1 Timothy 2 (BOGWICC)

1 Tsono choyamba ndikukupemphani kuti mupempherere anthu onse. Mapemphero anu akhale opemba, opempha, opempherera ena ndi oyamika. 2 Mupempherere mafumu ndi onse aulamuliro, kuti tikhale moyo wamtendere ndi bata, woopa Mulungu ndi oyera mtima. 3 Izi ndi zabwino ndipo zimakondweretsa Mulungu Mpulumutsi wathu, 4 amene amafuna kuti anthu onse apulumutsidwe ndipo kuti adziwe choonadi. 5 Pakuti pali Mulungu mmodzi yekha ndi Mʼkhalapakati mmodzi yekha pakati pa Mulungu ndi anthu, munthu uja Khristu Yesu. 6 Iyeyu anadzipereka kukhala dipo lowombolera anthu onse. Umenewu ndi umboni umene waperekedwa mu nthawi yake yoyenera. 7 Nʼchifukwa chake anandisankha kukhala mlaliki ndiponso mtumwi wophunzitsa anthu a mitundu ina mawu achikhulupiriro choona. Sindikunama ayi, ndikunena zoona. 8 Choncho ndikufuna kuti paliponse popemphera, amuna azikweza manja awo kwa Mulungu mopanda mkwiyo kapena kukangana. 9 Ndikufunanso kuti amayi azivala mwaulemu, modzilemekeza ndi moyenera. Adzikongoletse koma osati ndi tsitsi loluka mowonjeza muyeso kapena zokongoletsa zagolide kapena mikanda yamtengowapatali kapena ndi zovala zamtengowapatali. 10 Koma adzikongoletse ndi ntchito zabwino zoyenera mayi wopembedza Mulungu. 11 Amayi azikhala chete pophunzitsidwa ndi mtima ogonjera kwathunthu. 12 Ine sindikulola kuti amayi aziphunzitsa kapena kulamulira amuna; koma akhale chete. 13 Pakuti Adamu ndiye anayamba kupangidwa kenaka Hava. 14 Ndipo Adamu si amene ananyengedwa koma mkazi ndiye amene ananyengedwa nachimwa. 15 Ndipo mkazi adzapulumutsidwa pobereka mwana ngati apitiriza kukhala mʼchikhulupiriro, mʼchikondi ndi mʼkuyera mtima pamodzi ndi kudzichepetsa konse.

