1 Chronicles 1 (BOGWICC)

1 Adamu, Seti, Enosi 2 Kenani, Mahalaleli, Yaredi, 3 Enoki, Metusela, Lameki, Nowa. 4 Ana a Nowa,Semu, Hamu ndi Yafeti. 5 Ana aamuna a Yafeti anali:Gomeri, Magogi, Madai, Yavani, Tubala, Mesaki ndi Tirasi. 6 Ana aamuna a Gomeri anali:Asikenazi, Rifati ndi Togarima 7 Ana aamuna a Yavani anali:Elisa, Tarisisi, Kitimu ndi Rodanimu. 8 Ana aamuna a Hamu anali:Kusi, Miziraimu, Puti ndi Kanaani 9 Ana aamuna a Kusi anali:Seba, Havila, Sabita, Raama ndi SabitekaAna aamuna a Raama anali:Seba ndi Dedani. 10 Kusi anali abambo a Nimurodi amene anali wankhondo wamphamvukwambiri pa dziko lapansi. 11 Igupto ndiye kholo laAludi, Aanami, Alehabu, Anafutu, 12 Apaturusi, Akasilu (kumene kunachokera Afilisti) ndi Akafitori. 13 Kanaani anabereka mwana wake wachisamba Sidoni,ndipo anaberekanso Ahiti, 14 Ayebusi, Aamori, Agirigasi 15 Ahivi, Aariki, Asini 16 Aaravadi, Azemari ndi Ahamati. 17 Ana aamuna a Semu anali:Elamu, Asuri, Aripakisadi, Ludi ndi Aramu.Ana aamuna a Aramu anali:Uzi, Huri, Geteri ndi Mesaki. 18 Aripakisadi anabereka Selandipo Selayo anabereka Eberi: 19 Eberi anabereka ana aamuna awiri:wina anamutcha Pelegi, chifukwa pa nthawiyo anthu a pa dziko lapansi anagawikana. Dzina la mʼbale wake linali Yokitani. 20 Yokitani anaberekaAlimodadi, Selefi, Hazari-Maveti, Yera, 21 Hadoramu, Uzali, Dikila 22 Obali, Abimaeli, Seba, 23 Ofiri, Havila ndi Yobabu. Onsewa anali ana aamuna a Yokitani. 24 Semu, Aripakisadi, Sela 25 Eberi, Pelegi, Reu 26 Serugi, Nahori, Tera 27 ndi Abramu (amene ndi Abrahamu). 28 Ana a Abrahamu ndi awa:Isake ndi Ismaeli. 29 Zidzukulu zake zinali izi:Nebayoti ndiye anali mwana woyamba wa Ismaeli, kenaka Kedara, Adibeeli, Mibisamu, 30 Misima, Duma, Masa, Hadadi, Tema, 31 Yeturi, Nafisi ndi Kedema. Awa anali ana a Ismaeli. 32 Ana a Ketura mzikazi wa Abrahamu anali awa:Zimurani, Yokisani, Medani, Midiyani, Isibaki ndi Suwa.Ana a Yokisani ndi awa:Seba ndi Dedani 33 Ana aamuna a Midiyani anali,Efai, Eferi, Hanoki, Abida ndi Elida.Onsewa anali zidzukulu za Ketura. 34 Abrahamu anabereka Isake.Ana a Isake anali awa:Esau ndi Israeli. 35 Ana aamuna a Esau anali awa:Elifazi, Reueli, Yeusi, Yolamu ndi Kora. 36 Ana a Elifazi anali awa:Temani, Omari, Zefo, Gatamu ndi Kenazi:Amene anabereka ndi Timna: Amaleki. 37 Ana a Reueli anali awa:Nahati, Zera, Sama ndi Miza. 38 Ana a Seiri anali awa:Lotani, Sobala, Zibeoni, Ana, Disoni, Ezeri ndi Disani. 39 Ana aamuna a Lotani anali awa:Hori ndi Homamu. Timna anali mlongo wake wa Lotani. 40 Ana aamuna a Sobala anali awa:Alivani, Manahati, Ebala, Sefo ndi Onamu.Ana aamuna a Zibeoni anali awa:Ayiwa ndi Ana. 41 Mwana wa Ana analiDisoni.Ana a Disoni anali awa:Hemudani, Esibani, Itirani ndi Kerani 42 Ana aamuna a Ezeri anali awa:Bilihani, Zaavani ndi Yaakani.Ana aamuna a Disani anali awa:Uzi ndi Arani. 43 Awa ndi mafumu amene ankalamulira dziko la Edomu, mfumu iliyonse ya Israeli isanayambe kulamulira kumeneko:Bela mwana wa Beori, mzinda wake ankawutcha Dinihaba. 44 Bela atamwalira, Yobabu mwana wa Zera wochokera ku Bozira analowa ufumu mʼmalo mwake. 45 Yobabu atamwalira, Husamu wochokera ku dziko la Atemani, analowa ufumu mʼmalo mwake. 46 Husamu atamwalira, Hadadi mwana wa Bedadi, amene anagonjetsa Amidiyani mʼdziko la Mowabu, analowa ufumu mʼmalo mwake. Mzinda wake unkatchedwa Aviti. 47 Hadadi atamwalira, Samila wochokera ku Masireka analowa ufumu mʼmalo mwake. 48 Samila atamwalira, Sauli wochokera ku Rehoboti wa ku Mtsinje analowa ufumu mʼmalo mwake. 49 Sauli atamwalira, Baala-Hanani mwana wa Akibori analowa ufumu mʼmalo mwake. 50 Pamene Baala-Hanani anamwalira, Hadadi analowa ufumu mʼmalo mwake. Mzinda wake unkatchedwa Pau, ndipo dzina la mkazi wake linali Mehatabeli mwana wa Matiredi, mwana wamkazi wa Me-Zahabu. 51 Hadadi anamwaliranso. Mafumu a ku Edomu anali:Timna, Aliva, Yeteti, 52 Oholibama, Ela, Pinoni, 53 Kenazi, Temani, Mibezari, 54 Magidieli ndi Iramu. Awa anali mafumu a ku Edomu.

