2 Chronicles 27 (BOGWICC)

1 Yotamu anakhala mfumu ali ndi zaka 25 ndipo analamulira mu Yerusalemu kwa zaka 16. Dzina la amayi ake linali Yerusa mwana wa Zadoki. 2 Iye anachita zolungama pamaso pa Yehova, monga anachitira Uziya abambo ake, kupatula kuti iyeyo sanalowe mʼNyumba ya Yehova. Komabe anthu anapitirira kuchita zoyipa. 3 Yotamu anamanganso chipata chakumtunda cha Nyumba ya Yehova ndipo anagwira ntchito yayikulu yomanga khoma la ku phiri la Ofeli. 4 Iye anamanga mizinda mʼmapiri a ku Yuda ndipo anamanganso malinga ndi nsanja mʼmadera a ku nkhalango. 5 Yotamu anachita nkhondo ndi mfumu ya Aamoni ndipo anawagonjetsa. Chaka chimenecho Aamoni anapereka makilogalamu 3,400, matani 1,000 a tirigu ndiponso matani 1,000 a barele. Aamoni anabweretsa zinthu zomwezi chaka chachiwiri ndi chachitatu. 6 Yotamu anakula mphamvu chifukwa anayenda molungama pamaso pa Yehova Mulungu wake. 7 Zina ndi zina zokhudza ulamuliro wa Yotamu, kuphatikizapo nkhondo zake zonse ndi zinthu zina zimene anachita, zinalembedwa mʼbuku la mafumu a Israeli ndi Yuda. 8 Iye anakhala mfumu ali ndi zaka 25 ndipo analamulira mu Yerusalemu kwa zaka 16. 9 Yotamu anamwalira ndipo anayikidwa mʼmanda mu Mzinda wa Davide. Ndipo Ahazi mwana wake analowa ufumu mʼmalo mwake.

