1 Chronicles 24 (BOGWICC)
1 Magulu a ana a Aaroni anali awa:Ana a Aaroni anali Nadabu, Abihu, Eliezara ndi Itamara. 2 Koma Nadabu ndi Abihu anamwalira abambo awo asanamwalire, ndipo analibe ana aamuna. Kotero Eliezara ndi Itamara ankatumikira monga ansembe. 3 Mothandizidwa ndi Zadoki chidzukulu cha Eliezara ndi Ahimeleki chidzukulu cha Itamara, Davide anawagawa mʼmagulu molingana ndi ntchito yawo yotumikira. 4 Atsogoleri ambiri anapezeka pakati pa zidzukulu za Eliezara kusiyana ndi zidzukulu za Itamara ndipo anagawidwa moyenera: atsogoleri 16 a mabanja ochokera kwa Eliezara, ndipo atsogoleri asanu ndi atatu a mabanja ochokera kwa zidzukulu za Itamara. 5 Anawagawa mosakondera pochita maere, pakuti iwo anali akuluakulu a ku malo opatulika ndi akuluakulu a Mulungu pakati pa zidzukulu za Eliezara ndi Itamara. 6 Mlembi Semaya mwana wa Netaneli, Mlevi, analemba mayina awo pamaso pa mfumu ndi akuluakulu ake: wansembe Zadoki, Ahimeleki mwana wa Abiatara ndi atsogoleri a mabanja a ansembe ndiponso Alevi, banja limodzi kuchokera kwa Eliezara kenaka limodzi kuchokera kwa Itamara. 7 Maere woyamba anagwera Yehoyaribu,achiwiri anagwera Yedaya, 8 achitatu anagwera Harimu,achinayi anagwera Seorimu, 9 achisanu anagwera Malikiya,achisanu ndi chimodzi anagwera Miyamini, 10 achisanu ndi chiwiri anagwera Hakozi,achisanu ndi chitatu anagwera Abiya, 11 achisanu ndi chinayi anagwera Yesuwa,a khumi anagwera Sekaniya, 12 a 11 anagwera Eliyasibu,a 12 anagwera Yakimu, 13 a 13 anagwera Hupa,a 14 anagwera Yesebeabu, 14 a 15 anagwera Biliga,a 16 anagwera Imeri, 15 a 17 anagwera Heziri,a 18 anagwera Hapizezi, 16 a 19 anagwera Petahiya,a 20 anagwera Ezekieli, 17 a 21 anagwera Yakini,a 22 anagwera Gamuli, 18 a 23 anagwera Delaya,ndipo a 24 anagwera Maaziya. 19 Umu ndi mmene anasankhidwira kuti azigwira ntchito yotumikira pamene alowa mʼNyumba ya Yehova, motsatira dongosolo limene anapatsidwa ndi kholo lawo Aaroni, monga momwe Yehova Mulungu wa Israeli anamulamulira. 20 Za zidzukulu zina zonse za Levi:Kuchokera kwa ana a Amramu: Subaeli;kuchokera kwa ana a Subaeli: Yehideya. 21 Kwa Rehabiya, kuchokera kwa ana ake:Mtsogoleri anali Isiya. 22 Kuchokera ku banja la Izihari: Selomoti;kuchokera kwa ana a Selomoti: Yahati. 23 Ana a Hebroni: woyamba anali Yeriya, wachiwiri anali Amariya, wachitatu anali Yahazieli ndipo Yekameamu anali wachinayi. 24 Mwana wa Uzieli: Mika;kuchokera kwa ana a Mika: Samiri. 25 Mʼbale wa Mika: Isiya;kuchokera kwa ana a Isiya: Zekariya. 26 Ana a Merari: Mahili ndi Musi.Mwana wa Yaaziya: Beno. 27 Ana a Merari:Kuchokera kwa Yaaziya: Beno, Sohamu, Zakuri ndi Ibiri. 28 Kuchokera kwa Mahili: Eliezara, amene analibe ana aamuna. 29 Kuchokera kwa Kisi:Mwana wa Kisi: Yerahimeeli. 30 Ndipo ana a Musi: Mahili, Ederi ndi Yerimoti. Awa anali Alevi potsata mabanja a makolo awo. 31 Iwonso anachita maere, monga anachitira abale awo, zidzukulu za Aaroni, pamaso pa mfumu Davide, ndi Zadoki ndi Ahimeleki, atsogoleri a mabanja a ansembe ndi Alevi. Mabanja a mwana wamkulu anachita nawo mofanana ndi a mwana wamngʼono.
