2 Corinthians 10 (BOGWICC)
1 Mwa kufatsa ndi kuleza mtima kwa Khristu, ndikukupemphani, ine Paulo amene anthu ena amati ndimachita manyazi tikaonana maso ndi maso ndi inu, koma wosaopa pamene ndili kutali nanu! 2 Ndikukupemphani kuti ndikadzafika kumeneko ndisadzachite kuyankhula mwamphamvu monga mmene ndimayembekezera kudzachita kwa anthu ena amene amaganiza kuti machitidwe athu ndi ofanana ndi anthu a dziko lapansi. 3 Ngakhale ife timakhala mʼdziko lapansi, sitimenya nkhondo monga mmene dziko lapansi limachitira. 4 Pakuti zida zathu zankhondo si zida za dziko lapansi. Koma ndi mphamvu zochokera kwa Mulungu zotha kugwetsa malinga. 5 Timagonjetsa maganizo onse onyenga ndiponso kudzikuza kulikonse kolimbana ndi anthu kuti asadziwe Mulungu. Ndipo timagonjetsa ganizo lililonse kuti limvere Khristu. 6 Ndipo ife tidzakhala okonzeka kulanga aliyense wosamvera ngati inuyo mutakhala omvera kwenikweni. 7 Inu mukuweruza potengera zimene maso anu akuona. Ngati wina akutsimikiza kuti ndi wake wa Khristu, iye aganizenso kuti ifenso ndife a Khristu monga iye. 8 Tsono ngakhale nditadzitama momasuka za ulamuliro umene Ambuye anatipatsa woti tikukuzeni osati kukuwonongani, ndithu sindidzachita manyazi. 9 Ine sindikufuna kuoneka ngati ndikukuopsezani ndi makalata anga. 10 Pakuti ena amati, “Makalata ake ndi awukali ndi amphamvu koma maonekedwe a thupi lake ndi wosagwira mtima ndipo mayankhulidwe ake ndi achabechabe.” 11 Anthu oterewa ayenera kuzindikira kuti zomwe timalemba mʼmakalata tili kutali ndi zomwe tidzakhale tili komweko. 12 Sitikudziyika kapena kudzifananiza tokha ndi anthu ena amene amadziyenereza okha. Pamene akudzifanizira okha podziyerekeza ndi anzawo a mʼgulu lawo lomwe, ndi opanda nzeru. 13 Komabe, ifeyo sitidzitama modutsa malire ake enieni, koma kudzitama kwathu kudzalekeza mʼmalire amene Mulungu anatiyikira, malire ake ndi mpaka kwa inu. 14 Pakuti sitikudzitama modutsa malire ngati kuti sitinafike kwa inu, popeza tinali oyamba kufika kwa inu ndi Uthenga Wabwino wa Khristu. 15 Choncho sitinyadiranso ntchito imene ena anayigwira. Chiyembekezo chathu nʼchakuti, pamene chikhulupiriro chanu chikukulirakulira, dera lathu la ntchito pakati panu lidzakulanso kwambiri, 16 kuti tikalalikire Uthenga Wabwino mu zigawo zina kupitirira kwanuko. Pakuti sitikufuna kudzitama pa ntchito yogwira ena kale mʼdera la munthu wina. 17 Koma, “Ngati munthu akufuna kunyadira, anyadire mwa Ambuye.” 18 Pakuti munthu amene amavomerezedwa, si amene amadziyenereza yekha, koma munthu amene Ambuye amuyenereza.
In Other Versions
2 Corinthians 10 in the ANGEFD
2 Corinthians 10 in the ANTPNG2D
2 Corinthians 10 in the AS21
2 Corinthians 10 in the BAGH
2 Corinthians 10 in the BBPNG
2 Corinthians 10 in the BBT1E
2 Corinthians 10 in the BDS
2 Corinthians 10 in the BEV
2 Corinthians 10 in the BHAD
2 Corinthians 10 in the BIB
2 Corinthians 10 in the BLPT
2 Corinthians 10 in the BNT
2 Corinthians 10 in the BNTABOOT
2 Corinthians 10 in the BNTLV
2 Corinthians 10 in the BOATCB
2 Corinthians 10 in the BOATCB2
2 Corinthians 10 in the BOBCV
2 Corinthians 10 in the BOCNT
2 Corinthians 10 in the BOECS
2 Corinthians 10 in the BOHCB
2 Corinthians 10 in the BOHCV
2 Corinthians 10 in the BOHLNT
2 Corinthians 10 in the BOHNTLTAL
2 Corinthians 10 in the BOICB
2 Corinthians 10 in the BOILNTAP
2 Corinthians 10 in the BOITCV
2 Corinthians 10 in the BOKCV
2 Corinthians 10 in the BOKCV2
2 Corinthians 10 in the BOKHWOG
2 Corinthians 10 in the BOKSSV
2 Corinthians 10 in the BOLCB
2 Corinthians 10 in the BOLCB2
2 Corinthians 10 in the BOMCV
2 Corinthians 10 in the BONAV
2 Corinthians 10 in the BONCB
2 Corinthians 10 in the BONLT
2 Corinthians 10 in the BONUT2
