Psalms 66 (BOGWICC)
undefined Kwa mtsogoleri wa mayimbidwe. Salimo. 1 Fuwulani kwa Mulungu ndi chimwemwe, dziko lonse lapansi! 2 Imbani ulemerero wa dzina lake;kumutamanda kwake kukhale kwaulemerero. 3 Nenani kwa Mulungu, “Ntchito zanu ndi zoopsa ndithu!Mphamvu yanu ndi yayikulu kwambirikotero kuti adani anu amawerama pamaso panu. 4 Dziko lonse lapansi limaweramira inu;limayimba matamando kwa Inu;limayimba matamando pa dzina lanu.”Sela. 5 Bwerani mudzaone zimene Mulungu wachita,ntchito zanu ndi zoopsa ndithu pakati pa anthu. 6 Iye anasandutsa nyanja kukhala malo owuma,iwo anawoloka pa madzi ndi mapazi.Bwerani, tiyeni tikondwere mwa Iye. 7 Iye amalamulira ndi mphamvu zake mpaka muyaya,maso ake amayangʼanira anthu a mitundu ina.Anthu owukira asadzitukumule. 8 Tamandani Mulungu wathu, inu mitundu ya anthu,mulole kuti mawu a matamando ake amveke; 9 Iye watchinjiriza miyoyo yathundi kusunga mapazi athu kuti angaterereke. 10 Pakuti Inu Mulungu munatiyesa;munatiyenga ngati siliva. 11 Inu mwatilowetsa mʼndendendi kutisenzetsa zolemera pa misana yathu. 12 Inu munalola kuti anthu akwere pa mitu yathu;ife tinadutsa mʼmoto ndi mʼmadzi,koma Inu munatibweretsa ku malo a zinthu zochuluka. 13 Ine ndidzabwera ku Nyumba yanu ndi nsembe zopserezandi kukwaniritsa malumbiro anga. 14 Malumbiro amene milomo yanga inalonjezandi pakamwa panga panayankhula pamene ndinali pa mavuto. 15 Ndidzapereka nsembe nyama zonenepa kwa Inundi chopereka cha nkhosa zazimuna;ndidzapereka ngʼombe zamphongo ndi mbuzi. Sela 16 Bwerani ndipo mudzamve inu nonse amene mumaopa Mulungu.Ndidzakuwuzani zimene Iyeyo wandichitira. 17 Ndinafuwula kwa Iye ndi pakamwa panga,matamando ake anali pa lilime panga. 18 Ndikanasekerera tchimo mu mtima mwangaAmbuye sakanamvera; 19 koma ndithu Mulungu wamvetserandipo watchera khutu ku mawu a kupempha kwanga. 20 Matamando akhale kwa Mulunguamene sanakane pemphero langakapena kuletsa chikondi chake pa ine!
In Other Versions
Psalms 66 in the ANGEFD
Psalms 66 in the ANTPNG2D
Psalms 66 in the AS21
Psalms 66 in the BAGH
Psalms 66 in the BBPNG
Psalms 66 in the BBT1E
Psalms 66 in the BDS
Psalms 66 in the BEV
Psalms 66 in the BHAD
Psalms 66 in the BIB
Psalms 66 in the BLPT
Psalms 66 in the BNT
Psalms 66 in the BNTABOOT
Psalms 66 in the BNTLV
Psalms 66 in the BOATCB
Psalms 66 in the BOATCB2
Psalms 66 in the BOBCV
Psalms 66 in the BOCNT
Psalms 66 in the BOECS
Psalms 66 in the BOHCB
Psalms 66 in the BOHCV
Psalms 66 in the BOHLNT
Psalms 66 in the BOHNTLTAL
Psalms 66 in the BOICB
Psalms 66 in the BOILNTAP
Psalms 66 in the BOITCV
Psalms 66 in the BOKCV
Psalms 66 in the BOKCV2
Psalms 66 in the BOKHWOG
Psalms 66 in the BOKSSV
Psalms 66 in the BOLCB
Psalms 66 in the BOLCB2
Psalms 66 in the BOMCV
Psalms 66 in the BONAV
Psalms 66 in the BONCB
Psalms 66 in the BONLT
Psalms 66 in the BONUT2
