Esther 7 (BOGWICC)

1 Choncho mfumu ndi Hamani anabwera kudzadya phwando la mfumukazi Estere. 2 Pa tsiku lachiwiri akumwa vinyo, mfumu inafunsanso kuti, “Kodi iwe mfumukazi Estere, chimene ufuna kupempha nʼchiyani? Chimene uti upemphe ndidzakupatsa. Choncho ukufuna chiyani? Ngakhale utafuna theka la ufumu ndidzakupatsa.” 3 Kenaka mfumukazi Estere anayankha kuti, “Ngati mwandikomera mtima, inu mfumu, ndipo ngati chingakukomereni mfumu, pempho ndi chokhumba changa ndi ichi, mulole kuti ine ndi abale anga tisungidwe tonse ndi moyo. 4 Popeza ine ndi anthu a mtundu wanga tagulitsidwa kuti atiwononge, atiphe ndi kutifafaniziratu. Akanangotigulitsa kokha tikanakhala chete, chifukwa chimene mdani wathuyo akanakupatsani mfumu sibwenzi mutasowa nacho mtendere.” 5 Mfumu Ahasiwero anamufunsa mfumukazi Estere, “Kodi iyeyu ndi ndani ndipo ali kuti amene saopa kuchita chinthu chotere?” 6 Estere anati, “Wotizunza ndiponso mdani wathu! Munthu woyipayo ndi Hamani.”Kenaka Hamani anagwidwa ndi mantha pamaso pa mfumu ndi mfumukazi. 7 Mfumu itakwiya kwambiri inanyamuka pa phwando nipita ku munda wa maluwa wa nyumba yaufumu. Koma Hamani, pozindikira kuti mfumu yaganiza kale kumuchitira choyipa, anatsalira mʼnyumba kupempha Estere kuti apulumutse moyo wake. 8 Mfumu itabwerera kuchokera ku munda wa maluwa wa nyumba yaufumu uja ndi kulowanso mʼchipinda chaphwando, anapeza Hamani atagona chafufumimba pa mpando wa khutagone pomwe Estere anakhalapo.Mfumu inayankhula mokweza kuti, “Kodi afunanso kuvula mfumukazi momukakamiza pamene ine ndili mʼnyumba?”Mfumu isanatsirize kuyankhula mawu awa, atumiki ake anaphimba nkhope ya Hamani. 9 Haribona, mmodzi wa adindo ofulidwa amene ankatumikira mfumu anati, “Mtanda wotalika mamita 23 uli mʼnyumba ya Hamani. Mtandawu, Hamani anapangira Mordekai, uja amene anapulumutsa mfumu ku chiwembu.”Mfumu inati, “Mpachikeni pamenepo!” 10 Choncho anamupachika Hamani pa mtanda umene anakonzera Mordekai. Kenaka mkwiyo wa mfumu unatsika.

