1 Corinthians 16 (BOGWICC)

1 Tsopano za zopereka zothandiza anthu a Ambuye a ku Yerusalemu. Muchite zomwe ndinawuza mipingo ya ku Galatiya kuti ichite. 2 Pa tsiku loyamba la sabata lililonse, aliyense wa inu azipatula ndalama molingana ndi zomwe wapezera. Asunge, kuti ndikabwera pasadzakhalenso msonkhamsonkha. 3 Pamenepo, ndikadzafika, ndidzawapatsa makalata a umboni anthu amene mudzawasankhe ndi kuwatuma kuti akapereka mphatso zanu ku Yerusalemu. 4 Ngati kutaoneka kuti nʼkoyenera kuti ndipite nawo, adzapita nane limodzi. 5 Ndidzafika kwanuko nditadutsa ku Makedoniya pakuti ndikuyembekezera kudzera ku Makedoniyako. 6 Mwina ndidzakhala nanu kanthawi kochepa kapenanso nyengo yonse yozizira, kuti mudzandithandize kupitiriza ulendo wanga kulikonse kumene ndingapite. 7 Sindikufuna kuti ndikuoneni tsopano mongodutsa chabe, koma ndikuyembekezera kudzakhala nanu kwa kanthawi, ngati Ambuye alola. 8 Koma ndikhala ndili ku Efeso mpaka nthawi ya Pentekosite, 9 pakuti mwayi waukulu wapezeka woti nʼkugwira ntchito yaphindu, koma pali ambiri amene akutsutsana nane. 10 Ngati Timoteyo afike kwanuko, onetsetsani kuti pasakhale zina zomuchititsa mantha pamene ali pakati panu, pakuti iye akugwira ntchito ya Ambuye monga ine. 11 Wina aliyense asamunyoze. Muthandizeni kupitiriza ulendo wake mwamtendere kubwereranso kuli ine. Ndikumuyembekeza pamodzi ndi abale ena. 12 Tsono kunena za mʼbale wathu, Apolo, ndinamuwumiriza kwambiri kuti abwere kwa inu abale, ndipo iye sanafune kupita tsopano. Koma akadzapeza mpata wabwino adzabwera. 13 Khalani tcheru; khazikikani mʼchikhulupiriro chanu; limbani mtima; khalani amphamvu. 14 Chitani zonse mwachikondi. 15 Mukudziwa kuti a mʼbanja la Stefano ndiye anali oyamba kutembenuka mtima ku Akaya, ndipo akhala akudzipereka kutumikira oyera mtima. Choncho ndikukudandaulirani, inu abale, 16 kuti muziwamvera anthu oterewa, ndiponso aliyense wogwira nawo ntchitoyi modzipereka. 17 Ndikondwera kuti Stefano, Fortunato ndi Akayiko afika, chifukwa akhala akundithandiza pakuti inu simuli nane. 18 Pakuti anatsitsimutsa mzimu wanga ndi wanu womwe. Anthu a mtundu oterewa ngofunika kuwalemekeza. 19 Mpingo wa mʼchigawo cha ku Asiya ukupereka moni. Akula ndi Prisila akuperekanso moni wachisangalalo, mwa Ambuye, ndiponso mpingo umene umakumana mʼnyumba mwawo ukupereka moni. 20 Abale onse kuno akupereka moni wawo. Patsanani moni wachikondi chenicheni. 21 Ineyo Paulo, ndikulemba ndi dzanja langa mawu awa akuti moni. 22 Ngati wina sakonda Ambuye akhale wotembereredwa. Maranatha! (Ambuye athu bwerani)! 23 Chisomo cha Ambuye Yesu chikhale ndi inu. 24 Chikondi changa chikhale ndi nonsenu mwa Khristu Yesu.

