Psalms 51 (BOGWICC)
undefined Kwa mtsogoleri wa mayimbidwe. Salimo la Davide. Pamene Mneneri Natani anabwera kwa iye atachita chigololo ndi Batiseba. 1 Mundichitire chifundo, Inu Mulungu,molingana ndi chikondi chanu chosasinthika;molingana ndi chifundo chanu chachikulumufafanize mphulupulu zanga. 2 Munditsuke zolakwa zanga zonsendipo mundiyeretse kuchotsa tchimo langa. 3 Pakuti ndikudziwa mphulupulu zanga,ndipo tchimo langa lili pamaso panga nthawi zonse. 4 Motsutsana ndi Inu, Inu nokha, ndachimwandipo ndachita zoyipa pamaso panu,Kotero kuti inu mwapezeka kuti ndinu wolungamapamene muyankhula ndi pamene muweruza. 5 Zoonadi ine ndinali wochimwa pomwe ndimabadwa,wochimwa kuyambira pa nthawi imene amayi anga anakhala woyembekezera ine. 6 Zoonadi inu mumafuna choonadi mu ziwalo zamʼkati mwanga;mumandiphunzitsa nzeru mʼkati mwanga mwenimweni. 7 Mundiyeretse ndi hisope ndipo ndidzayera,munditsuke ndipo ndidzayera kuposa matalala 8 Mundilole ndimve chimwemwe ndi chisangalalo,mulole kuti mafupa amene mwawamphwanya akondwere. 9 Mufulatire machimo angandi kufafaniza zolakwa zanga zonse. 10 Mulenge mʼkati mwanga mtima woyera Inu Mulungundi kukonzanso mzimu wokhazikika mwa ine. 11 Musandichotse pamaso panukapena kuchotsa Mzimu wanu Woyera mwa ine. 12 Bwezeretsani mwa ine chimwemwe cha chipulumutso chanundipo mundipatse mzimu wofuna kumvera kuti undilimbitse. 13 Pamenepo ndidzaphunzitsa anthu amphulupulu njira zanukuti ochimwa adzabwerere kwa inu. 14 Mundipulumutse ku tchimo lokhetsa magazi, Inu Mulungu,Mulungu wa chipulumutso changa,ndipo lilime langa lidzayimba zachilungamo chanu. 15 Inu Ambuye tsekulani milomo yanga,ndipo pakamwa panga padzalengeza matamando anu. 16 Inu simusangalatsidwa ndi nsembe wamba.Ndikanapereka nsembe yopsereza, Inu simukondwera nayo. 17 Nsembe za Mulungu ndi mzimu wosweka;mtima wosweka ndi wachisoniInu Mulungu simudzawunyoza. 18 Mwa kukoma mtima kwanu mupange Ziyoni kuti alemere;mumange makoma a Yerusalemu. 19 Kotero kudzakhala nsembe zachilungamo,nsembe yonse yopsereza yokondweretsa Inu;ndipo ngʼombe zazimuna zidzaperekedwa pa guwa lanu la nsembe.
In Other Versions
Psalms 51 in the ANGEFD
Psalms 51 in the ANTPNG2D
Psalms 51 in the AS21
Psalms 51 in the BAGH
Psalms 51 in the BBPNG
Psalms 51 in the BBT1E
Psalms 51 in the BDS
Psalms 51 in the BEV
Psalms 51 in the BHAD
Psalms 51 in the BIB
Psalms 51 in the BLPT
Psalms 51 in the BNT
Psalms 51 in the BNTABOOT
Psalms 51 in the BNTLV
Psalms 51 in the BOATCB
Psalms 51 in the BOATCB2
Psalms 51 in the BOBCV
Psalms 51 in the BOCNT
Psalms 51 in the BOECS
Psalms 51 in the BOHCB
Psalms 51 in the BOHCV
Psalms 51 in the BOHLNT
Psalms 51 in the BOHNTLTAL
Psalms 51 in the BOICB
Psalms 51 in the BOILNTAP
Psalms 51 in the BOITCV
Psalms 51 in the BOKCV
Psalms 51 in the BOKCV2
Psalms 51 in the BOKHWOG
Psalms 51 in the BOKSSV
Psalms 51 in the BOLCB
Psalms 51 in the BOLCB2
Psalms 51 in the BOMCV
