2 Corinthians 6 (BOGWICC)

1 Pogwira naye ntchito pamodzi, tikukudandaulirani kuti musangolandira chisomo cha Mulungu pachabe. 2 Pakuti akunena kuti,“Pa nthawi yanga yabwino yokomera anthu mtima ndinakumvera,ndipo pa nthawi yopulumutsa ndinakuthandiza.Taonani, ndikukuwuzani kuti, ino ndiyo nthawi yabwino ya Ambuye, lero ndiye tsiku la chipulumutso.” 3 Ife sitikuyika chokhumudwitsa pa njira ya wina aliyense, kuti utumiki wathu usanyozeke. 4 Mʼmalo mwake, mwanjira iliyonse timasonyeza kuti ndife atumiki a Mulungu popirira kwambiri mʼmasautso, mʼzowawa ndi mʼzodetsa nkhawa. 5 Pomenyedwa, kuponyedwa mʼndende ndi mʼzipolowe. Pogwira ntchito mwamphamvu, posagona usiku onse, posowa chakudya; 6 pokhala moyo woyera mtima, pomvetsa zinthu, wokoma mtima ndi wachifundo mwa Mzimu Woyera ndi mwachikondi choonadi 7 ndi poyankhula choonadi mwamphamvu ya Mulungu. Zida zimene zili mʼdzanja lamanja ndi lamanzere ndizo chilungamo. 8 Timatumikira Mulungu ngakhale ena amatinyoza ndi ena amatilemekeza, ena amatinenera chipongwe, enanso amatiyamikira. Ena amatitenga kukhala ngati onena zoona, ndipo enanso amatitenga kukhala ngati onena zabodza. 9 Amatiyesa osadziwika komatu ndife odziwika kwambiri. Amatiyesa wooneka ngati tikufa, koma tikupitirirabe ndi moyo, okanthidwa, koma osaphedwa. 10 Amatiyesa achisoni, koma ndife achimwemwe nthawi zonse, aumphawi, koma olemeretsa ambiri; wopanda kanthu, koma tili ndi zonse. 11 Tayankhula momasuka kwa inu, Akorinto, ndipo tanena zonse za kumtima kwathu. 12 Ife sitikukubisirani chikondi chathu pa inu, koma inu mukubisa chikondi chanu pa ife. 13 Pofuna kufanana zochita ndi kuyankhula monga kwa ana anga, nanunso muzinena za kukhosi kwanu. 14 Musamasenze goli pamodzi ndi osakhulupirira. Kodi pali mgwirizano wanji pakati pa kulungama ndi kusalungama? Kapena kodi pali mgwirizano wanji pakati pa kuwala ndi mdima? 15 Pali mgwirizano wanji pakati pa Khristu ndi Beliyali? Kapena munthu wokhulupirira angayanjane bwanji ndi munthu wosakhulupirira? 16 Pali mgwirizano wanji pakati pa Nyumba ya Mulungu ndi nyumba ya mafano? Popezatu ndife Nyumba ya Mulungu wamoyo. Monga Mulungu wanena kuti,“Ndidzakhala mwa iwondipo ndidzayendayenda pakati pawo,ndipo ndidzakhala Mulungu wawo,ndipo adzakhala anthu anga.” 17 Nʼchifukwa chake“Tulukani pakati pawondi kudzipatula,akutero Ambuye.Musakhudze chodetsedwa chilichonse,ndipo ndidzakulandirani.” 18 Ndipo“Ndidzakhala Atate anu,ndipo inu mudzakhala ana anga aamuna ndi aakazi,akutero Ambuye, Wamphamvuzonse.”

