1 Chronicles 7 (BOGWICC)

1 Ana a Isakara anali awa:Tola, Puwa, Yasubu ndi Simironi ndipo onse analipo anayi. 2 Ana a Tola ndi awa:Uzi, Refaya, Yerieli, Yahimai, Ibisamu ndi Samueli. Awa anali atsogoleri a mabanja awo. Pa nthawi ya ulamuliro wa Davide zidzukulu za Tola zomwe zinali anthu odziwa kumenya nkhondo zinalipo 22,600. 3 Mwana wa Uzi analiIzirahiya.Ana a Izirahiya anali:Mikayeli, Obadiya, Yoweli ndi Isiya. Onse asanu anali atsogoleri a mabanja. 4 Monga mwa chiwerengero cha mabanja awo, panali anthu 36,000 odziwa kumenya nkhondo, pakuti iwo anali ndi akazi ndi ana ambiri. 5 Abale awo onse a mʼbanja la Isakara amene anali odziwa kumenya nkhondo analipo 87,000, olembedwa potsata mibado yawo. 6 Ana atatu a Benjamini anali awa:Bela, Bekeri ndi Yediaeli. 7 Ana a Bela anali awa:Eziboni, Uzi, Uzieli, Yerimoti ndi Iri. Iwowa anali atsogoleri a mabanja awo ndipo onse pamodzi analipo asanu. Pa mndandanda wa mʼbado wawo panali anthu 22,034 odziwa kumenya nkhondo. 8 Ana a Bekeri anali awa:Zemira, Yowasi, Eliezara, Eliyoenai, Omiri, Yeremoti, Abiya, Anatoti ndi Alemeti. Onsewa anali ana a Bekeri. 9 Pa mndandanda wa mʼbado wawo panali atsogoleri a mabanja ndi anthu 20,200 odziwa kumenya nkhondo. 10 Mwana wa Yediaeli analiBilihani.Ana a Bilihani anali awa:Yeusi, Benjamini, Ehudi, Kenaana, Zetani, Tarisisi ndi Ahisahara. 11 Ana onsewa a Yediaeli anali atsogoleri a mabanja. Analipo anthu 17,200 amene anali okonzeka kupita ku nkhondo. 12 Asupi ndi Ahupi anali zidzukulu za Iri, ndipo Ahusimu anali zidzukulu za Aheri. 13 Ana a Nafutali anali awa:Yahazieli, Guni, Yezeri ndi Salumu, zidzukulu za Biliha. 14 Ana a Manase anali awa:Asirieli ndi mwana amene anabereka kwa mzikazi wake wa ku Aramu. Mzikazi yemweyo anaberekanso Makiri abambo ake a Giliyadi. 15 Makiri anatenga mkazi wa banja la Ahupi ndi Asupi. Mlongo wake anali Maaka.Mwana wake wina anali Zelofehadi, amene anabereka ana aakazi okhaokha. 16 Maaka mkazi wa Makiri anabereka mwana wamwamuna ndipo anamutcha Perezi. Mʼbale wake anamutcha Seresi, ndipo ana ake anali Ulamu ndi Rakemu. 17 Mwana wa Ulamu analiBedani.Awa anali ana a Giliyadi mwana wa Makiri, mwana wa Manase. 18 Mlongo wake Hamoleketi anabereka Isihodi, Abiezeri ndi Mahila. 19 Ana a Semida anali:Ahiyani, Sekemu, Likihi ndi Aniyamu. 20 Ana a Efereimu anali awa:Sutela, Beredi,Tahati, Eliada,Tahati, 21 Zabadi,Sutela.Ezeri ndi Eladi anaphedwa ndi anthu a ku Gati, pamene anabwera kudzalanda zoweta zawo. 22 Efereimu, abambo awo, anawalira masiku ambiri, ndipo abale ake anabwera kudzamutonthoza. 23 Kenaka anagona ndi mkazi wake, ndipo anakhala woyembekezera nabala mwana wamwamuna. Anamutcha dzina lake Beriya, chifukwa tsoka linagwera banja lake. 24 Mwana wake wamkazi anali Seera, amene anamanga mzinda wa Beti-Horoni Wakumunsi, Wakumtunda kudzanso Uzeni-Seera. 25 Mwana wina wa Efereimu anali Refa amene zidzukulu zake zinali Resefu,Tela, Tahani, 26 Ladani, Amihudi,Elisama, 27 Nunindi Yoswa. 28 Malo amene ankakhala anali Beteli ndi midzi yozungulira, cha kummawa kunali Naarani, Gezeri ndi midzi yake ya kumadzulo ndi Sekemu ndi midzi yake mpaka ku Aya ndi midzi yake. 29 Mʼmbali mwa malire a Manase munali Beti-Seani, Taanaki, Megido ndi Dori, pamodzi ndi midzi yake. Zidzukulu za Yosefe mwana wa Israeli zimakhala mʼmizinda imeneyi. 30 Ana a Aseri anali awa:Imuna, Isiva, Isivi ndi Beriya. Mlongo wawo anali Sera. 31 Ana a Beriya anali awa:Heberi ndi Malikieli amene anabereka Birizaiti. 32 Heberi anabereka Yafuleti, Someri, Hotamu ndi Suwa, mlongo wawo. 33 Ana a Yafuleti anali awa:Pasaki, Bimuhali ndi Asivati.Awa anali ana a Yafuleti. 34 Ana a Someri anali awa:Ahi, Rohiga, Yehuba ndi Aramu. 35 Ana a mʼbale wake Helemu anali awa:Zofa, Imuna, Selesi ndi Amali. 36 Ana a Zofa anali awa:Suwa, Harineferi, Suwali, Beri, Imula, 37 Bezeri, Hodi, Sama, Silisa, Itirani ndi Bera. 38 Ana a Yeteri anali awa:Yefune, Pisipa ndi Ara. 39 Ana a Ula anali awa:Ara, Hanieli ndi Riziya. 40 Onsewa anali zidzukulu za Aseri, atsogoleri a mabanja, anthu omveka, ankhondo olimba mtima, ndi akuluakulu pakati pa atsogoleri anzawo. Chiwerengero cha anthu odziwa kumenya nkhondo chomwe chinalembedwa chinali 26,000.

