Psalms 77 (BOGWICC)

undefined Kwa mtsogoleri wa mayimbidwe. Potsata mayimbidwe a Yedutuni. Salimo la Asafu. 1 Ndinafuwulira Mulungu kupempha thandizo;ndinafuwula mokweza kwa Mulungu kuti anditcherere khutu. 2 Pamene ndinali pa masautso ndinafunafuna Ambuye;usiku ndinatambasula manja mosalekezandipo moyo wanga unakana kutonthozedwa. 3 Ndinakumbukira Inu Mulungu, ndipo ndinabuwula;ndinasinkhasinkha ndipo mzimu wanga unalefuka. Sela 4 Munagwira zikope zanga kuti ndisagonendipo ndinavutika kwambiri kuti ndiyankhule. 5 Ndinaganizira za masiku akale,zaka zamakedzana; 6 Ndinakumbukira nyimbo zanga usiku.Mtima wanga unasinkhasinkha ndipo mzimu wanga unafunsa kuti, 7 “Kodi Ambuye adzatikana mpaka muyaya?Kodi Iwo sadzaonetsanso kukoma mtima kwawo? 8 Kodi Chikondi chake chosatha chija chatheratu?Kodi malonjezo ake alephera nthawi yonse? 9 Kodi Mulungu wayiwala kukhala wokoma mtima?Kodi mu mkwiyo wake waleka chifundo chake?” 10 Ndipo ndinaganiza, “Pa izi ine ndidzapemphanso:zaka za dzanja lamanja la Wammwambamwamba. 11 Ine ndidzakumbukira ntchito za Yehova;Ine ndidzakumbukira zodabwitsa zanu za kalekale. 12 Ndidzakumbukira ntchito zanundi kulingalira zodabwitsa zanu.” 13 Njira zanu Mulungu ndi zoyera.Kodi ndi mulungu uti ali wamkulu kuposa Mulungu wathu? 14 Inu ndinu Mulungu wochita zodabwitsa;Mumaonetsera mphamvu yanu pakati pa mitundu ya anthu. 15 Ndi dzanja lanu lamphamvu munawombola anthu anu,zidzukulu za Yakobo ndi Yosefe. Sela 16 Madzi anakuonani Mulungu,madzi anakuonani ndipo anachita mantha;nyanja yozama inakomoka. 17 Mitambo inakhuthula madzi ake pansi,mu mlengalenga munamveka mabingu;mivi yanu inawuluka uku ndi uku. 18 Bingu lanu linamveka mʼmphepo ya kamvuluvulu,mphenzi yanu inawalitsa dziko lonse;dziko lapansi linanjenjemera ndi kugwedezeka. 19 Njira yanu inadutsa pa nyanja,njira yanu inadutsa pa madzi amphamvu,ngakhale zidindo za mapazi anu sizinaoneke. 20 Inu munatsogolera anthu anu ngati gulu la nkhosamwa dzanja la Mose ndi Aaroni.

