2 Chronicles 15 (BOGWICC)

1 Mzimu wa Mulungu unabwera pa Azariya mwana wa Odedi. 2 Iye anapita kukakumana ndi Asa ndipo anati kwa iye, “Tandimverani, inu Asa ndi Ayuda onse ndi Benjamini. Yehova ali ndi inu, inunso mukakhala naye. Ngati inu mumufunafuna Iye mudzamupeza, koma ngati mumusiya, Iye adzakusiyani. 3 Kwa nthawi yayitali Israeli anali wopanda Mulungu weniweni, wopanda wansembe wophunzitsa ndi wopanda malamulo. 4 Koma pamene anali pa mavuto anatembenukira kwa Yehova, Mulungu wa Israeli ndi kufunafuna Iye, ndipo anamupeza. 5 Masiku amenewo sikunali kwabwino kuyenda ulendo, pakuti anthu onse okhala mʼdziko anali pa mavuto aakulu. 6 Mtundu umodzi umakanthidwa ndi mtundu wina ndipo mzinda wina umakanthidwa ndi mzinda wina, pakuti Mulungu amawasautsa ndi mazunzo a mtundu uliwonse. 7 Koma inu, khalani amphamvu ndipo musataye mtima, pakuti mudzalandira mphotho ya ntchito yanu.” 8 Asa atamva mawu awa ndiponso uneneri wa Azariya mwana wa Odedi, analimba mtima. Iye anachotsa mafano onse onyansa mʼdziko lonse la Yuda ndi Benjamini ndi mʼmizinda yonse imene analanda a ku mapiri a Efereimu. Iye anakonzetsa guwa lansembe la Yehova limene linali kutsogolo kwa khonde la Nyumba ya Mulungu. 9 Kenaka anasonkhanitsa anthu onse a ku Yuda ndi Benjamini ndiponso anthu ochokera ku Efereimu, Manase ndi Simeoni amene ankakhala pakati pawo, pakuti gulu lalikulu linabwera kwa iye kuchokera ku Israeli litaona kuti anali ndi Yehova Mulungu wake. 10 Iwo anasonkhana mu Yerusalemu mwezi wachitatu wa chaka cha 15 cha ulamuliro wa Asa. 11 Pa nthawi imeneyi anapereka nsembe kwa Yehova, ngʼombe 700 ndiponso nkhosa ndi mbuzi 7,000 zochokera pa zolanda ku nkhondo zimene anabweretsa. 12 Iwo anachita pangano loti azifunafuna Yehova, Mulungu wa makolo awo, ndi mtima ndi moyo wawo wonse. 13 Aliyense wosafunafuna Yehova Mulungu wa Israeli aziphedwa, kaya ndi wamngʼono kapena wamkulu, mwamuna kapena mkazi. 14 Iwo analumbira kwa Yehova, mokweza mawu, akuyimba malipenga ndi mbetete. 15 Anthu onse a ku Yuda anakondwera pa kulumbirako chifukwa analumbira ndi mtima wawo wonse. Iwo anafunafuna Mulungu mwachidwi, ndipo anamupeza Iye. Kotero Yehova anawapatsa mpumulo mbali zonse. 16 Mfumu Asa anachotsanso Maaka agogo ake pa udindo wa amayi a mfumu chifukwa anapanga fano lonyansa la Asera. Asa anagwetsa fanolo, naliswa ndipo kenaka anakaliwotcha ku chigwa cha Kidroni. 17 Ngakhale kuti sanachotse malo opembedzerako mafano mu Israeli, mtima wa Asa unali wodzipereka kwathunthu kwa Yehova, masiku onse a moyo wake. 18 Iye anabweretsanso mʼNyumba ya Mulungu zipangizo zasiliva, golide ndi ziwiya zina zimene iyeyo ndi abambo ake anazipatula. 19 Panalibenso nkhondo mpaka chaka cha 35 cha ufumu wa Asa.

