Genesis 23 (BOGWICC)
1 Sara anakhala ndi moyo zaka 127. 2 Anamwalirira ku Kiriyati-Araba, kumeneku ndi ku Hebroni, mʼdziko la Kanaani, ndipo Abrahamu anapita kukakhuza maliro a Sara, namulirira. 3 Kenaka Abrahamu ananyamuka pamene panali mtembo wa mkazi wakepo kupita kukayankhula ndi anthu a ku Hiti. Ndipo anati, 4 “Ine ndine mlendo wongoyendayenda kwanu kuno. Bwanji mundigulitse malo woti akhale manda kuti ndiyikepo thupi la mkazi wanga.” 5 Anthu a ku Hiti aja anamuyankha Abrahamu kuti, 6 “Tatimverani mbuye wathu, inu ndinu mwana wa mfumu wamkulu pakati pathu. Chonde ikani thupi la mkazi wanu mʼmanda aliwonse amene mungafune. Palibe mmodzi wa ife amene adzakukanizani manda ake kuti musayike mkazi wanu.” 7 Tsono Abrahamu anayimirira naweramira anthu a dziko la Hiti aja 8 nati, “Ngati mwaloladi kuti ndiyike mkazi wanga kuno, ndiye ndimvereni. Mundipemphere kwa Efroni mwana wa Zohari 9 kuti andigulitse phanga la Makipela, limene lili kumapeto kwa munda wake. Mumupemphe kuti andigulitse pamtengo wake ndithu inu mukuona kuti akhale manda.” 10 Pamenepo nʼkuti Efroni Mhiti ali pomwepo pakati pa anthuwo amene anabwera ku chipata cha mzindawo. Ndipo onse akumva anamuyankha Abrahamu 11 nati, “Ayi mbuye wanga tandimverani, ine ndikukupatsani mundawo ndiponso phanga limene lili mʼmenemo. Ndikukupatsani malowa pamaso pa anthu a mtundu wanga. Chonde ikani mtembo wamkazi wanu.” 12 Apo Abrahamu anaweramanso mwaulemu pamaso pa anthu a mʼdzikolo 13 ndipo anthu onse akumva Abrahamu anati kwa Efroni, “Ngati kungatheke, chonde ndimvereni. Ine ndichita kugula mundawu. Landirani ndalama za mundawu kuti ine ndiyike mkazi wanga mʼmenemo.” 14 Koma Efroni anamuyankha Abrahamu nati, 15 “Mundimvere mbuye wanga; mundawo mtengo wake ndi masekeli asiliva okwana 400. Koma zimenezo nʼchiyani pakati pa ine ndi inu? Ikani mtembo wa mkazi wanu.” 16 Abrahamu anavomera mtengo umene ananena Efroni Ahiti onse akumva ndipo anamuwerengera masekeli asiliva okwana 400 monga mwa mtengo wa ndalama umene amalonda a nthawi imeneyo ankagwiritsa ntchito. 17 Choncho munda wa Efroni wa ku Makipela umene unali kufupi ndi Mamre, kuphatikiza munda, phanga linali mʼmenemo pamodzi ndi mitengo yonse ya mʼmundamo, zinaperekedwa 18 kwa Abrahamu ngati chuma chake pamaso pa anthu onse a ku Hiti amene anabwera ku chipata cha mzindawo. 19 Zitatha izi, Abrahamu anayika mkazi wake Sara mʼphanga la mʼmunda wa ku Makipela, kufupi ndi ku Mamre (kumene ndi ku Hebroni) mʼdziko la Kanaani. 20 Choncho Ahiti anapereka munda pamodzi ndi phanga la mʼmenemo kwa Abrahamu kuti akhale manda.
