Psalms 117 (BOGWICC)
1 Tamandani Yehova, inu anthu a mitundu yonse;mulemekezeni Iye, inu mitundu ya anthu. 2 Pakuti chikondi chake pa ife ndi chachikulu,ndipo kukhulupirika kwa Yehova nʼkosatha. Tamandani Yehova.