Psalms 55 (BOGWICC)

undefined Kwa mtsogoleri wa mayimbidwe. Ndakatulo ya Davide. Pa zoyimbira za zingwe. 1 Mvetserani pemphero langa, Inu Mulungu,musakufulatire kupempha kwanga, 2 mverani ndipo mundiyankhe.Maganizo anga akundisautsa ndipo ndathedwa nzeru 3 chifukwa cha mawu a adani anga,chifukwa cha kupondereza kwa anthu oyipa;pakuti andidzetsera masautsondipo akundizunza mu mkwiyo wawo. 4 Mtima wanga ukupweteka mʼkati mwanga;mantha a imfa andigwera. 5 Mantha ndi kunjenjemera zandizinga;mantha aakulu andithetsa nzeru. 6 Ndinati, “Ndithu, ndikanakhala ndi mapiko ankhunda!Ndikanawulukira kutali ndi kukapuma. 7 Ndikanathawira kutalindi kukakhala mʼchipululu. 8 Ndikanathamangira kumalo anga a chitetezo;kutali ndi mphepo yaukali ndi yamkuntho.” 9 Sokonezani maganizo a oyipa, Inu Ambuye, tsutsani mawu awo;pakuti ine ndikuona chiwawa ndi mkangano mu mzinda. 10 Usana ndi usiku iwo akuzungulirazungulira pa makoma ake;nkhwidzi ndi kuzunza kuli mʼkati mwake. 11 Mphamvu zowononga zili pa ntchito mu mzinda;kuopseza ndi mabodza sizichoka mʼmisewu yake. 12 Akanakhala mdani akundinyoza, inendikanapirira;akanakhala mdani akudzikweza yekha kutsutsana nane,ndikanakabisala. 13 Koma iweyo mnzanga, mnzanga woyenda naye,bwenzi langa la pondaapanʼpondepo, ndi amene ukuchita zimenezi. 14 Mnzanga amene nthawi ina tinkasangalalapa chiyanjano chokoma ku nyumba ya Mulungu. 15 Mulole imfa itenge adani anga mwadzidzidzi;alowe mʼmanda ali amoyopakuti choyipa chili pakati pawo. 16 Koma ine ndinafuwulira kwa Mulungu,ndipo Yehova anandipulumutsa. 17 Madzulo, mmawa ndi masanandimalira mowawidwa mtima,ndipo Iye amamva mawu anga. 18 Iye amandiwombola ine osavulazidwapa nkhondo imene yafika kulimbana nane,ngakhale kuti ndi ambiri amene akunditsutsa. 19 Mulungu amene ali pa mpando wake kwamuyaya,adzandimenyera nkhondo; adzawatsitsa adani anga,chifukwa safuna kusintha njira zawo zoyipandipo saopa Mulungu. 20 Mnzanga woyenda naye wathira nkhondo abwenzi ake;iye akuphwanya pangano ake. 21 Mawu ake ndi osalala kuposa batalakomabe nkhondo ili mu mtima mwake;mawu ake ndi osalala kwambiri kuposa mafuta,komatu mawuwo ndi malupanga osololoka. 22 Tulani nkhawa zanu kwa Yehovandipo Iye adzakulimbitsani;Iye sadzalola kuti wolungama agwe. 23 Koma Inu Mulungu mudzawatsitsa anthu oyipakulowa mʼdzenje lachiwonongeko;anthu okhetsa magazi ndi anthu achinyengosadzakhala moyo theka la masiku awo, koma ine ndimadalira Inu.

