2 Corinthians 2 (BOGWICC)

1 Kotero ndinatsimikiza maganizo anga kuti ndisachitenso ulendo wina owawa wobwera kwanuko. 2 Pakuti ngati ndikumvetsani chisoni, kodi angandisangalatse ndani, kupatula inuyo amene ndakumvetsani chisoni? 3 Nʼchifukwa chake ndinakulemberani monga ndinachitiramo kuti nditabwera kwanuko ndisadzamve chisoni ndi anthu oyenera kundisangalatsa. Ndinali ndi chikhulupiriro ndi inu nonse kuti inuyo mukakhala ndi chimwemwe poona kuti inenso ndili ndi chimwemwe. 4 Pakuti ndinakulemberani kalata ija ndili wopsinjika ndi wowawidwa mtima kwambiri ndi kutuluka misozi yambiri, osati pofuna kukumvetsani chisoni koma kuti ndikudziwitseni kuti ndimakukondani kwambiri. 5 Koma ngati wina wamvetsa chisoni, sanamvetse chisoni ine ndekha, koma koposa mosawonjezera wakhumudwitsa nonsenu, kunenatu mosawonjezera. 6 Chilango chimene ambiri a inu mwamupatsa munthu ameneyu nʼchokwanira. 7 Mʼmalo mwake tsono, muyenera kumukhululukira ndi kumulimbikitsa mtima kuti asamve chisoni choposa muyeso, angataye mtima. 8 Choncho ndikukupemphani kuti mutsimikizire chikondi chanu pa iye. 9 Cholinga china chimene ndinakulemberani kalata ija chinali chofuna kukuonani ngati mudzandimvera pa zonse. 10 Aliyense amene mumukhululukire, inenso ndimukhululukira. Ndipo ndikakhululukira, ngati pali kanthu koti ndikhululukire, ndiye kuti ndakhululuka chifukwa cha inu pamaso pa Khristu, 11 kupewa kuti Satana angapezere mpata pa ife, pajatu timadziwa machenjerero ake. 12 Tsono nditafika ku Trowa kuti ndilalikire Uthenga Wabwino wa Khristu, nʼkupeza kuti Ambuye anditsekulira khomo, 13 ndinasowa mtendere mu mtima mwanga, chifukwa sindinapezeko mʼbale wanga Tito. Choncho ndinatsanzikana ndi anthu kumeneko nʼkupita ku Makedoniya. 14 Koma tithokoze Mulungu amene amatitsogolera nthawi zonse monga ogwidwa ku nkhondo a Khristu pa chipambano chake. Tsono amatigwiritsa ntchito yofalitsa ponseponse nzeru zodziwira Khristu ngati fungo labwino. 15 Pakuti kwa Mulungu ndife fungo labwino la Khristu pakati pa iwo amene akupulumutsidwa ndi amene akuwonongeka. 16 Kwa amene akuwonongeka ndife fungo la imfa, limawapha. Ndipo kwa amene akupulumuka ndife fungo lamoyo, limawapatsa moyo. Ndani angayithe ntchito yotereyi? 17 Kusiyana ndi ena ambiri, ife sitilalikira Mawu a Mulungu kuti tipeza phindu. Mʼmalo mwake, ife mwa Khristu timayankhula pamaso pa Mulungu moona mtima, monga anthu otumidwa ndi Mulungu.