In Other Versions

1 Timothy 2 in the ANGEFD

1 Timothy 2 in the ANTPNG2D

1 Timothy 2 in the AS21

1 Timothy 2 in the BAGH

1 Timothy 2 in the BBPNG

1 Timothy 2 in the BBT1E

1 Timothy 2 in the BDS

1 Timothy 2 in the BEV

1 Timothy 2 in the BHAD

1 Timothy 2 in the BIB

1 Timothy 2 in the BLPT

1 Timothy 2 in the BNT

1 Timothy 2 in the BNTABOOT

1 Timothy 2 in the BNTLV

1 Timothy 2 in the BOATCB

1 Timothy 2 in the BOATCB2

1 Timothy 2 in the BOBCV

1 Timothy 2 in the BOCNT

1 Timothy 2 in the BOECS

1 Timothy 2 in the BOHCB

1 Timothy 2 in the BOHCV

1 Timothy 2 in the BOHLNT

1 Timothy 2 in the BOHNTLTAL

1 Timothy 2 in the BOICB

1 Timothy 2 in the BOILNTAP

1 Timothy 2 in the BOITCV

1 Timothy 2 in the BOKCV

1 Timothy 2 in the BOKCV2

1 Timothy 2 in the BOKHWOG

1 Timothy 2 in the BOKSSV

1 Timothy 2 in the BOLCB

1 Timothy 2 in the BOLCB2

1 Timothy 2 in the BOMCV

1 Timothy 2 in the BONAV

1 Timothy 2 in the BONCB

1 Timothy 2 in the BONLT

1 Timothy 2 in the BONUT2

1 Timothy 2 in the BOPLNT

1 Timothy 2 in the BOSCB

1 Timothy 2 in the BOSNC

1 Timothy 2 in the BOTLNT

1 Timothy 2 in the BOVCB

1 Timothy 2 in the BOYCB

1 Timothy 2 in the BPBB

1 Timothy 2 in the BPH

1 Timothy 2 in the BSB

1 Timothy 2 in the CCB

1 Timothy 2 in the CUV

1 Timothy 2 in the CUVS

1 Timothy 2 in the DBT

1 Timothy 2 in the DGDNT

1 Timothy 2 in the DHNT

1 Timothy 2 in the DNT

1 Timothy 2 in the ELBE

1 Timothy 2 in the EMTV

1 Timothy 2 in the ESV

1 Timothy 2 in the FBV

1 Timothy 2 in the FEB

1 Timothy 2 in the GGMNT

1 Timothy 2 in the GNT

1 Timothy 2 in the HARY

1 Timothy 2 in the HNT

1 Timothy 2 in the IRVA

1 Timothy 2 in the IRVB

1 Timothy 2 in the IRVG

1 Timothy 2 in the IRVH

1 Timothy 2 in the IRVK

1 Timothy 2 in the IRVM

1 Timothy 2 in the IRVM2

1 Timothy 2 in the IRVO

1 Timothy 2 in the IRVP

1 Timothy 2 in the IRVT

1 Timothy 2 in the IRVT2

1 Timothy 2 in the IRVU

1 Timothy 2 in the ISVN

1 Timothy 2 in the JSNT

1 Timothy 2 in the KAPI

1 Timothy 2 in the KBT1ETNIK

1 Timothy 2 in the KBV

1 Timothy 2 in the KJV

1 Timothy 2 in the KNFD

1 Timothy 2 in the LBA

1 Timothy 2 in the LBLA

1 Timothy 2 in the LNT

1 Timothy 2 in the LSV

1 Timothy 2 in the MAAL

1 Timothy 2 in the MBV

1 Timothy 2 in the MBV2

1 Timothy 2 in the MHNT

1 Timothy 2 in the MKNFD

1 Timothy 2 in the MNG

1 Timothy 2 in the MNT

1 Timothy 2 in the MNT2

1 Timothy 2 in the MRS1T

1 Timothy 2 in the NAA

1 Timothy 2 in the NASB

1 Timothy 2 in the NBLA

1 Timothy 2 in the NBS

1 Timothy 2 in the NBVTP

1 Timothy 2 in the NET2

1 Timothy 2 in the NIV11

1 Timothy 2 in the NNT

1 Timothy 2 in the NNT2

1 Timothy 2 in the NNT3

1 Timothy 2 in the PDDPT

1 Timothy 2 in the PFNT

1 Timothy 2 in the RMNT

1 Timothy 2 in the SBIAS

1 Timothy 2 in the SBIBS

1 Timothy 2 in the SBIBS2

1 Timothy 2 in the SBICS

1 Timothy 2 in the SBIDS

1 Timothy 2 in the SBIGS

1 Timothy 2 in the SBIHS

1 Timothy 2 in the SBIIS

1 Timothy 2 in the SBIIS2

1 Timothy 2 in the SBIIS3

1 Timothy 2 in the SBIKS

1 Timothy 2 in the SBIKS2

1 Timothy 2 in the SBIMS

1 Timothy 2 in the SBIOS

1 Timothy 2 in the SBIPS

1 Timothy 2 in the SBISS

1 Timothy 2 in the SBITS

1 Timothy 2 in the SBITS2

1 Timothy 2 in the SBITS3

1 Timothy 2 in the SBITS4

1 Timothy 2 in the SBIUS

1 Timothy 2 in the SBIVS

1 Timothy 2 in the SBT

1 Timothy 2 in the SBT1E

1 Timothy 2 in the SCHL

1 Timothy 2 in the SNT

1 Timothy 2 in the SUSU

1 Timothy 2 in the SUSU2

1 Timothy 2 in the SYNO

1 Timothy 2 in the TBIAOTANT

1 Timothy 2 in the TBT1E

1 Timothy 2 in the TBT1E2

1 Timothy 2 in the TFTIP

1 Timothy 2 in the TFTU

1 Timothy 2 in the TGNTATF3T

1 Timothy 2 in the THAI

1 Timothy 2 in the TNFD

1 Timothy 2 in the TNT

1 Timothy 2 in the TNTIK

1 Timothy 2 in the TNTIL

1 Timothy 2 in the TNTIN

1 Timothy 2 in the TNTIP

1 Timothy 2 in the TNTIZ

1 Timothy 2 in the TOMA

1 Timothy 2 in the TTENT

1 Timothy 2 in the UBG

1 Timothy 2 in the UGV

1 Timothy 2 in the UGV2

1 Timothy 2 in the UGV3

1 Timothy 2 in the VBL

1 Timothy 2 in the VDCC

1 Timothy 2 in the YALU

1 Timothy 2 in the YAPE

1 Timothy 2 in the YBVTP

1 Timothy 2 in the ZBP