1 Samuel 5 (BOGWICC)
1 Afilisti atalanda Bokosi la Mulungu lija, analitenga kuchoka ku Ebenezeri kupita ku Asidodi. 2 Kenaka anatenga Bokosi la Chipanganolo nabwera nalo ku nyumba ya Dagoni ndi kuliyika pambali pa Dagoni. 3 Anthu a ku Asidodi atadzuka mmawa mwake, anangoona Dagoni atagwa pansi chafufumimba pamaso pa Bokosi la Yehova! Iwo anatenga Dagoni ndi kumuyimika pamalo pake. 4 Koma mmawa mwakenso atadzuka, anaona Dagoni atagwa chafufumimba pamaso pa Bokosi la Yehova. Mutu wake ndi manja ake zinali zitaduka ndi kugwera pa khonde polowera, thunthu lake lokha ndilo linatsala. 5 Nʼchifukwa chake mpaka lero ansembe a Dagoni kapena wina aliyense amene amalowa mʼkachisi wa Dagoni ku Asidodi saponda pa khonde. 6 Yehova analanga koopsa anthu a ku Asidodi. Yehova anawawononga ndi kuwazunza ndi zithupsa Asidoniwa pamodzi ndi anthu a madera ozungulira. 7 Anthu a ku Asidodi ataona zimene zimachitika anati, “Bokosi la Mulungu wa Israeli lisakhale kuno chifukwa akutizunza ife pamodzi ndi mulungu wathu Dagoni.” 8 Choncho anayitana atsogoleri onse a Afilisti kuti asonkhane ndipo anawafunsa kuti, “Kodi Bokosi la Mulungu wa Israeli tichite nalo chiyani?”Iwo anayankha kuti, “Bokosi la Mulungu wa Israeli lipite ku Gati.” Kotero analichotsa Bokosi la Mulungu wa Israelilo. 9 Koma atafika nalo ku Gati, Yehova analanga mzindawo, ndipo anthu anachita mantha aakulu. Iye anazunza anthu a mu mzindawo, ana ndi akulu omwe, ndi zithupsa. 10 Choncho anatumiza Bokosi la Mulungu ku Ekroni.Koma Bokosi la Mulungu lija litangofika ku Ekroni, anthu a ku Ekroni analira kuti, “Abwera nalo Bokosi la Mulungu wa Israeli kwa ife kuti atiphe pamodzi ndi anthu athu.” 11 Kotero iwo anayitana atsogoleri onse a Afilisti kuti asonkhane ndipo anati, “Chotsani Bokosi la Mulungu wa Israeli, libwerere ku malo ake. Tikapanda kutero lidzatipha ife ndi anthu athu.” Pakuti mu mzinda monse munali mantha aakulu kwambiri ndipo Mulungu ankawalanga kwambiri anthu a kumeneko. 12 Anthu amene sanafe anavutika ndi zithupsa, ndipo kulira kwa anthu a mu mzindamo kunamveka kumwamba.
In Other Versions
1 Samuel 5 in the ANGEFD
1 Samuel 5 in the ANTPNG2D
1 Samuel 5 in the AS21
1 Samuel 5 in the BAGH
1 Samuel 5 in the BBPNG
1 Samuel 5 in the BBT1E
1 Samuel 5 in the BDS
1 Samuel 5 in the BEV
1 Samuel 5 in the BHAD
1 Samuel 5 in the BIB
1 Samuel 5 in the BLPT
1 Samuel 5 in the BNT
1 Samuel 5 in the BNTABOOT
1 Samuel 5 in the BNTLV
1 Samuel 5 in the BOATCB
1 Samuel 5 in the BOATCB2
1 Samuel 5 in the BOBCV
1 Samuel 5 in the BOCNT
1 Samuel 5 in the BOECS
1 Samuel 5 in the BOHCB
1 Samuel 5 in the BOHCV
1 Samuel 5 in the BOHLNT
1 Samuel 5 in the BOHNTLTAL
1 Samuel 5 in the BOICB
1 Samuel 5 in the BOILNTAP
1 Samuel 5 in the BOITCV
1 Samuel 5 in the BOKCV
1 Samuel 5 in the BOKCV2
1 Samuel 5 in the BOKHWOG
1 Samuel 5 in the BOKSSV
1 Samuel 5 in the BOLCB
1 Samuel 5 in the BOLCB2
1 Samuel 5 in the BOMCV
1 Samuel 5 in the BONAV
1 Samuel 5 in the BONCB
1 Samuel 5 in the BONLT