In Other Versions
1 Chronicles 24 in the ANGEFD
1 Chronicles 24 in the ANTPNG2D
1 Chronicles 24 in the AS21
1 Chronicles 24 in the BAGH
1 Chronicles 24 in the BBPNG
1 Chronicles 24 in the BBT1E
1 Chronicles 24 in the BDS
1 Chronicles 24 in the BEV
1 Chronicles 24 in the BHAD
1 Chronicles 24 in the BIB
1 Chronicles 24 in the BLPT
1 Chronicles 24 in the BNT
1 Chronicles 24 in the BNTABOOT
1 Chronicles 24 in the BNTLV
1 Chronicles 24 in the BOATCB
1 Chronicles 24 in the BOATCB2
1 Chronicles 24 in the BOBCV
1 Chronicles 24 in the BOCNT
1 Chronicles 24 in the BOECS
1 Chronicles 24 in the BOHCB
1 Chronicles 24 in the BOHCV
1 Chronicles 24 in the BOHLNT
1 Chronicles 24 in the BOHNTLTAL
1 Chronicles 24 in the BOICB
1 Chronicles 24 in the BOILNTAP
1 Chronicles 24 in the BOITCV
1 Chronicles 24 in the BOKCV
1 Chronicles 24 in the BOKCV2
1 Chronicles 24 in the BOKHWOG
1 Chronicles 24 in the BOKSSV
1 Chronicles 24 in the BOLCB
1 Chronicles 24 in the BOLCB2
1 Chronicles 24 in the BOMCV
1 Chronicles 24 in the BONAV
1 Chronicles 24 in the BONCB
1 Chronicles 24 in the BONLT
1 Chronicles 24 in the BONUT2
1 Chronicles 24 in the BOPLNT
1 Chronicles 24 in the BOSCB
1 Chronicles 24 in the BOSNC
1 Chronicles 24 in the BOTLNT
1 Chronicles 24 in the BOVCB
1 Chronicles 24 in the BOYCB
1 Chronicles 24 in the BPBB
1 Chronicles 24 in the BPH
1 Chronicles 24 in the BSB
1 Chronicles 24 in the CCB
1 Chronicles 24 in the CUV
1 Chronicles 24 in the CUVS
1 Chronicles 24 in the DBT
1 Chronicles 24 in the DGDNT
1 Chronicles 24 in the DHNT
1 Chronicles 24 in the DNT
1 Chronicles 24 in the ELBE
1 Chronicles 24 in the EMTV
1 Chronicles 24 in the ESV
1 Chronicles 24 in the FBV
1 Chronicles 24 in the FEB
1 Chronicles 24 in the GGMNT
1 Chronicles 24 in the GNT
1 Chronicles 24 in the HARY
1 Chronicles 24 in the HNT
1 Chronicles 24 in the IRVA
1 Chronicles 24 in the IRVB
1 Chronicles 24 in the IRVG
1 Chronicles 24 in the IRVH
1 Chronicles 24 in the IRVK
1 Chronicles 24 in the IRVM
1 Chronicles 24 in the IRVM2
1 Chronicles 24 in the IRVO
1 Chronicles 24 in the IRVP
1 Chronicles 24 in the IRVT
1 Chronicles 24 in the IRVT2
1 Chronicles 24 in the IRVU
1 Chronicles 24 in the ISVN
1 Chronicles 24 in the JSNT
1 Chronicles 24 in the KAPI
1 Chronicles 24 in the KBT1ETNIK
1 Chronicles 24 in the KBV
1 Chronicles 24 in the KJV
