Ecclesiastes 5 (BOGWICC)
1 Uzisamala mayendedwe ako pamene ukupita ku nyumba ya Mulungu. Upite pafupi kuti ukamvetsere mʼmalo mopereka nsembe ya zitsiru zimene sizizindikira kuti zikuchita zolakwa. 2 Usamafulumire kuyankhula,usafulumire mu mtima mwakokunena chilichonse pamaso pa Mulungu.Mulungu ali kumwambandipo iwe uli pa dziko lapansi,choncho mawu ako akhale ochepa. 3 Kuchuluka kwa mavuto mu mtima kumabweretsa maloto oyipa,ndipo kuchuluka kwa mawu kumadzetsa uchitsiru. 4 Pamene ulumbira kwa Mulungu usachedwe kukwaniritsa chimene walumbiracho. Iye sakondweretsedwa ndi chitsiru; kwaniritsa lumbiro lako. 5 Kuli bwino kusalumbira kusiyana ndi kulumbira koma osakwaniritsa lumbirolo. 6 Pakamwa pako pasakuchimwitse. Ndipo usanene kwa mthenga wa mʼNyumba ya Mulungu kuti, “Ndinalakwitsa polumbira.” Chifukwa chiyani ukufuna Mulungu akwiye ndi mawu ako ndiponso ntchito ya manja ako? 7 Maloto ochuluka ndi mawu ochuluka ndi zinthu zopandapake. Kotero lemekeza Mulungu. 8 Ngati uwona anthu osauka akuzunzika mʼdziko, ndiponso anthu ena akupsinja anzawo ndi kuwalanda ufulu wawo, usadabwe ndi zinthu zimenezi; pakuti woyangʼanira ali naye wina womuyangʼanira wamkulu, ndipo pamwamba pa awiriwa pali ena akuluakulu owaposa. 9 Anthu onse amatengako zokolola za mʼminda: koma ndi mfumu yokha imene imapeza phindu la mindayi. 10 Aliyense amene amakonda ndalama sakhutitsidwa ndi ndalamazo;aliyense amene amakonda chuma sakhutitsidwa ndi zimene amapeza.Izinso ndi zopandapake. 11 Chuma chikachulukaakudya nawo chumacho amachulukanso.Nanga mwini wake amapindulapo chiyanikuposa kumangochiyangʼana ndi maso ake? 12 Wantchito amagona tulo tabwinongakhale adye pangʼono kapena kudya kwambiri,koma munthu wolemera, chumasichimulola kuti agone. 13 Ine ndinaona choyipa chomvetsa chisoni pansi pano:chuma chokundikidwa chikupweteka mwini wake yemwe, 14 kapena chuma chowonongedwa pa nthawi yatsoka,kotero kuti pamene wabereka mwanaalibe kanthu koti amusiyire. 15 Munthu anabadwa wamaliseche kuchokera mʼmimba mwa amayi ake,ndipo monga iye anabadwira, adzapitanso choncho.Pa zonse zimene iye anakhetsera thukutapalibe nʼchimodzi chomwe chimene adzatenge mʼmanja mwake. 16 Izinso ndi zoyipa kwambiri:munthu adzapita monga momwe anabwerera,ndipo iye amapindula chiyani,pakuti amagwira ntchito yolemetsa yopanda phindu? 17 Masiku ake onse ndi odzaza ndi mdima,kukhumudwa kwakukulu, masautso ndi nkhawa. 18 Tsono ndinazindikira kuti nʼchabwino ndi choyenera kuti munthu azidya ndi kumwa, ndi kukhutitsidwa ndi ntchito yake yolemetsa imene amayigwira pansi pano pa nthawi yake yochepa imene Mulungu amamupatsa, poti ichi ndiye chake. 19 Komatu pamene Mulungu apereka chuma kwa munthu aliyense ndi zinthu zina, ndi kulola kuti akondwere ndi chumacho, munthuyo alandire chumacho ndi kusangalala ndi ntchito yake, imene ndi mphatso yochokera kwa Mulungu. 20 Munthu wotereyu saganizirapo za masiku a moyo wake, chifukwa Mulungu amamutanganidwitsa ndi chisangalalo cha mu mtima mwake.