In Other Versions

Esther 7 in the ANGEFD

Esther 7 in the ANTPNG2D

Esther 7 in the AS21

Esther 7 in the BAGH

Esther 7 in the BBPNG

Esther 7 in the BBT1E

Esther 7 in the BDS

Esther 7 in the BEV

Esther 7 in the BHAD

Esther 7 in the BIB

Esther 7 in the BLPT

Esther 7 in the BNT

Esther 7 in the BNTABOOT

Esther 7 in the BNTLV

Esther 7 in the BOATCB

Esther 7 in the BOATCB2

Esther 7 in the BOBCV

Esther 7 in the BOCNT

Esther 7 in the BOECS

Esther 7 in the BOHCB

Esther 7 in the BOHCV

Esther 7 in the BOHLNT

Esther 7 in the BOHNTLTAL

Esther 7 in the BOICB

Esther 7 in the BOILNTAP

Esther 7 in the BOITCV

Esther 7 in the BOKCV

Esther 7 in the BOKCV2

Esther 7 in the BOKHWOG

Esther 7 in the BOKSSV

Esther 7 in the BOLCB

Esther 7 in the BOLCB2

Esther 7 in the BOMCV

Esther 7 in the BONAV

Esther 7 in the BONCB

Esther 7 in the BONLT

Esther 7 in the BONUT2

Esther 7 in the BOPLNT

Esther 7 in the BOSCB

Esther 7 in the BOSNC

Esther 7 in the BOTLNT

Esther 7 in the BOVCB

Esther 7 in the BOYCB

Esther 7 in the BPBB

Esther 7 in the BPH

Esther 7 in the BSB

Esther 7 in the CCB

Esther 7 in the CUV

Esther 7 in the CUVS

Esther 7 in the DBT

Esther 7 in the DGDNT

Esther 7 in the DHNT

Esther 7 in the DNT

Esther 7 in the ELBE

Esther 7 in the EMTV

Esther 7 in the ESV

Esther 7 in the FBV

Esther 7 in the FEB

Esther 7 in the GGMNT

Esther 7 in the GNT

Esther 7 in the HARY

Esther 7 in the HNT

Esther 7 in the IRVA

Esther 7 in the IRVB

Esther 7 in the IRVG

Esther 7 in the IRVH

Esther 7 in the IRVK

Esther 7 in the IRVM

Esther 7 in the IRVM2

Esther 7 in the IRVO

Esther 7 in the IRVP

Esther 7 in the IRVT

Esther 7 in the IRVT2

Esther 7 in the IRVU

Esther 7 in the ISVN

Esther 7 in the JSNT

Esther 7 in the KAPI

Esther 7 in the KBT1ETNIK

Esther 7 in the KBV

Esther 7 in the KJV

Esther 7 in the KNFD

Esther 7 in the LBA

Esther 7 in the LBLA

Esther 7 in the LNT

Esther 7 in the LSV

Esther 7 in the MAAL

Esther 7 in the MBV

Esther 7 in the MBV2

Esther 7 in the MHNT

Esther 7 in the MKNFD

Esther 7 in the MNG

Esther 7 in the MNT

Esther 7 in the MNT2

Esther 7 in the MRS1T

Esther 7 in the NAA

Esther 7 in the NASB

Esther 7 in the NBLA

Esther 7 in the NBS

Esther 7 in the NBVTP

Esther 7 in the NET2

Esther 7 in the NIV11

Esther 7 in the NNT

Esther 7 in the NNT2

Esther 7 in the NNT3

Esther 7 in the PDDPT

Esther 7 in the PFNT

Esther 7 in the RMNT

Esther 7 in the SBIAS

Esther 7 in the SBIBS

Esther 7 in the SBIBS2

Esther 7 in the SBICS

Esther 7 in the SBIDS

Esther 7 in the SBIGS

Esther 7 in the SBIHS

Esther 7 in the SBIIS

Esther 7 in the SBIIS2

Esther 7 in the SBIIS3

Esther 7 in the SBIKS

Esther 7 in the SBIKS2

Esther 7 in the SBIMS

Esther 7 in the SBIOS

Esther 7 in the SBIPS

Esther 7 in the SBISS

Esther 7 in the SBITS

Esther 7 in the SBITS2

Esther 7 in the SBITS3

Esther 7 in the SBITS4

Esther 7 in the SBIUS

Esther 7 in the SBIVS

Esther 7 in the SBT

Esther 7 in the SBT1E

Esther 7 in the SCHL

Esther 7 in the SNT

Esther 7 in the SUSU

Esther 7 in the SUSU2

Esther 7 in the SYNO

Esther 7 in the TBIAOTANT

Esther 7 in the TBT1E

Esther 7 in the TBT1E2

Esther 7 in the TFTIP

Esther 7 in the TFTU

Esther 7 in the TGNTATF3T

Esther 7 in the THAI

Esther 7 in the TNFD

Esther 7 in the TNT

Esther 7 in the TNTIK

Esther 7 in the TNTIL

Esther 7 in the TNTIN

Esther 7 in the TNTIP

Esther 7 in the TNTIZ

Esther 7 in the TOMA

Esther 7 in the TTENT

Esther 7 in the UBG

Esther 7 in the UGV

Esther 7 in the UGV2

Esther 7 in the UGV3

Esther 7 in the VBL

Esther 7 in the VDCC

Esther 7 in the YALU

Esther 7 in the YAPE

Esther 7 in the YBVTP

Esther 7 in the ZBP