1 Chronicles 3 (BOGWICC)

1 Ana aamuna a Davide amene anabadwira ku Hebroni anali awa:Woyamba anali Amnoni, amayi ake anali Ahinoamu wa ku Yezireeli;wachiwiri anali Danieli, amayi ake anali Abigayeli wa ku Karimeli; 2 wachitatu anali Abisalomu, mwana wa Maaka mwana wa Talimai mfumu ya Gesuri;wachinayi anali Adoniya amayi ake anali Hagiti; 3 wachisanu anali Sefatiya, amayi ake anali Abitali;wachisanu ndi chimodzi anali Itireamu, amayi ake anali Egila. 4 Ana asanu ndi mmodzi awa a Davide anabadwira ku Hebroni kumene analamulirako zaka zisanu ndi ziwiri ndi miyezi isanu ndi umodzi.Davide analamuliranso mu Yerusalemu kwa zaka 33, 5 ndipo ana amene anabadwira ku Yerusalemuko anali awa:Samua, Sobabu, Natani ndi Solomoni. Ana anayi awa anali a Batisuwa mwana wa Amieli. 6 Anaberekanso Ibihari, Elisua, Elipeleti, 7 Noga, Nefegi, Yafiya, 8 Elisama, Eliada ndi Elifeleti, onse analipo asanu ndi anayi. 9 Onsewa anali ana a Davide, osawerengera ana a azikazi. Ndipo mlongo wawo anali Tamara. 10 Mwana wa Solomoni anali Rehabiamu,Rehabiamu anabereka Abiya,Abiya anabereka Asa,Asa anabereka Yehosafati, 11 Yehosafati anabereka Yehoramu,Yehoramu anabereka Ahaziya,Ahaziya anabereka Yowasi, 12 Yowasi anabereka Amaziya,Amaziya anabereka Azariya,Azariya anabereka Yotamu, 13 Yotamu anabereka Ahazi,Ahazi anabereka Hezekiya,Hezekiya anabereka Manase, 14 Manase anabereka Amoni,Amoni anabereka Yosiya. 15 Ana a Yosiya anali awa:Yohanani mwana wake woyamba,Yehoyakimu mwana wake wachiwiri,Zedekiya mwana wake wachitatu,Salumu mwana wake wachinayi. 16 Ana a Yehoyakimu:Yekoniyandi Zedekiya mwana wake. 17 Zidzukulu za Yekoniya wa mʼndende zinali izi:mwana wake Silatieli, 18 Malikiramu, Pedaya, Senazara, Yekamiya, Hosama ndi Nedabiya. 19 Ana a Pedaya anali awa:Zerubabeli ndi Simei.Ana a Zerubabeli anali awa:Mesulamu ndi Hananiya.Mlongo wawo anali Selomiti. 20 Panalinso ana ena asanu awa:Hasubu, Oheli, Berekiya, Hasabiya ndi Yusabu-Hesedi. 21 Zidzukulu za Hananiya zinali izi:Pelatiya ndi Yesaiya, ndiponso ana a Refaya, ana a Arinani, ana a Obadiya ndi ana a Sekaniya. 22 Zidzukulu za Sekaniya zinali izi:Semaya ndi ana ake:Hatusi, Igala, Bariya, Neariya ndi Safati. Onse anali asanu ndi mmodzi. 23 Ana a Neariya anali awa:Eliyoenai, Hezekiya ndi Azirikamu. Onse anali atatu. 24 Ana a Eliyoenai: Hodaviya, Eliyasibu, Pelaya, Akubu,Yohanani, Delaya ndi Anani, onse anali asanu ndi awiri.

