Job 32 (BOGWICC)

1 Tsono anthu atatuwa analeka kumuyankha Yobu, chifukwa chakuti iyeyo ankadziona kuti ndi wolungama. 2 Koma Elihu, mwana wa Barakeli, wa fuko la Buzi, wa banja la Ramu, anapsera mtima kwambiri Yobu chifukwa choti Yobuyo anakana kuvomera kuti anachimwa ndi kuti Mulungu anakhoza pomulanga. 3 Anapseranso mtima abwenzi ake atatu aja chifukwa sanapeze njira yomutsutsira Yobu, ngakhale iwo anamupeza kuti anali wolakwa. 4 Tsono Elihu anadikira kuti ayankhule ndi Yobu chifukwa choti abwenziwo anali akuluakulu kupambana iyeyo. 5 Koma Elihu ataona kuti anthu atatuwo analibe mawu oti ayankhulenso, iye anapsa mtima. 6 Choncho Elihu mwana wa Barakeli wa fuko la Buzi anati:“Ine ndine wamngʼono,inuyo ndinu akuluakulu,nʼchifukwa chake ndimaopa,ndimachita mantha kuti ndikuwuzeni zimene ndimadziwa. 7 Ndimaganiza kuti, ‘Ayambe ndi akuluakulu kuyankhula;anthu amvulazakale ndiwo amaphunzitsa nzeru.’ 8 Koma mzimu wa Mulungu mwa munthu,mpweya wa Wamphamvuzonse, ndi umene umapereka nzeru zomvetsa zinthu. 9 Si okalamba amene ali ndi nzeru,si amvulazakale okha amene ali ndi nzeru zomvetsa zinthu zimene zili zoyenera. 10 “Nʼchifukwa chake ndikuti, ‘Mvereni;inenso ndikukuwuzani zimene ndikuzidziwa.’ 11 Ndadikira nthawi yonseyi,ndimamvetsera mwachidwi zimene mumayankhula,pamene mumafunafuna mawu oti muyankhule, 12 ineyo ndinakumvetseranidi.Koma palibe ndi mmodzi yemwe wa inu amene anatsutsa Yobu;palibe aliyense wa inu amene anamuyankha mawu ake. 13 Musanene kuti, ‘Ife tapeza nzeru;Mulungu ndiye amutsutse, osati munthu.’ 14 Koma Yobu sanayankhule motsutsana ndi ine,ndipo ine sindimuyankha monga mmene inu mwamuyankhira. 15 “Iwo asokonezeka ndipo alibe choti ayankhulenso;mawu awathera. 16 Kodi ine ndidikire chifukwa iwo sakuyankhula tsopano,pakuti angoyima phee wopanda yankho? 17 Inenso ndiyankhulapo tsopano;nanenso ndinena zimene ndikudziwa. 18 Pakuti ndili nawo mawu ambiri,ndipo mtima wanga ukundikakamiza; 19 mʼkati mwanga ndili ngati botolo lodzaza ndi vinyo,ngati matumba a vinyo watsopano amene ali pafupi kuphulika. 20 Ndiyenera kuyankhula kuti mtima utsike;ndiyenera kutsekula pakamwa panga ndi kuyankha. 21 Sindidzakondera munthu wina aliyense,kapena kuyankhula zoshashalika, 22 pakuti ndikanakhala wa luso loyankhula moshashalika,Mlengi wanga akanandilanga msanga.”