In Other Versions

1 Chronicles 7 in the ANGEFD

1 Chronicles 7 in the ANTPNG2D

1 Chronicles 7 in the AS21

1 Chronicles 7 in the BAGH

1 Chronicles 7 in the BBPNG

1 Chronicles 7 in the BBT1E

1 Chronicles 7 in the BDS

1 Chronicles 7 in the BEV

1 Chronicles 7 in the BHAD

1 Chronicles 7 in the BIB

1 Chronicles 7 in the BLPT

1 Chronicles 7 in the BNT

1 Chronicles 7 in the BNTABOOT

1 Chronicles 7 in the BNTLV

1 Chronicles 7 in the BOATCB

1 Chronicles 7 in the BOATCB2

1 Chronicles 7 in the BOBCV

1 Chronicles 7 in the BOCNT

1 Chronicles 7 in the BOECS

1 Chronicles 7 in the BOHCB

1 Chronicles 7 in the BOHCV

1 Chronicles 7 in the BOHLNT

1 Chronicles 7 in the BOHNTLTAL

1 Chronicles 7 in the BOICB

1 Chronicles 7 in the BOILNTAP

1 Chronicles 7 in the BOITCV

1 Chronicles 7 in the BOKCV

1 Chronicles 7 in the BOKCV2

1 Chronicles 7 in the BOKHWOG

1 Chronicles 7 in the BOKSSV

1 Chronicles 7 in the BOLCB

1 Chronicles 7 in the BOLCB2

1 Chronicles 7 in the BOMCV

1 Chronicles 7 in the BONAV

1 Chronicles 7 in the BONCB

1 Chronicles 7 in the BONLT

1 Chronicles 7 in the BONUT2

1 Chronicles 7 in the BOPLNT

1 Chronicles 7 in the BOSCB

1 Chronicles 7 in the BOSNC

1 Chronicles 7 in the BOTLNT

1 Chronicles 7 in the BOVCB

1 Chronicles 7 in the BOYCB

1 Chronicles 7 in the BPBB

1 Chronicles 7 in the BPH

1 Chronicles 7 in the BSB

1 Chronicles 7 in the CCB

1 Chronicles 7 in the CUV

1 Chronicles 7 in the CUVS

1 Chronicles 7 in the DBT

1 Chronicles 7 in the DGDNT

1 Chronicles 7 in the DHNT

1 Chronicles 7 in the DNT

1 Chronicles 7 in the ELBE

1 Chronicles 7 in the EMTV

1 Chronicles 7 in the ESV

1 Chronicles 7 in the FBV

1 Chronicles 7 in the FEB

1 Chronicles 7 in the GGMNT

1 Chronicles 7 in the GNT

1 Chronicles 7 in the HARY

1 Chronicles 7 in the HNT

1 Chronicles 7 in the IRVA

1 Chronicles 7 in the IRVB

1 Chronicles 7 in the IRVG

1 Chronicles 7 in the IRVH

1 Chronicles 7 in the IRVK

1 Chronicles 7 in the IRVM

1 Chronicles 7 in the IRVM2

1 Chronicles 7 in the IRVO

1 Chronicles 7 in the IRVP

1 Chronicles 7 in the IRVT

1 Chronicles 7 in the IRVT2

1 Chronicles 7 in the IRVU

1 Chronicles 7 in the ISVN

1 Chronicles 7 in the JSNT

1 Chronicles 7 in the KAPI

1 Chronicles 7 in the KBT1ETNIK

1 Chronicles 7 in the KBV

1 Chronicles 7 in the KJV

