2 Chronicles 4 (BOGWICC)

1 Solomoni anapanga guwa lamkuwa limene mulitali mwake linali mamita asanu ndi anayi, mulifupi mwakenso mamita asanu ndi anayi ndipo msinkhu wake unali mamita anayi ndi theka. 2 Kenaka iye anapanga mbiya yayikulu yachitsulo. Inali yozungulira ndipo pakamwa pake panali pa mamita anayi ndi theka, poyeza modutsa pakati pake. Msinkhu wake unali wopitirirapo mamita awiri. Thunthu lake linali mamita 13. 3 Mʼmunsi mwa mkombero wa mbiyayo anajambulamo zithunzi zangʼombe zazimuna mozungulira, zithunzi khumi pa theka la mita. Ngʼombezo zimajambulidwa mʼmizere iwiri ndipo anazipangira kumodzi ndi mbiyayo. 4 Mbiyayo anayisanjika pa ngʼombe zamkuwa khumi ndi ziwiri, zitatu zoyangʼana kumpoto, zitatu zoyangʼana kumadzulo, zitatu zoyangʼana kummwera ndipo zitatu zoyangʼana kummawa. Mbiyayo inakhazikika pamwamba pa ngʼombezo, ndipo miyendo yake yonse yakumbuyo ya ngʼombezo inkaloza mʼkati. 5 Mbiyayo inali yochindikala ngati chikhatho ndipo mkombero wake unali ngati mkombero wa chikho, ngati duwa lokongola kwambiri. Mʼmbiyamo munkalowa madzi okwana malita 60,000. 6 Kenaka anapanga mabeseni khumi otsukira zinthu ndipo asanu amawayika mbali ya kummwera, asanu mbali ya kumpoto. Mʼmenemo amatsukiramo zinthu zimene zimagwiritsidwa ntchito pa nsembe zopsereza koma mbiyamo ndi mʼmene ankasambiramo ansembe. 7 Solomoni anapanga zoyikapo nyale khumi zagolide monga momwe kunalembedwera ndipo anaziyika mʼNyumba ya Mulungu, zisanu mbali ya kummwera, ndi zisanu mbali ya kumpoto. 8 Iye anapanga matebulo khumi ndipo anawayika mʼNyumba ya Mulungu, asanu mbali ya kummwera ndi asanu mbali ya kumpoto. Iye anapanganso mabeseni agolide okwanira 100. 9 Iye anapanga bwalo la ansembe, bwalo lalikulu ndi zitseko za bwalolo ndipo anakuta zitsekozo ndi mkuwa. 10 Anayika mbiya ija mbali yakummwera pamene mbali ya kummawa ndi kummwera zimakumana. 11 Iye anapanganso miphika ndi mafosholo ndi mabeseni owazira magazi.Kotero Hiramu anatsiriza ntchito yonse ya ku Nyumba ya Mulungu imene ankagwirira Mfumu Solomoni: 12 Nsanamira ziwiri;mbale ziwiri za mitu yapamwamba pa nsanamirazo;maukonde awiri okongoletsera mbale ziwiri za mitu yapamwamba pa nsanamirazo; 13 makangadza 400 a maukonde awiri okongoletserawo (mizere iwiri ya makangadza pa ukonde uliwonse, kukongoletsa mbale za mitu yapamwamba pa nsanamira); 14 miyendo pamodzi ndi mabeseni ake; 15 mbiya pamodzi ndi ngʼombe khumi ndi ziwiri zazimuna zosanjikapo mbiyayo. 16 Miphika, mafosholo, mafoloko otengera nyama ndi ziwiya zina zonse. Zipangizo zonse zimene Hiramu Abi anapangira Mfumu Solomoni za mʼNyumba ya Yehova zinali zamkuwa wonyezimira. 17 Mfumu inapangitsa zimenezi mʼchigwa cha Yorodani, ku malo amtapo amene anali pakati pa Sukoti ndi Zaretani. 18 Zinthu zonse zimene Solomoni anapanga zinali zochuluka kwambiri kotero kuti kulemera kwa mkuwa sikunadziwike. 19 Solomoni anapanganso ziwiya zonse zimene zinali mʼNyumba ya Mulungu: guwa lansembe lagolide;matebulo pamene ankayikapo buledi woperekedwa kwa Mulungu; 20 zoyikapo nyale zagolide ndi nyale zake zagolide weniweni, kuti ziziyaka mʼkati mwenimweni mwa malo opatulika monga analembera, 21 maluwa agolide, nyale ndi mbaniro. (Zinali zagolide mmodzi); 22 zozimitsira nyale zagolide weniweni, mbale zowazira magazi, mbale ndi zofukizira; ndiponso zitseko zagolide za Nyumba ya Mulungu, chitseko cha ku Malo Opatulika Kwambiri ndi zitseko za ku chipinda chachikulu.

