2 Chronicles 22 (BOGWICC)
1 Anthu a mu Yerusalemu anayika Ahaziya mwana wamngʼono kwambiri wa Yehoramu kukhala mfumu mʼmalo mwake, popeza gulu lankhondo limene linabwera ndi Aarabu ku misasa, linapha ana onse aakulu. Motero Ahaziya mwana wa Yehoramu mfumu ya Yuda anayamba kulamulira. 2 Ahaziya anali wa zaka 22 pamene anakhala mfumu ndipo analamulira mu Yerusalemu chaka chimodzi. Dzina la amayi ake linali Ataliya, chidzukulu cha Omuri. 3 Nayenso anayenda mʼnjira ya banja la Ahabu, pakuti amayi ake anamulimbikitsa kuchita zolakwika. 4 Iye anachita zoyipa pamaso pa Yehova monga momwe banja la Ahabu linachitira, pakuti atamwalira abambo ake, iwo anakhala alangizi ake, kumene kunali kudziwononga kwake. 5 Iyeyo anatsatiranso uphungu wawo pamene anapita ndi Yehoramu, mwana wa Ahabu, mfumu ya Israeli kukachita nkhondo ndi Hazaeli mfumu ya Aramu ku Ramoti Giliyadi. Aaramu anavulaza Yehoramu, 6 kotero iye anabwerera ku Yezireeli kuti akachire mabala amene anamuvulaza ku Ramoti pa nkhondo ndi Hazaeli mfumu ya Aaramu.Ndipo Ahaziya, mwana wa Yehoramu mfumu ya Yuda anapita ku Yezireeli kukaona Yehoramu mwana wa Ahabu chifukwa anavulazidwa. 7 Mulungu anakonza kuti Ahaziya akaphedwe pa ulendo wake wokacheza. Ahaziya atafika, iye ndi Yoramu anapita kukakumana ndi Yehu mwana wa Nimisi, amene Yehova anamudzoza kuti akawononge banja la Ahabu. 8 Pamene Yehu ankalanga banja la Ahabu anapeza atsogoleri a ku Yuda ndiponso ana aamuna a abale ake a Ahaziya amene amatumikira Ahaziya, ndipo anawapha. 9 Kenaka anapita kukafunafuna Ahaziya, ndipo anthu ake anagwira Ahaziya pamene amabisala mu Samariya. Anabwera naye kwa Yehu ndipo anaphedwa. Iwo anamuyika mʼmanda, pakuti anati, “Iyeyu anali mwana wa Yehosafati amene anafunafuna Yehova ndi mtima wake wonse.” Kotero panalibe wamphamvu mʼbanja la Ahaziya kuti nʼkukhala mfumu. 10 Ataliya, amayi ake a Ahaziya, ataona kuti mwana wawo wafa, ananyamuka nakapha onse a banja laufumu la Yuda. 11 Koma Yehoseba, mwana wamkazi wa mfumu Yehoramu, anatenga Yowasi mwana wa Ahaziya, momuba ndi kumuchotsa pakati pa ana aamuna a mfumu amene amati aphedwe ndipo anamuyika iye ndi mlezi wake mʼchipinda chogona. Motero Yehoseba, mwana wamkazi wa mfumu Yehoramu, mkazi wa wansembe Yehoyada, yemwe anali mlongo wake wa Ahaziya anamubisa mwanayo kuti Ataliya asamuphe. 12 Mwanayo anakhala mobisala pamodzi ndi iwo mu Nyumba ya Mulungu kwa zaka zisanu ndi chimodzi muulamuliro wa Ataliya.
