1 Chronicles 27 (BOGWICC)

1 Uwu ndi mndandanda wa Aisraeli, atsogoleri a mabanja, olamulira asilikali 1,000, olamulira asilikali 100 ndi akuluakulu awo, amene ankatumikira mfumu mʼzonse zokhudza magulu a ankhondo, amene amagwira ntchito mwezi ndi mwezi chaka chonse. Gulu lililonse linali ndi anthu 24,000. 2 Amene amalamulira gulu loyamba pa mwezi woyamba anali Yasobeamu mwana wa Zabidieli. Pa gulu lake panali asilikali 24,000. 3 Iyeyu anali chidzukulu cha Perezi ndipo anali mkulu wa atsogoleri onse a ankhondo mwezi woyamba. 4 Amene amalamulira gulu lachiwiri pa mwezi wachiwiri anali Dodai Mwahohi; Mikiloti ndiye anali mtsogoleri wa gulu lake. Pa gulu lake panali asilikali 24,000. 5 Wolamulira ankhondo wachitatu, pa mwezi wachitatu anali Benaya, mwana wa wansembe Yehoyada. Iye anali mtsogoleri ndipo pa gulu lake panali ankhondo 24,000. 6 Uyu ndi Benaya uja amene anali wamphamvu pa gulu la anthu makumi atatu ndipo ndiye amatsogolera anthu makumi atatu aja. Mwana wake Amizabadi ndiye amatsogolera gulu lake. 7 Wachinayi pa mwezi wachinayi anali Asaheli mʼbale wake wa Yowabu; ndipo mwana wake Zebadiya ndiye analowa mʼmalo mwake. Pa gulu lake panali asilikali 24,000. 8 Wachisanu pa mwezi wachisanu anali Samihuti, mdzukulu wa Izira. Pa gulu lake panali asilikali 24,000. 9 Wa 6 pa mwezi wa 6 anali Ira mwana wa Ikesi wa ku Tekowa. Pa gulu lake panali asilikali 24,000. 10 Wa 7 pa mwezi wa 7 anali Helezi Mpeloni wa fuko la Efereimu. Pa gulu lake panali asilikali 24,000. 11 Wa 8 pa mwezi wa 8 anali Sibekai Mhusati, wa mbumba ya Zera. Pa gulu lake panali asilikali 24,000 12 Wa 9 pa mwezi wa 9 anali Abiezeri wa banja la Anatoti, wa fuko la Benjamini. Pa gulu lake panali asilikali 24,000. 13 Wa khumi pa mwezi wa khumi anali Mahazayi wa ku Netofa, wa mbumba ya Zera. Pa gulu lake panali asilikali 24,000. 14 Mtsogoleri wa 11, pa mwezi wa 11 anali Benaya wa ku Piratoni, wa fuko la Efereimu. Pa gulu lake panali asilikali 24,000. 15 Mtsogoleri wa 12, pa mwezi wa 12 anali Helidai Mnetofa, wa banja la Otanieli. Pa gulu lake panali asilikali 24,000. 16 Akuluakulu amene amatsogolera mafuko a Israeli ndi awa: Mtsogoleri wa fuko la Rubeni: Eliezara mwana wa Zikiri;mtsogoleri wa fuko la Simeoni: Sefatiya mwana wa Maaka; 17 mtsogoleri wa fuko la Levi: Hasabiya mwana wa Kemueli,mtsogoleri wa banja la Aaroni: Zadoki; 18 mtsogoleri wa fuko la Yuda: Elihu, mʼbale wake wa Davide;mtsogoleri wa fuko la Isakara: Omuri mwana wa Mikayeli; 19 mtsogoleri wa fuko la Zebuloni: Isimaiya mwana wa Obadiya;mtsogoleri wa fuko la Nafutali: Yerimoti mwana wa Azirieli; 20 mtsogoleri wa fuko la Efereimu: Hoseya mwana wa Azaziya;mtsogoleri wa fuko la theka la Manase: Yoweli mwana wa Pedaya; 21 mtsogoleri wa fuko la theka la Manase limene linali ku Giliyadi: Ido mwana wa Zekariya;mtsogoleri wa fuko la Benjamini: Yaasieli mwana wa Abineri; 22 mtsogoleri wa fuko la Dani: Azareli mwana wa Yerohamu.Awa anali akuluakulu a mafuko a Israeli. 23 Davide sanawerenge amuna amene anali ndi zaka makumi awiri kapena kucheperapo, chifukwa Yehova analonjeza kuti adzachulukitsa Aisraeli ngati nyenyezi zamumlengalenga. 24 Yowabu mwana wa Zeruya anayamba kuwerenga amuna koma sanamalize. Mkwiyo unagwera Aisraeli chifukwa cha zimenezi ndipo chiwerengerochi sanachilowetse mʼbuku la mbiri ya mfumu Davide. 25 Azimaveti mwana wa Adieli ankayangʼanira nyumba zosungiramo katundu wa mfumu.Yonatani mwana wa Uziya ankayangʼanira nyumba zosungiramo katundu wa maboma ozungulira, mizinda, midzi ndi malo olondera. 26 Eziri mwana wa Kelubi ankayangʼanira anthu ogwira ntchito yolima ku munda. 27 Simei wa ku Rama ankayangʼanira minda ya mpesa.Zabidi wa ku Sifamu ankayangʼanira mphesa ndi mosungiramo mwake. 28 Baala-Hanani wa ku Gederi ankayangʼanira mitengo ya olivi ndi ya mikuyu ya ku Sefela.Yowasi ankayangʼanira mafuta a Olivi. 29 Sitirayi wa ku Saroni ankayangʼanira ziweto zimene amaweta ku Saroni.Safati mwana wa Adilayi ankayangʼanira ngʼombe zakuzigwa. 30 Obili Mwismaeli ankayangʼanira ngamira.Yehideya Mmerenoti ankayangʼanira abulu. 31 Yazizi Mhagiri akayangʼanira nkhosa ndi mbuzi.Onsewa anali akuluakulu oyangʼanira chuma cha mfumu Davide. 32 Yonatani, malume wake wa Davide, anali phungu wake ndipo anali munthu wanzeru komanso analinso mlembi. Yehieli mwana wa Hakimoni ankasamalira ana a mfumu. 33 Ahitofele anali phungu wa mfumu.Husai Mwariki anali bwenzi la mfumu. 34 Ahitofele atamwalira mʼmalo mwake munalowa Yehoyada mwana wa Benaya ndi Abiatara.Yowabu anali mtsogoleri wa gulu lankhondo la mfumu.