In Other Versions

2 Chronicles 15 in the ANGEFD

2 Chronicles 15 in the ANTPNG2D

2 Chronicles 15 in the AS21

2 Chronicles 15 in the BAGH

2 Chronicles 15 in the BBPNG

2 Chronicles 15 in the BBT1E

2 Chronicles 15 in the BDS

2 Chronicles 15 in the BEV

2 Chronicles 15 in the BHAD

2 Chronicles 15 in the BIB

2 Chronicles 15 in the BLPT

2 Chronicles 15 in the BNT

2 Chronicles 15 in the BNTABOOT

2 Chronicles 15 in the BNTLV

2 Chronicles 15 in the BOATCB

2 Chronicles 15 in the BOATCB2

2 Chronicles 15 in the BOBCV

2 Chronicles 15 in the BOCNT

2 Chronicles 15 in the BOECS

2 Chronicles 15 in the BOHCB

2 Chronicles 15 in the BOHCV

2 Chronicles 15 in the BOHLNT

2 Chronicles 15 in the BOHNTLTAL

2 Chronicles 15 in the BOICB

2 Chronicles 15 in the BOILNTAP

2 Chronicles 15 in the BOITCV

2 Chronicles 15 in the BOKCV

2 Chronicles 15 in the BOKCV2

2 Chronicles 15 in the BOKHWOG

2 Chronicles 15 in the BOKSSV

2 Chronicles 15 in the BOLCB

2 Chronicles 15 in the BOLCB2

2 Chronicles 15 in the BOMCV

2 Chronicles 15 in the BONAV

2 Chronicles 15 in the BONCB

2 Chronicles 15 in the BONLT

2 Chronicles 15 in the BONUT2

2 Chronicles 15 in the BOPLNT

2 Chronicles 15 in the BOSCB

2 Chronicles 15 in the BOSNC

2 Chronicles 15 in the BOTLNT

2 Chronicles 15 in the BOVCB

2 Chronicles 15 in the BOYCB

2 Chronicles 15 in the BPBB

2 Chronicles 15 in the BPH

2 Chronicles 15 in the BSB

2 Chronicles 15 in the CCB

2 Chronicles 15 in the CUV

2 Chronicles 15 in the CUVS

2 Chronicles 15 in the DBT

2 Chronicles 15 in the DGDNT

2 Chronicles 15 in the DHNT

2 Chronicles 15 in the DNT

2 Chronicles 15 in the ELBE

2 Chronicles 15 in the EMTV

2 Chronicles 15 in the ESV

2 Chronicles 15 in the FBV

2 Chronicles 15 in the FEB

2 Chronicles 15 in the GGMNT

2 Chronicles 15 in the GNT

2 Chronicles 15 in the HARY

2 Chronicles 15 in the HNT

2 Chronicles 15 in the IRVA

2 Chronicles 15 in the IRVB

2 Chronicles 15 in the IRVG

2 Chronicles 15 in the IRVH

2 Chronicles 15 in the IRVK

2 Chronicles 15 in the IRVM

2 Chronicles 15 in the IRVM2

2 Chronicles 15 in the IRVO

2 Chronicles 15 in the IRVP

2 Chronicles 15 in the IRVT

2 Chronicles 15 in the IRVT2

2 Chronicles 15 in the IRVU

2 Chronicles 15 in the ISVN

2 Chronicles 15 in the JSNT

2 Chronicles 15 in the KAPI

2 Chronicles 15 in the KBT1ETNIK

2 Chronicles 15 in the KBV

2 Chronicles 15 in the KJV

2 Chronicles 15 in the KNFD

2 Chronicles 15 in the LBA

2 Chronicles 15 in the LBLA

2 Chronicles 15 in the LNT

2 Chronicles 15 in the LSV

2 Chronicles 15 in the MAAL

2 Chronicles 15 in the MBV

2 Chronicles 15 in the MBV2

2 Chronicles 15 in the MHNT

2 Chronicles 15 in the MKNFD

2 Chronicles 15 in the MNG

2 Chronicles 15 in the MNT

2 Chronicles 15 in the MNT2

2 Chronicles 15 in the MRS1T

2 Chronicles 15 in the NAA

2 Chronicles 15 in the NASB

2 Chronicles 15 in the NBLA

2 Chronicles 15 in the NBS

2 Chronicles 15 in the NBVTP

2 Chronicles 15 in the NET2

2 Chronicles 15 in the NIV11

2 Chronicles 15 in the NNT

2 Chronicles 15 in the NNT2

2 Chronicles 15 in the NNT3

2 Chronicles 15 in the PDDPT

2 Chronicles 15 in the PFNT

2 Chronicles 15 in the RMNT

2 Chronicles 15 in the SBIAS

2 Chronicles 15 in the SBIBS

2 Chronicles 15 in the SBIBS2

2 Chronicles 15 in the SBICS

2 Chronicles 15 in the SBIDS

2 Chronicles 15 in the SBIGS

2 Chronicles 15 in the SBIHS

2 Chronicles 15 in the SBIIS

2 Chronicles 15 in the SBIIS2

2 Chronicles 15 in the SBIIS3

2 Chronicles 15 in the SBIKS

2 Chronicles 15 in the SBIKS2

2 Chronicles 15 in the SBIMS

2 Chronicles 15 in the SBIOS

2 Chronicles 15 in the SBIPS

2 Chronicles 15 in the SBISS

2 Chronicles 15 in the SBITS

2 Chronicles 15 in the SBITS2

2 Chronicles 15 in the SBITS3

2 Chronicles 15 in the SBITS4

2 Chronicles 15 in the SBIUS

2 Chronicles 15 in the SBIVS

2 Chronicles 15 in the SBT

2 Chronicles 15 in the SBT1E

2 Chronicles 15 in the SCHL

2 Chronicles 15 in the SNT

2 Chronicles 15 in the SUSU

2 Chronicles 15 in the SUSU2

2 Chronicles 15 in the SYNO

2 Chronicles 15 in the TBIAOTANT

2 Chronicles 15 in the TBT1E

2 Chronicles 15 in the TBT1E2

2 Chronicles 15 in the TFTIP

2 Chronicles 15 in the TFTU

2 Chronicles 15 in the TGNTATF3T

2 Chronicles 15 in the THAI

2 Chronicles 15 in the TNFD

2 Chronicles 15 in the TNT

2 Chronicles 15 in the TNTIK

2 Chronicles 15 in the TNTIL

2 Chronicles 15 in the TNTIN

2 Chronicles 15 in the TNTIP

2 Chronicles 15 in the TNTIZ

2 Chronicles 15 in the TOMA

2 Chronicles 15 in the TTENT

2 Chronicles 15 in the UBG

2 Chronicles 15 in the UGV

2 Chronicles 15 in the UGV2

2 Chronicles 15 in the UGV3

2 Chronicles 15 in the VBL

2 Chronicles 15 in the VDCC

2 Chronicles 15 in the YALU

2 Chronicles 15 in the YAPE

2 Chronicles 15 in the YBVTP

2 Chronicles 15 in the ZBP