Nehemiah 7 (BOGWICC)

1 Khoma linamangidwa ndipo zitseko zinayikidwa. Pambuyo pake alonda a Nyumba ya Mulungu, oyimba nyimbo ndiponso Alevi anasankhidwa. 2 Kenaka ine ndinasankha mʼbale wanga Hanani pamodzi ndi Hananiya woyangʼanira nsanja yankhondo kukhala olamulira Yerusalemu chifukwa iyeyu anali munthu odalirika ndi woopa Mulungu kuposa anthu ena. 3 Ine ndinawawuza kuti, “Musalole kuti zipata za Yerusalemu zitsekulidwe mpaka dzuwa litatentha, ndipo alonda asanaweruke aonetsetse kuti atseka zitseko ndi kuzipiringidza. Musankhe alonda pakati pa anthu okhala mu Yerusalemu, ena akhale pa malo pawo ndi ena akhale moyangʼanana ndi nyumba zawo.” 4 Tsono mzinda wa Yerusalemu unali wotambasuka ndiponso waukulu koma munali anthu ochepa ndipo nyumba zinali zisanamangidwe. 5 Ndipo Mulungu wanga anayika mu mtima mwanga maganizo oti ndisonkhanitse anthu olemekezeka, akuluakulu ndi anthu onse kuti alembetse mayina mwa mabanja awo. Ndinapeza buku limene munalembedwa mayina a mabanja a iwo amene anayamba kubwera kuchokera ku ukapolo. Izi ndi zimene ndinazipeza zitalembedwa mʼmenemo: 6 Awa ndi anthu a mʼchigawo cha Yuda amene anabwerera kuchokera ku ukapolo amene Nebukadinezara mfumu ya Babuloni anawatenga ukapolo. Iwo anabwerera ku Yerusalemu ndi ku Yuda, aliyense ku mzinda wa makolo ake. 7 Anabwera pamodzi ndi atsogoleri awa: Zerubabeli, Yesuwa, Nehemiya, Azariya, Raamiya, Nahamani, Mordekai, Bilisani, Misipereti, Bigivai, Nehumu ndi Baana. Tsono chiwerengero cha anthu a ku Israeli chinali chotere: 8 Zidzukulu za Parosi 2,172 9 Zidzukulu za Sefatiya 372 10 Zidzukulu za Ara 652 11 Zidzukulu za Pahati-Mowabu (kudzera mu mʼbado wa Yesuwa ndi Yowabu) 2,818 12 Zidzukulu za Elamu 1,254 13 Zidzukulu za Zatu 845 14 Zidzukulu za Zakai 760 15 Zidzukulu za Binuyi 648 16 Zidzukulu za Bebai 628 17 Zidzukulu za Azigadi 2,322 18 Zidzukulu za Adonikamu 667 19 Zidzukulu za Abigivai 2,067 20 Zidzukulu za Adini 655 21 Zidzukulu za Ateri (kudzera mwa Hezekiya) 98 22 Zidzukulu za Hasumu 328 23 Zidzukulu za Bezayi 324 24 Zidzukulu za Harifu 112 25 Zidzukulu za Gibiyoni 95. 26 Anthu a ku Betelehemu ndi Netofa188 27 Anthu a ku Anatoti 128 28 Anthu a ku Beti-Azimaveti 42 29 Anthu a ku Kiriati Yeyarimu Kefira ndi Beeroti 743 30 Anthu a ku Rama ndi Geba 621 31 Anthu a ku Mikimasi 122 32 Anthu a ku Beteli ndi Ai 123 33 Anthu a ku Nebo winayo 52 34 Ana a Elamu wina 1,254 35 Zidzukulu za Harimu 320 36 Zidzukulu za Yeriko 345 37 Zidzukulu za Lodi, Hadidi ndi Ono721 38 Zidzukulu za Senaya 3,930. 39 Ansembe anali awa: 40 Zidzukulu za Imeri 1,052 41 Zidzukulu za Pasi-Huri 1,247 42 Zidzukulu za Harimu 1,017. 