1 Corinthians 3 (BOGWICC)
1 Ndipo abale sindikanakuyankhulani ngati auzimu koma adziko lapansi, makanda chabe mwa Khristu. 2 Ndinakupatsani mkaka osati chakudya cholimba pakuti munali musanakonzeke kuchilandira. Zoonadi, simunakonzekebe. 3 Mukanali adziko lapansi. Pakuti pakati panu pali kaduka ndi kukangana, kodi si inu a dziko lapansi? Kodi simukuchita ngati anthu wamba? 4 Pamene wina anena kuti, “Ine ndimatsatira Paulo,” ndipo wina akuti, “Ine ndimatsatira Apolo,” Kodi si inu akunja? 5 Ndiponso kodi Apolo ndi ndani? Nanga Paulo ndi ndani? Otumikira chabe, omwe kudzera mwa iwo inu munakhulupirira monga Ambuye anawagawira aliyense ntchito yake. 6 Ine ndinadzala mbewu, Apolo anayithirira, koma Mulungu ndiye anayikulitsa. 7 Choncho kuphatikiza iye wodzala ndi iye wothirira, onse sali kanthu, koma Mulungu yekha amene amakulitsa zinthu. 8 Munthu wodzala ndi munthu wothirira ali ndi cholinga chimodzi, ndipo aliyense adzapatsidwa mphotho molingana ndi ntchito yake. 9 Pakuti ife ndife antchito anzake a Mulungu; inu ndinu munda wa Mulungu, Nyumba ya Mulungu. 10 Mwachisomo chimene Mulungu wandipatsa, ine ndinayika maziko monga mmisiri waluntha, ndipo ena akumangapo. Koma aliyense ayenera kuchenjera mmene akumangira. 11 Pakuti wina sangayikenso maziko ena oposera amene anakhazikitsidwa kale, amene ndi Yesu Khristu. 12 Ngati munthu aliyense amanga pa maziko awa pogwiritsa ntchito golide, siliva, miyala yamtengowapatali, milimo yamitengo, tsekera kapena udzu, 13 ntchito yake idzaonekera pamene Tsiku la chiweruzo lidzazionetsa poyera. Tsikulo lidzafika ndi moto, ndipo motowo ndi umene udzayesa ntchito ya munthu aliyense. 14 Ngati zimene zamangidwazo sizidzagwa, adzalandira mphotho yake. 15 Ndipo ngati zidzanyeke ndi moto, sadzalandira mphotho koma iye mwini adzapulumukabe, koma monga ngati munthu amene wapulumuka mʼmoto. 16 Kodi inu simukudziwa kuti ndinu Nyumba ya Mulungu ndipo kuti Mzimu wa Mulungu amakhala mwa inu? 17 Ngati wina aliyense awononga Nyumba ya Mulunguyo, Mulungu nayenso adzamuwononga ameneyo; popeza Nyumba ya Mulungu ndi yopatulika ndipo Nyumbayo ndi inu amene. 18 Choncho musadzinyenge. Ngati wina wa inu akuganiza kuti ndi wanzeru pa mulingo wa mʼbado uno, ayenera kukhala “wopusa” kuti athe kukhala wanzeru. 19 Pakuti nzeru ya dziko lapansi ndi yopusa pamaso pa Mulungu. Monga kwalembedwera kuti, “Iye amakola anthu ochenjera mu msampha wa kuchenjera kwawo,” 20 ndiponso, “Ambuye amadziwa kuti maganizo a wanzeru ndi opandapake.” 21 Choncho, wina asanyadire anthu chabe! Zonse ndi zanu, 22 kaya Paulo kapena Apolo kapena Kefa kapena dziko lapansi, kapena moyo, kapena imfa, kapena tsopano, kapena mʼtsogolo, zonse ndi zanu, 23 ndipo inu ndinu a Khristu, ndipo Khristu ndi wa Mulungu.
