Psalms 17 (BOGWICC)

undefined Pemphero la Davide. 1 Imvani Inu Yehova pempho langa lachilungamo;mverani kulira kwanga.Tcherani khutu kuti mumve pemphero langapopeza silikuchokera pakamwa pachinyengo. 2 Kusalakwa kwanga kuchokera kwa inu;maso anu aone chimene ndi cholungama. 3 Ngakhale Inu mutafufuza mtima wanga ndi kundisanthula usiku,ngakhale mutandiyesa, simudzapeza kanthu;Ine ndatsimikiza kuti pakamwa panga sipadzachimwa. 4 Kunena za ntchito za anthu,monga mwa mawu a pakamwa panu,Ine ndadzisunga ndekhaposatsata njira zachiwawa. 5 Mayendedwe anga akhazikika pa njira zanu;mapazi anga sanaterereke. 6 Ine ndikuyitana Inu, Mulungu wanga, pakuti mudzandiyankha;tcherani khutu lanu kwa ine ndipo mumve pemphero langa. 7 Onetsani kudabwitsa kwa chikondi chanu chachikulu,Inu amene mumapulumutsa ndi dzanja lanu lamanjaiwo amene amathawira kwa inu kuchoka kwa adani awo. 8 Mundisunge ine ngati mwanadiso;mundibise mu mthunzi wa mapiko anu, 9 kuchoka kwa oyipa amene amandizinga ine,kuchoka kwa anthu amene ndi adani anga, amene andizungulira ine. 10 Iwo amatseka mitima yawo yopanda chifundo,ndi pakamwa pawo amayankhula modzitamandira. 11 Andisaka, tsopano andizungulirandi maso awo atcheru, kuti andigwetse pansi. 12 Iwo ali ngati mkango wofuna nyama;ngati mkango waukulu wokhala mobisala. 13 Dzukani Yehova, mulimbane nawo ndipo muwagwetse pansi;landitseni kuchoka kwa oyipa ndi lupanga lanu. 14 Inu Yehova, pulumutseni ndi dzanja lanu kwa anthu otere,kwa anthu a dziko lino amene mphotho yawo ili mʼmoyo uno. Inu mumaletsa njala kwa amene asangalatsidwa nanu;ana awo aamuna ali ndi zinthu zambiri,ndipo iwo amasunga chuma cha ana awo. 15 Ndipo ine mʼchilungamo ndidzaona nkhope yanu;pamene ndidzadzuka, ndidzakondwera kwambiri poonana nanu.

