kwambiri;tsiku lonse ndimangolira. 7 Msana wanga wagwidwa ndi ululu wosasimbika,mulibe thanzi mʼthupi langa. 8 Ndilibe mphamvu ndipo ndakunthidwa kwathunthu;ndikubuwula ndi ululu wa mumtima. 9 Zokhumba zanga zonse zili poonekera pamaso panu Ambuye,kusisima kwanga sikunabisike kwa Inu. 10 Mtima wanga ukugunda, mphamvu zanga zikutha;ngakhale kuwala kwachoka mʼmaso mwanga. 11 Abwenzi anga ndi anzanga akundipewa chifukwa cha mabala anga;anansi anga akhala kutali nane. 12 Iwo amene akufunafuna moyo wanga atchera misampha yawo,oti andipwetekewo amayankhula za kuwonongeka kwanga;tsiku lonse amakonza zachinyengo. 13 Ine ndili ngati munthu wosamva amene sangamve,monga wosayankhula, amene sangathe kutsekula pakamwa pake; 14 Ndakhala ngati munthu amene samva,amene pakamwa pake sipangathe kuyankha. 15 Ndikudikira Inu Yehova;mudzayankha, Inu Ambuye Mulungu wanga. 16 Pakuti Ine ndinati, “Musawalole kuti akondwerekapena kudzikweza okha pa ine pamene phazi langa laterereka.” 17 Pakuti ndili pafupi kugwa,ndipo ndikumva kuwawa nthawi zonse. 18 Ndikuvomereza mphulupulu zanga;ndipo ndavutika ndi tchimo langa. 19 Ambiri ndi adani anga amphamvu;amene amandida popanda chifukwa alipo ochuluka kwambiri. 20 Iwo amene amandibwezera zoyipa mʼmalo mwa zabwinoamandinyoza pamene nditsatira zabwino. 21 Inu Yehova, musanditaye;musakhale kutali ndi ine Mulungu wanga. 22 Bwerani msanga kudzandithandiza,Inu Ambuye Mpulumutsi wanga.