In Other Versions

1 Chronicles 27 in the ANGEFD

1 Chronicles 27 in the ANTPNG2D

1 Chronicles 27 in the AS21

1 Chronicles 27 in the BAGH

1 Chronicles 27 in the BBPNG

1 Chronicles 27 in the BBT1E

1 Chronicles 27 in the BDS

1 Chronicles 27 in the BEV

1 Chronicles 27 in the BHAD

1 Chronicles 27 in the BIB

1 Chronicles 27 in the BLPT

1 Chronicles 27 in the BNT

1 Chronicles 27 in the BNTABOOT

1 Chronicles 27 in the BNTLV

1 Chronicles 27 in the BOATCB

1 Chronicles 27 in the BOATCB2

1 Chronicles 27 in the BOBCV

1 Chronicles 27 in the BOCNT

1 Chronicles 27 in the BOECS

1 Chronicles 27 in the BOHCB

1 Chronicles 27 in the BOHCV

1 Chronicles 27 in the BOHLNT

1 Chronicles 27 in the BOHNTLTAL

1 Chronicles 27 in the BOICB

1 Chronicles 27 in the BOILNTAP

1 Chronicles 27 in the BOITCV

1 Chronicles 27 in the BOKCV

1 Chronicles 27 in the BOKCV2

1 Chronicles 27 in the BOKHWOG

1 Chronicles 27 in the BOKSSV

1 Chronicles 27 in the BOLCB

1 Chronicles 27 in the BOLCB2

1 Chronicles 27 in the BOMCV

1 Chronicles 27 in the BONAV

1 Chronicles 27 in the BONCB

1 Chronicles 27 in the BONLT

1 Chronicles 27 in the BONUT2

1 Chronicles 27 in the BOPLNT

1 Chronicles 27 in the BOSCB

1 Chronicles 27 in the BOSNC

1 Chronicles 27 in the BOTLNT

1 Chronicles 27 in the BOVCB

1 Chronicles 27 in the BOYCB

1 Chronicles 27 in the BPBB

1 Chronicles 27 in the BPH

1 Chronicles 27 in the BSB

1 Chronicles 27 in the CCB

1 Chronicles 27 in the CUV

1 Chronicles 27 in the CUVS

1 Chronicles 27 in the DBT

1 Chronicles 27 in the DGDNT

1 Chronicles 27 in the DHNT

1 Chronicles 27 in the DNT

1 Chronicles 27 in the ELBE

1 Chronicles 27 in the EMTV

1 Chronicles 27 in the ESV

1 Chronicles 27 in the FBV

1 Chronicles 27 in the FEB

1 Chronicles 27 in the GGMNT

1 Chronicles 27 in the GNT

1 Chronicles 27 in the HARY

1 Chronicles 27 in the HNT

1 Chronicles 27 in the IRVA

1 Chronicles 27 in the IRVB

1 Chronicles 27 in the IRVG

1 Chronicles 27 in the IRVH

1 Chronicles 27 in the IRVK

1 Chronicles 27 in the IRVM

1 Chronicles 27 in the IRVM2

1 Chronicles 27 in the IRVO

1 Chronicles 27 in the IRVP

1 Chronicles 27 in the IRVT

1 Chronicles 27 in the IRVT2

1 Chronicles 27 in the IRVU

1 Chronicles 27 in the ISVN

1 Chronicles 27 in the JSNT

1 Chronicles 27 in the KAPI

1 Chronicles 27 in the KBT1ETNIK

1 Chronicles 27 in the KBV

1 Chronicles 27 in the KJV