In Other Versions

2 Chronicles 4 in the ANGEFD

2 Chronicles 4 in the ANTPNG2D

2 Chronicles 4 in the AS21

2 Chronicles 4 in the BAGH

2 Chronicles 4 in the BBPNG

2 Chronicles 4 in the BBT1E

2 Chronicles 4 in the BDS

2 Chronicles 4 in the BEV

2 Chronicles 4 in the BHAD

2 Chronicles 4 in the BIB

2 Chronicles 4 in the BLPT

2 Chronicles 4 in the BNT

2 Chronicles 4 in the BNTABOOT

2 Chronicles 4 in the BNTLV

2 Chronicles 4 in the BOATCB

2 Chronicles 4 in the BOATCB2

2 Chronicles 4 in the BOBCV

2 Chronicles 4 in the BOCNT

2 Chronicles 4 in the BOECS

2 Chronicles 4 in the BOHCB

2 Chronicles 4 in the BOHCV

2 Chronicles 4 in the BOHLNT

2 Chronicles 4 in the BOHNTLTAL

2 Chronicles 4 in the BOICB

2 Chronicles 4 in the BOILNTAP

2 Chronicles 4 in the BOITCV

2 Chronicles 4 in the BOKCV

2 Chronicles 4 in the BOKCV2

2 Chronicles 4 in the BOKHWOG

2 Chronicles 4 in the BOKSSV

2 Chronicles 4 in the BOLCB

2 Chronicles 4 in the BOLCB2

2 Chronicles 4 in the BOMCV

2 Chronicles 4 in the BONAV

2 Chronicles 4 in the BONCB

2 Chronicles 4 in the BONLT

2 Chronicles 4 in the BONUT2

2 Chronicles 4 in the BOPLNT

2 Chronicles 4 in the BOSCB

2 Chronicles 4 in the BOSNC

2 Chronicles 4 in the BOTLNT

2 Chronicles 4 in the BOVCB

2 Chronicles 4 in the BOYCB

2 Chronicles 4 in the BPBB

2 Chronicles 4 in the BPH

2 Chronicles 4 in the BSB

2 Chronicles 4 in the CCB

2 Chronicles 4 in the CUV

2 Chronicles 4 in the CUVS

2 Chronicles 4 in the DBT

2 Chronicles 4 in the DGDNT

2 Chronicles 4 in the DHNT

2 Chronicles 4 in the DNT

2 Chronicles 4 in the ELBE

2 Chronicles 4 in the EMTV

2 Chronicles 4 in the ESV

2 Chronicles 4 in the FBV

2 Chronicles 4 in the FEB

2 Chronicles 4 in the GGMNT

2 Chronicles 4 in the GNT

2 Chronicles 4 in the HARY

2 Chronicles 4 in the HNT

2 Chronicles 4 in the IRVA

2 Chronicles 4 in the IRVB

2 Chronicles 4 in the IRVG

2 Chronicles 4 in the IRVH

2 Chronicles 4 in the IRVK

2 Chronicles 4 in the IRVM

2 Chronicles 4 in the IRVM2

2 Chronicles 4 in the IRVO

2 Chronicles 4 in the IRVP

2 Chronicles 4 in the IRVT

2 Chronicles 4 in the IRVT2

2 Chronicles 4 in the IRVU

2 Chronicles 4 in the ISVN

2 Chronicles 4 in the JSNT

2 Chronicles 4 in the KAPI

2 Chronicles 4 in the KBT1ETNIK

2 Chronicles 4 in the KBV

2 Chronicles 4 in the KJV

