Micah 6 (BOGWICC)
1 Tamverani zimene Yehova akunena:“Nyamukani, fotokozani mlandu wanu pamaso pa mapiri;zitunda zimve zimene inu muti muyankhule. 2 Imvani mlandu wa Yehova, inu mapiri;tamverani, maziko amuyaya a dziko lapansi.Pakuti Yehova ali ndi mlandu ndi anthu ake;Iye akutsutsa Aisraeli. 3 “Anthu anga, kodi ndakuchitirani chiyani?Kodi ndakutopetsani bwanji? Ndiyankheni. 4 Ine ndinakutulutsani ku dziko la Iguptondi kukuwombolani ku nyumba ya ukapolo.Ndinatuma Mose kuti akutsogolereni,pamodzi ndi Aaroni ndi Miriamu. 5 Anthu anga, kumbukiranizimene Balaki mfumu ya ku Mowabu inafuna kukuchitiranindiponso zimene Balaamu mwana wa Beori anayankha.Kumbukirani zomwe zinachitika pa ulendo wochoka ku Sitimu kupita ku Giligala,kuti mudziwe machitidwe olungama a Yehova.” 6 Kodi ndidzatenga chiyani kupita nacho pamaso pa Yehovandi kukagwada pamaso pa Mulungu wakumwamba?Kodi ndidzabwera pamaso pake ndi nsembe yopsereza,ndi ana angʼombe a chaka chimodzi? 7 Kodi Yehova adzakondwera ndi nkhosa zazimuna 1,000,kapena ndi mitsinje yosalekeza ya mafuta?Kodi ndipereke nsembe mwana wanga woyamba kubadwa chifukwa cha zolakwa zanga?Chipatso cha thupi langa chifukwa cha tchimo la moyo wanga? 8 Munthu iwe, Yehova wakuonetsa kale chimene chili chabwino.Tsono kodi Yehova akuyembekezera chiyani kwa iwe?Uzichita zolungama ndi kukonda chifundondiponso kuyenda modzichepetsa pamaso pa Mulungu wako. 9 Tamverani! Yehova akuyitana anthu okhala mu mzindandi nzeru kuopa dzina lanu.“Mverani mfumu ndi Iye amene anayikhazikitsa. 10 Inu anthu oyipa, kodi Ine nʼkuyiwalachuma chanu chimene munachipeza mwachinyengo,ndiponso muyeso wanu woperewera umene ndi wotembereredwa? 11 Kodi ndimutenge ngati wosalakwa munthu amene ali ndi sikelo yachinyengo,ndiponso miyeso yabodza mʼthumba lake? 12 Anthu ake olemera amachita zachiwawa;anthu ake ndi abodzandipo pakamwa pawo pamayankhula zachinyengo. 13 Choncho, ndayamba kukuwonongani,kukusakazani chifukwa cha machimo anu. 14 Mudzadya, koma simudzakhuta;mudzakhalabe ndi njala.Mudzasunga zinthu, koma sizidzasungika,chifukwa zimene mudzasunga zidzawonongedwa ndi lupanga. 15 Mudzadzala, koma simudzakolola.Mudzayenga mafuta a olivi, koma simudzawagwiritsa ntchito.Mudzaponda mphesa, koma simudzamwa vinyo wake. 16 Inu mwatsatira malangizo a Omurindiponso machitidwe onse a banja la Ahabu,ndi khalidwe lawo lonse.Choncho Ine ndidzakuperekani kuti muwonongedwendiponso anthu anu kuti azunguzike mitu;mudzanyozedwa ndi anthu a mitundu ina.”