In Other Versions

Psalms 38 in the ANGEFD

Psalms 38 in the ANTPNG2D

Psalms 38 in the AS21

Psalms 38 in the BAGH

Psalms 38 in the BBPNG

Psalms 38 in the BBT1E

Psalms 38 in the BDS

Psalms 38 in the BEV

Psalms 38 in the BHAD

Psalms 38 in the BIB

Psalms 38 in the BLPT

Psalms 38 in the BNT

Psalms 38 in the BNTABOOT

Psalms 38 in the BNTLV

Psalms 38 in the BOATCB

Psalms 38 in the BOATCB2

Psalms 38 in the BOBCV

Psalms 38 in the BOCNT

Psalms 38 in the BOECS

Psalms 38 in the BOHCB

Psalms 38 in the BOHCV

Psalms 38 in the BOHLNT

Psalms 38 in the BOHNTLTAL

Psalms 38 in the BOICB

Psalms 38 in the BOILNTAP

Psalms 38 in the BOITCV

Psalms 38 in the BOKCV

Psalms 38 in the BOKCV2

Psalms 38 in the BOKHWOG

Psalms 38 in the BOKSSV

Psalms 38 in the BOLCB

Psalms 38 in the BOLCB2

Psalms 38 in the BOMCV

Psalms 38 in the BONAV

Psalms 38 in the BONCB

Psalms 38 in the BONLT

Psalms 38 in the BONUT2

Psalms 38 in the BOPLNT

Psalms 38 in the BOSCB

Psalms 38 in the BOSNC

Psalms 38 in the BOTLNT

Psalms 38 in the BOVCB

Psalms 38 in the BOYCB

Psalms 38 in the BPBB

Psalms 38 in the BPH

Psalms 38 in the BSB

Psalms 38 in the CCB

Psalms 38 in the CUV

Psalms 38 in the CUVS

Psalms 38 in the DBT

Psalms 38 in the DGDNT

Psalms 38 in the DHNT

Psalms 38 in the DNT

Psalms 38 in the ELBE

Psalms 38 in the EMTV

Psalms 38 in the ESV

Psalms 38 in the FBV

Psalms 38 in the FEB

Psalms 38 in the GGMNT

Psalms 38 in the GNT

Psalms 38 in the HARY

Psalms 38 in the HNT

Psalms 38 in the IRVA

Psalms 38 in the IRVB

Psalms 38 in the IRVG

Psalms 38 in the IRVH

Psalms 38 in the IRVK

Psalms 38 in the IRVM

Psalms 38 in the IRVM2

Psalms 38 in the IRVO

Psalms 38 in the IRVP

Psalms 38 in the IRVT

Psalms 38 in the IRVT2

Psalms 38 in the IRVU

Psalms 38 in the ISVN

Psalms 38 in the JSNT

Psalms 38 in the KAPI

Psalms 38 in the KBT1ETNIK

Psalms 38 in the KBV

Psalms 38 in the KJV

Psalms 38 in the KNFD

Psalms 38 in the LBA

Psalms 38 in the LBLA

Psalms 38 in the LNT

Psalms 38 in the LSV

Psalms 38 in the MAAL

Psalms 38 in the MBV

Psalms 38 in the MBV2

Psalms 38 in the MHNT

Psalms 38 in the MKNFD

Psalms 38 in the MNG

Psalms 38 in the MNT

Psalms 38 in the MNT2

Psalms 38 in the MRS1T

Psalms 38 in the NAA

Psalms 38 in the NASB

Psalms 38 in the NBLA

Psalms 38 in the NBS

Psalms 38 in the NBVTP

Psalms 38 in the NET2

Psalms 38 in the NIV11

Psalms 38 in the NNT

Psalms 38 in the NNT2

Psalms 38 in the NNT3

Psalms 38 in the PDDPT

Psalms 38 in the PFNT

Psalms 38 in the RMNT

Psalms 38 in the SBIAS

Psalms 38 in the SBIBS

Psalms 38 in the SBIBS2

Psalms 38 in the SBICS

Psalms 38 in the SBIDS

Psalms 38 in the SBIGS

Psalms 38 in the SBIHS

Psalms 38 in the SBIIS

Psalms 38 in the SBIIS2

Psalms 38 in the SBIIS3

Psalms 38 in the SBIKS

Psalms 38 in the SBIKS2

Psalms 38 in the SBIMS

Psalms 38 in the SBIOS

Psalms 38 in the SBIPS

Psalms 38 in the SBISS

Psalms 38 in the SBITS

Psalms 38 in the SBITS2

Psalms 38 in the SBITS3

Psalms 38 in the SBITS4

Psalms 38 in the SBIUS

Psalms 38 in the SBIVS

Psalms 38 in the SBT

Psalms 38 in the SBT1E

Psalms 38 in the SCHL

Psalms 38 in the SNT

Psalms 38 in the SUSU

Psalms 38 in the SUSU2

Psalms 38 in the SYNO

Psalms 38 in the TBIAOTANT

Psalms 38 in the TBT1E

Psalms 38 in the TBT1E2

Psalms 38 in the TFTIP

Psalms 38 in the TFTU

Psalms 38 in the TGNTATF3T

Psalms 38 in the THAI

Psalms 38 in the TNFD

Psalms 38 in the TNT

Psalms 38 in the TNTIK

Psalms 38 in the TNTIL

Psalms 38 in the TNTIN

Psalms 38 in the TNTIP

Psalms 38 in the TNTIZ

Psalms 38 in the TOMA

Psalms 38 in the TTENT

Psalms 38 in the UBG

Psalms 38 in the UGV

Psalms 38 in the UGV2

Psalms 38 in the UGV3

Psalms 38 in the VBL

Psalms 38 in the VDCC

Psalms 38 in the YALU

Psalms 38 in the YAPE

Psalms 38 in the YBVTP

Psalms 38 in the ZBP