Colossians 4 (BOGWICC)
1 Mabwana, antchito anu muzikhala nawo mwachilungamo ndi moyenera, podziwa kuti nanunso muli nawo Ambuye anu mmwamba. 2 Pempherani modzipereka, mukhale atcheru ndiponso oyamika. 3 Ndipo muzitipemphereranso ife kuti Mulungu atitsekulire khomo la uthenga wathu, kuti tilalikire chinsinsi cha Khristu, chimene ndine womangidwa nacho mʼndende. 4 Pempherani kuti ndilalikire momveka bwino, monga ndikuyenera. 5 Mayendedwe anu pakati pa akunja, akhale anzeru ndipo mugwiritse ntchito mpata uliwonse umene muli nawo. 6 Mayankhulidwe anu nthawi zonse akhale odzaza ndi chisomo ndi okoma, kuti mudziwe kuyankha aliyense. 7 Tukiko adzakuwuzani zonse za ine. Iye ndi mʼbale wokondedwa, mtumiki wokhulupirika ndiponso wantchito mnzanga mwa Ambuye. 8 Ine ndikumutumiza kwa inu ndi cholinga choti mudziwe zimene tikukumana nazo ndiponso kuti alimbikitse mitima yanu. 9 Iye akubwera ndi Onesimo, mʼbale wathu wokhulupirika ndi wokondedwa, amene ndi mmodzi mwa inu. Iwo adzakuwuzani zonse zimene zikuchitika kuno. 10 Aristariko, wamʼndende mnzanga akupereka moni, Marko akuperekanso moni, msuweni wa Barnaba. (Inu munawuzidwa kale za Iye. Iye akabwera kwanuko, mulandireni). 11 Yesu wotchedwa Yusto, akuperekanso moni. Amenewa ndi Ayuda okhawo pakati pa atumiki anzanga mu ufumu wa Mulungu, ndipo aonetsa kuti ndi chitonthozo kwa ine. 12 Epafra ndi mmodzi mwa inu ndiponso mtumiki wa Khristu Yesu, akupereka moni. Iyeyu nthawi zonse amakupemphererani mwamphamvu, kuti mukhazikike pa chifuniro chonse cha Mulungu, mukhale okhwima ndi otsimikiza kwathunthu. 13 Ine ndikumuchitira umboni kuti amagwira ntchito mwamphamvu chifukwa cha inu ndiponso kwa amene ali ku Laodikaya ndi Herapoli. 14 Luka, dotolo wathu wokondedwa ndi Dema, akupereka moni. 15 Perekani moni kwa abale a ku Laodikaya, ndiponso kwa Numfa ndi mpingo wa mʼnyumba mwake. 16 Kalata iyi ikawerengedwa pakati panu, muonetsetse kuti ikawerengedwenso ku mpingo wa ku Laodikaya ndipo inunso muwerenge kalata yochokera ku Laodikaya. 17 Uzani Arkipo kuti, “Wonetsetsa kuti wamaliza ntchito imene unayilandira mwa Ambuye.” 18 Ine Paulo, ndikulemba ndi dzanja langa moni uwu. Kumbukirani kuti ndili mu unyolo. Chisomo chikhale ndi inu.