In Other Versions

2 Corinthians 6 in the ANGEFD

2 Corinthians 6 in the ANTPNG2D

2 Corinthians 6 in the AS21

2 Corinthians 6 in the BAGH

2 Corinthians 6 in the BBPNG

2 Corinthians 6 in the BBT1E

2 Corinthians 6 in the BDS

2 Corinthians 6 in the BEV

2 Corinthians 6 in the BHAD

2 Corinthians 6 in the BIB

2 Corinthians 6 in the BLPT

2 Corinthians 6 in the BNT

2 Corinthians 6 in the BNTABOOT

2 Corinthians 6 in the BNTLV

2 Corinthians 6 in the BOATCB

2 Corinthians 6 in the BOATCB2

2 Corinthians 6 in the BOBCV

2 Corinthians 6 in the BOCNT

2 Corinthians 6 in the BOECS

2 Corinthians 6 in the BOHCB

2 Corinthians 6 in the BOHCV

2 Corinthians 6 in the BOHLNT

2 Corinthians 6 in the BOHNTLTAL

2 Corinthians 6 in the BOICB

2 Corinthians 6 in the BOILNTAP

2 Corinthians 6 in the BOITCV

2 Corinthians 6 in the BOKCV

2 Corinthians 6 in the BOKCV2

2 Corinthians 6 in the BOKHWOG

2 Corinthians 6 in the BOKSSV

2 Corinthians 6 in the BOLCB

2 Corinthians 6 in the BOLCB2

2 Corinthians 6 in the BOMCV

2 Corinthians 6 in the BONAV

2 Corinthians 6 in the BONCB

2 Corinthians 6 in the BONLT

2 Corinthians 6 in the BONUT2

2 Corinthians 6 in the BOPLNT

2 Corinthians 6 in the BOSCB

2 Corinthians 6 in the BOSNC

2 Corinthians 6 in the BOTLNT

2 Corinthians 6 in the BOVCB

2 Corinthians 6 in the BOYCB

2 Corinthians 6 in the BPBB

2 Corinthians 6 in the BPH

2 Corinthians 6 in the BSB

2 Corinthians 6 in the CCB

2 Corinthians 6 in the CUV

2 Corinthians 6 in the CUVS

2 Corinthians 6 in the DBT

2 Corinthians 6 in the DGDNT

2 Corinthians 6 in the DHNT

2 Corinthians 6 in the DNT

2 Corinthians 6 in the ELBE

2 Corinthians 6 in the EMTV

2 Corinthians 6 in the ESV

2 Corinthians 6 in the FBV

2 Corinthians 6 in the FEB

2 Corinthians 6 in the GGMNT

2 Corinthians 6 in the GNT

2 Corinthians 6 in the HARY

2 Corinthians 6 in the HNT

2 Corinthians 6 in the IRVA

2 Corinthians 6 in the IRVB

2 Corinthians 6 in the IRVG

2 Corinthians 6 in the IRVH

2 Corinthians 6 in the IRVK

2 Corinthians 6 in the IRVM

2 Corinthians 6 in the IRVM2

2 Corinthians 6 in the IRVO

2 Corinthians 6 in the IRVP

2 Corinthians 6 in the IRVT

2 Corinthians 6 in the IRVT2

2 Corinthians 6 in the IRVU

2 Corinthians 6 in the ISVN

2 Corinthians 6 in the JSNT

2 Corinthians 6 in the KAPI

2 Corinthians 6 in the KBT1ETNIK

2 Corinthians 6 in the KBV

2 Corinthians 6 in the KJV

2 Corinthians 6 in the KNFD

2 Corinthians 6 in the LBA

2 Corinthians 6 in the LBLA

2 Corinthians 6 in the LNT

2 Corinthians 6 in the LSV

2 Corinthians 6 in the MAAL

2 Corinthians 6 in the MBV

2 Corinthians 6 in the MBV2

2 Corinthians 6 in the MHNT

2 Corinthians 6 in the MKNFD

2 Corinthians 6 in the MNG

2 Corinthians 6 in the MNT

2 Corinthians 6 in the MNT2

2 Corinthians 6 in the MRS1T

2 Corinthians 6 in the NAA

2 Corinthians 6 in the NASB

2 Corinthians 6 in the NBLA

2 Corinthians 6 in the NBS

2 Corinthians 6 in the NBVTP

2 Corinthians 6 in the NET2

2 Corinthians 6 in the NIV11

2 Corinthians 6 in the NNT

2 Corinthians 6 in the NNT2

2 Corinthians 6 in the NNT3

2 Corinthians 6 in the PDDPT

2 Corinthians 6 in the PFNT

2 Corinthians 6 in the RMNT

2 Corinthians 6 in the SBIAS

2 Corinthians 6 in the SBIBS

2 Corinthians 6 in the SBIBS2

2 Corinthians 6 in the SBICS

2 Corinthians 6 in the SBIDS

2 Corinthians 6 in the SBIGS

2 Corinthians 6 in the SBIHS

2 Corinthians 6 in the SBIIS

2 Corinthians 6 in the SBIIS2

2 Corinthians 6 in the SBIIS3

2 Corinthians 6 in the SBIKS

2 Corinthians 6 in the SBIKS2

2 Corinthians 6 in the SBIMS

2 Corinthians 6 in the SBIOS

2 Corinthians 6 in the SBIPS

2 Corinthians 6 in the SBISS

2 Corinthians 6 in the SBITS

2 Corinthians 6 in the SBITS2

2 Corinthians 6 in the SBITS3

2 Corinthians 6 in the SBITS4

2 Corinthians 6 in the SBIUS

2 Corinthians 6 in the SBIVS

2 Corinthians 6 in the SBT

2 Corinthians 6 in the SBT1E

2 Corinthians 6 in the SCHL

2 Corinthians 6 in the SNT

2 Corinthians 6 in the SUSU

2 Corinthians 6 in the SUSU2

2 Corinthians 6 in the SYNO

2 Corinthians 6 in the TBIAOTANT

2 Corinthians 6 in the TBT1E

2 Corinthians 6 in the TBT1E2

2 Corinthians 6 in the TFTIP

2 Corinthians 6 in the TFTU

2 Corinthians 6 in the TGNTATF3T

2 Corinthians 6 in the THAI

2 Corinthians 6 in the TNFD

2 Corinthians 6 in the TNT

2 Corinthians 6 in the TNTIK

2 Corinthians 6 in the TNTIL

2 Corinthians 6 in the TNTIN

2 Corinthians 6 in the TNTIP

2 Corinthians 6 in the TNTIZ

2 Corinthians 6 in the TOMA

2 Corinthians 6 in the TTENT

2 Corinthians 6 in the UBG

2 Corinthians 6 in the UGV

2 Corinthians 6 in the UGV2

2 Corinthians 6 in the UGV3

2 Corinthians 6 in the VBL

2 Corinthians 6 in the VDCC

2 Corinthians 6 in the YALU

2 Corinthians 6 in the YAPE

2 Corinthians 6 in the YBVTP

2 Corinthians 6 in the ZBP