2 Chronicles 4 in the KNFD

2 Chronicles 4 in the LBA

2 Chronicles 4 in the LBLA

2 Chronicles 4 in the LNT

2 Chronicles 4 in the LSV

2 Chronicles 4 in the MAAL

2 Chronicles 4 in the MBV

2 Chronicles 4 in the MBV2

2 Chronicles 4 in the MHNT

2 Chronicles 4 in the MKNFD

2 Chronicles 4 in the MNG

2 Chronicles 4 in the MNT

2 Chronicles 4 in the MNT2

2 Chronicles 4 in the MRS1T

2 Chronicles 4 in the NAA

2 Chronicles 4 in the NASB

2 Chronicles 4 in the NBLA

2 Chronicles 4 in the NBS

2 Chronicles 4 in the NBVTP

2 Chronicles 4 in the NET2

2 Chronicles 4 in the NIV11

2 Chronicles 4 in the NNT

2 Chronicles 4 in the NNT2

2 Chronicles 4 in the NNT3

2 Chronicles 4 in the PDDPT

2 Chronicles 4 in the PFNT

2 Chronicles 4 in the RMNT

2 Chronicles 4 in the SBIAS

2 Chronicles 4 in the SBIBS

2 Chronicles 4 in the SBIBS2

2 Chronicles 4 in the SBICS

2 Chronicles 4 in the SBIDS

2 Chronicles 4 in the SBIGS

2 Chronicles 4 in the SBIHS

2 Chronicles 4 in the SBIIS

2 Chronicles 4 in the SBIIS2

2 Chronicles 4 in the SBIIS3

2 Chronicles 4 in the SBIKS

2 Chronicles 4 in the SBIKS2

2 Chronicles 4 in the SBIMS

2 Chronicles 4 in the SBIOS

2 Chronicles 4 in the SBIPS

2 Chronicles 4 in the SBISS

2 Chronicles 4 in the SBITS

2 Chronicles 4 in the SBITS2

2 Chronicles 4 in the SBITS3

2 Chronicles 4 in the SBITS4

2 Chronicles 4 in the SBIUS

2 Chronicles 4 in the SBIVS

2 Chronicles 4 in the SBT

2 Chronicles 4 in the SBT1E

2 Chronicles 4 in the SCHL

2 Chronicles 4 in the SNT

2 Chronicles 4 in the SUSU

2 Chronicles 4 in the SUSU2

2 Chronicles 4 in the SYNO

2 Chronicles 4 in the TBIAOTANT

2 Chronicles 4 in the TBT1E

2 Chronicles 4 in the TBT1E2

2 Chronicles 4 in the TFTIP

2 Chronicles 4 in the TFTU

2 Chronicles 4 in the TGNTATF3T

2 Chronicles 4 in the THAI

2 Chronicles 4 in the TNFD

2 Chronicles 4 in the TNT

2 Chronicles 4 in the TNTIK

2 Chronicles 4 in the TNTIL

2 Chronicles 4 in the TNTIN

2 Chronicles 4 in the TNTIP

2 Chronicles 4 in the TNTIZ

2 Chronicles 4 in the TOMA

2 Chronicles 4 in the TTENT

2 Chronicles 4 in the UBG

2 Chronicles 4 in the UGV

2 Chronicles 4 in the UGV2

2 Chronicles 4 in the UGV3

2 Chronicles 4 in the VBL

2 Chronicles 4 in the VDCC

2 Chronicles 4 in the YALU

2 Chronicles 4 in the YAPE

2 Chronicles 4 in the YBVTP

2 Chronicles 4 in the ZBP