1 Chronicles 7 in the KNFD

1 Chronicles 7 in the LBA

1 Chronicles 7 in the LBLA

1 Chronicles 7 in the LNT

1 Chronicles 7 in the LSV

1 Chronicles 7 in the MAAL

1 Chronicles 7 in the MBV

1 Chronicles 7 in the MBV2

1 Chronicles 7 in the MHNT

1 Chronicles 7 in the MKNFD

1 Chronicles 7 in the MNG

1 Chronicles 7 in the MNT

1 Chronicles 7 in the MNT2

1 Chronicles 7 in the MRS1T

1 Chronicles 7 in the NAA

1 Chronicles 7 in the NASB

1 Chronicles 7 in the NBLA

1 Chronicles 7 in the NBS

1 Chronicles 7 in the NBVTP

1 Chronicles 7 in the NET2

1 Chronicles 7 in the NIV11

1 Chronicles 7 in the NNT

1 Chronicles 7 in the NNT2

1 Chronicles 7 in the NNT3

1 Chronicles 7 in the PDDPT

1 Chronicles 7 in the PFNT

1 Chronicles 7 in the RMNT

1 Chronicles 7 in the SBIAS

1 Chronicles 7 in the SBIBS

1 Chronicles 7 in the SBIBS2

1 Chronicles 7 in the SBICS

1 Chronicles 7 in the SBIDS

1 Chronicles 7 in the SBIGS

1 Chronicles 7 in the SBIHS

1 Chronicles 7 in the SBIIS

1 Chronicles 7 in the SBIIS2

1 Chronicles 7 in the SBIIS3

1 Chronicles 7 in the SBIKS

1 Chronicles 7 in the SBIKS2

1 Chronicles 7 in the SBIMS

1 Chronicles 7 in the SBIOS

1 Chronicles 7 in the SBIPS

1 Chronicles 7 in the SBISS

1 Chronicles 7 in the SBITS

1 Chronicles 7 in the SBITS2

1 Chronicles 7 in the SBITS3

1 Chronicles 7 in the SBITS4

1 Chronicles 7 in the SBIUS

1 Chronicles 7 in the SBIVS

1 Chronicles 7 in the SBT

1 Chronicles 7 in the SBT1E

1 Chronicles 7 in the SCHL

1 Chronicles 7 in the SNT

1 Chronicles 7 in the SUSU

1 Chronicles 7 in the SUSU2

1 Chronicles 7 in the SYNO

1 Chronicles 7 in the TBIAOTANT

1 Chronicles 7 in the TBT1E

1 Chronicles 7 in the TBT1E2

1 Chronicles 7 in the TFTIP

1 Chronicles 7 in the TFTU

1 Chronicles 7 in the TGNTATF3T

1 Chronicles 7 in the THAI

1 Chronicles 7 in the TNFD

1 Chronicles 7 in the TNT

1 Chronicles 7 in the TNTIK

1 Chronicles 7 in the TNTIL

1 Chronicles 7 in the TNTIN

1 Chronicles 7 in the TNTIP

1 Chronicles 7 in the TNTIZ

1 Chronicles 7 in the TOMA

1 Chronicles 7 in the TTENT

1 Chronicles 7 in the UBG

1 Chronicles 7 in the UGV

1 Chronicles 7 in the UGV2

1 Chronicles 7 in the UGV3

1 Chronicles 7 in the VBL

1 Chronicles 7 in the VDCC

1 Chronicles 7 in the YALU

1 Chronicles 7 in the YAPE

1 Chronicles 7 in the YBVTP

1 Chronicles 7 in the ZBP