Proverbs 9 (BOGWICC)

1 Nzeru inamanga nyumba yake;inayimika nsanamira zake zisanu ndi ziwiri. 2 Inapha ziweto zake ndipo yasakaniza vinyo wake;inasakaniza vinyo wake ndi kuyala tebulo lake. 3 Nzeruyo inatuma adzakazi ake,kuti akakhale pamwamba penipeni pa mzinda ndi kukalengeza kuti, 4 “Aliyense amene ali munthu wamba, abwere kuno!”Kwa onse opanda nzeru inkanena kuti, 5 “Bwerani, dzadyeni chakudya changandipo dzamweni vinyo amene ndakonza. 6 Lekani zopusa zanu kuti mukhale ndi moyo;yendani njira ya nzeru yomvetsa zinthu.” 7 Aliyense amene amayesa kukonza munthu wonyoza amadziputira minyozo;aliyense amene amadzudzula munthu woyipa amadetsa mbiri yake. 8 Usadzudzule munthu wonyoza kuti angadzadane nawe;dzudzula munthu wanzeru ndipo adzakukonda. 9 Ukalangiza munthu wanzeru ndiye adzapitirira kukhala wanzeru;ukaphunzitsa munthu wolungama ndiye adzawonjezera kuphunzira kwake. 10 Kuopa Yehova ndiye chiyambi cha nzeru;kudziwa Woyerayo ndiko kukhala womvetsa bwino zinthu. 11 Chifukwa cha ine nzeru, masiku ako adzachuluka,ndipo zaka za moyo wako zidzawonjezeredwa. 12 Ngati ndiwe wanzeru, nzeru yakoyo idzakupindulitsa;ngati ndiwe wonyoza ena, udzavutika wekha. 13 Uchitsiru ndi mkazi waphokoso,wopulikira ndiponso wosadziwa zinthu. 14 Iye amakhala pa mpando, pa khomo la nyumba yake,pamalo aatali a mu mzinda, 15 kuti aziyitana anthu ongodutsa,amene akunka nayenda njira zawo. 16 Amati, “Onse amene ndi anthu wamba abwere kuno,”ndipo kwa wopanda nzeru amati, 17 “Madzi akuba ndiye amatsekemera;chakudya chodya mobisa ndi chokoma!” 18 Koma amunawo sadziwa kuti akufa ali kale komweko,ndi kuti alendo ake alowa kale mʼmanda akuya.

