1 Chronicles 8 (BOGWICC)

1 Benjamini anabereka Bela mwana wake woyamba,wachiwiri Asibeli, wachitatu Ahara, 2 wachinayi Noha ndipo wachisanu Rafa. 3 Ana a Bela anali awa:Adari, Gera, Abihudi, 4 Abisuwa, Naamani, Ahowa, 5 Gera, Sefufani ndi Hiramu. 6 Zidzukulu za Ehudi, zimene zinali atsogoleri a mabanja a amene amakhala ku Geba ndipo zinasamutsidwa kupita ku Manahati zinali izi: 7 Naamani, Ahiya ndi Gera, amene anawasamutsa ndipo anabereka Uza ndi Ahihudi. 8 Saharaimu anabereka ana ku Mowabu atalekana ndi akazi ake, Husimu ndi Baara. 9 Mwa mkazi wake Hodesi anabereka Yobabu, Zibiya, Mesa, Malikamu, 10 Yeusi, Sakiya ndi Mirima. Awa ndiye ana ake, atsogoleri a mabanja awo. 11 Mwa mkazi wake Husimu anabereka Abitubi ndi Elipaala. 12 Ana a Elipaala anali awa:Eberi, Misamu, Semedi (amene anamanga mizinda ya Ono ndi Lodi ndi midzi yake yozungulira) 13 ndiponso Beriya ndi Sema, amene anali atsogoleri a mabanja a amene ankakhala ku Ayaloni ndipo anathamangitsa nzika za ku Gati. 14 Ahiyo, Sasaki, Yeremoti, 15 Zebadiya, Aradi, Ederi, 16 Mikayeli, Isipa ndi Yoha anali ana a Beriya. 17 Zebadiya, Mesulamu, Hiziki, Heberi, 18 Isimerai, Iziliya ndi Yobabu anali ana a Elipaala. 19 Yakimu, Zikiri, Zabidi, 20 Elienai, Ziletai, Elieli, 21 Adaya, Beraya ndi Simirati anali ana a Simei. 22 Isipani, Eberi, Elieli, 23 Abidoni, Zikiri, Hanani, 24 Hananiya, Elamu, Anitotiya, 25 Ifideya ndi Penueli anali ana a Sasaki. 26 Samuserai, Sehariya, Ataliya, 27 Yaaresiya, Eliya ndi Zikiri anali ana a Yerohamu. 28 Onsewa anali atsogoleri a mabanja, anthu otchuka potsata mibado yawo, ndipo ankakhala mu Yerusalemu. 29 Yeiyeli amene amabereka Gibiyoni ankakhala ku Gibiyoni.Dzina la mkazi wake linali Maaka, 30 ndipo mwana wake woyamba anali Abidoni, motsatana ndi Zuri, Kisi, Baala, Neri, Nadabu, 31 Gedori, Ahiyo, Zekeri 32 ndi Mikiloti, amene anabereka Simea. Iwowa ankakhalanso ku Yerusalemu ndi abale awo. 33 Neri anabereka Kisi. Kisi anabereka Sauli, ndipo Sauli anabereka Yonatani, Maliki-Suwa, Abinadabu ndi Esibaala. 34 Mwana wa Yonatani analiMeri-Baala, amene anabereka Mika. 35 Ana a Mika anali awa:Pitoni, Meleki, Tareya ndi Ahazi. 36 Ahazi anabereka Yehoyada, Yehoyada anabereka Alemeti, Azimaveti ndi Zimuri, ndipo Zimuri anabereka Moza. 37 Moza anabereka Bineya. Ana ake anali Rafa, Eleasa ndi Azeli. 38 Azeli anali ndi ana asanu ndi mmodzi, ndipo mayina awo anali awa:Azirikamu, Bokeru, Ismaeli, Seariya, Obadiya ndi Hanani. Onsewa anali ana a Azeli. 39 Ana a Eseki mʼbale wake anali awa:Mwana wake woyamba Ulamu, wachiwiri Yeusi ndipo wachitatu Elifeleti. 40 Ana a Ulamu anali asilikali olimba mtima amene amadziwa kugwiritsa ntchito uta. Iwo anali ndi ana ndi adzukulu ambiri ndipo onse analipo 150.Onsewa anali adzukulu a Benjamini.