43 Alevi anali awa: 44 Anthu oyimba: 45 Alonda a ku Nyumba ya Mulungu anali awa: 46 Anthu ogwira ntchito ku Nyumba ya Mulungu anali awa: 47 Zidzukulu Kerosi, zidzukulu za Siya, zidzukulu za Padoni 48 Zidzukulu za Lebana za Hagaba, ndi za Salimayi, 49 Zidzukulu za Hanani, zidzukulu za Gideli, zidzukulu za Gahari, 50 Zidzukulu za Reyaya, zidzukulu za Rezini, zidzukulu za Nehoda, 51 Zidzukulu za Gazamu, zidzukulu za Uza, zidzukulu za Paseya, 52 Zidzukulu za Besai, zidzukulu za Meunimu, zidzukulu za Nefusimu, 53 Zidzukulu za Bakibuku, zidzukulu za Hakufa, zidzukulu za Harihuri, 54 Zidzukulu za Baziliti, zidzukulu za Mehida, zidzukulu za Harisa, 55 Zidzukulu za Barikosi, zidzukulu za Sisera, zidzukulu za Tema 56 Zidzukulu za Neziya, ndi zidzukulu za Hatifa. 57 Zidzukulu za antchito a Solomoni: 58 zidzukulu za Yaala, zidzukulu za Darikoni, zidzukulu za Gideli, 59 zidzukulu za Sefatiya, zidzukulu za Hatilu 60 Anthu onse ogwira ntchito ku Nyumba ya Mulungu pamodzi ndi zidzukulu za antchito a Solomoni analipo 392. 61 Ali munsiwa anachokera ku Teli-Mela, Teri-Harisa, Kerubi, Adoni, ndi Imeri, koma sanathe kunena mwa tchutchutchu kuti makolo awo kapena mafuko awo analidi Aisraeli kapena ayi. 62 Zidzukulu za 63 Ndiponso ena pakati pa ansembe anali awa:zidzukulu zaHobiya, zidzukulu za Hakozi ndi zidzukulu za Barizilai (munthu amene anakwatira mwana wamkazi wa Barizilai wa ku Giliyadi ndipo amatchedwa dzina limenelo). 64 Iwowa anafufuzafufuza mayina awo mʼbuku la mibado ya mabanja awo ndipo sanapeze mayina awo kotero anachotsedwa pa unsembe nawerengedwa ngati odetsedwa pa chipembedzo. 65 Choncho bwanamkubwa anawawuza anthuwo kuti asamadye nawo chakudya china chilichonse choperekedwa kwa Mulungu mpaka patapezeka wansembe wodziwa kugwiritsa bwino ntchito ya Urimu ndi Tumimu. 66 Chiwerengero chonse cha anthuwa chinali 42,360. 67 Kuwonjezera pamenepa panali antchito awo aamuna ndi aakazi 7,337 ndiponso anthu aamuna ndi aakazi oyimba nyimbo okwanira 245. 68 Panali akavalo 736, abulu angʼonoangʼono 245. 69 Ngamira zawo zinalipo 435 ndipo abulu analipo 6,720. 70 Atsogoleri ena a mabanja anapereka mphatso zothandizira ntchito. Bwanamkubwa anapereka ku thumba losungira chuma, ndalama zagolide za makilogalamu asanu ndi atatu, mabeseni makumi asanu ndi zovala za ansembe 530. 71 Atsogoleri ena amabanja anapereka ku thumba losungira chuma ndalama zagolide zokwana makilogalamu 168, ndiponso ndalama za siliva zokwana makilogalamu 1,250. 72 Anthu ena onse otsala anapereka ndalama zagolide zokwana makilogalamu 168, ndalama za siliva zokwana makilogalamu 140, ndiponso zovala za ansembe 67. 73 Choncho ansembe, Alevi, alonda a Nyumba ya Mulungu, anthu oyimba nyimbo, ena mwa anthu wamba, ogwira ntchito ku Nyumba ya Mulungu pamodzi ndi Aisraeli ena onse ankakhala mʼmizinda yawo.Pofika mwezi wachisanu ndi chiwiri Aisraeli onse anali atakhazikika mʼmizinda yawo.