In Other Versions

2 Chronicles 27 in the ANGEFD

2 Chronicles 27 in the ANTPNG2D

2 Chronicles 27 in the AS21

2 Chronicles 27 in the BAGH

2 Chronicles 27 in the BBPNG

2 Chronicles 27 in the BBT1E

2 Chronicles 27 in the BDS

2 Chronicles 27 in the BEV

2 Chronicles 27 in the BHAD

2 Chronicles 27 in the BIB

2 Chronicles 27 in the BLPT

2 Chronicles 27 in the BNT

2 Chronicles 27 in the BNTABOOT

2 Chronicles 27 in the BNTLV

2 Chronicles 27 in the BOATCB

2 Chronicles 27 in the BOATCB2

2 Chronicles 27 in the BOBCV

2 Chronicles 27 in the BOCNT

2 Chronicles 27 in the BOECS

2 Chronicles 27 in the BOHCB

2 Chronicles 27 in the BOHCV

2 Chronicles 27 in the BOHLNT

2 Chronicles 27 in the BOHNTLTAL

2 Chronicles 27 in the BOICB

2 Chronicles 27 in the BOILNTAP

2 Chronicles 27 in the BOITCV

2 Chronicles 27 in the BOKCV

2 Chronicles 27 in the BOKCV2

2 Chronicles 27 in the BOKHWOG

2 Chronicles 27 in the BOKSSV

2 Chronicles 27 in the BOLCB

2 Chronicles 27 in the BOLCB2

2 Chronicles 27 in the BOMCV

2 Chronicles 27 in the BONAV

2 Chronicles 27 in the BONCB

2 Chronicles 27 in the BONLT

2 Chronicles 27 in the BONUT2

2 Chronicles 27 in the BOPLNT

2 Chronicles 27 in the BOSCB

2 Chronicles 27 in the BOSNC

2 Chronicles 27 in the BOTLNT

2 Chronicles 27 in the BOVCB

2 Chronicles 27 in the BOYCB

2 Chronicles 27 in the BPBB

2 Chronicles 27 in the BPH

2 Chronicles 27 in the BSB

2 Chronicles 27 in the CCB

2 Chronicles 27 in the CUV

2 Chronicles 27 in the CUVS

2 Chronicles 27 in the DBT

2 Chronicles 27 in the DGDNT

2 Chronicles 27 in the DHNT

2 Chronicles 27 in the DNT

2 Chronicles 27 in the ELBE

2 Chronicles 27 in the EMTV

2 Chronicles 27 in the ESV

2 Chronicles 27 in the FBV

2 Chronicles 27 in the FEB

2 Chronicles 27 in the GGMNT

2 Chronicles 27 in the GNT

2 Chronicles 27 in the HARY

2 Chronicles 27 in the HNT

2 Chronicles 27 in the IRVA

2 Chronicles 27 in the IRVB

2 Chronicles 27 in the IRVG

2 Chronicles 27 in the IRVH

2 Chronicles 27 in the IRVK

2 Chronicles 27 in the IRVM

2 Chronicles 27 in the IRVM2

2 Chronicles 27 in the IRVO

2 Chronicles 27 in the IRVP

2 Chronicles 27 in the IRVT

2 Chronicles 27 in the IRVT2

2 Chronicles 27 in the IRVU

2 Chronicles 27 in the ISVN

2 Chronicles 27 in the JSNT

2 Chronicles 27 in the KAPI

2 Chronicles 27 in the KBT1ETNIK

2 Chronicles 27 in the KBV

2 Chronicles 27 in the KJV

2 Chronicles 27 in the KNFD

2 Chronicles 27 in the LBA

2 Chronicles 27 in the LBLA

2 Chronicles 27 in the LNT

2 Chronicles 27 in the LSV

2 Chronicles 27 in the MAAL

2 Chronicles 27 in the MBV

2 Chronicles 27 in the MBV2

2 Chronicles 27 in the MHNT

2 Chronicles 27 in the MKNFD

2 Chronicles 27 in the MNG

2 Chronicles 27 in the MNT

2 Chronicles 27 in the MNT2

2 Chronicles 27 in the MRS1T

2 Chronicles 27 in the NAA

2 Chronicles 27 in the NASB

2 Chronicles 27 in the NBLA

2 Chronicles 27 in the NBS

2 Chronicles 27 in the NBVTP

2 Chronicles 27 in the NET2

2 Chronicles 27 in the NIV11

2 Chronicles 27 in the NNT

2 Chronicles 27 in the NNT2

2 Chronicles 27 in the NNT3

2 Chronicles 27 in the PDDPT

2 Chronicles 27 in the PFNT

2 Chronicles 27 in the RMNT

2 Chronicles 27 in the SBIAS

2 Chronicles 27 in the SBIBS

2 Chronicles 27 in the SBIBS2

2 Chronicles 27 in the SBICS

2 Chronicles 27 in the SBIDS

2 Chronicles 27 in the SBIGS

2 Chronicles 27 in the SBIHS

2 Chronicles 27 in the SBIIS

2 Chronicles 27 in the SBIIS2

2 Chronicles 27 in the SBIIS3

2 Chronicles 27 in the SBIKS

2 Chronicles 27 in the SBIKS2

2 Chronicles 27 in the SBIMS

2 Chronicles 27 in the SBIOS

2 Chronicles 27 in the SBIPS

2 Chronicles 27 in the SBISS

2 Chronicles 27 in the SBITS

2 Chronicles 27 in the SBITS2

2 Chronicles 27 in the SBITS3

2 Chronicles 27 in the SBITS4

2 Chronicles 27 in the SBIUS

2 Chronicles 27 in the SBIVS

2 Chronicles 27 in the SBT

2 Chronicles 27 in the SBT1E

2 Chronicles 27 in the SCHL

2 Chronicles 27 in the SNT

2 Chronicles 27 in the SUSU

2 Chronicles 27 in the SUSU2

2 Chronicles 27 in the SYNO

2 Chronicles 27 in the TBIAOTANT

2 Chronicles 27 in the TBT1E

2 Chronicles 27 in the TBT1E2

2 Chronicles 27 in the TFTIP

2 Chronicles 27 in the TFTU

2 Chronicles 27 in the TGNTATF3T

2 Chronicles 27 in the THAI

2 Chronicles 27 in the TNFD

2 Chronicles 27 in the TNT

2 Chronicles 27 in the TNTIK

2 Chronicles 27 in the TNTIL

2 Chronicles 27 in the TNTIN

2 Chronicles 27 in the TNTIP

2 Chronicles 27 in the TNTIZ

2 Chronicles 27 in the TOMA

2 Chronicles 27 in the TTENT

2 Chronicles 27 in the UBG

2 Chronicles 27 in the UGV

2 Chronicles 27 in the UGV2

2 Chronicles 27 in the UGV3

2 Chronicles 27 in the VBL

2 Chronicles 27 in the VDCC

2 Chronicles 27 in the YALU

2 Chronicles 27 in the YAPE

2 Chronicles 27 in the YBVTP

2 Chronicles 27 in the ZBP