Psalms 135 (BOGWICC)
1 Tamandani Yehova. Tamandani dzina la Yehova;mutamandeni, inu atumiki a Yehova, 2 amene mumatumikira mʼnyumba ya Yehova,mʼmabwalo a nyumba ya Mulungu wathu. 3 Tamandani Yehova, pakuti Yehova ndi wabwino;imbani nyimbo zotamanda dzina lake, pakuti nʼkokoma kutero, 4 Pakuti Yehova wasankha Yakobo kuti akhale wake,Israeli kuti akhale chuma chake chapamtima. 5 Ndikudziwa kuti Yehova ndi wamkulu,kuti Ambuye athu ndi wamkulu kuposa milungu yonse. 6 Yehova amachita chilichonse chimene chimamukomera,kumwamba ndi dziko lapansi,ku nyanja zazikulu ndi ku malo ake onse akuya. 7 Iye amatulutsa mitambo kuchokera ku malekezero a dziko lapansi,amatumiza zingʼaningʼani pamodzi ndi mvulandipo amatulutsa mphepo ku malo ake osungiramo. 8 Anakantha ana oyamba kubadwa a Igupto,ana oyamba kubadwa a anthu ndi nyama. 9 Iye anatumiza zizindikiro zozizwitsa ndi zodabwitsa pakati pako, iwe Igupto,kutsutsana ndi Farao pamodzi ndi atumiki ake onse. 10 Iye anakantha mitundu yambiri ya anthundi kupha mafumu amphamvu: 11 Sihoni mfumu ya Aamori,Ogi mfumu ya Basani,ndi maufumu onse a ku Kanaani; 12 ndipo anapereka dziko lawo ngati cholowa,cholowa cha anthu ake Aisraeli. 13 Dzina lanu, Inu Yehova, ndi losatha mpaka muyaya,mbiri yanu, Inu Yehova, idziwika mibado yonse. 14 Pakuti Yehova adzaonetsa kuti anthu ake ngosalakwa,ndipo adzachitira chifundo atumiki ake. 15 Mafano a mitundu ya anthu ndi siliva ndi golide,opangidwa ndi manja a anthu. 16 Pakamwa ali napo koma sayankhulamaso ali nawo, koma sapenya; 17 makutu ali nawo, koma sakumvandipo mʼkamwa mwawo mulibe mpweya uliwonse. 18 Iwo amene amapanga mafanowo adzakhala ngati mafanowo,chimodzimodzinso iwo amene amadalira mafanowo. 19 Inu nyumba ya Israeli, tamandani Yehova;inu nyumba ya Aaroni, tamandani Yehova; 20 Inu nyumba ya Levi, tamandani Yehova;Inu amene mumaopa Iye, tamandani Yehova. 21 Wodalitsika ndi Yehova kuchokera mʼZiyoni,amene amakhala mu Yerusalemu. Tamandani Yehova.
In Other Versions
Psalms 135 in the ANGEFD
Psalms 135 in the ANTPNG2D
Psalms 135 in the AS21
Psalms 135 in the BAGH
Psalms 135 in the BBPNG
Psalms 135 in the BBT1E
Psalms 135 in the BDS
Psalms 135 in the BEV
Psalms 135 in the BHAD
Psalms 135 in the BIB
Psalms 135 in the BLPT
Psalms 135 in the BNT
Psalms 135 in the BNTABOOT
Psalms 135 in the BNTLV
Psalms 135 in the BOATCB
Psalms 135 in the BOATCB2
Psalms 135 in the BOBCV
Psalms 135 in the BOCNT
Psalms 135 in the BOECS
Psalms 135 in the BOHCB
Psalms 135 in the BOHCV
Psalms 135 in the BOHLNT
Psalms 135 in the BOHNTLTAL
Psalms 135 in the BOICB
Psalms 135 in the BOILNTAP
Psalms 135 in the BOITCV
Psalms 135 in the BOKCV
Psalms 135 in the BOKCV2
Psalms 135 in the BOKHWOG
Psalms 135 in the BOKSSV
Psalms 135 in the BOLCB
Psalms 135 in the BOLCB2
Psalms 135 in the BOMCV
Psalms 135 in the BONAV
Psalms 135 in the BONCB
Psalms 135 in the BONLT
Psalms 135 in the BONUT2
Psalms 135 in the BOPLNT