In Other Versions

Nehemiah 7 in the ANGEFD

Nehemiah 7 in the ANTPNG2D

Nehemiah 7 in the AS21

Nehemiah 7 in the BAGH

Nehemiah 7 in the BBPNG

Nehemiah 7 in the BBT1E

Nehemiah 7 in the BDS

Nehemiah 7 in the BEV

Nehemiah 7 in the BHAD

Nehemiah 7 in the BIB

Nehemiah 7 in the BLPT

Nehemiah 7 in the BNT

Nehemiah 7 in the BNTABOOT

Nehemiah 7 in the BNTLV

Nehemiah 7 in the BOATCB

Nehemiah 7 in the BOATCB2

Nehemiah 7 in the BOBCV

Nehemiah 7 in the BOCNT

Nehemiah 7 in the BOECS

Nehemiah 7 in the BOHCB

Nehemiah 7 in the BOHCV

Nehemiah 7 in the BOHLNT

Nehemiah 7 in the BOHNTLTAL

Nehemiah 7 in the BOICB

Nehemiah 7 in the BOILNTAP

Nehemiah 7 in the BOITCV

Nehemiah 7 in the BOKCV

Nehemiah 7 in the BOKCV2

Nehemiah 7 in the BOKHWOG

Nehemiah 7 in the BOKSSV

Nehemiah 7 in the BOLCB

Nehemiah 7 in the BOLCB2

Nehemiah 7 in the BOMCV

Nehemiah 7 in the BONAV

Nehemiah 7 in the BONCB

Nehemiah 7 in the BONLT

Nehemiah 7 in the BONUT2

Nehemiah 7 in the BOPLNT

Nehemiah 7 in the BOSCB

Nehemiah 7 in the BOSNC

Nehemiah 7 in the BOTLNT

Nehemiah 7 in the BOVCB

Nehemiah 7 in the BOYCB

Nehemiah 7 in the BPBB

Nehemiah 7 in the BPH

Nehemiah 7 in the BSB

Nehemiah 7 in the CCB

Nehemiah 7 in the CUV

Nehemiah 7 in the CUVS

Nehemiah 7 in the DBT

Nehemiah 7 in the DGDNT

Nehemiah 7 in the DHNT

Nehemiah 7 in the DNT

Nehemiah 7 in the ELBE

Nehemiah 7 in the EMTV

Nehemiah 7 in the ESV

Nehemiah 7 in the FBV

Nehemiah 7 in the FEB

Nehemiah 7 in the GGMNT

Nehemiah 7 in the GNT

Nehemiah 7 in the HARY

Nehemiah 7 in the HNT

Nehemiah 7 in the IRVA

Nehemiah 7 in the IRVB

Nehemiah 7 in the IRVG

Nehemiah 7 in the IRVH

Nehemiah 7 in the IRVK

Nehemiah 7 in the IRVM

Nehemiah 7 in the IRVM2

Nehemiah 7 in the IRVO

Nehemiah 7 in the IRVP

Nehemiah 7 in the IRVT

Nehemiah 7 in the IRVT2

Nehemiah 7 in the IRVU

Nehemiah 7 in the ISVN

Nehemiah 7 in the JSNT

Nehemiah 7 in the KAPI

Nehemiah 7 in the KBT1ETNIK

Nehemiah 7 in the KBV

Nehemiah 7 in the KJV

Nehemiah 7 in the KNFD

Nehemiah 7 in the LBA

Nehemiah 7 in the LBLA

Nehemiah 7 in the LNT

Nehemiah 7 in the LSV

Nehemiah 7 in the MAAL

Nehemiah 7 in the MBV

Nehemiah 7 in the MBV2

Nehemiah 7 in the MHNT

Nehemiah 7 in the MKNFD

Nehemiah 7 in the MNG

Nehemiah 7 in the MNT

Nehemiah 7 in the MNT2

Nehemiah 7 in the MRS1T

Nehemiah 7 in the NAA

Nehemiah 7 in the NASB

Nehemiah 7 in the NBLA

Nehemiah 7 in the NBS

Nehemiah 7 in the NBVTP

Nehemiah 7 in the NET2

Nehemiah 7 in the NIV11

Nehemiah 7 in the NNT

Nehemiah 7 in the NNT2

Nehemiah 7 in the NNT3

Nehemiah 7 in the PDDPT

Nehemiah 7 in the PFNT

Nehemiah 7 in the RMNT

Nehemiah 7 in the SBIAS

Nehemiah 7 in the SBIBS

Nehemiah 7 in the SBIBS2

Nehemiah 7 in the SBICS

Nehemiah 7 in the SBIDS

Nehemiah 7 in the SBIGS

Nehemiah 7 in the SBIHS

Nehemiah 7 in the SBIIS

Nehemiah 7 in the SBIIS2

Nehemiah 7 in the SBIIS3

Nehemiah 7 in the SBIKS

Nehemiah 7 in the SBIKS2

Nehemiah 7 in the SBIMS

Nehemiah 7 in the SBIOS

Nehemiah 7 in the SBIPS

Nehemiah 7 in the SBISS

Nehemiah 7 in the SBITS

Nehemiah 7 in the SBITS2

Nehemiah 7 in the SBITS3

Nehemiah 7 in the SBITS4

Nehemiah 7 in the SBIUS

Nehemiah 7 in the SBIVS

Nehemiah 7 in the SBT

Nehemiah 7 in the SBT1E

Nehemiah 7 in the SCHL

Nehemiah 7 in the SNT

Nehemiah 7 in the SUSU

Nehemiah 7 in the SUSU2

Nehemiah 7 in the SYNO

Nehemiah 7 in the TBIAOTANT

Nehemiah 7 in the TBT1E

Nehemiah 7 in the TBT1E2

Nehemiah 7 in the TFTIP

Nehemiah 7 in the TFTU

Nehemiah 7 in the TGNTATF3T

Nehemiah 7 in the THAI

Nehemiah 7 in the TNFD

Nehemiah 7 in the TNT

Nehemiah 7 in the TNTIK

Nehemiah 7 in the TNTIL

Nehemiah 7 in the TNTIN

Nehemiah 7 in the TNTIP

Nehemiah 7 in the TNTIZ

Nehemiah 7 in the TOMA

Nehemiah 7 in the TTENT

Nehemiah 7 in the UBG

Nehemiah 7 in the UGV

Nehemiah 7 in the UGV2

Nehemiah 7 in the UGV3

Nehemiah 7 in the VBL

Nehemiah 7 in the VDCC

Nehemiah 7 in the YALU

Nehemiah 7 in the YAPE

Nehemiah 7 in the YBVTP

Nehemiah 7 in the ZBP