Psalms 66 in the BOPLNT
Psalms 66 in the BOSCB
Psalms 66 in the BOSNC
Psalms 66 in the BOTLNT
Psalms 66 in the BOVCB
Psalms 66 in the BOYCB
Psalms 66 in the BPBB
Psalms 66 in the BPH
Psalms 66 in the BSB
Psalms 66 in the CCB
Psalms 66 in the CUV
Psalms 66 in the CUVS
Psalms 66 in the DBT
Psalms 66 in the DGDNT
Psalms 66 in the DHNT
Psalms 66 in the DNT
Psalms 66 in the ELBE
Psalms 66 in the EMTV
Psalms 66 in the ESV
Psalms 66 in the FBV
Psalms 66 in the FEB
Psalms 66 in the GGMNT
Psalms 66 in the GNT
Psalms 66 in the HARY
Psalms 66 in the HNT
Psalms 66 in the IRVA
Psalms 66 in the IRVB
Psalms 66 in the IRVG
Psalms 66 in the IRVH
Psalms 66 in the IRVK
Psalms 66 in the IRVM
Psalms 66 in the IRVM2
Psalms 66 in the IRVO
Psalms 66 in the IRVP
Psalms 66 in the IRVT
Psalms 66 in the IRVT2
Psalms 66 in the IRVU
Psalms 66 in the ISVN
Psalms 66 in the JSNT
Psalms 66 in the KAPI
Psalms 66 in the KBT1ETNIK
Psalms 66 in the KBV
Psalms 66 in the KJV
Psalms 66 in the KNFD
Psalms 66 in the LBA
Psalms 66 in the LBLA
Psalms 66 in the LNT
Psalms 66 in the LSV
Psalms 66 in the MAAL
Psalms 66 in the MBV
Psalms 66 in the MBV2
Psalms 66 in the MHNT
Psalms 66 in the MKNFD
Psalms 66 in the MNG
Psalms 66 in the MNT
Psalms 66 in the MNT2
Psalms 66 in the MRS1T
Psalms 66 in the NAA
Psalms 66 in the NASB
Psalms 66 in the NBLA
Psalms 66 in the NBS
Psalms 66 in the NBVTP
Psalms 66 in the NET2
Psalms 66 in the NIV11
Psalms 66 in the NNT
Psalms 66 in the NNT2
Psalms 66 in the NNT3
Psalms 66 in the PDDPT
Psalms 66 in the PFNT
Psalms 66 in the RMNT
Psalms 66 in the SBIAS
Psalms 66 in the SBIBS
Psalms 66 in the SBIBS2
Psalms 66 in the SBICS
Psalms 66 in the SBIDS
Psalms 66 in the SBIGS
Psalms 66 in the SBIHS
Psalms 66 in the SBIIS
Psalms 66 in the SBIIS2
Psalms 66 in the SBIIS3
Psalms 66 in the SBIKS
Psalms 66 in the SBIKS2
Psalms 66 in the SBIMS
Psalms 66 in the SBIOS
Psalms 66 in the SBIPS
Psalms 66 in the SBISS
Psalms 66 in the SBITS
Psalms 66 in the SBITS2
Psalms 66 in the SBITS3
Psalms 66 in the SBITS4
Psalms 66 in the SBIUS
Psalms 66 in the SBIVS
Psalms 66 in the SBT
Psalms 66 in the SBT1E
Psalms 66 in the SCHL
Psalms 66 in the SNT
Psalms 66 in the SUSU
Psalms 66 in the SUSU2
Psalms 66 in the SYNO
Psalms 66 in the TBIAOTANT
Psalms 66 in the TBT1E
Psalms 66 in the TBT1E2
Psalms 66 in the TFTIP
Psalms 66 in the TFTU
Psalms 66 in the TGNTATF3T
Psalms 66 in the THAI
Psalms 66 in the TNFD
Psalms 66 in the TNT
Psalms 66 in the TNTIK
Psalms 66 in the TNTIL
Psalms 66 in the TNTIN
Psalms 66 in the TNTIP
Psalms 66 in the TNTIZ
Psalms 66 in the TOMA
Psalms 66 in the TTENT
Psalms 66 in the UBG
Psalms 66 in the UGV
Psalms 66 in the UGV2
Psalms 66 in the UGV3
Psalms 66 in the VBL
Psalms 66 in the VDCC
Psalms 66 in the YALU
Psalms 66 in the YAPE
Psalms 66 in the YBVTP
Psalms 66 in the ZBP