Psalms 51 in the BONAV
Psalms 51 in the BONCB
Psalms 51 in the BONLT
Psalms 51 in the BONUT2
Psalms 51 in the BOPLNT
Psalms 51 in the BOSCB
Psalms 51 in the BOSNC
Psalms 51 in the BOTLNT
Psalms 51 in the BOVCB
Psalms 51 in the BOYCB
Psalms 51 in the BPBB
Psalms 51 in the BPH
Psalms 51 in the BSB
Psalms 51 in the CCB
Psalms 51 in the CUV
Psalms 51 in the CUVS
Psalms 51 in the DBT
Psalms 51 in the DGDNT
Psalms 51 in the DHNT
Psalms 51 in the DNT
Psalms 51 in the ELBE
Psalms 51 in the EMTV
Psalms 51 in the ESV
Psalms 51 in the FBV
Psalms 51 in the FEB
Psalms 51 in the GGMNT
Psalms 51 in the GNT
Psalms 51 in the HARY
Psalms 51 in the HNT
Psalms 51 in the IRVA
Psalms 51 in the IRVB
Psalms 51 in the IRVG
Psalms 51 in the IRVH
Psalms 51 in the IRVK
Psalms 51 in the IRVM
Psalms 51 in the IRVM2
Psalms 51 in the IRVO
Psalms 51 in the IRVP
Psalms 51 in the IRVT
Psalms 51 in the IRVT2
Psalms 51 in the IRVU
Psalms 51 in the ISVN
Psalms 51 in the JSNT
Psalms 51 in the KAPI
Psalms 51 in the KBT1ETNIK
Psalms 51 in the KBV
Psalms 51 in the KJV
Psalms 51 in the KNFD
Psalms 51 in the LBA
Psalms 51 in the LBLA
Psalms 51 in the LNT
Psalms 51 in the LSV
Psalms 51 in the MAAL
Psalms 51 in the MBV
Psalms 51 in the MBV2
Psalms 51 in the MHNT
Psalms 51 in the MKNFD
Psalms 51 in the MNG
Psalms 51 in the MNT
Psalms 51 in the MNT2
Psalms 51 in the MRS1T
Psalms 51 in the NAA
Psalms 51 in the NASB
Psalms 51 in the NBLA
Psalms 51 in the NBS
Psalms 51 in the NBVTP
Psalms 51 in the NET2
Psalms 51 in the NIV11
Psalms 51 in the NNT
Psalms 51 in the NNT2
Psalms 51 in the NNT3
Psalms 51 in the PDDPT
Psalms 51 in the PFNT
Psalms 51 in the RMNT
Psalms 51 in the SBIAS
Psalms 51 in the SBIBS
Psalms 51 in the SBIBS2
Psalms 51 in the SBICS
Psalms 51 in the SBIDS
Psalms 51 in the SBIGS
Psalms 51 in the SBIHS
Psalms 51 in the SBIIS
Psalms 51 in the SBIIS2
Psalms 51 in the SBIIS3
Psalms 51 in the SBIKS
Psalms 51 in the SBIKS2
Psalms 51 in the SBIMS
Psalms 51 in the SBIOS
Psalms 51 in the SBIPS
Psalms 51 in the SBISS
Psalms 51 in the SBITS
Psalms 51 in the SBITS2
Psalms 51 in the SBITS3
Psalms 51 in the SBITS4
Psalms 51 in the SBIUS
Psalms 51 in the SBIVS
Psalms 51 in the SBT
Psalms 51 in the SBT1E
Psalms 51 in the SCHL
Psalms 51 in the SNT
Psalms 51 in the SUSU
Psalms 51 in the SUSU2
Psalms 51 in the SYNO
Psalms 51 in the TBIAOTANT
Psalms 51 in the TBT1E
Psalms 51 in the TBT1E2
Psalms 51 in the TFTIP
Psalms 51 in the TFTU
Psalms 51 in the TGNTATF3T
Psalms 51 in the THAI
Psalms 51 in the TNFD
Psalms 51 in the TNT
Psalms 51 in the TNTIK
Psalms 51 in the TNTIL
Psalms 51 in the TNTIN
Psalms 51 in the TNTIP
Psalms 51 in the TNTIZ
Psalms 51 in the TOMA
Psalms 51 in the TTENT
Psalms 51 in the UBG
Psalms 51 in the UGV
Psalms 51 in the UGV2
Psalms 51 in the UGV3
Psalms 51 in the VBL
Psalms 51 in the VDCC
Psalms 51 in the YALU
Psalms 51 in the YAPE
Psalms 51 in the YBVTP
Psalms 51 in the ZBP