Genesis 5 (BOGWICC)
1 Ndondomeko ya mibado ya Adamu ndi iyi: Pamene Mulungu analenga munthu, anamulenga mʼchifaniziro cha Mulungu. 2 Iye analenga mwamuna ndi mkazi. Anawadalitsa ndipo anawatcha “Munthu.” 3 Pamene Adamu anali ndi zaka 130, anabereka mwana wamwamuna wofanana naye ndipo anamutcha Seti. 4 Atabadwa Seti, Adamu anakhala ndi moyo zaka zina 800 ndipo anabereka ana ena aamuna ndi aakazi. 5 Zaka zonse za Adamu zinali 930 ndipo anamwalira. 6 Pamene Seti anali ndi zaka 105, anabereka Enosi. 7 Atabadwa Enosi, Seti anakhala ndi moyo zaka zina 807 ndipo anabereka ana ena aamuna ndi aakazi. 8 Zaka zonse za Seti zinali 912 ndipo anamwalira. 9 Pamene Enosi anali ndi zaka 90, anabereka Kenani. 10 Atabadwa Kenani, Enosi anakhala ndi moyo zaka zina 815 ndipo anabereka ana ena aamuna ndi aakazi. 11 Zaka zonse za Enosi pamodzi zinali 905 ndipo anamwalira. 12 Pamene Kenani anali ndi zaka 70, anabereka Mahalaleli. 13 Atabadwa Mahalaleli, Kenani anakhala ndi moyo zaka zina 840 ndipo anabereka ana ena aamuna ndi aakazi. 14 Zaka zonse za Kenani zinali 910, ndipo anamwalira. 15 Pamene Mahalaleli anali ndi zaka 65, anabereka Yaredi. 16 Atabadwa Yaredi, Mahalaleli anakhala ndi moyo zaka zina 830 ndipo anabereka ana ena aamuna ndi aakazi. 17 Zaka zonse za Mahalaleli zinali 895 ndipo anamwalira. 18 Pamene Yaredi anali ndi zaka 162, anabereka Enoki. 19 Atabadwa Enoki, Yaredi anakhala ndi moyo zaka zina 800 ndipo anabereka ana ena aamuna ndi aakazi. 20 Zaka zonse za Yaredi zinali 962 ndipo anamwalira. 21 Pamene Enoki anali ndi zaka 65, anabereka Metusela. 22 Atabadwa Metusela, Enoki anayenda ndi Mulungu zaka 300 ndipo anabereka ana ena aamuna ndi aakazi. 23 Zaka zonse za Enoki zinali 365. 24 Enoki anayenda ndi Mulungu; ndipo iye sanaonekenso chifukwa Mulungu anamutenga. 25 Pamene Metusela anali ndi zaka 187, anabereka Lameki. 26 Ndipo atabadwa Lameki, Metusela anakhala ndi moyo zaka zina 782 ndipo anabereka ana ena aamuna ndi aakazi. 27 Zaka zonse za Metusela zinali 969, ndipo anamwalira. 28 Pamene Lameki anali ndi zaka 182, anabereka mwana wamwamuna. 29 Ndipo anamutcha Nowa ndipo anati, “Iyeyu adzatipumulitsa ku ntchito zathu zolemetsazi, zolima nthaka imene Yehova anayitemberera.” 30 Atabadwa Nowa, Lameki anakhala zaka zina 595 ndipo anabereka ana ena aamuna ndi aakazi. 31 Zaka zonse za Lameki zinali 777, ndipo kenaka anamwalira. 32 Pamene Nowa anali ndi zaka 500, anabereka Semu, Hamu ndi Yafeti.