In Other Versions
Colossians 4 in the ANGEFD
Colossians 4 in the ANTPNG2D
Colossians 4 in the AS21
Colossians 4 in the BAGH
Colossians 4 in the BBPNG
Colossians 4 in the BBT1E
Colossians 4 in the BDS
Colossians 4 in the BEV
Colossians 4 in the BHAD
Colossians 4 in the BIB
Colossians 4 in the BLPT
Colossians 4 in the BNT
Colossians 4 in the BNTABOOT
Colossians 4 in the BNTLV
Colossians 4 in the BOATCB
Colossians 4 in the BOATCB2
Colossians 4 in the BOBCV
Colossians 4 in the BOCNT
Colossians 4 in the BOECS
Colossians 4 in the BOHCB
Colossians 4 in the BOHCV
Colossians 4 in the BOHLNT
Colossians 4 in the BOHNTLTAL
Colossians 4 in the BOICB
Colossians 4 in the BOILNTAP
Colossians 4 in the BOITCV
Colossians 4 in the BOKCV
Colossians 4 in the BOKCV2
Colossians 4 in the BOKHWOG
Colossians 4 in the BOKSSV
Colossians 4 in the BOLCB
Colossians 4 in the BOLCB2
Colossians 4 in the BOMCV
Colossians 4 in the BONAV
Colossians 4 in the BONCB
Colossians 4 in the BONLT
Colossians 4 in the BONUT2
Colossians 4 in the BOPLNT
Colossians 4 in the BOSCB
Colossians 4 in the BOSNC
Colossians 4 in the BOTLNT
Colossians 4 in the BOVCB
Colossians 4 in the BOYCB
Colossians 4 in the BPBB
Colossians 4 in the BPH
Colossians 4 in the BSB
Colossians 4 in the CCB
Colossians 4 in the CUV
Colossians 4 in the CUVS
Colossians 4 in the DBT
Colossians 4 in the DGDNT
Colossians 4 in the DHNT
Colossians 4 in the DNT
Colossians 4 in the ELBE
Colossians 4 in the EMTV
Colossians 4 in the ESV
Colossians 4 in the FBV
Colossians 4 in the FEB
Colossians 4 in the GGMNT
Colossians 4 in the GNT
Colossians 4 in the HARY
Colossians 4 in the HNT
Colossians 4 in the IRVA
Colossians 4 in the IRVB
Colossians 4 in the IRVG
Colossians 4 in the IRVH
Colossians 4 in the IRVK
Colossians 4 in the IRVM
Colossians 4 in the IRVM2
Colossians 4 in the IRVO
Colossians 4 in the IRVP
Colossians 4 in the IRVT
Colossians 4 in the IRVT2
Colossians 4 in the IRVU
Colossians 4 in the ISVN
Colossians 4 in the JSNT
Colossians 4 in the KAPI
Colossians 4 in the KBT1ETNIK
Colossians 4 in the KBV
Colossians 4 in the KJV
Colossians 4 in the KNFD
Colossians 4 in the LBA
Colossians 4 in the LBLA
Colossians 4 in the LNT
Colossians 4 in the LSV
Colossians 4 in the MAAL
Colossians 4 in the MBV
Colossians 4 in the MBV2
Colossians 4 in the MHNT
Colossians 4 in the MKNFD
Colossians 4 in the MNG
Colossians 4 in the MNT
Colossians 4 in the MNT2
Colossians 4 in the MRS1T
Colossians 4 in the NAA
Colossians 4 in the NASB
Colossians 4 in the NBLA
Colossians 4 in the NBS
Colossians 4 in the NBVTP
Colossians 4 in the NET2
Colossians 4 in the NIV11
Colossians 4 in the NNT
Colossians 4 in the NNT2
Colossians 4 in the NNT3
Colossians 4 in the PDDPT
Colossians 4 in the PFNT
Colossians 4 in the RMNT
Colossians 4 in the SBIAS
Colossians 4 in the SBIBS
Colossians 4 in the SBIBS2
Colossians 4 in the SBICS
Colossians 4 in the SBIDS
Colossians 4 in the SBIGS
Colossians 4 in the SBIHS
Colossians 4 in the SBIIS
Colossians 4 in the SBIIS2
Colossians 4 in the SBIIS3
Colossians 4 in the SBIKS
Colossians 4 in the SBIKS2
Colossians 4 in the SBIMS
Colossians 4 in the SBIOS
Colossians 4 in the SBIPS
Colossians 4 in the SBISS
Colossians 4 in the SBITS
Colossians 4 in the SBITS2
Colossians 4 in the SBITS3
Colossians 4 in the SBITS4
Colossians 4 in the SBIUS
Colossians 4 in the SBIVS
Colossians 4 in the SBT
Colossians 4 in the SBT1E
Colossians 4 in the SCHL
Colossians 4 in the SNT
Colossians 4 in the SUSU
Colossians 4 in the SUSU2
Colossians 4 in the SYNO
Colossians 4 in the TBIAOTANT
Colossians 4 in the TBT1E
Colossians 4 in the TBT1E2
Colossians 4 in the TFTIP
Colossians 4 in the TFTU
Colossians 4 in the TGNTATF3T
Colossians 4 in the THAI
Colossians 4 in the TNFD
Colossians 4 in the TNT
Colossians 4 in the TNTIK
Colossians 4 in the TNTIL
Colossians 4 in the TNTIN
Colossians 4 in the TNTIP
Colossians 4 in the TNTIZ
Colossians 4 in the TOMA
Colossians 4 in the TTENT
Colossians 4 in the UBG
Colossians 4 in the UGV
Colossians 4 in the UGV2
Colossians 4 in the UGV3
Colossians 4 in the VBL
Colossians 4 in the VDCC
Colossians 4 in the YALU
Colossians 4 in the YAPE
Colossians 4 in the YBVTP
Colossians 4 in the ZBP