Job 12 (BOGWICC)

1 Pamenepo Yobu anayankha kuti, 2 “Ndithudi inuyo ndinu anthundipo nzeru zanu zidzafera nanu pamodzi! 3 Koma inenso ndili nazo nzeru ngati inu;ineyo sindine munthu wamba kwa inu.Ndani amene sadziwa zonse zimene mwanenazi? 4 “Ndasanduka chinthu choseketsa kwa abwenzi anga,ngakhale ndinkapemphera kwa Mulungu ndipo Iye ankandiyankha.Ine ndasanduka chinthu chongoseketsa, ngakhale ndili wolungama ndi wosalakwa! 5 Anthu amene ali pabwino amanyoza anzawo amene ali pa tsoka.Tsokalo limagwa pa amene wayamba kale kugwa. 6 Nyumba za anthu achifwamba zimakhala pa mtendere,ndipo anthu amene amaputa Mulungu amakhala pabwino,amene amanyamula milungu yawo mʼmanja. 7 “Koma funsa nyama zakuthengo ndipo zidzakuphunzitsa,kapena mbalame zamumlengalenga ndipo zidzakuwuza; 8 kapena uyankhule ndi dziko lapansi ndipo lidzakuphunzitsa,kapena ulole nsomba zamʼnyanja kuti zikufotokozere. 9 Kodi mwa zonsezi ndi chiti chimene sichidziwakuti lachita zimenezi ndi dzanja la Yehova? 10 Mʼmanja mwake ndi mʼmene muli moyo wa cholengedwa chilichonse,ndiponso moyo wa anthu a mitundu yonse. 11 Kodi khutu sindiye limene limamva mawumonga mmene lilime limalawira chakudya? 12 Kodi nzeru sipezeka pakati pa anthu okalamba?Kodi moyo wautali sumabweretsa nzeru zomvetsa zinthu? 13 “Kwa Mulungu ndiye kuli nzeru ndi mphamvu;uphungu ndi kumvetsa zinthu ndi zake. 14 Chimene Iye wapasula palibe angachimangenso.Akatsekera munthu mʼndende palibe angamutulutse. 15 Iyeyo akamanga mvula dziko limawuma;akamasula mvulayo, madzi amasefukira pa dziko. 16 Kwa Iye kuli mphamvu ndi kupambana;munthu wopusitsidwa ndiponso wopusitsa onse ali mu ulamuliro wake. 17 Iye amalanda aphungu nzeru zawondipo amapusitsa oweruza. 18 Iye amachotsa zingwe zimene mafumu anawamanga nazondipo amawamanga lamba mʼchiwuno mwawo. 19 Iye amasocheretsa ansembe atawalanda nzeru zawondipo amagonjetsa anthu amphamvu amene ndi okhazikika. 20 Iye amakhalitsa chete aphungu odalirikandipo amalanda chidziwitso cha anthu akuluakulu. 21 Iye amanyoza anthu otchukandipo anthu anyonga amawatha mphamvu. 22 Iye amatulutsira poyera zinthu zozama za mu mdimandipo mdima wandiweyaniwo amawusandutsa kuwala. 23 Iye amakuza mitundu ya anthu ndipo amayiwononganso;amachulukitsa mitundu ya anthu ndipo amayimwazanso. 24 Iye amalanda nzeru za atsogoleri a dziko lapansi;amawayendetsa mʼthengo mopanda njira. 25 Iwo amafufuzafufuza njira mu mdima wopanda chowunikira;Iye amawayendetsa dzandidzandi ngati oledzera.