In Other Versions

1 Chronicles 8 in the ANGEFD

1 Chronicles 8 in the ANTPNG2D

1 Chronicles 8 in the AS21

1 Chronicles 8 in the BAGH

1 Chronicles 8 in the BBPNG

1 Chronicles 8 in the BBT1E

1 Chronicles 8 in the BDS

1 Chronicles 8 in the BEV

1 Chronicles 8 in the BHAD

1 Chronicles 8 in the BIB

1 Chronicles 8 in the BLPT

1 Chronicles 8 in the BNT

1 Chronicles 8 in the BNTABOOT

1 Chronicles 8 in the BNTLV

1 Chronicles 8 in the BOATCB

1 Chronicles 8 in the BOATCB2

1 Chronicles 8 in the BOBCV

1 Chronicles 8 in the BOCNT

1 Chronicles 8 in the BOECS

1 Chronicles 8 in the BOHCB

1 Chronicles 8 in the BOHCV

1 Chronicles 8 in the BOHLNT

1 Chronicles 8 in the BOHNTLTAL

1 Chronicles 8 in the BOICB

1 Chronicles 8 in the BOILNTAP

1 Chronicles 8 in the BOITCV

1 Chronicles 8 in the BOKCV

1 Chronicles 8 in the BOKCV2

1 Chronicles 8 in the BOKHWOG

1 Chronicles 8 in the BOKSSV

1 Chronicles 8 in the BOLCB

1 Chronicles 8 in the BOLCB2

1 Chronicles 8 in the BOMCV

1 Chronicles 8 in the BONAV

1 Chronicles 8 in the BONCB

1 Chronicles 8 in the BONLT

1 Chronicles 8 in the BONUT2

1 Chronicles 8 in the BOPLNT

1 Chronicles 8 in the BOSCB

1 Chronicles 8 in the BOSNC

1 Chronicles 8 in the BOTLNT

1 Chronicles 8 in the BOVCB

1 Chronicles 8 in the BOYCB

1 Chronicles 8 in the BPBB

1 Chronicles 8 in the BPH

1 Chronicles 8 in the BSB

1 Chronicles 8 in the CCB

1 Chronicles 8 in the CUV

1 Chronicles 8 in the CUVS

1 Chronicles 8 in the DBT

1 Chronicles 8 in the DGDNT

1 Chronicles 8 in the DHNT

1 Chronicles 8 in the DNT

1 Chronicles 8 in the ELBE

1 Chronicles 8 in the EMTV

1 Chronicles 8 in the ESV

1 Chronicles 8 in the FBV

1 Chronicles 8 in the FEB

1 Chronicles 8 in the GGMNT

1 Chronicles 8 in the GNT

1 Chronicles 8 in the HARY

1 Chronicles 8 in the HNT

1 Chronicles 8 in the IRVA

1 Chronicles 8 in the IRVB

1 Chronicles 8 in the IRVG

1 Chronicles 8 in the IRVH

1 Chronicles 8 in the IRVK

1 Chronicles 8 in the IRVM

1 Chronicles 8 in the IRVM2

1 Chronicles 8 in the IRVO

1 Chronicles 8 in the IRVP

1 Chronicles 8 in the IRVT

1 Chronicles 8 in the IRVT2

1 Chronicles 8 in the IRVU

1 Chronicles 8 in the ISVN

1 Chronicles 8 in the JSNT

1 Chronicles 8 in the KAPI

1 Chronicles 8 in the KBT1ETNIK

1 Chronicles 8 in the KBV

1 Chronicles 8 in the KJV

1 Chronicles 8 in the KNFD

1 Chronicles 8 in the LBA

1 Chronicles 8 in the LBLA

1 Chronicles 8 in the LNT

1 Chronicles 8 in the LSV

1 Chronicles 8 in the MAAL

1 Chronicles 8 in the MBV

1 Chronicles 8 in the MBV2

1 Chronicles 8 in the MHNT

1 Chronicles 8 in the MKNFD

1 Chronicles 8 in the MNG

1 Chronicles 8 in the MNT

1 Chronicles 8 in the MNT2

1 Chronicles 8 in the MRS1T

1 Chronicles 8 in the NAA

1 Chronicles 8 in the NASB

1 Chronicles 8 in the NBLA

1 Chronicles 8 in the NBS

1 Chronicles 8 in the NBVTP

1 Chronicles 8 in the NET2

1 Chronicles 8 in the NIV11

1 Chronicles 8 in the NNT

1 Chronicles 8 in the NNT2

1 Chronicles 8 in the NNT3

1 Chronicles 8 in the PDDPT

1 Chronicles 8 in the PFNT

1 Chronicles 8 in the RMNT

1 Chronicles 8 in the SBIAS

1 Chronicles 8 in the SBIBS

1 Chronicles 8 in the SBIBS2

1 Chronicles 8 in the SBICS

1 Chronicles 8 in the SBIDS

1 Chronicles 8 in the SBIGS

1 Chronicles 8 in the SBIHS

1 Chronicles 8 in the SBIIS

1 Chronicles 8 in the SBIIS2

1 Chronicles 8 in the SBIIS3

1 Chronicles 8 in the SBIKS

1 Chronicles 8 in the SBIKS2

1 Chronicles 8 in the SBIMS

1 Chronicles 8 in the SBIOS

1 Chronicles 8 in the SBIPS

1 Chronicles 8 in the SBISS

1 Chronicles 8 in the SBITS

1 Chronicles 8 in the SBITS2

1 Chronicles 8 in the SBITS3

1 Chronicles 8 in the SBITS4

1 Chronicles 8 in the SBIUS

1 Chronicles 8 in the SBIVS

1 Chronicles 8 in the SBT

1 Chronicles 8 in the SBT1E

1 Chronicles 8 in the SCHL

1 Chronicles 8 in the SNT

1 Chronicles 8 in the SUSU

1 Chronicles 8 in the SUSU2

1 Chronicles 8 in the SYNO

1 Chronicles 8 in the TBIAOTANT

1 Chronicles 8 in the TBT1E

1 Chronicles 8 in the TBT1E2

1 Chronicles 8 in the TFTIP

1 Chronicles 8 in the TFTU

1 Chronicles 8 in the TGNTATF3T

1 Chronicles 8 in the THAI

1 Chronicles 8 in the TNFD

1 Chronicles 8 in the TNT

1 Chronicles 8 in the TNTIK

1 Chronicles 8 in the TNTIL

1 Chronicles 8 in the TNTIN

1 Chronicles 8 in the TNTIP

1 Chronicles 8 in the TNTIZ

1 Chronicles 8 in the TOMA

1 Chronicles 8 in the TTENT

1 Chronicles 8 in the UBG

1 Chronicles 8 in the UGV

1 Chronicles 8 in the UGV2

1 Chronicles 8 in the UGV3

1 Chronicles 8 in the VBL

1 Chronicles 8 in the VDCC

1 Chronicles 8 in the YALU

1 Chronicles 8 in the YAPE

1 Chronicles 8 in the YBVTP

1 Chronicles 8 in the ZBP