In Other Versions
Genesis 5 in the ANGEFD
Genesis 5 in the ANTPNG2D
Genesis 5 in the AS21
Genesis 5 in the BAGH
Genesis 5 in the BBPNG
Genesis 5 in the BBT1E
Genesis 5 in the BDS
Genesis 5 in the BEV
Genesis 5 in the BHAD
Genesis 5 in the BIB
Genesis 5 in the BLPT
Genesis 5 in the BNT
Genesis 5 in the BNTABOOT
Genesis 5 in the BNTLV
Genesis 5 in the BOATCB
Genesis 5 in the BOATCB2
Genesis 5 in the BOBCV
Genesis 5 in the BOCNT
Genesis 5 in the BOECS
Genesis 5 in the BOHCB
Genesis 5 in the BOHCV
Genesis 5 in the BOHLNT
Genesis 5 in the BOHNTLTAL
Genesis 5 in the BOICB
Genesis 5 in the BOILNTAP
Genesis 5 in the BOITCV
Genesis 5 in the BOKCV
Genesis 5 in the BOKCV2
Genesis 5 in the BOKHWOG
Genesis 5 in the BOKSSV
Genesis 5 in the BOLCB
Genesis 5 in the BOLCB2
Genesis 5 in the BOMCV
Genesis 5 in the BONAV
Genesis 5 in the BONCB
Genesis 5 in the BONLT
Genesis 5 in the BONUT2
Genesis 5 in the BOPLNT
Genesis 5 in the BOSCB
Genesis 5 in the BOSNC
Genesis 5 in the BOTLNT
Genesis 5 in the BOVCB
Genesis 5 in the BOYCB
Genesis 5 in the BPBB
Genesis 5 in the BPH
Genesis 5 in the BSB
Genesis 5 in the CCB
Genesis 5 in the CUV
Genesis 5 in the CUVS
Genesis 5 in the DBT
Genesis 5 in the DGDNT
Genesis 5 in the DHNT
Genesis 5 in the DNT
Genesis 5 in the ELBE
Genesis 5 in the EMTV
Genesis 5 in the ESV
Genesis 5 in the FBV
Genesis 5 in the FEB
Genesis 5 in the GGMNT
Genesis 5 in the GNT
Genesis 5 in the HARY
Genesis 5 in the HNT
Genesis 5 in the IRVA
Genesis 5 in the IRVB
Genesis 5 in the IRVG
Genesis 5 in the IRVH
Genesis 5 in the IRVK
Genesis 5 in the IRVM
Genesis 5 in the IRVM2
Genesis 5 in the IRVO
Genesis 5 in the IRVP
Genesis 5 in the IRVT
Genesis 5 in the IRVT2
Genesis 5 in the IRVU
Genesis 5 in the ISVN
Genesis 5 in the JSNT
Genesis 5 in the KAPI
Genesis 5 in the KBT1ETNIK
Genesis 5 in the KBV
Genesis 5 in the KJV
Genesis 5 in the KNFD
Genesis 5 in the LBA
Genesis 5 in the LBLA
Genesis 5 in the LNT
Genesis 5 in the LSV
Genesis 5 in the MAAL
Genesis 5 in the MBV
Genesis 5 in the MBV2
Genesis 5 in the MHNT
Genesis 5 in the MKNFD
Genesis 5 in the MNG
Genesis 5 in the MNT
Genesis 5 in the MNT2
Genesis 5 in the MRS1T
Genesis 5 in the NAA
Genesis 5 in the NASB
Genesis 5 in the NBLA
Genesis 5 in the NBS
Genesis 5 in the NBVTP
Genesis 5 in the NET2
Genesis 5 in the NIV11
Genesis 5 in the NNT
Genesis 5 in the NNT2
Genesis 5 in the NNT3
Genesis 5 in the PDDPT
Genesis 5 in the PFNT
Genesis 5 in the RMNT
Genesis 5 in the SBIAS
Genesis 5 in the SBIBS
Genesis 5 in the SBIBS2
Genesis 5 in the SBICS
Genesis 5 in the SBIDS
Genesis 5 in the SBIGS
Genesis 5 in the SBIHS
Genesis 5 in the SBIIS
Genesis 5 in the SBIIS2
Genesis 5 in the SBIIS3
Genesis 5 in the SBIKS
Genesis 5 in the SBIKS2
Genesis 5 in the SBIMS
Genesis 5 in the SBIOS
Genesis 5 in the SBIPS
Genesis 5 in the SBISS
Genesis 5 in the SBITS
Genesis 5 in the SBITS2
Genesis 5 in the SBITS3
Genesis 5 in the SBITS4
Genesis 5 in the SBIUS
Genesis 5 in the SBIVS
Genesis 5 in the SBT
Genesis 5 in the SBT1E
Genesis 5 in the SCHL
Genesis 5 in the SNT
Genesis 5 in the SUSU
Genesis 5 in the SUSU2
Genesis 5 in the SYNO
Genesis 5 in the TBIAOTANT
Genesis 5 in the TBT1E
Genesis 5 in the TBT1E2
Genesis 5 in the TFTIP
Genesis 5 in the TFTU
Genesis 5 in the TGNTATF3T
Genesis 5 in the THAI
Genesis 5 in the TNFD
Genesis 5 in the TNT
Genesis 5 in the TNTIK
Genesis 5 in the TNTIL
Genesis 5 in the TNTIN
Genesis 5 in the TNTIP
Genesis 5 in the TNTIZ
Genesis 5 in the TOMA
Genesis 5 in the TTENT
Genesis 5 in the UBG
Genesis 5 in the UGV
Genesis 5 in the UGV2
Genesis 5 in the UGV3
Genesis 5 in the VBL
Genesis 5 in the VDCC
Genesis 5 in the YALU
Genesis 5 in the YAPE
Genesis 5 in the YBVTP
Genesis 5 in the ZBP