Numbers 12 (BOGWICC)

1 Miriamu ndi Aaroni anayamba kuyankhula motsutsana ndi Mose chifukwa cha mkazi wa ku Kusi, popeza Moseyo anakwatira Mkusi. 2 Iwowo anafunsa kuti, “Kodi Yehova anayankhula kudzera mwa Mose yekha? Kodi sanayankhule kudzeranso mwa ife?” Ndipo Yehova anamva zimenezi. 3 (Koma Mose anali munthu wodzichepetsa kwambiri kuposa munthu aliyense pa dziko lapansi). 4 Nthawi yomweyo Yehova anati kwa Mose, Aaroni ndi Miriamu, “Bwerani ku tenti ya msonkhano nonse atatu.” Ndipo atatuwo anapitadi kumeneko. 5 Tsono Yehova anatsika mu mtambo, nayima pa khomo la chihema. Kenaka anayitana Aaroni ndi Miriamu. Ndipo onse awiri atapita patsogolo, 6 Mulungu anati, “Mverani mawu anga:“Pakakhala mneneri wa Yehova pakati panu,ndimadzionetsera kwa iyeyo mʼmasomphenya,ndimayankhula naye mʼmaloto. 7 Koma sinditero ndi Mose mtumiki wanga;Iyeyu ndi wokhulupirika mʼnyumba yanga yonse. 8 Ndimayankhula naye maso ndi maso,momveka bwino osati mophiphiritsa;ndipo amaona maonekedwe a Yehova.Nʼchifukwa chiyani simunaopekuyankhula motsutsana ndi Mose mtumiki wanga?” 9 Ndipo Yehova anawakwiyira, nachoka. 10 Pamene mtambo unachoka pamwamba pa Chihema, taonani, Miriamu anagwidwa ndi khate. Aaroni atachewuka anaona Miriamu ali ndi khate; 11 ndipo Aaroni anawuza Mose kuti, “Pepani mbuye wanga, musatilange chifukwa cha tchimo limene tachita mopusa. 12 Musalole kuti Miriamu akhale ngati mwana wobadwa wakufa kuchoka mʼmimba mwa amayi ake, thupi lake litawonongeka.” 13 Tsono Mose anafuwulira Yehova kuti, “Chonde Inu Mulungu, muchiritseni!” 14 Yehova anayankha Mose kuti, “Abambo ake akanamulavulira malovu mʼmaso, kodi sakanakhala wonyozeka masiku asanu ndi awiri? Mutsekereni kunja kwa msasa masiku asanu ndi awiri, kenaka mumulowetsenso.” 15 Choncho anamutsekera Miriamu kunja kwa msasa masiku asanu ndi awiri ndipo anthu sanayende ulendo wawo mpaka Miriamu atamulowetsanso. 16 Pambuyo pake anthu ananyamuka ku Heziroti ndi kukamanga mʼchipululu cha Parani.