In Other Versions

Psalms 55 in the ANGEFD

Psalms 55 in the ANTPNG2D

Psalms 55 in the AS21

Psalms 55 in the BAGH

Psalms 55 in the BBPNG

Psalms 55 in the BBT1E

Psalms 55 in the BDS

Psalms 55 in the BEV

Psalms 55 in the BHAD

Psalms 55 in the BIB

Psalms 55 in the BLPT

Psalms 55 in the BNT

Psalms 55 in the BNTABOOT

Psalms 55 in the BNTLV

Psalms 55 in the BOATCB

Psalms 55 in the BOATCB2

Psalms 55 in the BOBCV

Psalms 55 in the BOCNT

Psalms 55 in the BOECS

Psalms 55 in the BOHCB

Psalms 55 in the BOHCV

Psalms 55 in the BOHLNT

Psalms 55 in the BOHNTLTAL

Psalms 55 in the BOICB

Psalms 55 in the BOILNTAP

Psalms 55 in the BOITCV

Psalms 55 in the BOKCV

Psalms 55 in the BOKCV2

Psalms 55 in the BOKHWOG

Psalms 55 in the BOKSSV

Psalms 55 in the BOLCB

Psalms 55 in the BOLCB2

Psalms 55 in the BOMCV

Psalms 55 in the BONAV

Psalms 55 in the BONCB

Psalms 55 in the BONLT

Psalms 55 in the BONUT2

Psalms 55 in the BOPLNT

Psalms 55 in the BOSCB

Psalms 55 in the BOSNC

Psalms 55 in the BOTLNT

Psalms 55 in the BOVCB

Psalms 55 in the BOYCB

Psalms 55 in the BPBB

Psalms 55 in the BPH

Psalms 55 in the BSB

Psalms 55 in the CCB

Psalms 55 in the CUV

Psalms 55 in the CUVS

Psalms 55 in the DBT

Psalms 55 in the DGDNT

Psalms 55 in the DHNT

Psalms 55 in the DNT

Psalms 55 in the ELBE

Psalms 55 in the EMTV

Psalms 55 in the ESV

Psalms 55 in the FBV

Psalms 55 in the FEB

Psalms 55 in the GGMNT

Psalms 55 in the GNT

Psalms 55 in the HARY

Psalms 55 in the HNT

Psalms 55 in the IRVA

Psalms 55 in the IRVB

Psalms 55 in the IRVG

Psalms 55 in the IRVH

Psalms 55 in the IRVK

Psalms 55 in the IRVM

Psalms 55 in the IRVM2

Psalms 55 in the IRVO

Psalms 55 in the IRVP

Psalms 55 in the IRVT

Psalms 55 in the IRVT2

Psalms 55 in the IRVU

Psalms 55 in the ISVN

Psalms 55 in the JSNT

Psalms 55 in the KAPI

Psalms 55 in the KBT1ETNIK

Psalms 55 in the KBV

Psalms 55 in the KJV

Psalms 55 in the KNFD

Psalms 55 in the LBA

Psalms 55 in the LBLA

Psalms 55 in the LNT

Psalms 55 in the LSV

Psalms 55 in the MAAL

Psalms 55 in the MBV

Psalms 55 in the MBV2

Psalms 55 in the MHNT

Psalms 55 in the MKNFD

Psalms 55 in the MNG

Psalms 55 in the MNT

Psalms 55 in the MNT2

Psalms 55 in the MRS1T

Psalms 55 in the NAA

Psalms 55 in the NASB

Psalms 55 in the NBLA

Psalms 55 in the NBS

Psalms 55 in the NBVTP

Psalms 55 in the NET2

Psalms 55 in the NIV11

Psalms 55 in the NNT

Psalms 55 in the NNT2

Psalms 55 in the NNT3

Psalms 55 in the PDDPT

Psalms 55 in the PFNT

Psalms 55 in the RMNT

Psalms 55 in the SBIAS

Psalms 55 in the SBIBS

Psalms 55 in the SBIBS2

Psalms 55 in the SBICS

Psalms 55 in the SBIDS

Psalms 55 in the SBIGS

Psalms 55 in the SBIHS

Psalms 55 in the SBIIS

Psalms 55 in the SBIIS2

Psalms 55 in the SBIIS3

Psalms 55 in the SBIKS

Psalms 55 in the SBIKS2

Psalms 55 in the SBIMS

Psalms 55 in the SBIOS

Psalms 55 in the SBIPS

Psalms 55 in the SBISS

Psalms 55 in the SBITS

Psalms 55 in the SBITS2

Psalms 55 in the SBITS3

Psalms 55 in the SBITS4

Psalms 55 in the SBIUS

Psalms 55 in the SBIVS

Psalms 55 in the SBT

Psalms 55 in the SBT1E

Psalms 55 in the SCHL

Psalms 55 in the SNT

Psalms 55 in the SUSU

Psalms 55 in the SUSU2

Psalms 55 in the SYNO

Psalms 55 in the TBIAOTANT

Psalms 55 in the TBT1E

Psalms 55 in the TBT1E2

Psalms 55 in the TFTIP

Psalms 55 in the TFTU

Psalms 55 in the TGNTATF3T

Psalms 55 in the THAI

Psalms 55 in the TNFD

Psalms 55 in the TNT

Psalms 55 in the TNTIK

Psalms 55 in the TNTIL

Psalms 55 in the TNTIN

Psalms 55 in the TNTIP

Psalms 55 in the TNTIZ

Psalms 55 in the TOMA

Psalms 55 in the TTENT

Psalms 55 in the UBG

Psalms 55 in the UGV

Psalms 55 in the UGV2

Psalms 55 in the UGV3

Psalms 55 in the VBL

Psalms 55 in the VDCC

Psalms 55 in the YALU

Psalms 55 in the YAPE

Psalms 55 in the YBVTP

Psalms 55 in the ZBP