In Other Versions

Job 12 in the ANGEFD

Job 12 in the ANTPNG2D

Job 12 in the AS21

Job 12 in the BAGH

Job 12 in the BBPNG

Job 12 in the BBT1E

Job 12 in the BDS

Job 12 in the BEV

Job 12 in the BHAD

Job 12 in the BIB

Job 12 in the BLPT

Job 12 in the BNT

Job 12 in the BNTABOOT

Job 12 in the BNTLV

Job 12 in the BOATCB

Job 12 in the BOATCB2

Job 12 in the BOBCV

Job 12 in the BOCNT

Job 12 in the BOECS

Job 12 in the BOHCB

Job 12 in the BOHCV

Job 12 in the BOHLNT

Job 12 in the BOHNTLTAL

Job 12 in the BOICB

Job 12 in the BOILNTAP

Job 12 in the BOITCV

Job 12 in the BOKCV

Job 12 in the BOKCV2

Job 12 in the BOKHWOG

Job 12 in the BOKSSV

Job 12 in the BOLCB

Job 12 in the BOLCB2

Job 12 in the BOMCV

Job 12 in the BONAV

Job 12 in the BONCB

Job 12 in the BONLT

Job 12 in the BONUT2

Job 12 in the BOPLNT

Job 12 in the BOSCB

Job 12 in the BOSNC

Job 12 in the BOTLNT

Job 12 in the BOVCB

Job 12 in the BOYCB

Job 12 in the BPBB

Job 12 in the BPH

Job 12 in the BSB

Job 12 in the CCB

Job 12 in the CUV

Job 12 in the CUVS

Job 12 in the DBT

Job 12 in the DGDNT

Job 12 in the DHNT

Job 12 in the DNT

Job 12 in the ELBE

Job 12 in the EMTV

Job 12 in the ESV

Job 12 in the FBV

Job 12 in the FEB

Job 12 in the GGMNT

Job 12 in the GNT

Job 12 in the HARY

Job 12 in the HNT

Job 12 in the IRVA

Job 12 in the IRVB

Job 12 in the IRVG

Job 12 in the IRVH

Job 12 in the IRVK

Job 12 in the IRVM

Job 12 in the IRVM2

Job 12 in the IRVO

Job 12 in the IRVP

Job 12 in the IRVT

Job 12 in the IRVT2

Job 12 in the IRVU

Job 12 in the ISVN

Job 12 in the JSNT

Job 12 in the KAPI

Job 12 in the KBT1ETNIK

Job 12 in the KBV

Job 12 in the KJV

Job 12 in the KNFD

Job 12 in the LBA

Job 12 in the LBLA

Job 12 in the LNT

Job 12 in the LSV

Job 12 in the MAAL

Job 12 in the MBV

Job 12 in the MBV2

Job 12 in the MHNT

Job 12 in the MKNFD

Job 12 in the MNG

Job 12 in the MNT

Job 12 in the MNT2

Job 12 in the MRS1T

Job 12 in the NAA

Job 12 in the NASB

Job 12 in the NBLA

Job 12 in the NBS

Job 12 in the NBVTP

Job 12 in the NET2

Job 12 in the NIV11

Job 12 in the NNT

Job 12 in the NNT2

Job 12 in the NNT3

Job 12 in the PDDPT

Job 12 in the PFNT

Job 12 in the RMNT

Job 12 in the SBIAS

Job 12 in the SBIBS

Job 12 in the SBIBS2

Job 12 in the SBICS

Job 12 in the SBIDS

Job 12 in the SBIGS

Job 12 in the SBIHS

Job 12 in the SBIIS

Job 12 in the SBIIS2

Job 12 in the SBIIS3

Job 12 in the SBIKS

Job 12 in the SBIKS2

Job 12 in the SBIMS

Job 12 in the SBIOS

Job 12 in the SBIPS

Job 12 in the SBISS

Job 12 in the SBITS

Job 12 in the SBITS2

Job 12 in the SBITS3

Job 12 in the SBITS4

Job 12 in the SBIUS

Job 12 in the SBIVS

Job 12 in the SBT

Job 12 in the SBT1E

Job 12 in the SCHL

Job 12 in the SNT

Job 12 in the SUSU

Job 12 in the SUSU2

Job 12 in the SYNO

Job 12 in the TBIAOTANT

Job 12 in the TBT1E

Job 12 in the TBT1E2

Job 12 in the TFTIP

Job 12 in the TFTU

Job 12 in the TGNTATF3T

Job 12 in the THAI

Job 12 in the TNFD

Job 12 in the TNT

Job 12 in the TNTIK

Job 12 in the TNTIL

Job 12 in the TNTIN

Job 12 in the TNTIP

Job 12 in the TNTIZ

Job 12 in the TOMA

Job 12 in the TTENT

Job 12 in the UBG

Job 12 in the UGV

Job 12 in the UGV2

Job 12 in the UGV3

Job 12 in the VBL

Job 12 in the VDCC

Job 12 in the YALU

Job 12 in the YAPE

Job 12 in the YBVTP

Job 12 in the ZBP