Psalms 73 (BOGWICC)
undefined Salimo la Asafu. 1 Mulungu ndi wabwino ndithu kwa Israeli,kwa iwo amene ndi oyera mtima. 2 Koma kunena za ine, mapazi anga anali pafupi kuterereka;ndinatsala pangʼono kugwa. 3 Pakuti ndinkachitira nsanje odzitamandira,pamene ndinaona mtendere wa anthu oyipa. 4 Iwo alibe zosautsa;matupi awo ndi athanzi ndi amphamvu. 5 Saona mavuto monga anthu ena;sazunzika ngati anthu ena onse. 6 Nʼchifukwa chake kunyada kuli monga mkanda wa mʼkhosi mwawo;amadziveka chiwawa. 7 Mʼmitima yawo yokhota mumachokera zolakwa;zoyipa zochokera mʼmaganizo awo sizidziwa malire. 8 Iwowo amanyogodola ndi kumayankhula zoyipa;mwa kudzikuza kwawo amaopseza ena nʼkumati, “Tikuponderezani.” 9 Pakamwa pawo pamayankhula monyoza Mulungu kumwambandipo lilime lawo limayenda pa dziko lapansi. 10 Nʼchifukwa chake anthu awo amapita kwa iwowondi kumwa madzi mochuluka. 11 Iwo amati, “Kodi Mulungu angadziwe bwanji?Kodi Wammwambamwamba angadziwe kalikonse?” 12 Umu ndi mmene oyipa alili;nthawi zonse ali pabwino ndipo chuma chawo chimachulukirachulukira. 13 Ndithudi ine ndawusunga pachabe mtima wanga woyera;pachabe ndasamba mʼmanja mwanga mwa kusalakwa kwanga. 14 Tsiku lonse ndapeza mavuto;ndakhala ndi kulangidwa mmawa uliwonse. 15 Ndikanati, “Ndidzayankhula motere,”ndikanachita chosakhulupirika kwa ana anu. 16 Pamene ndinayesa kuti ndimvetse zonsezi,zinandisautsa kwambiri 17 kufikira nditalowa mʼmalo opatulika a Mulungu;pamenepo ndinamvetsa mathero awo. 18 Zoonadi Inu munawayika pa malo woterera;Mumawagwetsa pansi kuti awonongeke. 19 Mwamsangamsanga iwo amawonongedwa,amasesedwa kwathunthu ndi mantha! 20 Monga loto pamene wina adzuka,kotero pamene Inu muuka, Inu Ambuye,mudzawanyoza ngati maloto chabe. 21 Pamene mtima wanga unasautsidwandi kuwawidwa mu mzimu mwanga, 22 ndinali wopusa ndi wosadziwa;ndinali chirombo chopanda nzeru pamaso panu. 23 Komabe ineyo ndili ndi Inu nthawi zonse;mumandigwira dzanja langa lamanja. 24 Inu mumanditsogolera ndi malangizo anundipo pambuyo pake mudzanditenga ku ulemerero. 25 Kodi kumwamba ndili ndi yani kupatula Inu?Ndipo dziko lapansi lilibe chilichonse chimene ndimachilakalaka koposa Inuyo. 26 Thupi ndi mtima wanga zitha kufowoka,koma Mulungu ndiye mphamvu ya mtima wangandi cholandira changa kwamuyaya. 27 Iwo amene ali kutali ndi Inu adzawonongeka;Inu mumawononga onse osakhulupirika pamaso panu. 28 Koma kunena za Ine ndi kwabwino kukhala pafupi ndi Mulungu.Ndatsimikiza kuti Ambuye Yehova ndiwo pothawirapo pangandipo ndidzalalika ntchito zanu zonse.
