Nehemiah 11 (BOGWICC)

1 Nthawi imeneyo atsogoleri a anthu ankakhala ku Yerusalemu. Tsono anthu ena onse anachita maere kuti apeze munthu mmodzi pa anthu khumi aliwonse kuti azikhala ku Yerusalemu, mzinda wopatulika. Anthu asanu ndi anayi otsalawo ankakhala mʼmidzi yawo. 2 Anthu anayamikira onse amene anadzipereka kuti azikhala mu Yerusalemu. 3 Aisraeli wamba, ansembe, Alevi, ogwira ntchito ku Nyumba ya Mulungu ndiponso zidzukulu za antchito a Solomoni ankakhala mʼmidzi yawo, aliyense mu dera lake. Koma atsogoleri a chigawo cha Yuda anali atakhazikika mu Yerusalemu. 4 Ku Yerusalemu kunkakhalanso anthu ena a mafuko a Yuda ndi Benjamini. Ena mwa zidzukulu za Yuda ndi awa:Ataya, mwana wa Uziya, mwana wa Zekariya, mwana wa Amariya mwana wa Sefatiya, mwana wa Mahalaleli. Onsewa anali ana a Perezi. 5 Ena ndi awa: Maaseya mwana wa Baruki, mwana wa Koli-Hoze mwana wa Hazaya, mwana wa Adaya, mwana wa Yowaribu, Zekariya mwana wa Msiloni. 6 Zidzukulu zonse za Perezi, anthu amphamvu zawo amene ankakhala ku Yerusalemu analipo anthu okwanira 468. 7 Nazi zidzukulu za Benjamini:Salu mwana wa Mesulamu, mwana wa Yowedi, mwana wa Pedaya, mwana wa Kolaya, mwana wa Maaseiya, mwana wa Itieli, mwana wa Yesaiya. 8 Abale ake anali Gabayi ndi Salaya. Onse pamodzi anali 928. 9 Yoweli mwana wa Zikiri ndiye anali mtsogoleri wawo, ndipo Yuda mwana wa Hasenuya ndiye amayangʼanira chigawo cha chiwiri cha mzinda. 10 Ansembe anali awa:Yedaya mwana wa Yowaribu; Yakini; 11 Seraya mwana wa Hilikiya mwana wa Mesulamu, mwana wa Zadoki, mwana wa Merayoti, mwana wa Ahitubi amene anali woyangʼanira Nyumba ya Mulungu, 12 ndi abale awo, amene ankagwira ntchito ku Nyumba ya Mulungu. Onse pamodzi anali 822. Panalinso Adaya mwana wa Yerohamu, mwana wa Pelaliya, mwana wa Amizi, mwana wa Zekariya, mwana wa Pasi-Huri, mwana wa Malikiya, 13 ndi abale ake, amene anali atsogoleri a mabanja. Onse pamodzi anali 242. Kuphatikiza apo panalinso Amasisai mwana wa Azaireli, mwana wa Ahazayi, mwana wa Mesilemoti, mwana wa Imeri 14 ndi abale ake. Onse pamodzi anali 128 ndipo anali anthu olimba mtima kwambiri. Mtsogoleri wawo wamkulu anali Zabidieli mwana wa Hagedolimu. 15 Alevi anali awa:Semaya mwana wa Hasubu, mwana wa Azirikamu, mwana wa Hasabiya, mwana wa Buni. 16 Sabetayi ndi Yozabadi anali atsogoleri amene ankayangʼanira ntchito ya kunja kwa Nyumba ya Mulungu. 17 Mataniya mwana wa Mika, mwana wa Zabidi, mwana wa Asafu ndiye anali wotsogolera pa mapemphero achiyamiko. Panalinso Bakibukiya amene anali wachiwiri pakati pa abale ake. Kuwonjezera apo panalinso Abida mwana wa Samuwa, mwana wa Galali, mwana wa Yedutuni. 18 Alevi onse amene anali mu mzinda woyera analipo 284. 19 Alonda a ku Nyumba ya Mulungu anali awa:Akubu, Talimoni ndi abale awo. Onse pamodzi anali 172. 20 Aisraeli ena onse pamodzi ndi ansembe ndi Alevi ankakhala mʼmizinda ya Yuda, ndipo aliyense ankakhala mʼdera la makolo ake. 21 Koma antchito a ku Nyumba ya Mulungu ankakhala pa phiri la Ofeli, ndipo Ziha ndi Gisipa ndiwo anali kuwayangʼanira. 22 Wamkulu wa Alevi mu Yerusalemu anali Uzi mwana wa Bani, mwana wa Hasabiya, mwana wa Mataniya, mwana wa Mika. Uzi anali mmodzi wa zidzukulu za Asafu, amene anali oyimba nyimbo pa nthawi zachipembedzo mʼNyumba ya Mulungu. 23 Pakuti mfumu inalamula kuti tsiku ndi tsiku pa nthawi zachipembedzo oyimba nyimbowo azikhalapo. 24 Petahiya mwana wa Mesezabeli, mmodzi mwa zidzukulu za Zera mwana wa Yuda ndiye ankayimirira Aisraeli pa bwalo la mfumu ya Perisiya. 25 Anthu ena a fuko la Yuda ankakhala ku Kiriyati-Ariba ndi midzi yake, ku Diboni ndi midzi yake, ku Yekabizeeli ndi midzi yake, 26 ku Yesuwa, Molada, Beti-Peleti, 27 Hazari-Suwali, Beeriseba ndi midzi yawo. 28 Ku Zikilagi, Mekona ndi midzi yawo, 29 ku Eni-Rimoni, Zora, Yarimuti, 30 Zanowa, Adulamu ndi midzi yake, ku Lakisi ndi minda yake, ku Beeriseba mpaka ku chigwa cha Hinomu. 31 Nazonso zidzukulu za Benjamini zinkakhala mʼdera lawo kuyambira ku Geba mpaka ku Mikimasi, Ayiya, Beteli ndi midzi yake, 32 ku Anatoti, Nobu ndi Ananiya, 33 ku Hazori, Rama ndi Gitaimu, 34 ku Hadidi, Zeboimu ndi Nebalati, 35 ku Lodi, Ono ndi ku chigwa cha Amisiri. 36 Magulu ena a Alevi a ku Yuda ankakhala ku Benjamini.