In Other Versions

Job 32 in the ANGEFD

Job 32 in the ANTPNG2D

Job 32 in the AS21

Job 32 in the BAGH

Job 32 in the BBPNG

Job 32 in the BBT1E

Job 32 in the BDS

Job 32 in the BEV

Job 32 in the BHAD

Job 32 in the BIB

Job 32 in the BLPT

Job 32 in the BNT

Job 32 in the BNTABOOT

Job 32 in the BNTLV

Job 32 in the BOATCB

Job 32 in the BOATCB2

Job 32 in the BOBCV

Job 32 in the BOCNT

Job 32 in the BOECS

Job 32 in the BOHCB

Job 32 in the BOHCV

Job 32 in the BOHLNT

Job 32 in the BOHNTLTAL

Job 32 in the BOICB

Job 32 in the BOILNTAP

Job 32 in the BOITCV

Job 32 in the BOKCV

Job 32 in the BOKCV2

Job 32 in the BOKHWOG

Job 32 in the BOKSSV

Job 32 in the BOLCB

Job 32 in the BOLCB2

Job 32 in the BOMCV

Job 32 in the BONAV

Job 32 in the BONCB

Job 32 in the BONLT

Job 32 in the BONUT2

Job 32 in the BOPLNT

Job 32 in the BOSCB

Job 32 in the BOSNC

Job 32 in the BOTLNT

Job 32 in the BOVCB

Job 32 in the BOYCB

Job 32 in the BPBB

Job 32 in the BPH

Job 32 in the BSB

Job 32 in the CCB

Job 32 in the CUV

Job 32 in the CUVS

Job 32 in the DBT

Job 32 in the DGDNT

Job 32 in the DHNT

Job 32 in the DNT

Job 32 in the ELBE

Job 32 in the EMTV

Job 32 in the ESV

Job 32 in the FBV

Job 32 in the FEB

Job 32 in the GGMNT

Job 32 in the GNT

Job 32 in the HARY

Job 32 in the HNT

Job 32 in the IRVA

Job 32 in the IRVB

Job 32 in the IRVG

Job 32 in the IRVH

Job 32 in the IRVK

Job 32 in the IRVM

Job 32 in the IRVM2

Job 32 in the IRVO

Job 32 in the IRVP

Job 32 in the IRVT

Job 32 in the IRVT2

Job 32 in the IRVU

Job 32 in the ISVN

Job 32 in the JSNT

Job 32 in the KAPI

Job 32 in the KBT1ETNIK

Job 32 in the KBV

Job 32 in the KJV

Job 32 in the KNFD

Job 32 in the LBA

Job 32 in the LBLA

Job 32 in the LNT

Job 32 in the LSV

Job 32 in the MAAL

Job 32 in the MBV

Job 32 in the MBV2

Job 32 in the MHNT

Job 32 in the MKNFD

Job 32 in the MNG

Job 32 in the MNT

Job 32 in the MNT2

Job 32 in the MRS1T

Job 32 in the NAA

Job 32 in the NASB

Job 32 in the NBLA

Job 32 in the NBS

Job 32 in the NBVTP

Job 32 in the NET2

Job 32 in the NIV11

Job 32 in the NNT

Job 32 in the NNT2

Job 32 in the NNT3

Job 32 in the PDDPT

Job 32 in the PFNT

Job 32 in the RMNT

Job 32 in the SBIAS

Job 32 in the SBIBS

Job 32 in the SBIBS2

Job 32 in the SBICS

Job 32 in the SBIDS

Job 32 in the SBIGS

Job 32 in the SBIHS

Job 32 in the SBIIS

Job 32 in the SBIIS2

Job 32 in the SBIIS3

Job 32 in the SBIKS

Job 32 in the SBIKS2

Job 32 in the SBIMS

Job 32 in the SBIOS

Job 32 in the SBIPS

Job 32 in the SBISS

Job 32 in the SBITS

Job 32 in the SBITS2

Job 32 in the SBITS3

Job 32 in the SBITS4

Job 32 in the SBIUS

Job 32 in the SBIVS

Job 32 in the SBT

Job 32 in the SBT1E

Job 32 in the SCHL

Job 32 in the SNT

Job 32 in the SUSU

Job 32 in the SUSU2

Job 32 in the SYNO

Job 32 in the TBIAOTANT

Job 32 in the TBT1E

Job 32 in the TBT1E2

Job 32 in the TFTIP

Job 32 in the TFTU

Job 32 in the TGNTATF3T

Job 32 in the THAI

Job 32 in the TNFD

Job 32 in the TNT

Job 32 in the TNTIK

Job 32 in the TNTIL

Job 32 in the TNTIN

Job 32 in the TNTIP

Job 32 in the TNTIZ

Job 32 in the TOMA

Job 32 in the TTENT

Job 32 in the UBG

Job 32 in the UGV

Job 32 in the UGV2

Job 32 in the UGV3

Job 32 in the VBL

Job 32 in the VDCC

Job 32 in the YALU

Job 32 in the YAPE

Job 32 in the YBVTP

Job 32 in the ZBP