In Other Versions
Ecclesiastes 5 in the ANGEFD
Ecclesiastes 5 in the ANTPNG2D
Ecclesiastes 5 in the AS21
Ecclesiastes 5 in the BAGH
Ecclesiastes 5 in the BBPNG
Ecclesiastes 5 in the BBT1E
Ecclesiastes 5 in the BDS
Ecclesiastes 5 in the BEV
Ecclesiastes 5 in the BHAD
Ecclesiastes 5 in the BIB
Ecclesiastes 5 in the BLPT
Ecclesiastes 5 in the BNT
Ecclesiastes 5 in the BNTABOOT
Ecclesiastes 5 in the BNTLV
Ecclesiastes 5 in the BOATCB
Ecclesiastes 5 in the BOATCB2
Ecclesiastes 5 in the BOBCV
Ecclesiastes 5 in the BOCNT
Ecclesiastes 5 in the BOECS
Ecclesiastes 5 in the BOHCB
Ecclesiastes 5 in the BOHCV
Ecclesiastes 5 in the BOHLNT
Ecclesiastes 5 in the BOHNTLTAL
Ecclesiastes 5 in the BOICB
Ecclesiastes 5 in the BOILNTAP
Ecclesiastes 5 in the BOITCV
Ecclesiastes 5 in the BOKCV
Ecclesiastes 5 in the BOKCV2
Ecclesiastes 5 in the BOKHWOG
Ecclesiastes 5 in the BOKSSV
Ecclesiastes 5 in the BOLCB
Ecclesiastes 5 in the BOLCB2
Ecclesiastes 5 in the BOMCV
Ecclesiastes 5 in the BONAV
Ecclesiastes 5 in the BONCB
Ecclesiastes 5 in the BONLT
Ecclesiastes 5 in the BONUT2
Ecclesiastes 5 in the BOPLNT
Ecclesiastes 5 in the BOSCB
Ecclesiastes 5 in the BOSNC
Ecclesiastes 5 in the BOTLNT
Ecclesiastes 5 in the BOVCB
Ecclesiastes 5 in the BOYCB
Ecclesiastes 5 in the BPBB
Ecclesiastes 5 in the BPH
Ecclesiastes 5 in the BSB
Ecclesiastes 5 in the CCB
Ecclesiastes 5 in the CUV
Ecclesiastes 5 in the CUVS
Ecclesiastes 5 in the DBT
Ecclesiastes 5 in the DGDNT
Ecclesiastes 5 in the DHNT
Ecclesiastes 5 in the DNT
Ecclesiastes 5 in the ELBE
Ecclesiastes 5 in the EMTV
Ecclesiastes 5 in the ESV
Ecclesiastes 5 in the FBV
Ecclesiastes 5 in the FEB
Ecclesiastes 5 in the GGMNT
Ecclesiastes 5 in the GNT
Ecclesiastes 5 in the HARY
Ecclesiastes 5 in the HNT
Ecclesiastes 5 in the IRVA
Ecclesiastes 5 in the IRVB
Ecclesiastes 5 in the IRVG
Ecclesiastes 5 in the IRVH
Ecclesiastes 5 in the IRVK
Ecclesiastes 5 in the IRVM
Ecclesiastes 5 in the IRVM2
Ecclesiastes 5 in the IRVO
Ecclesiastes 5 in the IRVP
Ecclesiastes 5 in the IRVT
Ecclesiastes 5 in the IRVT2
Ecclesiastes 5 in the IRVU
Ecclesiastes 5 in the ISVN
Ecclesiastes 5 in the JSNT
Ecclesiastes 5 in the KAPI
Ecclesiastes 5 in the KBT1ETNIK
Ecclesiastes 5 in the KBV
Ecclesiastes 5 in the KJV