In Other Versions

1 Corinthians 16 in the ANGEFD

1 Corinthians 16 in the ANTPNG2D

1 Corinthians 16 in the AS21

1 Corinthians 16 in the BAGH

1 Corinthians 16 in the BBPNG

1 Corinthians 16 in the BBT1E

1 Corinthians 16 in the BDS

1 Corinthians 16 in the BEV

1 Corinthians 16 in the BHAD

1 Corinthians 16 in the BIB

1 Corinthians 16 in the BLPT

1 Corinthians 16 in the BNT

1 Corinthians 16 in the BNTABOOT

1 Corinthians 16 in the BNTLV

1 Corinthians 16 in the BOATCB

1 Corinthians 16 in the BOATCB2

1 Corinthians 16 in the BOBCV

1 Corinthians 16 in the BOCNT

1 Corinthians 16 in the BOECS

1 Corinthians 16 in the BOHCB

1 Corinthians 16 in the BOHCV

1 Corinthians 16 in the BOHLNT

1 Corinthians 16 in the BOHNTLTAL

1 Corinthians 16 in the BOICB

1 Corinthians 16 in the BOILNTAP

1 Corinthians 16 in the BOITCV

1 Corinthians 16 in the BOKCV

1 Corinthians 16 in the BOKCV2

1 Corinthians 16 in the BOKHWOG

1 Corinthians 16 in the BOKSSV

1 Corinthians 16 in the BOLCB

1 Corinthians 16 in the BOLCB2

1 Corinthians 16 in the BOMCV

1 Corinthians 16 in the BONAV

1 Corinthians 16 in the BONCB

1 Corinthians 16 in the BONLT

1 Corinthians 16 in the BONUT2

1 Corinthians 16 in the BOPLNT

1 Corinthians 16 in the BOSCB

1 Corinthians 16 in the BOSNC

1 Corinthians 16 in the BOTLNT

1 Corinthians 16 in the BOVCB

1 Corinthians 16 in the BOYCB

1 Corinthians 16 in the BPBB

1 Corinthians 16 in the BPH

1 Corinthians 16 in the BSB

1 Corinthians 16 in the CCB

1 Corinthians 16 in the CUV

1 Corinthians 16 in the CUVS

1 Corinthians 16 in the DBT

1 Corinthians 16 in the DGDNT

1 Corinthians 16 in the DHNT

1 Corinthians 16 in the DNT

1 Corinthians 16 in the ELBE

1 Corinthians 16 in the EMTV

1 Corinthians 16 in the ESV

1 Corinthians 16 in the FBV

1 Corinthians 16 in the FEB

1 Corinthians 16 in the GGMNT

1 Corinthians 16 in the GNT

1 Corinthians 16 in the HARY

1 Corinthians 16 in the HNT

1 Corinthians 16 in the IRVA

1 Corinthians 16 in the IRVB

1 Corinthians 16 in the IRVG

1 Corinthians 16 in the IRVH

1 Corinthians 16 in the IRVK

1 Corinthians 16 in the IRVM

1 Corinthians 16 in the IRVM2

1 Corinthians 16 in the IRVO

1 Corinthians 16 in the IRVP

1 Corinthians 16 in the IRVT

1 Corinthians 16 in the IRVT2

1 Corinthians 16 in the IRVU

1 Corinthians 16 in the ISVN

1 Corinthians 16 in the JSNT

1 Corinthians 16 in the KAPI

1 Corinthians 16 in the KBT1ETNIK

1 Corinthians 16 in the KBV

1 Corinthians 16 in the KJV

1 Corinthians 16 in the KNFD

1 Corinthians 16 in the LBA

1 Corinthians 16 in the LBLA

1 Corinthians 16 in the LNT

1 Corinthians 16 in the LSV

1 Corinthians 16 in the MAAL

1 Corinthians 16 in the MBV

1 Corinthians 16 in the MBV2

1 Corinthians 16 in the MHNT

1 Corinthians 16 in the MKNFD

1 Corinthians 16 in the MNG

1 Corinthians 16 in the MNT

1 Corinthians 16 in the MNT2

1 Corinthians 16 in the MRS1T

1 Corinthians 16 in the NAA

1 Corinthians 16 in the NASB

1 Corinthians 16 in the NBLA

1 Corinthians 16 in the NBS

1 Corinthians 16 in the NBVTP

1 Corinthians 16 in the NET2

1 Corinthians 16 in the NIV11

1 Corinthians 16 in the NNT

1 Corinthians 16 in the NNT2

1 Corinthians 16 in the NNT3

1 Corinthians 16 in the PDDPT

1 Corinthians 16 in the PFNT

1 Corinthians 16 in the RMNT

1 Corinthians 16 in the SBIAS

1 Corinthians 16 in the SBIBS

1 Corinthians 16 in the SBIBS2

1 Corinthians 16 in the SBICS

1 Corinthians 16 in the SBIDS

1 Corinthians 16 in the SBIGS

1 Corinthians 16 in the SBIHS

1 Corinthians 16 in the SBIIS

1 Corinthians 16 in the SBIIS2

1 Corinthians 16 in the SBIIS3

1 Corinthians 16 in the SBIKS

1 Corinthians 16 in the SBIKS2

1 Corinthians 16 in the SBIMS

1 Corinthians 16 in the SBIOS

1 Corinthians 16 in the SBIPS

1 Corinthians 16 in the SBISS

1 Corinthians 16 in the SBITS

1 Corinthians 16 in the SBITS2

1 Corinthians 16 in the SBITS3

1 Corinthians 16 in the SBITS4

1 Corinthians 16 in the SBIUS

1 Corinthians 16 in the SBIVS

1 Corinthians 16 in the SBT

1 Corinthians 16 in the SBT1E

1 Corinthians 16 in the SCHL

1 Corinthians 16 in the SNT

1 Corinthians 16 in the SUSU

1 Corinthians 16 in the SUSU2

1 Corinthians 16 in the SYNO

1 Corinthians 16 in the TBIAOTANT

1 Corinthians 16 in the TBT1E

1 Corinthians 16 in the TBT1E2

1 Corinthians 16 in the TFTIP

1 Corinthians 16 in the TFTU

1 Corinthians 16 in the TGNTATF3T

1 Corinthians 16 in the THAI

1 Corinthians 16 in the TNFD

1 Corinthians 16 in the TNT

1 Corinthians 16 in the TNTIK

1 Corinthians 16 in the TNTIL

1 Corinthians 16 in the TNTIN

1 Corinthians 16 in the TNTIP

1 Corinthians 16 in the TNTIZ

1 Corinthians 16 in the TOMA

1 Corinthians 16 in the TTENT

1 Corinthians 16 in the UBG

1 Corinthians 16 in the UGV

1 Corinthians 16 in the UGV2

1 Corinthians 16 in the UGV3

1 Corinthians 16 in the VBL

1 Corinthians 16 in the VDCC

1 Corinthians 16 in the YALU

1 Corinthians 16 in the YAPE

1 Corinthians 16 in the YBVTP

1 Corinthians 16 in the ZBP