In Other Versions

1 Chronicles 1 in the ANGEFD

1 Chronicles 1 in the ANTPNG2D

1 Chronicles 1 in the AS21

1 Chronicles 1 in the BAGH

1 Chronicles 1 in the BBPNG

1 Chronicles 1 in the BBT1E

1 Chronicles 1 in the BDS

1 Chronicles 1 in the BEV

1 Chronicles 1 in the BHAD

1 Chronicles 1 in the BIB

1 Chronicles 1 in the BLPT

1 Chronicles 1 in the BNT

1 Chronicles 1 in the BNTABOOT

1 Chronicles 1 in the BNTLV

1 Chronicles 1 in the BOATCB

1 Chronicles 1 in the BOATCB2

1 Chronicles 1 in the BOBCV

1 Chronicles 1 in the BOCNT

1 Chronicles 1 in the BOECS

1 Chronicles 1 in the BOHCB

1 Chronicles 1 in the BOHCV

1 Chronicles 1 in the BOHLNT

1 Chronicles 1 in the BOHNTLTAL

1 Chronicles 1 in the BOICB

1 Chronicles 1 in the BOILNTAP

1 Chronicles 1 in the BOITCV

1 Chronicles 1 in the BOKCV

1 Chronicles 1 in the BOKCV2

1 Chronicles 1 in the BOKHWOG

1 Chronicles 1 in the BOKSSV

1 Chronicles 1 in the BOLCB

1 Chronicles 1 in the BOLCB2

1 Chronicles 1 in the BOMCV

1 Chronicles 1 in the BONAV

1 Chronicles 1 in the BONCB

1 Chronicles 1 in the BONLT

1 Chronicles 1 in the BONUT2

1 Chronicles 1 in the BOPLNT

1 Chronicles 1 in the BOSCB

1 Chronicles 1 in the BOSNC

1 Chronicles 1 in the BOTLNT

1 Chronicles 1 in the BOVCB

1 Chronicles 1 in the BOYCB

1 Chronicles 1 in the BPBB

1 Chronicles 1 in the BPH

1 Chronicles 1 in the BSB

1 Chronicles 1 in the CCB

1 Chronicles 1 in the CUV

1 Chronicles 1 in the CUVS

1 Chronicles 1 in the DBT

1 Chronicles 1 in the DGDNT

1 Chronicles 1 in the DHNT

1 Chronicles 1 in the DNT

1 Chronicles 1 in the ELBE

1 Chronicles 1 in the EMTV

1 Chronicles 1 in the ESV

1 Chronicles 1 in the FBV

1 Chronicles 1 in the FEB

1 Chronicles 1 in the GGMNT

1 Chronicles 1 in the GNT

1 Chronicles 1 in the HARY

1 Chronicles 1 in the HNT

1 Chronicles 1 in the IRVA

1 Chronicles 1 in the IRVB

1 Chronicles 1 in the IRVG

1 Chronicles 1 in the IRVH

1 Chronicles 1 in the IRVK

1 Chronicles 1 in the IRVM

1 Chronicles 1 in the IRVM2

1 Chronicles 1 in the IRVO

1 Chronicles 1 in the IRVP

1 Chronicles 1 in the IRVT

1 Chronicles 1 in the IRVT2

1 Chronicles 1 in the IRVU

1 Chronicles 1 in the ISVN

1 Chronicles 1 in the JSNT

1 Chronicles 1 in the KAPI

1 Chronicles 1 in the KBT1ETNIK

1 Chronicles 1 in the KBV

1 Chronicles 1 in the KJV