In Other Versions

1 Chronicles 3 in the ANGEFD

1 Chronicles 3 in the ANTPNG2D

1 Chronicles 3 in the AS21

1 Chronicles 3 in the BAGH

1 Chronicles 3 in the BBPNG

1 Chronicles 3 in the BBT1E

1 Chronicles 3 in the BDS

1 Chronicles 3 in the BEV

1 Chronicles 3 in the BHAD

1 Chronicles 3 in the BIB

1 Chronicles 3 in the BLPT

1 Chronicles 3 in the BNT

1 Chronicles 3 in the BNTABOOT

1 Chronicles 3 in the BNTLV

1 Chronicles 3 in the BOATCB

1 Chronicles 3 in the BOATCB2

1 Chronicles 3 in the BOBCV

1 Chronicles 3 in the BOCNT

1 Chronicles 3 in the BOECS

1 Chronicles 3 in the BOHCB

1 Chronicles 3 in the BOHCV

1 Chronicles 3 in the BOHLNT

1 Chronicles 3 in the BOHNTLTAL

1 Chronicles 3 in the BOICB

1 Chronicles 3 in the BOILNTAP

1 Chronicles 3 in the BOITCV

1 Chronicles 3 in the BOKCV

1 Chronicles 3 in the BOKCV2

1 Chronicles 3 in the BOKHWOG

1 Chronicles 3 in the BOKSSV

1 Chronicles 3 in the BOLCB

1 Chronicles 3 in the BOLCB2

1 Chronicles 3 in the BOMCV

1 Chronicles 3 in the BONAV

1 Chronicles 3 in the BONCB

1 Chronicles 3 in the BONLT

1 Chronicles 3 in the BONUT2

1 Chronicles 3 in the BOPLNT

1 Chronicles 3 in the BOSCB

1 Chronicles 3 in the BOSNC

1 Chronicles 3 in the BOTLNT

1 Chronicles 3 in the BOVCB

1 Chronicles 3 in the BOYCB

1 Chronicles 3 in the BPBB

1 Chronicles 3 in the BPH

1 Chronicles 3 in the BSB

1 Chronicles 3 in the CCB

1 Chronicles 3 in the CUV

1 Chronicles 3 in the CUVS

1 Chronicles 3 in the DBT

1 Chronicles 3 in the DGDNT

1 Chronicles 3 in the DHNT

1 Chronicles 3 in the DNT

1 Chronicles 3 in the ELBE

1 Chronicles 3 in the EMTV

1 Chronicles 3 in the ESV

1 Chronicles 3 in the FBV

1 Chronicles 3 in the FEB

1 Chronicles 3 in the GGMNT

1 Chronicles 3 in the GNT

1 Chronicles 3 in the HARY

1 Chronicles 3 in the HNT

1 Chronicles 3 in the IRVA

1 Chronicles 3 in the IRVB

1 Chronicles 3 in the IRVG

1 Chronicles 3 in the IRVH

1 Chronicles 3 in the IRVK

1 Chronicles 3 in the IRVM

1 Chronicles 3 in the IRVM2

1 Chronicles 3 in the IRVO

1 Chronicles 3 in the IRVP

1 Chronicles 3 in the IRVT

1 Chronicles 3 in the IRVT2

1 Chronicles 3 in the IRVU

1 Chronicles 3 in the ISVN

1 Chronicles 3 in the JSNT

1 Chronicles 3 in the KAPI

1 Chronicles 3 in the KBT1ETNIK

1 Chronicles 3 in the KBV

1 Chronicles 3 in the KJV

1 Chronicles 3 in the KNFD

1 Chronicles 3 in the LBA

1 Chronicles 3 in the LBLA

1 Chronicles 3 in the LNT

1 Chronicles 3 in the LSV

1 Chronicles 3 in the MAAL

1 Chronicles 3 in the MBV

1 Chronicles 3 in the MBV2

1 Chronicles 3 in the MHNT

1 Chronicles 3 in the MKNFD

1 Chronicles 3 in the MNG

1 Chronicles 3 in the MNT

1 Chronicles 3 in the MNT2

1 Chronicles 3 in the MRS1T

1 Chronicles 3 in the NAA

1 Chronicles 3 in the NASB

1 Chronicles 3 in the NBLA

1 Chronicles 3 in the NBS

1 Chronicles 3 in the NBVTP

1 Chronicles 3 in the NET2

1 Chronicles 3 in the NIV11

1 Chronicles 3 in the NNT

1 Chronicles 3 in the NNT2

1 Chronicles 3 in the NNT3

1 Chronicles 3 in the PDDPT

1 Chronicles 3 in the PFNT

1 Chronicles 3 in the RMNT

1 Chronicles 3 in the SBIAS

1 Chronicles 3 in the SBIBS

1 Chronicles 3 in the SBIBS2

1 Chronicles 3 in the SBICS

1 Chronicles 3 in the SBIDS

1 Chronicles 3 in the SBIGS

1 Chronicles 3 in the SBIHS

1 Chronicles 3 in the SBIIS

1 Chronicles 3 in the SBIIS2

1 Chronicles 3 in the SBIIS3

1 Chronicles 3 in the SBIKS

1 Chronicles 3 in the SBIKS2

1 Chronicles 3 in the SBIMS

1 Chronicles 3 in the SBIOS

1 Chronicles 3 in the SBIPS

1 Chronicles 3 in the SBISS

1 Chronicles 3 in the SBITS

1 Chronicles 3 in the SBITS2

1 Chronicles 3 in the SBITS3

1 Chronicles 3 in the SBITS4

1 Chronicles 3 in the SBIUS

1 Chronicles 3 in the SBIVS

1 Chronicles 3 in the SBT

1 Chronicles 3 in the SBT1E

1 Chronicles 3 in the SCHL

1 Chronicles 3 in the SNT

1 Chronicles 3 in the SUSU

1 Chronicles 3 in the SUSU2

1 Chronicles 3 in the SYNO

1 Chronicles 3 in the TBIAOTANT

1 Chronicles 3 in the TBT1E

1 Chronicles 3 in the TBT1E2

1 Chronicles 3 in the TFTIP

1 Chronicles 3 in the TFTU

1 Chronicles 3 in the TGNTATF3T

1 Chronicles 3 in the THAI

1 Chronicles 3 in the TNFD

1 Chronicles 3 in the TNT

1 Chronicles 3 in the TNTIK

1 Chronicles 3 in the TNTIL

1 Chronicles 3 in the TNTIN

1 Chronicles 3 in the TNTIP

1 Chronicles 3 in the TNTIZ

1 Chronicles 3 in the TOMA

1 Chronicles 3 in the TTENT

1 Chronicles 3 in the UBG

1 Chronicles 3 in the UGV

1 Chronicles 3 in the UGV2

1 Chronicles 3 in the UGV3

1 Chronicles 3 in the VBL

1 Chronicles 3 in the VDCC

1 Chronicles 3 in the YALU

1 Chronicles 3 in the YAPE

1 Chronicles 3 in the YBVTP

1 Chronicles 3 in the ZBP