In Other Versions

Proverbs 9 in the ANGEFD

Proverbs 9 in the ANTPNG2D

Proverbs 9 in the AS21

Proverbs 9 in the BAGH

Proverbs 9 in the BBPNG

Proverbs 9 in the BBT1E

Proverbs 9 in the BDS

Proverbs 9 in the BEV

Proverbs 9 in the BHAD

Proverbs 9 in the BIB

Proverbs 9 in the BLPT

Proverbs 9 in the BNT

Proverbs 9 in the BNTABOOT

Proverbs 9 in the BNTLV

Proverbs 9 in the BOATCB

Proverbs 9 in the BOATCB2

Proverbs 9 in the BOBCV

Proverbs 9 in the BOCNT

Proverbs 9 in the BOECS

Proverbs 9 in the BOHCB

Proverbs 9 in the BOHCV

Proverbs 9 in the BOHLNT

Proverbs 9 in the BOHNTLTAL

Proverbs 9 in the BOICB

Proverbs 9 in the BOILNTAP

Proverbs 9 in the BOITCV

Proverbs 9 in the BOKCV

Proverbs 9 in the BOKCV2

Proverbs 9 in the BOKHWOG

Proverbs 9 in the BOKSSV

Proverbs 9 in the BOLCB

Proverbs 9 in the BOLCB2

Proverbs 9 in the BOMCV

Proverbs 9 in the BONAV

Proverbs 9 in the BONCB

Proverbs 9 in the BONLT

Proverbs 9 in the BONUT2

Proverbs 9 in the BOPLNT

Proverbs 9 in the BOSCB

Proverbs 9 in the BOSNC

Proverbs 9 in the BOTLNT

Proverbs 9 in the BOVCB

Proverbs 9 in the BOYCB

Proverbs 9 in the BPBB

Proverbs 9 in the BPH

Proverbs 9 in the BSB

Proverbs 9 in the CCB

Proverbs 9 in the CUV

Proverbs 9 in the CUVS

Proverbs 9 in the DBT

Proverbs 9 in the DGDNT

Proverbs 9 in the DHNT

Proverbs 9 in the DNT

Proverbs 9 in the ELBE

Proverbs 9 in the EMTV

Proverbs 9 in the ESV

Proverbs 9 in the FBV

Proverbs 9 in the FEB

Proverbs 9 in the GGMNT

Proverbs 9 in the GNT

Proverbs 9 in the HARY

Proverbs 9 in the HNT

Proverbs 9 in the IRVA

Proverbs 9 in the IRVB

Proverbs 9 in the IRVG

Proverbs 9 in the IRVH

Proverbs 9 in the IRVK

Proverbs 9 in the IRVM

Proverbs 9 in the IRVM2

Proverbs 9 in the IRVO

Proverbs 9 in the IRVP

Proverbs 9 in the IRVT

Proverbs 9 in the IRVT2

Proverbs 9 in the IRVU

Proverbs 9 in the ISVN

Proverbs 9 in the JSNT

Proverbs 9 in the KAPI

Proverbs 9 in the KBT1ETNIK

Proverbs 9 in the KBV

Proverbs 9 in the KJV

Proverbs 9 in the KNFD

Proverbs 9 in the LBA

Proverbs 9 in the LBLA

Proverbs 9 in the LNT

Proverbs 9 in the LSV

Proverbs 9 in the MAAL

Proverbs 9 in the MBV

Proverbs 9 in the MBV2

Proverbs 9 in the MHNT

Proverbs 9 in the MKNFD

Proverbs 9 in the MNG

Proverbs 9 in the MNT

Proverbs 9 in the MNT2

Proverbs 9 in the MRS1T

Proverbs 9 in the NAA

Proverbs 9 in the NASB

Proverbs 9 in the NBLA

Proverbs 9 in the NBS

Proverbs 9 in the NBVTP

Proverbs 9 in the NET2

Proverbs 9 in the NIV11

Proverbs 9 in the NNT

Proverbs 9 in the NNT2

Proverbs 9 in the NNT3

Proverbs 9 in the PDDPT

Proverbs 9 in the PFNT

Proverbs 9 in the RMNT

Proverbs 9 in the SBIAS

Proverbs 9 in the SBIBS

Proverbs 9 in the SBIBS2

Proverbs 9 in the SBICS

Proverbs 9 in the SBIDS

Proverbs 9 in the SBIGS

Proverbs 9 in the SBIHS

Proverbs 9 in the SBIIS

Proverbs 9 in the SBIIS2

Proverbs 9 in the SBIIS3

Proverbs 9 in the SBIKS

Proverbs 9 in the SBIKS2

Proverbs 9 in the SBIMS

Proverbs 9 in the SBIOS

Proverbs 9 in the SBIPS

Proverbs 9 in the SBISS

Proverbs 9 in the SBITS

Proverbs 9 in the SBITS2

Proverbs 9 in the SBITS3

Proverbs 9 in the SBITS4

Proverbs 9 in the SBIUS

Proverbs 9 in the SBIVS

Proverbs 9 in the SBT

Proverbs 9 in the SBT1E

Proverbs 9 in the SCHL

Proverbs 9 in the SNT

Proverbs 9 in the SUSU

Proverbs 9 in the SUSU2

Proverbs 9 in the SYNO

Proverbs 9 in the TBIAOTANT

Proverbs 9 in the TBT1E

Proverbs 9 in the TBT1E2

Proverbs 9 in the TFTIP

Proverbs 9 in the TFTU

Proverbs 9 in the TGNTATF3T

Proverbs 9 in the THAI

Proverbs 9 in the TNFD

Proverbs 9 in the TNT

Proverbs 9 in the TNTIK

Proverbs 9 in the TNTIL

Proverbs 9 in the TNTIN

Proverbs 9 in the TNTIP

Proverbs 9 in the TNTIZ

Proverbs 9 in the TOMA

Proverbs 9 in the TTENT

Proverbs 9 in the UBG

Proverbs 9 in the UGV

Proverbs 9 in the UGV2

Proverbs 9 in the UGV3

Proverbs 9 in the VBL

Proverbs 9 in the VDCC

Proverbs 9 in the YALU

Proverbs 9 in the YAPE

Proverbs 9 in the YBVTP

Proverbs 9 in the ZBP