In Other Versions
1 Corinthians 3 in the ANGEFD
1 Corinthians 3 in the ANTPNG2D
1 Corinthians 3 in the AS21
1 Corinthians 3 in the BAGH
1 Corinthians 3 in the BBPNG
1 Corinthians 3 in the BBT1E
1 Corinthians 3 in the BDS
1 Corinthians 3 in the BEV
1 Corinthians 3 in the BHAD
1 Corinthians 3 in the BIB
1 Corinthians 3 in the BLPT
1 Corinthians 3 in the BNT
1 Corinthians 3 in the BNTABOOT
1 Corinthians 3 in the BNTLV
1 Corinthians 3 in the BOATCB
1 Corinthians 3 in the BOATCB2
1 Corinthians 3 in the BOBCV
1 Corinthians 3 in the BOCNT
1 Corinthians 3 in the BOECS
1 Corinthians 3 in the BOHCB
1 Corinthians 3 in the BOHCV
1 Corinthians 3 in the BOHLNT
1 Corinthians 3 in the BOHNTLTAL
1 Corinthians 3 in the BOICB
1 Corinthians 3 in the BOILNTAP
1 Corinthians 3 in the BOITCV
1 Corinthians 3 in the BOKCV
1 Corinthians 3 in the BOKCV2
1 Corinthians 3 in the BOKHWOG
1 Corinthians 3 in the BOKSSV
1 Corinthians 3 in the BOLCB
1 Corinthians 3 in the BOLCB2
1 Corinthians 3 in the BOMCV
1 Corinthians 3 in the BONAV
1 Corinthians 3 in the BONCB
1 Corinthians 3 in the BONLT
1 Corinthians 3 in the BONUT2
1 Corinthians 3 in the BOPLNT
1 Corinthians 3 in the BOSCB
1 Corinthians 3 in the BOSNC
1 Corinthians 3 in the BOTLNT
1 Corinthians 3 in the BOVCB
1 Corinthians 3 in the BOYCB
1 Corinthians 3 in the BPBB
1 Corinthians 3 in the BPH
1 Corinthians 3 in the BSB
1 Corinthians 3 in the CCB
1 Corinthians 3 in the CUV
1 Corinthians 3 in the CUVS
1 Corinthians 3 in the DBT
1 Corinthians 3 in the DGDNT
1 Corinthians 3 in the DHNT
1 Corinthians 3 in the DNT
1 Corinthians 3 in the ELBE
1 Corinthians 3 in the EMTV
1 Corinthians 3 in the ESV
1 Corinthians 3 in the FBV
1 Corinthians 3 in the FEB
1 Corinthians 3 in the GGMNT
1 Corinthians 3 in the GNT
1 Corinthians 3 in the HARY
1 Corinthians 3 in the HNT
1 Corinthians 3 in the IRVA
1 Corinthians 3 in the IRVB
1 Corinthians 3 in the IRVG
1 Corinthians 3 in the IRVH
1 Corinthians 3 in the IRVK
1 Corinthians 3 in the IRVM
1 Corinthians 3 in the IRVM2
1 Corinthians 3 in the IRVO
1 Corinthians 3 in the IRVP
1 Corinthians 3 in the IRVT
1 Corinthians 3 in the IRVT2
1 Corinthians 3 in the IRVU
1 Corinthians 3 in the ISVN
1 Corinthians 3 in the JSNT
1 Corinthians 3 in the KAPI
1 Corinthians 3 in the KBT1ETNIK
1 Corinthians 3 in the KBV
1 Corinthians 3 in the KJV
1 Corinthians 3 in the KNFD
1 Corinthians 3 in the LBA
1 Corinthians 3 in the LBLA
1 Corinthians 3 in the LNT
1 Corinthians 3 in the LSV
1 Corinthians 3 in the MAAL
1 Corinthians 3 in the MBV
1 Corinthians 3 in the MBV2
1 Corinthians 3 in the MHNT
1 Corinthians 3 in the MKNFD
1 Corinthians 3 in the MNG
1 Corinthians 3 in the MNT
1 Corinthians 3 in the MNT2
1 Corinthians 3 in the MRS1T
1 Corinthians 3 in the NAA
1 Corinthians 3 in the NASB
1 Corinthians 3 in the NBLA
1 Corinthians 3 in the NBS
1 Corinthians 3 in the NBVTP
1 Corinthians 3 in the NET2
1 Corinthians 3 in the NIV11
1 Corinthians 3 in the NNT
1 Corinthians 3 in the NNT2
1 Corinthians 3 in the NNT3
1 Corinthians 3 in the PDDPT
1 Corinthians 3 in the PFNT
1 Corinthians 3 in the RMNT
1 Corinthians 3 in the SBIAS
1 Corinthians 3 in the SBIBS
1 Corinthians 3 in the SBIBS2
1 Corinthians 3 in the SBICS
1 Corinthians 3 in the SBIDS
1 Corinthians 3 in the SBIGS
1 Corinthians 3 in the SBIHS
1 Corinthians 3 in the SBIIS
1 Corinthians 3 in the SBIIS2
1 Corinthians 3 in the SBIIS3
1 Corinthians 3 in the SBIKS
1 Corinthians 3 in the SBIKS2
1 Corinthians 3 in the SBIMS
1 Corinthians 3 in the SBIOS
1 Corinthians 3 in the SBIPS
1 Corinthians 3 in the SBISS
1 Corinthians 3 in the SBITS
1 Corinthians 3 in the SBITS2
1 Corinthians 3 in the SBITS3
1 Corinthians 3 in the SBITS4
1 Corinthians 3 in the SBIUS
1 Corinthians 3 in the SBIVS
1 Corinthians 3 in the SBT
1 Corinthians 3 in the SBT1E
1 Corinthians 3 in the SCHL
1 Corinthians 3 in the SNT
1 Corinthians 3 in the SUSU
1 Corinthians 3 in the SUSU2
1 Corinthians 3 in the SYNO
1 Corinthians 3 in the TBIAOTANT
1 Corinthians 3 in the TBT1E
1 Corinthians 3 in the TBT1E2
1 Corinthians 3 in the TFTIP
1 Corinthians 3 in the TFTU
1 Corinthians 3 in the TGNTATF3T
1 Corinthians 3 in the THAI
1 Corinthians 3 in the TNFD
1 Corinthians 3 in the TNT
1 Corinthians 3 in the TNTIK
1 Corinthians 3 in the TNTIL
1 Corinthians 3 in the TNTIN
1 Corinthians 3 in the TNTIP
1 Corinthians 3 in the TNTIZ
1 Corinthians 3 in the TOMA
1 Corinthians 3 in the TTENT
1 Corinthians 3 in the UBG
1 Corinthians 3 in the UGV
1 Corinthians 3 in the UGV2
1 Corinthians 3 in the UGV3
1 Corinthians 3 in the VBL
1 Corinthians 3 in the VDCC
1 Corinthians 3 in the YALU
1 Corinthians 3 in the YAPE
1 Corinthians 3 in the YBVTP
1 Corinthians 3 in the ZBP