2 Corinthians 10 in the BOPLNT
2 Corinthians 10 in the BOSCB
2 Corinthians 10 in the BOSNC
2 Corinthians 10 in the BOTLNT
2 Corinthians 10 in the BOVCB
2 Corinthians 10 in the BOYCB
2 Corinthians 10 in the BPBB
2 Corinthians 10 in the BPH
2 Corinthians 10 in the BSB
2 Corinthians 10 in the CCB
2 Corinthians 10 in the CUV
2 Corinthians 10 in the CUVS
2 Corinthians 10 in the DBT
2 Corinthians 10 in the DGDNT
2 Corinthians 10 in the DHNT
2 Corinthians 10 in the DNT
2 Corinthians 10 in the ELBE
2 Corinthians 10 in the EMTV
2 Corinthians 10 in the ESV
2 Corinthians 10 in the FBV
2 Corinthians 10 in the FEB
2 Corinthians 10 in the GGMNT
2 Corinthians 10 in the GNT
2 Corinthians 10 in the HARY
2 Corinthians 10 in the HNT
2 Corinthians 10 in the IRVA
2 Corinthians 10 in the IRVB
2 Corinthians 10 in the IRVG
2 Corinthians 10 in the IRVH
2 Corinthians 10 in the IRVK
2 Corinthians 10 in the IRVM
2 Corinthians 10 in the IRVM2
2 Corinthians 10 in the IRVO
2 Corinthians 10 in the IRVP
2 Corinthians 10 in the IRVT
2 Corinthians 10 in the IRVT2
2 Corinthians 10 in the IRVU
2 Corinthians 10 in the ISVN
2 Corinthians 10 in the JSNT
2 Corinthians 10 in the KAPI
2 Corinthians 10 in the KBT1ETNIK
2 Corinthians 10 in the KBV
2 Corinthians 10 in the KJV
2 Corinthians 10 in the KNFD
2 Corinthians 10 in the LBA
2 Corinthians 10 in the LBLA
2 Corinthians 10 in the LNT
2 Corinthians 10 in the LSV
2 Corinthians 10 in the MAAL
2 Corinthians 10 in the MBV
2 Corinthians 10 in the MBV2
2 Corinthians 10 in the MHNT
2 Corinthians 10 in the MKNFD
2 Corinthians 10 in the MNG
2 Corinthians 10 in the MNT
2 Corinthians 10 in the MNT2
2 Corinthians 10 in the MRS1T
2 Corinthians 10 in the NAA
2 Corinthians 10 in the NASB
2 Corinthians 10 in the NBLA
2 Corinthians 10 in the NBS
2 Corinthians 10 in the NBVTP
2 Corinthians 10 in the NET2
2 Corinthians 10 in the NIV11
2 Corinthians 10 in the NNT
2 Corinthians 10 in the NNT2
2 Corinthians 10 in the NNT3
2 Corinthians 10 in the PDDPT
2 Corinthians 10 in the PFNT
2 Corinthians 10 in the RMNT
2 Corinthians 10 in the SBIAS
2 Corinthians 10 in the SBIBS
2 Corinthians 10 in the SBIBS2
2 Corinthians 10 in the SBICS
2 Corinthians 10 in the SBIDS
2 Corinthians 10 in the SBIGS
2 Corinthians 10 in the SBIHS
2 Corinthians 10 in the SBIIS
2 Corinthians 10 in the SBIIS2
2 Corinthians 10 in the SBIIS3
2 Corinthians 10 in the SBIKS
2 Corinthians 10 in the SBIKS2
2 Corinthians 10 in the SBIMS
2 Corinthians 10 in the SBIOS
2 Corinthians 10 in the SBIPS
2 Corinthians 10 in the SBISS
2 Corinthians 10 in the SBITS
2 Corinthians 10 in the SBITS2
2 Corinthians 10 in the SBITS3
2 Corinthians 10 in the SBITS4
2 Corinthians 10 in the SBIUS
2 Corinthians 10 in the SBIVS
2 Corinthians 10 in the SBT
2 Corinthians 10 in the SBT1E
2 Corinthians 10 in the SCHL
2 Corinthians 10 in the SNT
2 Corinthians 10 in the SUSU
2 Corinthians 10 in the SUSU2
2 Corinthians 10 in the SYNO
2 Corinthians 10 in the TBIAOTANT
2 Corinthians 10 in the TBT1E
2 Corinthians 10 in the TBT1E2
2 Corinthians 10 in the TFTIP
2 Corinthians 10 in the TFTU
2 Corinthians 10 in the TGNTATF3T
2 Corinthians 10 in the THAI
2 Corinthians 10 in the TNFD
2 Corinthians 10 in the TNT
2 Corinthians 10 in the TNTIK
2 Corinthians 10 in the TNTIL
2 Corinthians 10 in the TNTIN
2 Corinthians 10 in the TNTIP
2 Corinthians 10 in the TNTIZ
2 Corinthians 10 in the TOMA
2 Corinthians 10 in the TTENT
2 Corinthians 10 in the UBG
2 Corinthians 10 in the UGV
2 Corinthians 10 in the UGV2
2 Corinthians 10 in the UGV3
2 Corinthians 10 in the VBL
2 Corinthians 10 in the VDCC
2 Corinthians 10 in the YALU
2 Corinthians 10 in the YAPE
2 Corinthians 10 in the YBVTP
2 Corinthians 10 in the ZBP