Psalms 45 (BOGWICC)
undefined Kwa mtsogoleri wamayimbidwe. Monga mwa mayimbidwe a “Maluwa a Kakombo.” Salimo la ana a Kora. Nyimbo ya pa ukwati. 1 Mtima wanga watakasika ndi nkhani yokomapamene ndikulakatula mawu anga kwa mfumu;lilime langa ndi cholembera cha wolemba waluso. 2 Inu ndinu abwino kwambiri kuposa anthu onsendipo milomo yanu inadzozedwa ndi chikondi cha Mulungu chosasinthika,popeza Mulungu wakudalitsani kwamuyaya. 3 Mangirirani lupanga lanu mʼchiwuno mwanu, inu munthu wamphamvu;mudziveke nokha ndi ulemerero ndi ukulu wanu. 4 Mu ukulu wanu mupite mutakwera mwachigonjetsomʼmalo mwa choonadi, kudzichepetsa ndi chilungamo;dzanja lanu lamanja lionetsere ntchito zanu zoopsa. 5 Mivi yanu yakuthwa ilase mitima ya adani a mfumu,mitundu ya anthu igwe pansi pa mapazi anu. 6 Mpando wanu waufumu, Inu Mulungu, udzakhala ku nthawi za nthawi;ndodo yaufumu yachilungamo idzakhala ndodo yaufumu ya ufumu wanu. 7 Inu mumakonda chilungamo ndi kudana ndi zoyipa;choncho Mulungu, Mulungu wanu, wakukhazikani pamwamba pa anzanupokudzozani ndi mafuta a chimwemwe. 8 Mikanjo yanu yonse ndi yonunkhira ndi mure ndi aloe ndi kasiya;kuchokera ku nyumba zaufumu zokongoletsedwa ndi mnyanga wanjovunyimbo za zoyimbira zazingwe zimakusangalatsani. 9 Ana aakazi a mafumu ali pakati pa akazi anu olemekezeka;ku dzanja lanu lamanja kuli mkwatibwi waufumu ali mu golide wa ku Ofiri. 10 Tamvera, iwe mwana wa mkazi ganizira ndipo tchera khutu;iwala anthu ako ndi nyumba ya abambo ako. 11 Mfumu yathedwa nzeru chifukwa cha kukongola kwako;mulemekeze pakuti iyeyo ndiye mbuye wako. 12 Mwana wa mkazi wa ku Turo adzabwera ndi mphatso,amuna a chuma adzafunafuna kukoma mtima kwako. 13 Wokongola kwambiri ndi mwana wa mfumu ali mʼchipinda mwake,chovala chake ndi cholukidwa ndi thonje ndi golide. 14 Atavala zovala zamaluwamaluwa akupita naye kwa mfumu;anamwali okhala naye akumutsatirandipo abweretsedwa kwa inu. 15 Iwo akuwaperekeza ndi chimwemwe ndi chisangalalo;akulowa mʼnyumba yaufumu. 16 Ana ako aamuna adzatenga malo a makolo ako;udzachititsa kuti akhale ana a mfumu mʼdziko lonse. 17 Ndidzabukitsa mbiri yako mʼmibado yonse;choncho mitundu yonse idzakutamanda ku nthawi za nthawi.