In Other Versions

Nehemiah 11 in the ANGEFD

Nehemiah 11 in the ANTPNG2D

Nehemiah 11 in the AS21

Nehemiah 11 in the BAGH

Nehemiah 11 in the BBPNG

Nehemiah 11 in the BBT1E

Nehemiah 11 in the BDS

Nehemiah 11 in the BEV

Nehemiah 11 in the BHAD

Nehemiah 11 in the BIB

Nehemiah 11 in the BLPT

Nehemiah 11 in the BNT

Nehemiah 11 in the BNTABOOT

Nehemiah 11 in the BNTLV

Nehemiah 11 in the BOATCB

Nehemiah 11 in the BOATCB2

Nehemiah 11 in the BOBCV

Nehemiah 11 in the BOCNT

Nehemiah 11 in the BOECS

Nehemiah 11 in the BOHCB

Nehemiah 11 in the BOHCV

Nehemiah 11 in the BOHLNT

Nehemiah 11 in the BOHNTLTAL

Nehemiah 11 in the BOICB

Nehemiah 11 in the BOILNTAP

Nehemiah 11 in the BOITCV

Nehemiah 11 in the BOKCV

Nehemiah 11 in the BOKCV2

Nehemiah 11 in the BOKHWOG

Nehemiah 11 in the BOKSSV

Nehemiah 11 in the BOLCB

Nehemiah 11 in the BOLCB2

Nehemiah 11 in the BOMCV

Nehemiah 11 in the BONAV

Nehemiah 11 in the BONCB

Nehemiah 11 in the BONLT

Nehemiah 11 in the BONUT2

Nehemiah 11 in the BOPLNT

Nehemiah 11 in the BOSCB

Nehemiah 11 in the BOSNC

Nehemiah 11 in the BOTLNT

Nehemiah 11 in the BOVCB

Nehemiah 11 in the BOYCB

Nehemiah 11 in the BPBB

Nehemiah 11 in the BPH

Nehemiah 11 in the BSB

Nehemiah 11 in the CCB

Nehemiah 11 in the CUV

Nehemiah 11 in the CUVS

Nehemiah 11 in the DBT

Nehemiah 11 in the DGDNT

Nehemiah 11 in the DHNT

Nehemiah 11 in the DNT

Nehemiah 11 in the ELBE

Nehemiah 11 in the EMTV

Nehemiah 11 in the ESV

Nehemiah 11 in the FBV

Nehemiah 11 in the FEB

Nehemiah 11 in the GGMNT

Nehemiah 11 in the GNT

Nehemiah 11 in the HARY

Nehemiah 11 in the HNT

Nehemiah 11 in the IRVA

Nehemiah 11 in the IRVB

Nehemiah 11 in the IRVG

Nehemiah 11 in the IRVH

Nehemiah 11 in the IRVK

Nehemiah 11 in the IRVM

Nehemiah 11 in the IRVM2

Nehemiah 11 in the IRVO

Nehemiah 11 in the IRVP

Nehemiah 11 in the IRVT

Nehemiah 11 in the IRVT2

Nehemiah 11 in the IRVU

Nehemiah 11 in the ISVN

Nehemiah 11 in the JSNT

Nehemiah 11 in the KAPI

Nehemiah 11 in the KBT1ETNIK

Nehemiah 11 in the KBV

Nehemiah 11 in the KJV