In Other Versions
Micah 6 in the ANGEFD
Micah 6 in the ANTPNG2D
Micah 6 in the AS21
Micah 6 in the BAGH
Micah 6 in the BBPNG
Micah 6 in the BBT1E
Micah 6 in the BDS
Micah 6 in the BEV
Micah 6 in the BHAD
Micah 6 in the BIB
Micah 6 in the BLPT
Micah 6 in the BNT
Micah 6 in the BNTABOOT
Micah 6 in the BNTLV
Micah 6 in the BOATCB
Micah 6 in the BOATCB2
Micah 6 in the BOBCV
Micah 6 in the BOCNT
Micah 6 in the BOECS
Micah 6 in the BOHCB
Micah 6 in the BOHCV
Micah 6 in the BOHLNT
Micah 6 in the BOHNTLTAL
Micah 6 in the BOICB
Micah 6 in the BOILNTAP
Micah 6 in the BOITCV
Micah 6 in the BOKCV
Micah 6 in the BOKCV2
Micah 6 in the BOKHWOG
Micah 6 in the BOKSSV
Micah 6 in the BOLCB
Micah 6 in the BOLCB2
Micah 6 in the BOMCV
Micah 6 in the BONAV
Micah 6 in the BONCB
Micah 6 in the BONLT
Micah 6 in the BONUT2
Micah 6 in the BOPLNT
Micah 6 in the BOSCB
Micah 6 in the BOSNC
Micah 6 in the BOTLNT
Micah 6 in the BOVCB
Micah 6 in the BOYCB
Micah 6 in the BPBB
Micah 6 in the BPH
Micah 6 in the BSB
Micah 6 in the CCB
Micah 6 in the CUV
Micah 6 in the CUVS
Micah 6 in the DBT
Micah 6 in the DGDNT
Micah 6 in the DHNT
Micah 6 in the DNT
Micah 6 in the ELBE
Micah 6 in the EMTV
Micah 6 in the ESV
Micah 6 in the FBV
Micah 6 in the FEB
Micah 6 in the GGMNT
Micah 6 in the GNT
Micah 6 in the HARY
Micah 6 in the HNT
Micah 6 in the IRVA
Micah 6 in the IRVB
Micah 6 in the IRVG
Micah 6 in the IRVH
Micah 6 in the IRVK
Micah 6 in the IRVM
Micah 6 in the IRVM2
Micah 6 in the IRVO
Micah 6 in the IRVP
Micah 6 in the IRVT
Micah 6 in the IRVT2
Micah 6 in the IRVU
Micah 6 in the ISVN
Micah 6 in the JSNT
Micah 6 in the KAPI
Micah 6 in the KBT1ETNIK
Micah 6 in the KBV
Micah 6 in the KJV
Micah 6 in the KNFD
Micah 6 in the LBA
Micah 6 in the LBLA
Micah 6 in the LNT
Micah 6 in the LSV
Micah 6 in the MAAL
Micah 6 in the MBV
Micah 6 in the MBV2
Micah 6 in the MHNT
Micah 6 in the MKNFD
Micah 6 in the MNG
Micah 6 in the MNT
Micah 6 in the MNT2
Micah 6 in the MRS1T
Micah 6 in the NAA
Micah 6 in the NASB
Micah 6 in the NBLA
Micah 6 in the NBS
Micah 6 in the NBVTP
Micah 6 in the NET2
Micah 6 in the NIV11
Micah 6 in the NNT
Micah 6 in the NNT2
Micah 6 in the NNT3
Micah 6 in the PDDPT
Micah 6 in the PFNT
Micah 6 in the RMNT
Micah 6 in the SBIAS
Micah 6 in the SBIBS
Micah 6 in the SBIBS2
Micah 6 in the SBICS
Micah 6 in the SBIDS
Micah 6 in the SBIGS
Micah 6 in the SBIHS
Micah 6 in the SBIIS
Micah 6 in the SBIIS2
Micah 6 in the SBIIS3
Micah 6 in the SBIKS
Micah 6 in the SBIKS2
Micah 6 in the SBIMS
Micah 6 in the SBIOS
Micah 6 in the SBIPS
Micah 6 in the SBISS
Micah 6 in the SBITS
Micah 6 in the SBITS2
Micah 6 in the SBITS3
Micah 6 in the SBITS4
Micah 6 in the SBIUS
Micah 6 in the SBIVS
Micah 6 in the SBT
Micah 6 in the SBT1E
Micah 6 in the SCHL
Micah 6 in the SNT
Micah 6 in the SUSU
Micah 6 in the SUSU2
Micah 6 in the SYNO
Micah 6 in the TBIAOTANT
Micah 6 in the TBT1E
Micah 6 in the TBT1E2
Micah 6 in the TFTIP
Micah 6 in the TFTU
Micah 6 in the TGNTATF3T
Micah 6 in the THAI
Micah 6 in the TNFD
Micah 6 in the TNT
Micah 6 in the TNTIK
Micah 6 in the TNTIL
Micah 6 in the TNTIN
Micah 6 in the TNTIP
Micah 6 in the TNTIZ
Micah 6 in the TOMA
Micah 6 in the TTENT
Micah 6 in the UBG
Micah 6 in the UGV
Micah 6 in the UGV2
Micah 6 in the UGV3
Micah 6 in the VBL
Micah 6 in the VDCC
Micah 6 in the YALU
Micah 6 in the YAPE
Micah 6 in the YBVTP
Micah 6 in the ZBP