Judges 12 (BOGWICC)
1 Gulu la nkhondo la fuko la Efereimu linayitanidwa ndipo anawolokera ku Zafoni nakafunsa Yefita kuti, “Nʼchifukwa chiyani unawoloka kukachita nkhondo ndi Aamoni osatiyitana kuti tipite nawe? Ife tikutenthera mʼnyumba mwakomu.” 2 Yefita anayankha kuti, “Ine ndi anthu anga tinakangana kwambiri ndi Aamoni. Ndinakuyitanani koma inu simunandipulumutse mʼmanja mwawo. 3 Nditaona kuti simundithandiza, ndinayika moyo wanga pa chiswe ndipo ndinawoloka kukachita nkhondo ndi a Aamoni. Yehova anandithandiza ndipo ndinawagonjetsa. Nanga nʼchifukwa chiyani mwabwera kwa ine lero kuti muchite nane nkhondo?” 4 Choncho Yefita anasonkhanitsa anthu a ku Giliyadi ndi kuchita nkhondo ndi Aefereimu. Ndipo Agiliyadi anagonjetsa Aefereimu chifukwa Aefereimuwo amati, “Inu a Giliyadi ndinu othawa kuchokera ku Efereimu ndi pakati pa Amanase.” 5 Choncho Agiliyadi analanda Aefereimu madooko a mtsinje wa Yorodani. Munthu aliyense wothawa ku Efereimu amati akanena kuti, “Ndiloleni ndiwoloke,” Agaliyadi ankafunsa kuti, “Kodi ndiwe mu Efurati?” Ngati iye ayankha kuti, “Ayi” 6 Ndiye amamuwuza kuti, “Nena kuti ‘Shiboleti.’ ” Tsono munthuyo akanena kuti Siboleti popeza samatha kutchula bwino mawuwa, ankamugwira ndi kumupha pomwepo pa madooko a mtsinje wa Yorodani. Nthawi imeneyo anaphedwa Aefereimu 42,000. 7 Yefita anatsogolera Israeli zaka zisanu ndi chimodzi. Kenaka Yefita wa ku Giliyadi anamwalira, ndipo anayikidwa mu mzinda wake ku Giliyadi. 8 Atamwalira Yefita, Ibizani wa ku Betelehemu anatsogolera Israeli. 9 Iye anali ndi ana aamuna makumi atatu ndi ana aakazi makumi atatu. Anakwatitsa ana ake akaziwo kwa anthu a fuko lina, ndipo ana ake aamuna aja anawabweretsera atsikana makumi atatu kuti awakwatire amenenso anali a fuko lina. Ibizani anatsogolera Israeli kwa zaka zisanu ndi ziwiri. 10 Kenaka Ibizani anamwalira, ndipo anayikidwa mu Betelehemu. 11 Iye atamwalira, Eloni wa fuko la Zebuloni anakhala mtsogoleri wa Aisraeli, ndipo anatsogolera Aisraeli kwa zaka khumi. 12 Kenaka Eloni anamwalira ndipo anayikidwa ku Ayaloni mʼdziko la Zebuloni. 13 Iye atamwalira, Abidoni mwana wa Hilelo wochokera ku Piratoni, anatsogolera Israeli. 14 Iye anali ndi ana aamuna makumi anayi ndi zidzukulu makumi atatu, amene ankakwera pa abulu 70. Iye anatsogolera Israeli kwa zaka zisanu ndi zitatu. 15 Ndipo Abidoni mwana wa Hilelo Mpiratoni uja anamwalira, nayikidwa ku Piratoni, mʼdziko la Efereimu, dziko lamapiri la Aamaleki.