1 Chronicles 27 in the KNFD

1 Chronicles 27 in the LBA

1 Chronicles 27 in the LBLA

1 Chronicles 27 in the LNT

1 Chronicles 27 in the LSV

1 Chronicles 27 in the MAAL

1 Chronicles 27 in the MBV

1 Chronicles 27 in the MBV2

1 Chronicles 27 in the MHNT

1 Chronicles 27 in the MKNFD

1 Chronicles 27 in the MNG

1 Chronicles 27 in the MNT

1 Chronicles 27 in the MNT2

1 Chronicles 27 in the MRS1T

1 Chronicles 27 in the NAA

1 Chronicles 27 in the NASB

1 Chronicles 27 in the NBLA

1 Chronicles 27 in the NBS

1 Chronicles 27 in the NBVTP

1 Chronicles 27 in the NET2

1 Chronicles 27 in the NIV11

1 Chronicles 27 in the NNT

1 Chronicles 27 in the NNT2

1 Chronicles 27 in the NNT3

1 Chronicles 27 in the PDDPT

1 Chronicles 27 in the PFNT

1 Chronicles 27 in the RMNT

1 Chronicles 27 in the SBIAS

1 Chronicles 27 in the SBIBS

1 Chronicles 27 in the SBIBS2

1 Chronicles 27 in the SBICS

1 Chronicles 27 in the SBIDS

1 Chronicles 27 in the SBIGS

1 Chronicles 27 in the SBIHS

1 Chronicles 27 in the SBIIS

1 Chronicles 27 in the SBIIS2

1 Chronicles 27 in the SBIIS3

1 Chronicles 27 in the SBIKS

1 Chronicles 27 in the SBIKS2

1 Chronicles 27 in the SBIMS

1 Chronicles 27 in the SBIOS

1 Chronicles 27 in the SBIPS

1 Chronicles 27 in the SBISS

1 Chronicles 27 in the SBITS

1 Chronicles 27 in the SBITS2

1 Chronicles 27 in the SBITS3

1 Chronicles 27 in the SBITS4

1 Chronicles 27 in the SBIUS

1 Chronicles 27 in the SBIVS

1 Chronicles 27 in the SBT

1 Chronicles 27 in the SBT1E

1 Chronicles 27 in the SCHL

1 Chronicles 27 in the SNT

1 Chronicles 27 in the SUSU

1 Chronicles 27 in the SUSU2

1 Chronicles 27 in the SYNO

1 Chronicles 27 in the TBIAOTANT

1 Chronicles 27 in the TBT1E

1 Chronicles 27 in the TBT1E2

1 Chronicles 27 in the TFTIP

1 Chronicles 27 in the TFTU

1 Chronicles 27 in the TGNTATF3T

1 Chronicles 27 in the THAI

1 Chronicles 27 in the TNFD

1 Chronicles 27 in the TNT

1 Chronicles 27 in the TNTIK

1 Chronicles 27 in the TNTIL

1 Chronicles 27 in the TNTIN

1 Chronicles 27 in the TNTIP

1 Chronicles 27 in the TNTIZ

1 Chronicles 27 in the TOMA

1 Chronicles 27 in the TTENT

1 Chronicles 27 in the UBG

1 Chronicles 27 in the UGV

1 Chronicles 27 in the UGV2

1 Chronicles 27 in the UGV3

1 Chronicles 27 in the VBL

1 Chronicles 27 in the VDCC

1 Chronicles 27 in the YALU

1 Chronicles 27 in the YAPE

1 Chronicles 27 in the YBVTP

1 Chronicles 27 in the ZBP