1 Chronicles 20 (BOGWICC)

1 Nthawi ya mphukira, nthawi imene mafumu amapita ku nkhondo, Yowabu anatsogolera gulu la ankhondo. Iye anawononga Aamoni, kenaka anapita ku mzinda wa Raba ndipo anawuzungulira, koma Davide anatsala ku Yerusalemu. Yowabu anathira nkhondo mzinda wa Raba ndipo anawuwononga. 2 Davide anachotsa chipewa chaufumu pamutu pa mfumu yawo. Chipewacho chinkalemera makilogalamu asanu agolide ndiponso chinali ndi miyala yokongola. Ndipo Davide anavala chipewacho. Iye anatenga katundu wambiri kuchokera mu mzindawo, 3 ndipo anatulutsa anthu amene anali mʼmenemo, nawayika kuti azigwira ntchito ya macheka, yosula makasu ndi nkhwangwa. Davide anachita izi ndi mizinda yonse ya Aamoni. Kenaka Davide pamodzi ndi gulu lake lonse lankhondo anabwerera ku Yerusalemu. 4 Patapita nthawi, nkhondo inayambika pakati pa Aisraeli ndi Afilisti ku Gezeri. Nthawi imeneyo Sibekai Mhusati anapha Sipai, mmodzi mwa zidzukulu za Arefai, ndipo Afilisti anagonja. 5 Pa nkhondo inanso ndi Afilisti, Elihanani mwana wa Yairi anapha Lahimi mʼbale wake wa Goliati Mgiti, amene mkondo wake unali ngati ndodo yowombera nsalu. 6 Pa nkhondo inanso imene inachitika ku Gati, panali munthu wina wamtali kwambiri, wa zala zisanu ndi chimodzi mʼmanja ndi mʼmapazi ndipo zonse pamodzi zinalipo 24. Iyenso anali chidzukulu cha Rafa. 7 Pamene iye ankanyoza Aisraeli, Yonatani mwana wa Simea, mʼbale wake wa Davide anamupha. 8 Anthu amenewa anali zidzukulu za Rafa ku Gati, ndipo anaphedwa ndi Davide ndi ankhondo ake.