In Other Versions

Numbers 12 in the ANGEFD

Numbers 12 in the ANTPNG2D

Numbers 12 in the AS21

Numbers 12 in the BAGH

Numbers 12 in the BBPNG

Numbers 12 in the BBT1E

Numbers 12 in the BDS

Numbers 12 in the BEV

Numbers 12 in the BHAD

Numbers 12 in the BIB

Numbers 12 in the BLPT

Numbers 12 in the BNT

Numbers 12 in the BNTABOOT

Numbers 12 in the BNTLV

Numbers 12 in the BOATCB

Numbers 12 in the BOATCB2

Numbers 12 in the BOBCV

Numbers 12 in the BOCNT

Numbers 12 in the BOECS

Numbers 12 in the BOHCB

Numbers 12 in the BOHCV

Numbers 12 in the BOHLNT

Numbers 12 in the BOHNTLTAL

Numbers 12 in the BOICB

Numbers 12 in the BOILNTAP

Numbers 12 in the BOITCV

Numbers 12 in the BOKCV

Numbers 12 in the BOKCV2

Numbers 12 in the BOKHWOG

Numbers 12 in the BOKSSV

Numbers 12 in the BOLCB

Numbers 12 in the BOLCB2

Numbers 12 in the BOMCV

Numbers 12 in the BONAV

Numbers 12 in the BONCB

Numbers 12 in the BONLT

Numbers 12 in the BONUT2

Numbers 12 in the BOPLNT

Numbers 12 in the BOSCB

Numbers 12 in the BOSNC

Numbers 12 in the BOTLNT

Numbers 12 in the BOVCB

Numbers 12 in the BOYCB

Numbers 12 in the BPBB

Numbers 12 in the BPH

Numbers 12 in the BSB

Numbers 12 in the CCB

Numbers 12 in the CUV

Numbers 12 in the CUVS

Numbers 12 in the DBT

Numbers 12 in the DGDNT

Numbers 12 in the DHNT

Numbers 12 in the DNT

Numbers 12 in the ELBE

Numbers 12 in the EMTV

Numbers 12 in the ESV

Numbers 12 in the FBV

Numbers 12 in the FEB

Numbers 12 in the GGMNT

Numbers 12 in the GNT

Numbers 12 in the HARY

Numbers 12 in the HNT

Numbers 12 in the IRVA

Numbers 12 in the IRVB

Numbers 12 in the IRVG

Numbers 12 in the IRVH

Numbers 12 in the IRVK

Numbers 12 in the IRVM

Numbers 12 in the IRVM2

Numbers 12 in the IRVO

Numbers 12 in the IRVP

Numbers 12 in the IRVT

Numbers 12 in the IRVT2

Numbers 12 in the IRVU

Numbers 12 in the ISVN

Numbers 12 in the JSNT

Numbers 12 in the KAPI

Numbers 12 in the KBT1ETNIK

Numbers 12 in the KBV

Numbers 12 in the KJV

Numbers 12 in the KNFD

Numbers 12 in the LBA

Numbers 12 in the LBLA

Numbers 12 in the LNT

Numbers 12 in the LSV

Numbers 12 in the MAAL

Numbers 12 in the MBV

Numbers 12 in the MBV2

Numbers 12 in the MHNT

Numbers 12 in the MKNFD

Numbers 12 in the MNG

Numbers 12 in the MNT

Numbers 12 in the MNT2

Numbers 12 in the MRS1T

Numbers 12 in the NAA

Numbers 12 in the NASB

Numbers 12 in the NBLA

Numbers 12 in the NBS

Numbers 12 in the NBVTP

Numbers 12 in the NET2

Numbers 12 in the NIV11

Numbers 12 in the NNT

Numbers 12 in the NNT2

Numbers 12 in the NNT3

Numbers 12 in the PDDPT

Numbers 12 in the PFNT

Numbers 12 in the RMNT

Numbers 12 in the SBIAS

Numbers 12 in the SBIBS

Numbers 12 in the SBIBS2

Numbers 12 in the SBICS

Numbers 12 in the SBIDS

Numbers 12 in the SBIGS

Numbers 12 in the SBIHS

Numbers 12 in the SBIIS

Numbers 12 in the SBIIS2

Numbers 12 in the SBIIS3

Numbers 12 in the SBIKS

Numbers 12 in the SBIKS2

Numbers 12 in the SBIMS

Numbers 12 in the SBIOS

Numbers 12 in the SBIPS

Numbers 12 in the SBISS

Numbers 12 in the SBITS

Numbers 12 in the SBITS2

Numbers 12 in the SBITS3

Numbers 12 in the SBITS4

Numbers 12 in the SBIUS

Numbers 12 in the SBIVS

Numbers 12 in the SBT

Numbers 12 in the SBT1E

Numbers 12 in the SCHL

Numbers 12 in the SNT

Numbers 12 in the SUSU

Numbers 12 in the SUSU2

Numbers 12 in the SYNO

Numbers 12 in the TBIAOTANT

Numbers 12 in the TBT1E

Numbers 12 in the TBT1E2

Numbers 12 in the TFTIP

Numbers 12 in the TFTU

Numbers 12 in the TGNTATF3T

Numbers 12 in the THAI

Numbers 12 in the TNFD

Numbers 12 in the TNT

Numbers 12 in the TNTIK

Numbers 12 in the TNTIL

Numbers 12 in the TNTIN

Numbers 12 in the TNTIP

Numbers 12 in the TNTIZ

Numbers 12 in the TOMA

Numbers 12 in the TTENT

Numbers 12 in the UBG

Numbers 12 in the UGV

Numbers 12 in the UGV2

Numbers 12 in the UGV3

Numbers 12 in the VBL

Numbers 12 in the VDCC

Numbers 12 in the YALU

Numbers 12 in the YAPE

Numbers 12 in the YBVTP

Numbers 12 in the ZBP