In Other Versions
Judges 12 in the ANGEFD
Judges 12 in the ANTPNG2D
Judges 12 in the AS21
Judges 12 in the BAGH
Judges 12 in the BBPNG
Judges 12 in the BBT1E
Judges 12 in the BDS
Judges 12 in the BEV
Judges 12 in the BHAD
Judges 12 in the BIB
Judges 12 in the BLPT
Judges 12 in the BNT
Judges 12 in the BNTABOOT
Judges 12 in the BNTLV
Judges 12 in the BOATCB
Judges 12 in the BOATCB2
Judges 12 in the BOBCV
Judges 12 in the BOCNT
Judges 12 in the BOECS
Judges 12 in the BOHCB
Judges 12 in the BOHCV
Judges 12 in the BOHLNT
Judges 12 in the BOHNTLTAL
Judges 12 in the BOICB
Judges 12 in the BOILNTAP
Judges 12 in the BOITCV
Judges 12 in the BOKCV
Judges 12 in the BOKCV2
Judges 12 in the BOKHWOG
Judges 12 in the BOKSSV
Judges 12 in the BOLCB
Judges 12 in the BOLCB2
Judges 12 in the BOMCV
Judges 12 in the BONAV
Judges 12 in the BONCB
Judges 12 in the BONLT
Judges 12 in the BONUT2
Judges 12 in the BOPLNT
Judges 12 in the BOSCB
Judges 12 in the BOSNC
Judges 12 in the BOTLNT
Judges 12 in the BOVCB
Judges 12 in the BOYCB
Judges 12 in the BPBB
Judges 12 in the BPH
Judges 12 in the BSB
Judges 12 in the CCB
Judges 12 in the CUV
Judges 12 in the CUVS
Judges 12 in the DBT
Judges 12 in the DGDNT
Judges 12 in the DHNT
Judges 12 in the DNT
Judges 12 in the ELBE
Judges 12 in the EMTV
Judges 12 in the ESV
Judges 12 in the FBV
Judges 12 in the FEB
Judges 12 in the GGMNT
Judges 12 in the GNT
Judges 12 in the HARY
Judges 12 in the HNT
Judges 12 in the IRVA
Judges 12 in the IRVB
Judges 12 in the IRVG
Judges 12 in the IRVH
Judges 12 in the IRVK
Judges 12 in the IRVM
Judges 12 in the IRVM2
Judges 12 in the IRVO
Judges 12 in the IRVP
Judges 12 in the IRVT
Judges 12 in the IRVT2
Judges 12 in the IRVU
Judges 12 in the ISVN
Judges 12 in the JSNT
Judges 12 in the KAPI
Judges 12 in the KBT1ETNIK
Judges 12 in the KBV
Judges 12 in the KJV
Judges 12 in the KNFD
Judges 12 in the LBA
Judges 12 in the LBLA
Judges 12 in the LNT
Judges 12 in the LSV
Judges 12 in the MAAL
Judges 12 in the MBV
Judges 12 in the MBV2
Judges 12 in the MHNT
Judges 12 in the MKNFD
Judges 12 in the MNG
Judges 12 in the MNT
Judges 12 in the MNT2
Judges 12 in the MRS1T
Judges 12 in the NAA
Judges 12 in the NASB
Judges 12 in the NBLA
Judges 12 in the NBS
Judges 12 in the NBVTP
Judges 12 in the NET2
Judges 12 in the NIV11
Judges 12 in the NNT
Judges 12 in the NNT2
Judges 12 in the NNT3
Judges 12 in the PDDPT
Judges 12 in the PFNT
Judges 12 in the RMNT
Judges 12 in the SBIAS
Judges 12 in the SBIBS
Judges 12 in the SBIBS2
Judges 12 in the SBICS
Judges 12 in the SBIDS
Judges 12 in the SBIGS
Judges 12 in the SBIHS
Judges 12 in the SBIIS
Judges 12 in the SBIIS2
Judges 12 in the SBIIS3
Judges 12 in the SBIKS
Judges 12 in the SBIKS2
Judges 12 in the SBIMS
Judges 12 in the SBIOS
Judges 12 in the SBIPS
Judges 12 in the SBISS
Judges 12 in the SBITS
Judges 12 in the SBITS2
Judges 12 in the SBITS3
Judges 12 in the SBITS4
Judges 12 in the SBIUS
Judges 12 in the SBIVS
Judges 12 in the SBT
Judges 12 in the SBT1E
Judges 12 in the SCHL
Judges 12 in the SNT
Judges 12 in the SUSU
Judges 12 in the SUSU2
Judges 12 in the SYNO
Judges 12 in the TBIAOTANT
Judges 12 in the TBT1E
Judges 12 in the TBT1E2
Judges 12 in the TFTIP
Judges 12 in the TFTU
Judges 12 in the TGNTATF3T
Judges 12 in the THAI
Judges 12 in the TNFD
Judges 12 in the TNT
Judges 12 in the TNTIK
Judges 12 in the TNTIL
Judges 12 in the TNTIN
Judges 12 in the TNTIP
Judges 12 in the TNTIZ
Judges 12 in the TOMA
Judges 12 in the TTENT
Judges 12 in the UBG
Judges 12 in the UGV
Judges 12 in the UGV2
Judges 12 in the UGV3
Judges 12 in the VBL
Judges 12 in the VDCC
Judges 12 in the YALU
Judges 12 in the YAPE
Judges 12 in the YBVTP
Judges 12 in the ZBP