1 Chronicles 1 in the KNFD

1 Chronicles 1 in the LBA

1 Chronicles 1 in the LBLA

1 Chronicles 1 in the LNT

1 Chronicles 1 in the LSV

1 Chronicles 1 in the MAAL

1 Chronicles 1 in the MBV

1 Chronicles 1 in the MBV2

1 Chronicles 1 in the MHNT

1 Chronicles 1 in the MKNFD

1 Chronicles 1 in the MNG

1 Chronicles 1 in the MNT

1 Chronicles 1 in the MNT2

1 Chronicles 1 in the MRS1T

1 Chronicles 1 in the NAA

1 Chronicles 1 in the NASB

1 Chronicles 1 in the NBLA

1 Chronicles 1 in the NBS

1 Chronicles 1 in the NBVTP

1 Chronicles 1 in the NET2

1 Chronicles 1 in the NIV11

1 Chronicles 1 in the NNT

1 Chronicles 1 in the NNT2

1 Chronicles 1 in the NNT3

1 Chronicles 1 in the PDDPT

1 Chronicles 1 in the PFNT

1 Chronicles 1 in the RMNT

1 Chronicles 1 in the SBIAS

1 Chronicles 1 in the SBIBS

1 Chronicles 1 in the SBIBS2

1 Chronicles 1 in the SBICS

1 Chronicles 1 in the SBIDS

1 Chronicles 1 in the SBIGS

1 Chronicles 1 in the SBIHS

1 Chronicles 1 in the SBIIS

1 Chronicles 1 in the SBIIS2

1 Chronicles 1 in the SBIIS3

1 Chronicles 1 in the SBIKS

1 Chronicles 1 in the SBIKS2

1 Chronicles 1 in the SBIMS

1 Chronicles 1 in the SBIOS

1 Chronicles 1 in the SBIPS

1 Chronicles 1 in the SBISS

1 Chronicles 1 in the SBITS

1 Chronicles 1 in the SBITS2

1 Chronicles 1 in the SBITS3

1 Chronicles 1 in the SBITS4

1 Chronicles 1 in the SBIUS

1 Chronicles 1 in the SBIVS

1 Chronicles 1 in the SBT

1 Chronicles 1 in the SBT1E

1 Chronicles 1 in the SCHL

1 Chronicles 1 in the SNT

1 Chronicles 1 in the SUSU

1 Chronicles 1 in the SUSU2

1 Chronicles 1 in the SYNO

1 Chronicles 1 in the TBIAOTANT

1 Chronicles 1 in the TBT1E

1 Chronicles 1 in the TBT1E2

1 Chronicles 1 in the TFTIP

1 Chronicles 1 in the TFTU

1 Chronicles 1 in the TGNTATF3T

1 Chronicles 1 in the THAI

1 Chronicles 1 in the TNFD

1 Chronicles 1 in the TNT

1 Chronicles 1 in the TNTIK

1 Chronicles 1 in the TNTIL

1 Chronicles 1 in the TNTIN

1 Chronicles 1 in the TNTIP

1 Chronicles 1 in the TNTIZ

1 Chronicles 1 in the TOMA

1 Chronicles 1 in the TTENT

1 Chronicles 1 in the UBG

1 Chronicles 1 in the UGV

1 Chronicles 1 in the UGV2

1 Chronicles 1 in the UGV3

1 Chronicles 1 in the VBL

1 Chronicles 1 in the VDCC

1 Chronicles 1 in the YALU

1 Chronicles 1 in the YAPE

1 Chronicles 1 in the YBVTP

1 Chronicles 1 in the ZBP