Nehemiah 11 in the KNFD

Nehemiah 11 in the LBA

Nehemiah 11 in the LBLA

Nehemiah 11 in the LNT

Nehemiah 11 in the LSV

Nehemiah 11 in the MAAL

Nehemiah 11 in the MBV

Nehemiah 11 in the MBV2

Nehemiah 11 in the MHNT

Nehemiah 11 in the MKNFD

Nehemiah 11 in the MNG

Nehemiah 11 in the MNT

Nehemiah 11 in the MNT2

Nehemiah 11 in the MRS1T

Nehemiah 11 in the NAA

Nehemiah 11 in the NASB

Nehemiah 11 in the NBLA

Nehemiah 11 in the NBS

Nehemiah 11 in the NBVTP

Nehemiah 11 in the NET2

Nehemiah 11 in the NIV11

Nehemiah 11 in the NNT

Nehemiah 11 in the NNT2

Nehemiah 11 in the NNT3

Nehemiah 11 in the PDDPT

Nehemiah 11 in the PFNT

Nehemiah 11 in the RMNT

Nehemiah 11 in the SBIAS

Nehemiah 11 in the SBIBS

Nehemiah 11 in the SBIBS2

Nehemiah 11 in the SBICS

Nehemiah 11 in the SBIDS

Nehemiah 11 in the SBIGS

Nehemiah 11 in the SBIHS

Nehemiah 11 in the SBIIS

Nehemiah 11 in the SBIIS2

Nehemiah 11 in the SBIIS3

Nehemiah 11 in the SBIKS

Nehemiah 11 in the SBIKS2

Nehemiah 11 in the SBIMS

Nehemiah 11 in the SBIOS

Nehemiah 11 in the SBIPS

Nehemiah 11 in the SBISS

Nehemiah 11 in the SBITS

Nehemiah 11 in the SBITS2

Nehemiah 11 in the SBITS3

Nehemiah 11 in the SBITS4

Nehemiah 11 in the SBIUS

Nehemiah 11 in the SBIVS

Nehemiah 11 in the SBT

Nehemiah 11 in the SBT1E

Nehemiah 11 in the SCHL

Nehemiah 11 in the SNT

Nehemiah 11 in the SUSU

Nehemiah 11 in the SUSU2

Nehemiah 11 in the SYNO

Nehemiah 11 in the TBIAOTANT

Nehemiah 11 in the TBT1E

Nehemiah 11 in the TBT1E2

Nehemiah 11 in the TFTIP

Nehemiah 11 in the TFTU

Nehemiah 11 in the TGNTATF3T

Nehemiah 11 in the THAI

Nehemiah 11 in the TNFD

Nehemiah 11 in the TNT

Nehemiah 11 in the TNTIK

Nehemiah 11 in the TNTIL

Nehemiah 11 in the TNTIN

Nehemiah 11 in the TNTIP

Nehemiah 11 in the TNTIZ

Nehemiah 11 in the TOMA

Nehemiah 11 in the TTENT

Nehemiah 11 in the UBG

Nehemiah 11 in the UGV

Nehemiah 11 in the UGV2

Nehemiah 11 in the UGV3

Nehemiah 11 in the VBL

Nehemiah 11 in the VDCC

Nehemiah 11 in the YALU

Nehemiah 11 in the YAPE

Nehemiah 11 in the YBVTP

Nehemiah 11 in the ZBP