Ecclesiastes 5 in the KNFD
Ecclesiastes 5 in the LBA
Ecclesiastes 5 in the LBLA
Ecclesiastes 5 in the LNT
Ecclesiastes 5 in the LSV
Ecclesiastes 5 in the MAAL
Ecclesiastes 5 in the MBV
Ecclesiastes 5 in the MBV2
Ecclesiastes 5 in the MHNT
Ecclesiastes 5 in the MKNFD
Ecclesiastes 5 in the MNG
Ecclesiastes 5 in the MNT
Ecclesiastes 5 in the MNT2
Ecclesiastes 5 in the MRS1T
Ecclesiastes 5 in the NAA
Ecclesiastes 5 in the NASB
Ecclesiastes 5 in the NBLA
Ecclesiastes 5 in the NBS
Ecclesiastes 5 in the NBVTP
Ecclesiastes 5 in the NET2
Ecclesiastes 5 in the NIV11
Ecclesiastes 5 in the NNT
Ecclesiastes 5 in the NNT2
Ecclesiastes 5 in the NNT3
Ecclesiastes 5 in the PDDPT
Ecclesiastes 5 in the PFNT
Ecclesiastes 5 in the RMNT
Ecclesiastes 5 in the SBIAS
Ecclesiastes 5 in the SBIBS
Ecclesiastes 5 in the SBIBS2
Ecclesiastes 5 in the SBICS
Ecclesiastes 5 in the SBIDS
Ecclesiastes 5 in the SBIGS
Ecclesiastes 5 in the SBIHS
Ecclesiastes 5 in the SBIIS
Ecclesiastes 5 in the SBIIS2
Ecclesiastes 5 in the SBIIS3
Ecclesiastes 5 in the SBIKS
Ecclesiastes 5 in the SBIKS2
Ecclesiastes 5 in the SBIMS
Ecclesiastes 5 in the SBIOS
Ecclesiastes 5 in the SBIPS
Ecclesiastes 5 in the SBISS
Ecclesiastes 5 in the SBITS
Ecclesiastes 5 in the SBITS2
Ecclesiastes 5 in the SBITS3
Ecclesiastes 5 in the SBITS4
Ecclesiastes 5 in the SBIUS
Ecclesiastes 5 in the SBIVS
Ecclesiastes 5 in the SBT
Ecclesiastes 5 in the SBT1E
Ecclesiastes 5 in the SCHL
Ecclesiastes 5 in the SNT
Ecclesiastes 5 in the SUSU
Ecclesiastes 5 in the SUSU2
Ecclesiastes 5 in the SYNO
Ecclesiastes 5 in the TBIAOTANT
Ecclesiastes 5 in the TBT1E
Ecclesiastes 5 in the TBT1E2
Ecclesiastes 5 in the TFTIP
Ecclesiastes 5 in the TFTU
Ecclesiastes 5 in the TGNTATF3T
Ecclesiastes 5 in the THAI
Ecclesiastes 5 in the TNFD
Ecclesiastes 5 in the TNT
Ecclesiastes 5 in the TNTIK
Ecclesiastes 5 in the TNTIL
Ecclesiastes 5 in the TNTIN
Ecclesiastes 5 in the TNTIP
Ecclesiastes 5 in the TNTIZ
Ecclesiastes 5 in the TOMA
Ecclesiastes 5 in the TTENT
Ecclesiastes 5 in the UBG
Ecclesiastes 5 in the UGV
Ecclesiastes 5 in the UGV2
Ecclesiastes 5 in the UGV3
Ecclesiastes 5 in the VBL
Ecclesiastes 5 in the VDCC
Ecclesiastes 5 in the YALU
Ecclesiastes 5 in the YAPE
Ecclesiastes 5 in the YBVTP
Ecclesiastes 5 in the ZBP