In Other Versions

Psalms 17 in the ANGEFD

Psalms 17 in the ANTPNG2D

Psalms 17 in the AS21

Psalms 17 in the BAGH

Psalms 17 in the BBPNG

Psalms 17 in the BBT1E

Psalms 17 in the BDS

Psalms 17 in the BEV

Psalms 17 in the BHAD

Psalms 17 in the BIB

Psalms 17 in the BLPT

Psalms 17 in the BNT

Psalms 17 in the BNTABOOT

Psalms 17 in the BNTLV

Psalms 17 in the BOATCB

Psalms 17 in the BOATCB2

Psalms 17 in the BOBCV

Psalms 17 in the BOCNT

Psalms 17 in the BOECS

Psalms 17 in the BOHCB

Psalms 17 in the BOHCV

Psalms 17 in the BOHLNT

Psalms 17 in the BOHNTLTAL

Psalms 17 in the BOICB

Psalms 17 in the BOILNTAP

Psalms 17 in the BOITCV

Psalms 17 in the BOKCV

Psalms 17 in the BOKCV2

Psalms 17 in the BOKHWOG

Psalms 17 in the BOKSSV

Psalms 17 in the BOLCB

Psalms 17 in the BOLCB2

Psalms 17 in the BOMCV

Psalms 17 in the BONAV

Psalms 17 in the BONCB

Psalms 17 in the BONLT

Psalms 17 in the BONUT2

Psalms 17 in the BOPLNT

Psalms 17 in the BOSCB

Psalms 17 in the BOSNC

Psalms 17 in the BOTLNT

Psalms 17 in the BOVCB

Psalms 17 in the BOYCB

Psalms 17 in the BPBB

Psalms 17 in the BPH

Psalms 17 in the BSB

Psalms 17 in the CCB

Psalms 17 in the CUV

Psalms 17 in the CUVS

Psalms 17 in the DBT

Psalms 17 in the DGDNT

Psalms 17 in the DHNT

Psalms 17 in the DNT

Psalms 17 in the ELBE

Psalms 17 in the EMTV

Psalms 17 in the ESV

Psalms 17 in the FBV

Psalms 17 in the FEB

Psalms 17 in the GGMNT

Psalms 17 in the GNT

Psalms 17 in the HARY

Psalms 17 in the HNT

Psalms 17 in the IRVA

Psalms 17 in the IRVB

Psalms 17 in the IRVG

Psalms 17 in the IRVH

Psalms 17 in the IRVK

Psalms 17 in the IRVM

Psalms 17 in the IRVM2

Psalms 17 in the IRVO

Psalms 17 in the IRVP

Psalms 17 in the IRVT

Psalms 17 in the IRVT2

Psalms 17 in the IRVU

Psalms 17 in the ISVN

Psalms 17 in the JSNT

Psalms 17 in the KAPI

Psalms 17 in the KBT1ETNIK

Psalms 17 in the KBV

Psalms 17 in the KJV

Psalms 17 in the KNFD

Psalms 17 in the LBA

Psalms 17 in the LBLA

Psalms 17 in the LNT

Psalms 17 in the LSV

Psalms 17 in the MAAL

Psalms 17 in the MBV

Psalms 17 in the MBV2

Psalms 17 in the MHNT

Psalms 17 in the MKNFD

Psalms 17 in the MNG

Psalms 17 in the MNT

Psalms 17 in the MNT2

Psalms 17 in the MRS1T

Psalms 17 in the NAA

Psalms 17 in the NASB

Psalms 17 in the NBLA

Psalms 17 in the NBS

Psalms 17 in the NBVTP

Psalms 17 in the NET2

Psalms 17 in the NIV11

Psalms 17 in the NNT

Psalms 17 in the NNT2

Psalms 17 in the NNT3

Psalms 17 in the PDDPT

Psalms 17 in the PFNT

Psalms 17 in the RMNT

Psalms 17 in the SBIAS

Psalms 17 in the SBIBS

Psalms 17 in the SBIBS2

Psalms 17 in the SBICS

Psalms 17 in the SBIDS

Psalms 17 in the SBIGS

Psalms 17 in the SBIHS

Psalms 17 in the SBIIS

Psalms 17 in the SBIIS2

Psalms 17 in the SBIIS3

Psalms 17 in the SBIKS

Psalms 17 in the SBIKS2

Psalms 17 in the SBIMS

Psalms 17 in the SBIOS

Psalms 17 in the SBIPS

Psalms 17 in the SBISS

Psalms 17 in the SBITS

Psalms 17 in the SBITS2

Psalms 17 in the SBITS3

Psalms 17 in the SBITS4

Psalms 17 in the SBIUS

Psalms 17 in the SBIVS

Psalms 17 in the SBT

Psalms 17 in the SBT1E

Psalms 17 in the SCHL

Psalms 17 in the SNT

Psalms 17 in the SUSU

Psalms 17 in the SUSU2

Psalms 17 in the SYNO

Psalms 17 in the TBIAOTANT

Psalms 17 in the TBT1E

Psalms 17 in the TBT1E2

Psalms 17 in the TFTIP

Psalms 17 in the TFTU

Psalms 17 in the TGNTATF3T

Psalms 17 in the THAI

Psalms 17 in the TNFD

Psalms 17 in the TNT

Psalms 17 in the TNTIK

Psalms 17 in the TNTIL

Psalms 17 in the TNTIN

Psalms 17 in the TNTIP

Psalms 17 in the TNTIZ

Psalms 17 in the TOMA

Psalms 17 in the TTENT

Psalms 17 in the UBG

Psalms 17 in the UGV

Psalms 17 in the UGV2

Psalms 17 in the UGV3

Psalms 17 in the VBL

Psalms 17 in the VDCC

Psalms 17 in the YALU

Psalms 17 in the YAPE

Psalms 17 in the YBVTP

Psalms 17 in the ZBP