Psalms 135 in the BOSCB
Psalms 135 in the BOSNC
Psalms 135 in the BOTLNT
Psalms 135 in the BOVCB
Psalms 135 in the BOYCB
Psalms 135 in the BPBB
Psalms 135 in the BPH
Psalms 135 in the BSB
Psalms 135 in the CCB
Psalms 135 in the CUV
Psalms 135 in the CUVS
Psalms 135 in the DBT
Psalms 135 in the DGDNT
Psalms 135 in the DHNT
Psalms 135 in the DNT
Psalms 135 in the ELBE
Psalms 135 in the EMTV
Psalms 135 in the ESV
Psalms 135 in the FBV
Psalms 135 in the FEB
Psalms 135 in the GGMNT
Psalms 135 in the GNT
Psalms 135 in the HARY
Psalms 135 in the HNT
Psalms 135 in the IRVA
Psalms 135 in the IRVB
Psalms 135 in the IRVG
Psalms 135 in the IRVH
Psalms 135 in the IRVK
Psalms 135 in the IRVM
Psalms 135 in the IRVM2
Psalms 135 in the IRVO
Psalms 135 in the IRVP
Psalms 135 in the IRVT
Psalms 135 in the IRVT2
Psalms 135 in the IRVU
Psalms 135 in the ISVN
Psalms 135 in the JSNT
Psalms 135 in the KAPI
Psalms 135 in the KBT1ETNIK
Psalms 135 in the KBV
Psalms 135 in the KJV
Psalms 135 in the KNFD
Psalms 135 in the LBA
Psalms 135 in the LBLA
Psalms 135 in the LNT
Psalms 135 in the LSV
Psalms 135 in the MAAL
Psalms 135 in the MBV
Psalms 135 in the MBV2
Psalms 135 in the MHNT
Psalms 135 in the MKNFD
Psalms 135 in the MNG
Psalms 135 in the MNT
Psalms 135 in the MNT2
Psalms 135 in the MRS1T
Psalms 135 in the NAA
Psalms 135 in the NASB
Psalms 135 in the NBLA
Psalms 135 in the NBS
Psalms 135 in the NBVTP
Psalms 135 in the NET2
Psalms 135 in the NIV11
Psalms 135 in the NNT
Psalms 135 in the NNT2
Psalms 135 in the NNT3
Psalms 135 in the PDDPT
Psalms 135 in the PFNT
Psalms 135 in the RMNT
Psalms 135 in the SBIAS
Psalms 135 in the SBIBS
Psalms 135 in the SBIBS2
Psalms 135 in the SBICS
Psalms 135 in the SBIDS
Psalms 135 in the SBIGS
Psalms 135 in the SBIHS
Psalms 135 in the SBIIS
Psalms 135 in the SBIIS2
Psalms 135 in the SBIIS3
Psalms 135 in the SBIKS
Psalms 135 in the SBIKS2
Psalms 135 in the SBIMS
Psalms 135 in the SBIOS
Psalms 135 in the SBIPS
Psalms 135 in the SBISS
Psalms 135 in the SBITS
Psalms 135 in the SBITS2
Psalms 135 in the SBITS3
Psalms 135 in the SBITS4
Psalms 135 in the SBIUS
Psalms 135 in the SBIVS
Psalms 135 in the SBT
Psalms 135 in the SBT1E
Psalms 135 in the SCHL
Psalms 135 in the SNT
Psalms 135 in the SUSU
Psalms 135 in the SUSU2
Psalms 135 in the SYNO
Psalms 135 in the TBIAOTANT
Psalms 135 in the TBT1E
Psalms 135 in the TBT1E2
Psalms 135 in the TFTIP
Psalms 135 in the TFTU
Psalms 135 in the TGNTATF3T
Psalms 135 in the THAI
Psalms 135 in the TNFD
Psalms 135 in the TNT
Psalms 135 in the TNTIK
Psalms 135 in the TNTIL
Psalms 135 in the TNTIN
Psalms 135 in the TNTIP
Psalms 135 in the TNTIZ
Psalms 135 in the TOMA
Psalms 135 in the TTENT
Psalms 135 in the UBG
Psalms 135 in the UGV
Psalms 135 in the UGV2
Psalms 135 in the UGV3
Psalms 135 in the VBL
Psalms 135 in the VDCC
Psalms 135 in the YALU
Psalms 135 in the YAPE
Psalms 135 in the YBVTP
Psalms 135 in the ZBP