1 Timothy 3 (BOGWICC)

1 Mawu woona ndi awa: Ngati munthu akufunitsitsa atakhala woyangʼanira, ndiye kuti akufuna ntchito yabwino. 2 Tsono woyangʼanira ayenera kukhala munthu wopanda chotsutsika nacho, mwamuna wa mkazi mmodzi yekha, woganiza bwino, wodziretsa, waulemu, wosamala bwino alendo, wodziwa kuphunzitsa. 3 Asakhale chidakwa, asakhale wandewu, koma wofatsa, asakhale wokonda mikangano, kapena wokonda ndalama. 4 Akhale wodziwa kusamala bwino banja lake ndi kulera ana ake bwino, kuti akhale omvera ndi aulemu weniweni. 5 (Ngati munthu sadziwa kusamala banja lake lomwe, angathe bwanji kusamala mpingo wa Mulungu?) 6 Asakhale wongotembenuka mtima kumene kuopa kuti angadzitukumule napezeka pa chilango monga Satana. 7 Ayeneranso kukhala munthu wambiri yabwino ndi akunja, kuti anthu asamutonze nagwa mu msampha wa Satana. 8 Momwemonso atumiki, akhale anthu oyenera ulemu, woona mtima, osakhala okonda zoledzeretsa, osakonda kupeza zinthu mwachinyengo. 9 Ayenera kugwiritsa mozama choonadi cha chikhulupiriro ndi kukhala ndi chikumbumtima chabwino. 10 Ayambe ayesedwa kaye, ndipo ngati palibe kanthu kowatsutsa, aloleni akhale atumiki. 11 Momwemonso, akazi akhale olemekezeka, osasinjirira koma oganiza bwino ndi odalirika pa chilichonse. 12 Mtumiki akhale wokhulupirika kwa mkazi wake ndipo ayenera kukhala wosamalira bwino ana ake ndi onse a pa khomo pake. 13 Iwo amene atumikira bwino amakhala ndi mbiri yabwino ndipo amakhala chitsimikizo chachikulu cha chikhulupiriro chawo mwa Khristu Yesu. 14 Ngakhale ndili ndi chiyembekezo choti ndifika komweko posachedwapa, ndikukulemberani malangizo awa. 15 Ine zina zikandichedwetsa kubwera, mudziwe za mmene anthu ayenera kukhalira mʼNyumba ya Mulungu, imene ndi mpingo wa Mulungu wamoyo, mzati ndi maziko achoonadi. 16 Mosakayikira, chinsinsi cha chikhulupiriro chathu chachikulu:Khristu anaonekera ali ndi thupi la munthu,Mzimu anamuchitira umboni,angelo anamuona,analalikidwa pakati pa mitundu yonse,dziko lapansi linamukhulupirira,anatengedwa kupita kumwamba mwa ulemerero.