In Other Versions
Psalms 45 in the ANGEFD
Psalms 45 in the ANTPNG2D
Psalms 45 in the AS21
Psalms 45 in the BAGH
Psalms 45 in the BBPNG
Psalms 45 in the BBT1E
Psalms 45 in the BDS
Psalms 45 in the BEV
Psalms 45 in the BHAD
Psalms 45 in the BIB
Psalms 45 in the BLPT
Psalms 45 in the BNT
Psalms 45 in the BNTABOOT
Psalms 45 in the BNTLV
Psalms 45 in the BOATCB
Psalms 45 in the BOATCB2
Psalms 45 in the BOBCV
Psalms 45 in the BOCNT
Psalms 45 in the BOECS
Psalms 45 in the BOHCB
Psalms 45 in the BOHCV
Psalms 45 in the BOHLNT
Psalms 45 in the BOHNTLTAL
Psalms 45 in the BOICB
Psalms 45 in the BOILNTAP
Psalms 45 in the BOITCV
Psalms 45 in the BOKCV
Psalms 45 in the BOKCV2
Psalms 45 in the BOKHWOG
Psalms 45 in the BOKSSV
Psalms 45 in the BOLCB
Psalms 45 in the BOLCB2
Psalms 45 in the BOMCV
Psalms 45 in the BONAV
Psalms 45 in the BONCB
Psalms 45 in the BONLT
Psalms 45 in the BONUT2
Psalms 45 in the BOPLNT
Psalms 45 in the BOSCB
Psalms 45 in the BOSNC
Psalms 45 in the BOTLNT
Psalms 45 in the BOVCB
Psalms 45 in the BOYCB
Psalms 45 in the BPBB
Psalms 45 in the BPH
Psalms 45 in the BSB
Psalms 45 in the CCB
Psalms 45 in the CUV
Psalms 45 in the CUVS
Psalms 45 in the DBT
Psalms 45 in the DGDNT
Psalms 45 in the DHNT
Psalms 45 in the DNT
Psalms 45 in the ELBE
Psalms 45 in the EMTV
Psalms 45 in the ESV
Psalms 45 in the FBV
Psalms 45 in the FEB
Psalms 45 in the GGMNT
Psalms 45 in the GNT
Psalms 45 in the HARY
Psalms 45 in the HNT
Psalms 45 in the IRVA
Psalms 45 in the IRVB
Psalms 45 in the IRVG
Psalms 45 in the IRVH
Psalms 45 in the IRVK
Psalms 45 in the IRVM
Psalms 45 in the IRVM2
Psalms 45 in the IRVO
Psalms 45 in the IRVP
Psalms 45 in the IRVT
Psalms 45 in the IRVT2
Psalms 45 in the IRVU
Psalms 45 in the ISVN
Psalms 45 in the JSNT
Psalms 45 in the KAPI
Psalms 45 in the KBT1ETNIK
Psalms 45 in the KBV
Psalms 45 in the KJV
Psalms 45 in the KNFD
Psalms 45 in the LBA
Psalms 45 in the LBLA
Psalms 45 in the LNT
Psalms 45 in the LSV
Psalms 45 in the MAAL
Psalms 45 in the MBV
Psalms 45 in the MBV2
Psalms 45 in the MHNT
Psalms 45 in the MKNFD
Psalms 45 in the MNG
Psalms 45 in the MNT
Psalms 45 in the MNT2
Psalms 45 in the MRS1T
Psalms 45 in the NAA
Psalms 45 in the NASB
Psalms 45 in the NBLA
Psalms 45 in the NBS
Psalms 45 in the NBVTP
Psalms 45 in the NET2
Psalms 45 in the NIV11
Psalms 45 in the NNT
Psalms 45 in the NNT2
Psalms 45 in the NNT3
Psalms 45 in the PDDPT
Psalms 45 in the PFNT
Psalms 45 in the RMNT
Psalms 45 in the SBIAS
Psalms 45 in the SBIBS
Psalms 45 in the SBIBS2
Psalms 45 in the SBICS
Psalms 45 in the SBIDS
Psalms 45 in the SBIGS
Psalms 45 in the SBIHS
Psalms 45 in the SBIIS
Psalms 45 in the SBIIS2
Psalms 45 in the SBIIS3
Psalms 45 in the SBIKS
Psalms 45 in the SBIKS2
Psalms 45 in the SBIMS
Psalms 45 in the SBIOS
Psalms 45 in the SBIPS
Psalms 45 in the SBISS
Psalms 45 in the SBITS
Psalms 45 in the SBITS2
Psalms 45 in the SBITS3
Psalms 45 in the SBITS4
Psalms 45 in the SBIUS
Psalms 45 in the SBIVS
Psalms 45 in the SBT
Psalms 45 in the SBT1E
Psalms 45 in the SCHL
Psalms 45 in the SNT
Psalms 45 in the SUSU
Psalms 45 in the SUSU2
Psalms 45 in the SYNO
Psalms 45 in the TBIAOTANT
Psalms 45 in the TBT1E
Psalms 45 in the TBT1E2
Psalms 45 in the TFTIP
Psalms 45 in the TFTU
Psalms 45 in the TGNTATF3T
Psalms 45 in the THAI
Psalms 45 in the TNFD
Psalms 45 in the TNT
Psalms 45 in the TNTIK
Psalms 45 in the TNTIL
Psalms 45 in the TNTIN
Psalms 45 in the TNTIP
Psalms 45 in the TNTIZ
Psalms 45 in the TOMA
Psalms 45 in the TTENT
Psalms 45 in the UBG
Psalms 45 in the UGV
Psalms 45 in the UGV2
Psalms 45 in the UGV3
Psalms 45 in the VBL
Psalms 45 in the VDCC
Psalms 45 in the YALU
Psalms 45 in the YAPE
Psalms 45 in the YBVTP
Psalms 45 in the ZBP