In Other Versions
Genesis 23 in the ANGEFD
Genesis 23 in the ANTPNG2D
Genesis 23 in the AS21
Genesis 23 in the BAGH
Genesis 23 in the BBPNG
Genesis 23 in the BBT1E
Genesis 23 in the BDS
Genesis 23 in the BEV
Genesis 23 in the BHAD
Genesis 23 in the BIB
Genesis 23 in the BLPT
Genesis 23 in the BNT
Genesis 23 in the BNTABOOT
Genesis 23 in the BNTLV
Genesis 23 in the BOATCB
Genesis 23 in the BOATCB2
Genesis 23 in the BOBCV
Genesis 23 in the BOCNT
Genesis 23 in the BOECS
Genesis 23 in the BOHCB
Genesis 23 in the BOHCV
Genesis 23 in the BOHLNT
Genesis 23 in the BOHNTLTAL
Genesis 23 in the BOICB
Genesis 23 in the BOILNTAP
Genesis 23 in the BOITCV
Genesis 23 in the BOKCV
Genesis 23 in the BOKCV2
Genesis 23 in the BOKHWOG
Genesis 23 in the BOKSSV
Genesis 23 in the BOLCB
Genesis 23 in the BOLCB2
Genesis 23 in the BOMCV
Genesis 23 in the BONAV
Genesis 23 in the BONCB
Genesis 23 in the BONLT
Genesis 23 in the BONUT2
Genesis 23 in the BOPLNT
Genesis 23 in the BOSCB
Genesis 23 in the BOSNC
Genesis 23 in the BOTLNT
Genesis 23 in the BOVCB
Genesis 23 in the BOYCB
Genesis 23 in the BPBB
Genesis 23 in the BPH
Genesis 23 in the BSB
Genesis 23 in the CCB
Genesis 23 in the CUV
Genesis 23 in the CUVS
Genesis 23 in the DBT
Genesis 23 in the DGDNT
Genesis 23 in the DHNT
Genesis 23 in the DNT
Genesis 23 in the ELBE
Genesis 23 in the EMTV
Genesis 23 in the ESV
Genesis 23 in the FBV
Genesis 23 in the FEB
Genesis 23 in the GGMNT
Genesis 23 in the GNT
Genesis 23 in the HARY
Genesis 23 in the HNT
Genesis 23 in the IRVA
Genesis 23 in the IRVB
Genesis 23 in the IRVG
Genesis 23 in the IRVH
Genesis 23 in the IRVK
Genesis 23 in the IRVM
Genesis 23 in the IRVM2
Genesis 23 in the IRVO
Genesis 23 in the IRVP
Genesis 23 in the IRVT
Genesis 23 in the IRVT2
Genesis 23 in the IRVU
Genesis 23 in the ISVN
Genesis 23 in the JSNT
Genesis 23 in the KAPI
Genesis 23 in the KBT1ETNIK
Genesis 23 in the KBV
Genesis 23 in the KJV
Genesis 23 in the KNFD
Genesis 23 in the LBA
Genesis 23 in the LBLA
Genesis 23 in the LNT
Genesis 23 in the LSV
Genesis 23 in the MAAL
Genesis 23 in the MBV
Genesis 23 in the MBV2
Genesis 23 in the MHNT
Genesis 23 in the MKNFD
Genesis 23 in the MNG
Genesis 23 in the MNT
Genesis 23 in the MNT2
Genesis 23 in the MRS1T
Genesis 23 in the NAA
Genesis 23 in the NASB
Genesis 23 in the NBLA
Genesis 23 in the NBS
Genesis 23 in the NBVTP
Genesis 23 in the NET2
Genesis 23 in the NIV11
Genesis 23 in the NNT
Genesis 23 in the NNT2
Genesis 23 in the NNT3
Genesis 23 in the PDDPT
Genesis 23 in the PFNT
Genesis 23 in the RMNT
Genesis 23 in the SBIAS
Genesis 23 in the SBIBS
Genesis 23 in the SBIBS2
Genesis 23 in the SBICS
Genesis 23 in the SBIDS
Genesis 23 in the SBIGS
Genesis 23 in the SBIHS
Genesis 23 in the SBIIS
Genesis 23 in the SBIIS2
Genesis 23 in the SBIIS3
Genesis 23 in the SBIKS
Genesis 23 in the SBIKS2
Genesis 23 in the SBIMS
Genesis 23 in the SBIOS
Genesis 23 in the SBIPS
Genesis 23 in the SBISS
Genesis 23 in the SBITS
Genesis 23 in the SBITS2
Genesis 23 in the SBITS3
Genesis 23 in the SBITS4
Genesis 23 in the SBIUS
Genesis 23 in the SBIVS
Genesis 23 in the SBT
Genesis 23 in the SBT1E
Genesis 23 in the SCHL
Genesis 23 in the SNT
Genesis 23 in the SUSU
Genesis 23 in the SUSU2
Genesis 23 in the SYNO
Genesis 23 in the TBIAOTANT
Genesis 23 in the TBT1E
Genesis 23 in the TBT1E2
Genesis 23 in the TFTIP
Genesis 23 in the TFTU
Genesis 23 in the TGNTATF3T
Genesis 23 in the THAI
Genesis 23 in the TNFD
Genesis 23 in the TNT
Genesis 23 in the TNTIK
Genesis 23 in the TNTIL
Genesis 23 in the TNTIN
Genesis 23 in the TNTIP
Genesis 23 in the TNTIZ
Genesis 23 in the TOMA
Genesis 23 in the TTENT
Genesis 23 in the UBG
Genesis 23 in the UGV
Genesis 23 in the UGV2
Genesis 23 in the UGV3
Genesis 23 in the VBL
Genesis 23 in the VDCC
Genesis 23 in the YALU
Genesis 23 in the YAPE
Genesis 23 in the YBVTP
Genesis 23 in the ZBP