In Other Versions

2 Corinthians 2 in the ANGEFD

2 Corinthians 2 in the ANTPNG2D

2 Corinthians 2 in the AS21

2 Corinthians 2 in the BAGH

2 Corinthians 2 in the BBPNG

2 Corinthians 2 in the BBT1E

2 Corinthians 2 in the BDS

2 Corinthians 2 in the BEV

2 Corinthians 2 in the BHAD

2 Corinthians 2 in the BIB

2 Corinthians 2 in the BLPT

2 Corinthians 2 in the BNT

2 Corinthians 2 in the BNTABOOT

2 Corinthians 2 in the BNTLV

2 Corinthians 2 in the BOATCB

2 Corinthians 2 in the BOATCB2

2 Corinthians 2 in the BOBCV

2 Corinthians 2 in the BOCNT

2 Corinthians 2 in the BOECS

2 Corinthians 2 in the BOHCB

2 Corinthians 2 in the BOHCV

2 Corinthians 2 in the BOHLNT

2 Corinthians 2 in the BOHNTLTAL

2 Corinthians 2 in the BOICB

2 Corinthians 2 in the BOILNTAP

2 Corinthians 2 in the BOITCV

2 Corinthians 2 in the BOKCV

2 Corinthians 2 in the BOKCV2

2 Corinthians 2 in the BOKHWOG

2 Corinthians 2 in the BOKSSV

2 Corinthians 2 in the BOLCB

2 Corinthians 2 in the BOLCB2

2 Corinthians 2 in the BOMCV

2 Corinthians 2 in the BONAV

2 Corinthians 2 in the BONCB

2 Corinthians 2 in the BONLT

2 Corinthians 2 in the BONUT2

2 Corinthians 2 in the BOPLNT

2 Corinthians 2 in the BOSCB

2 Corinthians 2 in the BOSNC

2 Corinthians 2 in the BOTLNT

2 Corinthians 2 in the BOVCB

2 Corinthians 2 in the BOYCB

2 Corinthians 2 in the BPBB

2 Corinthians 2 in the BPH

2 Corinthians 2 in the BSB

2 Corinthians 2 in the CCB

2 Corinthians 2 in the CUV

2 Corinthians 2 in the CUVS

2 Corinthians 2 in the DBT

2 Corinthians 2 in the DGDNT

2 Corinthians 2 in the DHNT

2 Corinthians 2 in the DNT

2 Corinthians 2 in the ELBE

2 Corinthians 2 in the EMTV

2 Corinthians 2 in the ESV

2 Corinthians 2 in the FBV

2 Corinthians 2 in the FEB

2 Corinthians 2 in the GGMNT

2 Corinthians 2 in the GNT

2 Corinthians 2 in the HARY

2 Corinthians 2 in the HNT

2 Corinthians 2 in the IRVA

2 Corinthians 2 in the IRVB

2 Corinthians 2 in the IRVG

2 Corinthians 2 in the IRVH

2 Corinthians 2 in the IRVK

2 Corinthians 2 in the IRVM

2 Corinthians 2 in the IRVM2

2 Corinthians 2 in the IRVO

2 Corinthians 2 in the IRVP

2 Corinthians 2 in the IRVT

2 Corinthians 2 in the IRVT2

2 Corinthians 2 in the IRVU

2 Corinthians 2 in the ISVN

2 Corinthians 2 in the JSNT

2 Corinthians 2 in the KAPI

2 Corinthians 2 in the KBT1ETNIK

2 Corinthians 2 in the KBV

2 Corinthians 2 in the KJV

2 Corinthians 2 in the KNFD

2 Corinthians 2 in the LBA

2 Corinthians 2 in the LBLA

2 Corinthians 2 in the LNT

2 Corinthians 2 in the LSV

2 Corinthians 2 in the MAAL

2 Corinthians 2 in the MBV

2 Corinthians 2 in the MBV2

2 Corinthians 2 in the MHNT

2 Corinthians 2 in the MKNFD

2 Corinthians 2 in the MNG

2 Corinthians 2 in the MNT

2 Corinthians 2 in the MNT2

2 Corinthians 2 in the MRS1T

2 Corinthians 2 in the NAA

2 Corinthians 2 in the NASB

2 Corinthians 2 in the NBLA

2 Corinthians 2 in the NBS

2 Corinthians 2 in the NBVTP

2 Corinthians 2 in the NET2

2 Corinthians 2 in the NIV11

2 Corinthians 2 in the NNT

2 Corinthians 2 in the NNT2

2 Corinthians 2 in the NNT3

2 Corinthians 2 in the PDDPT

2 Corinthians 2 in the PFNT

2 Corinthians 2 in the RMNT

2 Corinthians 2 in the SBIAS

2 Corinthians 2 in the SBIBS

2 Corinthians 2 in the SBIBS2

2 Corinthians 2 in the SBICS

2 Corinthians 2 in the SBIDS

2 Corinthians 2 in the SBIGS

2 Corinthians 2 in the SBIHS

2 Corinthians 2 in the SBIIS

2 Corinthians 2 in the SBIIS2

2 Corinthians 2 in the SBIIS3

2 Corinthians 2 in the SBIKS

2 Corinthians 2 in the SBIKS2

2 Corinthians 2 in the SBIMS

2 Corinthians 2 in the SBIOS

2 Corinthians 2 in the SBIPS

2 Corinthians 2 in the SBISS

2 Corinthians 2 in the SBITS

2 Corinthians 2 in the SBITS2

2 Corinthians 2 in the SBITS3

2 Corinthians 2 in the SBITS4

2 Corinthians 2 in the SBIUS

2 Corinthians 2 in the SBIVS

2 Corinthians 2 in the SBT

2 Corinthians 2 in the SBT1E

2 Corinthians 2 in the SCHL

2 Corinthians 2 in the SNT

2 Corinthians 2 in the SUSU

2 Corinthians 2 in the SUSU2

2 Corinthians 2 in the SYNO

2 Corinthians 2 in the TBIAOTANT

2 Corinthians 2 in the TBT1E

2 Corinthians 2 in the TBT1E2

2 Corinthians 2 in the TFTIP

2 Corinthians 2 in the TFTU

2 Corinthians 2 in the TGNTATF3T

2 Corinthians 2 in the THAI

2 Corinthians 2 in the TNFD

2 Corinthians 2 in the TNT

2 Corinthians 2 in the TNTIK

2 Corinthians 2 in the TNTIL

2 Corinthians 2 in the TNTIN

2 Corinthians 2 in the TNTIP

2 Corinthians 2 in the TNTIZ

2 Corinthians 2 in the TOMA

2 Corinthians 2 in the TTENT

2 Corinthians 2 in the UBG

2 Corinthians 2 in the UGV

2 Corinthians 2 in the UGV2

2 Corinthians 2 in the UGV3

2 Corinthians 2 in the VBL

2 Corinthians 2 in the VDCC

2 Corinthians 2 in the YALU

2 Corinthians 2 in the YAPE

2 Corinthians 2 in the YBVTP

2 Corinthians 2 in the ZBP