In Other Versions

1 Chronicles 20 in the ANGEFD

1 Chronicles 20 in the ANTPNG2D

1 Chronicles 20 in the AS21

1 Chronicles 20 in the BAGH

1 Chronicles 20 in the BBPNG

1 Chronicles 20 in the BBT1E

1 Chronicles 20 in the BDS

1 Chronicles 20 in the BEV

1 Chronicles 20 in the BHAD

1 Chronicles 20 in the BIB

1 Chronicles 20 in the BLPT

1 Chronicles 20 in the BNT

1 Chronicles 20 in the BNTABOOT

1 Chronicles 20 in the BNTLV

1 Chronicles 20 in the BOATCB

1 Chronicles 20 in the BOATCB2

1 Chronicles 20 in the BOBCV

1 Chronicles 20 in the BOCNT

1 Chronicles 20 in the BOECS

1 Chronicles 20 in the BOHCB

1 Chronicles 20 in the BOHCV

1 Chronicles 20 in the BOHLNT

1 Chronicles 20 in the BOHNTLTAL

1 Chronicles 20 in the BOICB

1 Chronicles 20 in the BOILNTAP

1 Chronicles 20 in the BOITCV

1 Chronicles 20 in the BOKCV

1 Chronicles 20 in the BOKCV2

1 Chronicles 20 in the BOKHWOG

1 Chronicles 20 in the BOKSSV

1 Chronicles 20 in the BOLCB

1 Chronicles 20 in the BOLCB2

1 Chronicles 20 in the BOMCV

1 Chronicles 20 in the BONAV

1 Chronicles 20 in the BONCB

1 Chronicles 20 in the BONLT

1 Chronicles 20 in the BONUT2

1 Chronicles 20 in the BOPLNT

1 Chronicles 20 in the BOSCB

1 Chronicles 20 in the BOSNC

1 Chronicles 20 in the BOTLNT

1 Chronicles 20 in the BOVCB

1 Chronicles 20 in the BOYCB

1 Chronicles 20 in the BPBB

1 Chronicles 20 in the BPH

1 Chronicles 20 in the BSB

1 Chronicles 20 in the CCB

1 Chronicles 20 in the CUV

1 Chronicles 20 in the CUVS

1 Chronicles 20 in the DBT

1 Chronicles 20 in the DGDNT

1 Chronicles 20 in the DHNT

1 Chronicles 20 in the DNT

1 Chronicles 20 in the ELBE

1 Chronicles 20 in the EMTV

1 Chronicles 20 in the ESV

1 Chronicles 20 in the FBV

1 Chronicles 20 in the FEB

1 Chronicles 20 in the GGMNT

1 Chronicles 20 in the GNT

1 Chronicles 20 in the HARY

1 Chronicles 20 in the HNT

1 Chronicles 20 in the IRVA

1 Chronicles 20 in the IRVB

1 Chronicles 20 in the IRVG

1 Chronicles 20 in the IRVH

1 Chronicles 20 in the IRVK

1 Chronicles 20 in the IRVM

1 Chronicles 20 in the IRVM2

1 Chronicles 20 in the IRVO

1 Chronicles 20 in the IRVP

1 Chronicles 20 in the IRVT

1 Chronicles 20 in the IRVT2

1 Chronicles 20 in the IRVU

1 Chronicles 20 in the ISVN

1 Chronicles 20 in the JSNT

1 Chronicles 20 in the KAPI

1 Chronicles 20 in the KBT1ETNIK

1 Chronicles 20 in the KBV

1 Chronicles 20 in the KJV

1 Chronicles 20 in the KNFD

1 Chronicles 20 in the LBA

1 Chronicles 20 in the LBLA

1 Chronicles 20 in the LNT

1 Chronicles 20 in the LSV

1 Chronicles 20 in the MAAL

1 Chronicles 20 in the MBV

1 Chronicles 20 in the MBV2

1 Chronicles 20 in the MHNT

1 Chronicles 20 in the MKNFD

1 Chronicles 20 in the MNG

1 Chronicles 20 in the MNT

1 Chronicles 20 in the MNT2

1 Chronicles 20 in the MRS1T

1 Chronicles 20 in the NAA

1 Chronicles 20 in the NASB

1 Chronicles 20 in the NBLA

1 Chronicles 20 in the NBS

1 Chronicles 20 in the NBVTP

1 Chronicles 20 in the NET2

1 Chronicles 20 in the NIV11

1 Chronicles 20 in the NNT

1 Chronicles 20 in the NNT2

1 Chronicles 20 in the NNT3

1 Chronicles 20 in the PDDPT

1 Chronicles 20 in the PFNT

1 Chronicles 20 in the RMNT

1 Chronicles 20 in the SBIAS

1 Chronicles 20 in the SBIBS

1 Chronicles 20 in the SBIBS2

1 Chronicles 20 in the SBICS

1 Chronicles 20 in the SBIDS

1 Chronicles 20 in the SBIGS

1 Chronicles 20 in the SBIHS

1 Chronicles 20 in the SBIIS

1 Chronicles 20 in the SBIIS2

1 Chronicles 20 in the SBIIS3

1 Chronicles 20 in the SBIKS

1 Chronicles 20 in the SBIKS2

1 Chronicles 20 in the SBIMS

1 Chronicles 20 in the SBIOS

1 Chronicles 20 in the SBIPS

1 Chronicles 20 in the SBISS

1 Chronicles 20 in the SBITS

1 Chronicles 20 in the SBITS2

1 Chronicles 20 in the SBITS3

1 Chronicles 20 in the SBITS4

1 Chronicles 20 in the SBIUS

1 Chronicles 20 in the SBIVS

1 Chronicles 20 in the SBT

1 Chronicles 20 in the SBT1E

1 Chronicles 20 in the SCHL

1 Chronicles 20 in the SNT

1 Chronicles 20 in the SUSU

1 Chronicles 20 in the SUSU2

1 Chronicles 20 in the SYNO

1 Chronicles 20 in the TBIAOTANT

1 Chronicles 20 in the TBT1E

1 Chronicles 20 in the TBT1E2

1 Chronicles 20 in the TFTIP

1 Chronicles 20 in the TFTU

1 Chronicles 20 in the TGNTATF3T

1 Chronicles 20 in the THAI

1 Chronicles 20 in the TNFD

1 Chronicles 20 in the TNT

1 Chronicles 20 in the TNTIK

1 Chronicles 20 in the TNTIL

1 Chronicles 20 in the TNTIN

1 Chronicles 20 in the TNTIP

1 Chronicles 20 in the TNTIZ

1 Chronicles 20 in the TOMA

1 Chronicles 20 in the TTENT

1 Chronicles 20 in the UBG

1 Chronicles 20 in the UGV

1 Chronicles 20 in the UGV2

1 Chronicles 20 in the UGV3

1 Chronicles 20 in the VBL

1 Chronicles 20 in the VDCC

1 Chronicles 20 in the YALU

1 Chronicles 20 in the YAPE

1 Chronicles 20 in the YBVTP

1 Chronicles 20 in the ZBP