In Other Versions

Psalms 77 in the ANGEFD

Psalms 77 in the ANTPNG2D

Psalms 77 in the AS21

Psalms 77 in the BAGH

Psalms 77 in the BBPNG

Psalms 77 in the BBT1E

Psalms 77 in the BDS

Psalms 77 in the BEV

Psalms 77 in the BHAD

Psalms 77 in the BIB

Psalms 77 in the BLPT

Psalms 77 in the BNT

Psalms 77 in the BNTABOOT

Psalms 77 in the BNTLV

Psalms 77 in the BOATCB

Psalms 77 in the BOATCB2

Psalms 77 in the BOBCV

Psalms 77 in the BOCNT

Psalms 77 in the BOECS

Psalms 77 in the BOHCB

Psalms 77 in the BOHCV

Psalms 77 in the BOHLNT

Psalms 77 in the BOHNTLTAL

Psalms 77 in the BOICB

Psalms 77 in the BOILNTAP

Psalms 77 in the BOITCV

Psalms 77 in the BOKCV

Psalms 77 in the BOKCV2

Psalms 77 in the BOKHWOG

Psalms 77 in the BOKSSV

Psalms 77 in the BOLCB

Psalms 77 in the BOLCB2

Psalms 77 in the BOMCV

Psalms 77 in the BONAV

Psalms 77 in the BONCB

Psalms 77 in the BONLT

Psalms 77 in the BONUT2

Psalms 77 in the BOPLNT

Psalms 77 in the BOSCB

Psalms 77 in the BOSNC

Psalms 77 in the BOTLNT

Psalms 77 in the BOVCB

Psalms 77 in the BOYCB

Psalms 77 in the BPBB

Psalms 77 in the BPH

Psalms 77 in the BSB

Psalms 77 in the CCB

Psalms 77 in the CUV

Psalms 77 in the CUVS

Psalms 77 in the DBT

Psalms 77 in the DGDNT

Psalms 77 in the DHNT

Psalms 77 in the DNT

Psalms 77 in the ELBE

Psalms 77 in the EMTV

Psalms 77 in the ESV

Psalms 77 in the FBV

Psalms 77 in the FEB

Psalms 77 in the GGMNT

Psalms 77 in the GNT

Psalms 77 in the HARY

Psalms 77 in the HNT

Psalms 77 in the IRVA

Psalms 77 in the IRVB

Psalms 77 in the IRVG

Psalms 77 in the IRVH

Psalms 77 in the IRVK

Psalms 77 in the IRVM

Psalms 77 in the IRVM2

Psalms 77 in the IRVO

Psalms 77 in the IRVP

Psalms 77 in the IRVT

Psalms 77 in the IRVT2

Psalms 77 in the IRVU

Psalms 77 in the ISVN

Psalms 77 in the JSNT

Psalms 77 in the KAPI

Psalms 77 in the KBT1ETNIK

Psalms 77 in the KBV

Psalms 77 in the KJV

Psalms 77 in the KNFD

Psalms 77 in the LBA

Psalms 77 in the LBLA

Psalms 77 in the LNT

Psalms 77 in the LSV

Psalms 77 in the MAAL

Psalms 77 in the MBV

Psalms 77 in the MBV2

Psalms 77 in the MHNT

Psalms 77 in the MKNFD

Psalms 77 in the MNG

Psalms 77 in the MNT

Psalms 77 in the MNT2

Psalms 77 in the MRS1T

Psalms 77 in the NAA

Psalms 77 in the NASB

Psalms 77 in the NBLA

Psalms 77 in the NBS

Psalms 77 in the NBVTP

Psalms 77 in the NET2

Psalms 77 in the NIV11

Psalms 77 in the NNT

Psalms 77 in the NNT2

Psalms 77 in the NNT3

Psalms 77 in the PDDPT

Psalms 77 in the PFNT

Psalms 77 in the RMNT

Psalms 77 in the SBIAS

Psalms 77 in the SBIBS

Psalms 77 in the SBIBS2

Psalms 77 in the SBICS

Psalms 77 in the SBIDS

Psalms 77 in the SBIGS

Psalms 77 in the SBIHS

Psalms 77 in the SBIIS

Psalms 77 in the SBIIS2

Psalms 77 in the SBIIS3

Psalms 77 in the SBIKS

Psalms 77 in the SBIKS2

Psalms 77 in the SBIMS

Psalms 77 in the SBIOS

Psalms 77 in the SBIPS

Psalms 77 in the SBISS

Psalms 77 in the SBITS

Psalms 77 in the SBITS2

Psalms 77 in the SBITS3

Psalms 77 in the SBITS4

Psalms 77 in the SBIUS

Psalms 77 in the SBIVS

Psalms 77 in the SBT

Psalms 77 in the SBT1E

Psalms 77 in the SCHL

Psalms 77 in the SNT

Psalms 77 in the SUSU

Psalms 77 in the SUSU2

Psalms 77 in the SYNO

Psalms 77 in the TBIAOTANT

Psalms 77 in the TBT1E

Psalms 77 in the TBT1E2

Psalms 77 in the TFTIP

Psalms 77 in the TFTU

Psalms 77 in the TGNTATF3T

Psalms 77 in the THAI

Psalms 77 in the TNFD

Psalms 77 in the TNT

Psalms 77 in the TNTIK

Psalms 77 in the TNTIL

Psalms 77 in the TNTIN

Psalms 77 in the TNTIP

Psalms 77 in the TNTIZ

Psalms 77 in the TOMA

Psalms 77 in the TTENT

Psalms 77 in the UBG

Psalms 77 in the UGV

Psalms 77 in the UGV2

Psalms 77 in the UGV3

Psalms 77 in the VBL

Psalms 77 in the VDCC

Psalms 77 in the YALU

Psalms 77 in the YAPE

Psalms 77 in the YBVTP

Psalms 77 in the ZBP