1 Samuel 5 in the BONUT2
1 Samuel 5 in the BOPLNT
1 Samuel 5 in the BOSCB
1 Samuel 5 in the BOSNC
1 Samuel 5 in the BOTLNT
1 Samuel 5 in the BOVCB
1 Samuel 5 in the BOYCB
1 Samuel 5 in the BPBB
1 Samuel 5 in the BPH
1 Samuel 5 in the BSB
1 Samuel 5 in the CCB
1 Samuel 5 in the CUV
1 Samuel 5 in the CUVS
1 Samuel 5 in the DBT
1 Samuel 5 in the DGDNT
1 Samuel 5 in the DHNT
1 Samuel 5 in the DNT
1 Samuel 5 in the ELBE
1 Samuel 5 in the EMTV
1 Samuel 5 in the ESV
1 Samuel 5 in the FBV
1 Samuel 5 in the FEB
1 Samuel 5 in the GGMNT
1 Samuel 5 in the GNT
1 Samuel 5 in the HARY
1 Samuel 5 in the HNT
1 Samuel 5 in the IRVA
1 Samuel 5 in the IRVB
1 Samuel 5 in the IRVG
1 Samuel 5 in the IRVH
1 Samuel 5 in the IRVK
1 Samuel 5 in the IRVM
1 Samuel 5 in the IRVM2
1 Samuel 5 in the IRVO
1 Samuel 5 in the IRVP
1 Samuel 5 in the IRVT
1 Samuel 5 in the IRVT2
1 Samuel 5 in the IRVU
1 Samuel 5 in the ISVN
1 Samuel 5 in the JSNT
1 Samuel 5 in the KAPI
1 Samuel 5 in the KBT1ETNIK
1 Samuel 5 in the KBV
1 Samuel 5 in the KJV
1 Samuel 5 in the KNFD
1 Samuel 5 in the LBA
1 Samuel 5 in the LBLA
1 Samuel 5 in the LNT
1 Samuel 5 in the LSV
1 Samuel 5 in the MAAL
1 Samuel 5 in the MBV
1 Samuel 5 in the MBV2
1 Samuel 5 in the MHNT
1 Samuel 5 in the MKNFD
1 Samuel 5 in the MNG
1 Samuel 5 in the MNT
1 Samuel 5 in the MNT2
1 Samuel 5 in the MRS1T
1 Samuel 5 in the NAA
1 Samuel 5 in the NASB
1 Samuel 5 in the NBLA
1 Samuel 5 in the NBS
1 Samuel 5 in the NBVTP
1 Samuel 5 in the NET2
1 Samuel 5 in the NIV11
1 Samuel 5 in the NNT
1 Samuel 5 in the NNT2
1 Samuel 5 in the NNT3
1 Samuel 5 in the PDDPT
1 Samuel 5 in the PFNT
1 Samuel 5 in the RMNT
1 Samuel 5 in the SBIAS
1 Samuel 5 in the SBIBS
1 Samuel 5 in the SBIBS2
1 Samuel 5 in the SBICS
1 Samuel 5 in the SBIDS
1 Samuel 5 in the SBIGS
1 Samuel 5 in the SBIHS
1 Samuel 5 in the SBIIS
1 Samuel 5 in the SBIIS2
1 Samuel 5 in the SBIIS3
1 Samuel 5 in the SBIKS
1 Samuel 5 in the SBIKS2
1 Samuel 5 in the SBIMS
1 Samuel 5 in the SBIOS
1 Samuel 5 in the SBIPS
1 Samuel 5 in the SBISS
1 Samuel 5 in the SBITS
1 Samuel 5 in the SBITS2
1 Samuel 5 in the SBITS3
1 Samuel 5 in the SBITS4
1 Samuel 5 in the SBIUS
1 Samuel 5 in the SBIVS
1 Samuel 5 in the SBT
1 Samuel 5 in the SBT1E
1 Samuel 5 in the SCHL
1 Samuel 5 in the SNT
1 Samuel 5 in the SUSU
1 Samuel 5 in the SUSU2
1 Samuel 5 in the SYNO
1 Samuel 5 in the TBIAOTANT
1 Samuel 5 in the TBT1E
1 Samuel 5 in the TBT1E2
1 Samuel 5 in the TFTIP
1 Samuel 5 in the TFTU
1 Samuel 5 in the TGNTATF3T
1 Samuel 5 in the THAI
1 Samuel 5 in the TNFD
1 Samuel 5 in the TNT
1 Samuel 5 in the TNTIK
1 Samuel 5 in the TNTIL
1 Samuel 5 in the TNTIN
1 Samuel 5 in the TNTIP
1 Samuel 5 in the TNTIZ
1 Samuel 5 in the TOMA
1 Samuel 5 in the TTENT
1 Samuel 5 in the UBG
1 Samuel 5 in the UGV
1 Samuel 5 in the UGV2
1 Samuel 5 in the UGV3
1 Samuel 5 in the VBL
1 Samuel 5 in the VDCC
1 Samuel 5 in the YALU
1 Samuel 5 in the YAPE
1 Samuel 5 in the YBVTP
1 Samuel 5 in the ZBP