In Other Versions

1 Timothy 3 in the ANGEFD

1 Timothy 3 in the ANTPNG2D

1 Timothy 3 in the AS21

1 Timothy 3 in the BAGH

1 Timothy 3 in the BBPNG

1 Timothy 3 in the BBT1E

1 Timothy 3 in the BDS

1 Timothy 3 in the BEV

1 Timothy 3 in the BHAD

1 Timothy 3 in the BIB

1 Timothy 3 in the BLPT

1 Timothy 3 in the BNT

1 Timothy 3 in the BNTABOOT

1 Timothy 3 in the BNTLV

1 Timothy 3 in the BOATCB

1 Timothy 3 in the BOATCB2

1 Timothy 3 in the BOBCV

1 Timothy 3 in the BOCNT

1 Timothy 3 in the BOECS

1 Timothy 3 in the BOHCB

1 Timothy 3 in the BOHCV

1 Timothy 3 in the BOHLNT

1 Timothy 3 in the BOHNTLTAL

1 Timothy 3 in the BOICB

1 Timothy 3 in the BOILNTAP

1 Timothy 3 in the BOITCV

1 Timothy 3 in the BOKCV

1 Timothy 3 in the BOKCV2

1 Timothy 3 in the BOKHWOG

1 Timothy 3 in the BOKSSV

1 Timothy 3 in the BOLCB

1 Timothy 3 in the BOLCB2

1 Timothy 3 in the BOMCV

1 Timothy 3 in the BONAV

1 Timothy 3 in the BONCB

1 Timothy 3 in the BONLT

1 Timothy 3 in the BONUT2

1 Timothy 3 in the BOPLNT

1 Timothy 3 in the BOSCB

1 Timothy 3 in the BOSNC

1 Timothy 3 in the BOTLNT

1 Timothy 3 in the BOVCB

1 Timothy 3 in the BOYCB

1 Timothy 3 in the BPBB

1 Timothy 3 in the BPH

1 Timothy 3 in the BSB

1 Timothy 3 in the CCB

1 Timothy 3 in the CUV

1 Timothy 3 in the CUVS

1 Timothy 3 in the DBT

1 Timothy 3 in the DGDNT

1 Timothy 3 in the DHNT

1 Timothy 3 in the DNT

1 Timothy 3 in the ELBE

1 Timothy 3 in the EMTV

1 Timothy 3 in the ESV

1 Timothy 3 in the FBV

1 Timothy 3 in the FEB

1 Timothy 3 in the GGMNT

1 Timothy 3 in the GNT

1 Timothy 3 in the HARY

1 Timothy 3 in the HNT

1 Timothy 3 in the IRVA

1 Timothy 3 in the IRVB

1 Timothy 3 in the IRVG

1 Timothy 3 in the IRVH

1 Timothy 3 in the IRVK

1 Timothy 3 in the IRVM

1 Timothy 3 in the IRVM2

1 Timothy 3 in the IRVO

1 Timothy 3 in the IRVP

1 Timothy 3 in the IRVT

1 Timothy 3 in the IRVT2

1 Timothy 3 in the IRVU

1 Timothy 3 in the ISVN

1 Timothy 3 in the JSNT

1 Timothy 3 in the KAPI

1 Timothy 3 in the KBT1ETNIK

1 Timothy 3 in the KBV

1 Timothy 3 in the KJV

1 Timothy 3 in the KNFD

1 Timothy 3 in the LBA

1 Timothy 3 in the LBLA

1 Timothy 3 in the LNT

1 Timothy 3 in the LSV

1 Timothy 3 in the MAAL

1 Timothy 3 in the MBV

1 Timothy 3 in the MBV2

1 Timothy 3 in the MHNT

1 Timothy 3 in the MKNFD

1 Timothy 3 in the MNG

1 Timothy 3 in the MNT

1 Timothy 3 in the MNT2

1 Timothy 3 in the MRS1T

1 Timothy 3 in the NAA

1 Timothy 3 in the NASB

1 Timothy 3 in the NBLA

1 Timothy 3 in the NBS

1 Timothy 3 in the NBVTP

1 Timothy 3 in the NET2

1 Timothy 3 in the NIV11

1 Timothy 3 in the NNT

1 Timothy 3 in the NNT2

1 Timothy 3 in the NNT3

1 Timothy 3 in the PDDPT

1 Timothy 3 in the PFNT

1 Timothy 3 in the RMNT

1 Timothy 3 in the SBIAS

1 Timothy 3 in the SBIBS

1 Timothy 3 in the SBIBS2

1 Timothy 3 in the SBICS

1 Timothy 3 in the SBIDS

1 Timothy 3 in the SBIGS

1 Timothy 3 in the SBIHS

1 Timothy 3 in the SBIIS

1 Timothy 3 in the SBIIS2

1 Timothy 3 in the SBIIS3

1 Timothy 3 in the SBIKS

1 Timothy 3 in the SBIKS2

1 Timothy 3 in the SBIMS

1 Timothy 3 in the SBIOS

1 Timothy 3 in the SBIPS

1 Timothy 3 in the SBISS

1 Timothy 3 in the SBITS

1 Timothy 3 in the SBITS2

1 Timothy 3 in the SBITS3

1 Timothy 3 in the SBITS4

1 Timothy 3 in the SBIUS

1 Timothy 3 in the SBIVS

1 Timothy 3 in the SBT

1 Timothy 3 in the SBT1E

1 Timothy 3 in the SCHL

1 Timothy 3 in the SNT

1 Timothy 3 in the SUSU

1 Timothy 3 in the SUSU2

1 Timothy 3 in the SYNO

1 Timothy 3 in the TBIAOTANT

1 Timothy 3 in the TBT1E

1 Timothy 3 in the TBT1E2

1 Timothy 3 in the TFTIP

1 Timothy 3 in the TFTU

1 Timothy 3 in the TGNTATF3T

1 Timothy 3 in the THAI

1 Timothy 3 in the TNFD

1 Timothy 3 in the TNT

1 Timothy 3 in the TNTIK

1 Timothy 3 in the TNTIL

1 Timothy 3 in the TNTIN

1 Timothy 3 in the TNTIP

1 Timothy 3 in the TNTIZ

1 Timothy 3 in the TOMA

1 Timothy 3 in the TTENT

1 Timothy 3 in the UBG

1 Timothy 3 in the UGV

1 Timothy 3 in the UGV2

1 Timothy 3 in the UGV3

1 Timothy 3 in the VBL

1 Timothy 3 in the VDCC

1 Timothy 3 in the YALU

1 Timothy 3 in the YAPE

1 Timothy 3 in the YBVTP

1 Timothy 3 in the ZBP