In Other Versions
Psalms 73 in the ANGEFD
Psalms 73 in the ANTPNG2D
Psalms 73 in the AS21
Psalms 73 in the BAGH
Psalms 73 in the BBPNG
Psalms 73 in the BBT1E
Psalms 73 in the BDS
Psalms 73 in the BEV
Psalms 73 in the BHAD
Psalms 73 in the BIB
Psalms 73 in the BLPT
Psalms 73 in the BNT
Psalms 73 in the BNTABOOT
Psalms 73 in the BNTLV
Psalms 73 in the BOATCB
Psalms 73 in the BOATCB2
Psalms 73 in the BOBCV
Psalms 73 in the BOCNT
Psalms 73 in the BOECS
Psalms 73 in the BOHCB
Psalms 73 in the BOHCV
Psalms 73 in the BOHLNT
Psalms 73 in the BOHNTLTAL
Psalms 73 in the BOICB
Psalms 73 in the BOILNTAP
Psalms 73 in the BOITCV
Psalms 73 in the BOKCV
Psalms 73 in the BOKCV2
Psalms 73 in the BOKHWOG
Psalms 73 in the BOKSSV
Psalms 73 in the BOLCB
Psalms 73 in the BOLCB2
Psalms 73 in the BOMCV
Psalms 73 in the BONAV
Psalms 73 in the BONCB
Psalms 73 in the BONLT
Psalms 73 in the BONUT2
Psalms 73 in the BOPLNT
Psalms 73 in the BOSCB
Psalms 73 in the BOSNC
Psalms 73 in the BOTLNT
Psalms 73 in the BOVCB
Psalms 73 in the BOYCB
Psalms 73 in the BPBB
Psalms 73 in the BPH
Psalms 73 in the BSB
Psalms 73 in the CCB
Psalms 73 in the CUV
Psalms 73 in the CUVS
Psalms 73 in the DBT
Psalms 73 in the DGDNT
Psalms 73 in the DHNT
Psalms 73 in the DNT
Psalms 73 in the ELBE
Psalms 73 in the EMTV
Psalms 73 in the ESV
Psalms 73 in the FBV
Psalms 73 in the FEB
Psalms 73 in the GGMNT
Psalms 73 in the GNT
Psalms 73 in the HARY
Psalms 73 in the HNT
Psalms 73 in the IRVA
Psalms 73 in the IRVB
Psalms 73 in the IRVG
Psalms 73 in the IRVH
Psalms 73 in the IRVK
Psalms 73 in the IRVM
Psalms 73 in the IRVM2
Psalms 73 in the IRVO
Psalms 73 in the IRVP
Psalms 73 in the IRVT
Psalms 73 in the IRVT2
Psalms 73 in the IRVU
Psalms 73 in the ISVN
Psalms 73 in the JSNT
Psalms 73 in the KAPI
Psalms 73 in the KBT1ETNIK
Psalms 73 in the KBV
Psalms 73 in the KJV
Psalms 73 in the KNFD
Psalms 73 in the LBA
Psalms 73 in the LBLA
Psalms 73 in the LNT
Psalms 73 in the LSV
Psalms 73 in the MAAL
Psalms 73 in the MBV
Psalms 73 in the MBV2
Psalms 73 in the MHNT
Psalms 73 in the MKNFD
Psalms 73 in the MNG
Psalms 73 in the MNT
Psalms 73 in the MNT2
Psalms 73 in the MRS1T
Psalms 73 in the NAA
Psalms 73 in the NASB
Psalms 73 in the NBLA
Psalms 73 in the NBS
Psalms 73 in the NBVTP
Psalms 73 in the NET2
Psalms 73 in the NIV11
Psalms 73 in the NNT
Psalms 73 in the NNT2
Psalms 73 in the NNT3
Psalms 73 in the PDDPT
Psalms 73 in the PFNT
Psalms 73 in the RMNT
Psalms 73 in the SBIAS
Psalms 73 in the SBIBS
Psalms 73 in the SBIBS2
Psalms 73 in the SBICS
Psalms 73 in the SBIDS
Psalms 73 in the SBIGS
Psalms 73 in the SBIHS
Psalms 73 in the SBIIS
Psalms 73 in the SBIIS2
Psalms 73 in the SBIIS3
Psalms 73 in the SBIKS
Psalms 73 in the SBIKS2
Psalms 73 in the SBIMS
Psalms 73 in the SBIOS
Psalms 73 in the SBIPS
Psalms 73 in the SBISS
Psalms 73 in the SBITS
Psalms 73 in the SBITS2
Psalms 73 in the SBITS3
Psalms 73 in the SBITS4
Psalms 73 in the SBIUS
Psalms 73 in the SBIVS
Psalms 73 in the SBT
Psalms 73 in the SBT1E
Psalms 73 in the SCHL
Psalms 73 in the SNT
Psalms 73 in the SUSU
Psalms 73 in the SUSU2
Psalms 73 in the SYNO
Psalms 73 in the TBIAOTANT
Psalms 73 in the TBT1E
Psalms 73 in the TBT1E2
Psalms 73 in the TFTIP
Psalms 73 in the TFTU
Psalms 73 in the TGNTATF3T
Psalms 73 in the THAI
Psalms 73 in the TNFD
Psalms 73 in the TNT
Psalms 73 in the TNTIK
Psalms 73 in the TNTIL
Psalms 73 in the TNTIN
Psalms 73 in the TNTIP
Psalms 73 in the TNTIZ
Psalms 73 in the TOMA
Psalms 73 in the TTENT
Psalms 73 in the UBG
Psalms 73 in the UGV
Psalms 73 in the UGV2
Psalms 73 in the UGV3
Psalms 73 in the VBL
Psalms 73 in the VDCC
Psalms 73 in the YALU
Psalms 73 in the YAPE
Psalms 73 in the YBVTP
Psalms 73 in the ZBP