1 Chronicles 24 in the KNFD
1 Chronicles 24 in the LBA
1 Chronicles 24 in the LBLA
1 Chronicles 24 in the LNT
1 Chronicles 24 in the LSV
1 Chronicles 24 in the MAAL
1 Chronicles 24 in the MBV
1 Chronicles 24 in the MBV2
1 Chronicles 24 in the MHNT
1 Chronicles 24 in the MKNFD
1 Chronicles 24 in the MNG
1 Chronicles 24 in the MNT
1 Chronicles 24 in the MNT2
1 Chronicles 24 in the MRS1T
1 Chronicles 24 in the NAA
1 Chronicles 24 in the NASB
1 Chronicles 24 in the NBLA
1 Chronicles 24 in the NBS
1 Chronicles 24 in the NBVTP
1 Chronicles 24 in the NET2
1 Chronicles 24 in the NIV11
1 Chronicles 24 in the NNT
1 Chronicles 24 in the NNT2
1 Chronicles 24 in the NNT3
1 Chronicles 24 in the PDDPT
1 Chronicles 24 in the PFNT
1 Chronicles 24 in the RMNT
1 Chronicles 24 in the SBIAS
1 Chronicles 24 in the SBIBS
1 Chronicles 24 in the SBIBS2
1 Chronicles 24 in the SBICS
1 Chronicles 24 in the SBIDS
1 Chronicles 24 in the SBIGS
1 Chronicles 24 in the SBIHS
1 Chronicles 24 in the SBIIS
1 Chronicles 24 in the SBIIS2
1 Chronicles 24 in the SBIIS3
1 Chronicles 24 in the SBIKS
1 Chronicles 24 in the SBIKS2
1 Chronicles 24 in the SBIMS
1 Chronicles 24 in the SBIOS
1 Chronicles 24 in the SBIPS
1 Chronicles 24 in the SBISS
1 Chronicles 24 in the SBITS
1 Chronicles 24 in the SBITS2
1 Chronicles 24 in the SBITS3
1 Chronicles 24 in the SBITS4
1 Chronicles 24 in the SBIUS
1 Chronicles 24 in the SBIVS
1 Chronicles 24 in the SBT
1 Chronicles 24 in the SBT1E
1 Chronicles 24 in the SCHL
1 Chronicles 24 in the SNT
1 Chronicles 24 in the SUSU
1 Chronicles 24 in the SUSU2
1 Chronicles 24 in the SYNO
1 Chronicles 24 in the TBIAOTANT
1 Chronicles 24 in the TBT1E
1 Chronicles 24 in the TBT1E2
1 Chronicles 24 in the TFTIP
1 Chronicles 24 in the TFTU
1 Chronicles 24 in the TGNTATF3T
1 Chronicles 24 in the THAI
1 Chronicles 24 in the TNFD
1 Chronicles 24 in the TNT
1 Chronicles 24 in the TNTIK
1 Chronicles 24 in the TNTIL
1 Chronicles 24 in the TNTIN
1 Chronicles 24 in the TNTIP
1 Chronicles 24 in the TNTIZ
1 Chronicles 24 in the TOMA
1 Chronicles 24 in the TTENT
1 Chronicles 24 in the UBG
1 Chronicles 24 in the UGV
1 Chronicles 24 in the UGV2
1 Chronicles 24 in the UGV3
1 Chronicles 24 in the VBL
1 Chronicles 24 in the VDCC
1 Chronicles 24 in the YALU
1 Chronicles 24 in the YAPE
1 Chronicles 24 in the YBVTP
1 Chronicles 24 in the ZBP