In Other Versions
2 Chronicles 22 in the ANGEFD
2 Chronicles 22 in the ANTPNG2D
2 Chronicles 22 in the AS21
2 Chronicles 22 in the BAGH
2 Chronicles 22 in the BBPNG
2 Chronicles 22 in the BBT1E
2 Chronicles 22 in the BDS
2 Chronicles 22 in the BEV
2 Chronicles 22 in the BHAD
2 Chronicles 22 in the BIB
2 Chronicles 22 in the BLPT
2 Chronicles 22 in the BNT
2 Chronicles 22 in the BNTABOOT
2 Chronicles 22 in the BNTLV
2 Chronicles 22 in the BOATCB
2 Chronicles 22 in the BOATCB2
2 Chronicles 22 in the BOBCV
2 Chronicles 22 in the BOCNT
2 Chronicles 22 in the BOECS
2 Chronicles 22 in the BOHCB
2 Chronicles 22 in the BOHCV
2 Chronicles 22 in the BOHLNT
2 Chronicles 22 in the BOHNTLTAL
2 Chronicles 22 in the BOICB
2 Chronicles 22 in the BOILNTAP
2 Chronicles 22 in the BOITCV
2 Chronicles 22 in the BOKCV
2 Chronicles 22 in the BOKCV2
2 Chronicles 22 in the BOKHWOG
2 Chronicles 22 in the BOKSSV
2 Chronicles 22 in the BOLCB
2 Chronicles 22 in the BOLCB2
2 Chronicles 22 in the BOMCV
2 Chronicles 22 in the BONAV
2 Chronicles 22 in the BONCB
2 Chronicles 22 in the BONLT
2 Chronicles 22 in the BONUT2
2 Chronicles 22 in the BOPLNT
2 Chronicles 22 in the BOSCB
2 Chronicles 22 in the BOSNC
2 Chronicles 22 in the BOTLNT
2 Chronicles 22 in the BOVCB
2 Chronicles 22 in the BOYCB
2 Chronicles 22 in the BPBB
2 Chronicles 22 in the BPH
2 Chronicles 22 in the BSB
2 Chronicles 22 in the CCB
2 Chronicles 22 in the CUV
2 Chronicles 22 in the CUVS
2 Chronicles 22 in the DBT
2 Chronicles 22 in the DGDNT
2 Chronicles 22 in the DHNT
2 Chronicles 22 in the DNT
2 Chronicles 22 in the ELBE
2 Chronicles 22 in the EMTV
2 Chronicles 22 in the ESV
2 Chronicles 22 in the FBV
2 Chronicles 22 in the FEB
2 Chronicles 22 in the GGMNT
2 Chronicles 22 in the GNT
2 Chronicles 22 in the HARY
2 Chronicles 22 in the HNT
2 Chronicles 22 in the IRVA
2 Chronicles 22 in the IRVB
2 Chronicles 22 in the IRVG
2 Chronicles 22 in the IRVH
2 Chronicles 22 in the IRVK
2 Chronicles 22 in the IRVM
2 Chronicles 22 in the IRVM2
2 Chronicles 22 in the IRVO
2 Chronicles 22 in the IRVP
2 Chronicles 22 in the IRVT
2 Chronicles 22 in the IRVT2
2 Chronicles 22 in the IRVU
2 Chronicles 22 in the ISVN
2 Chronicles 22 in the JSNT
2 Chronicles 22 in the KAPI
2 Chronicles 22 in the KBT1ETNIK
2 Chronicles 22 in the KBV
2 Chronicles 22 in the KJV
2 Chronicles 22 in the KNFD
2 Chronicles 22 in the LBA
2 Chronicles 22 in the LBLA
2 Chronicles 22 in the LNT
2 Chronicles 22 in the LSV
2 Chronicles 22 in the MAAL
2 Chronicles 22 in the MBV
2 Chronicles 22 in the MBV2
2 Chronicles 22 in the MHNT
2 Chronicles 22 in the MKNFD
2 Chronicles 22 in the MNG
2 Chronicles 22 in the MNT
2 Chronicles 22 in the MNT2
2 Chronicles 22 in the MRS1T
2 Chronicles 22 in the NAA
2 Chronicles 22 in the NASB
2 Chronicles 22 in the NBLA
2 Chronicles 22 in the NBS
2 Chronicles 22 in the NBVTP
2 Chronicles 22 in the NET2
2 Chronicles 22 in the NIV11
2 Chronicles 22 in the NNT
2 Chronicles 22 in the NNT2
2 Chronicles 22 in the NNT3
2 Chronicles 22 in the PDDPT
2 Chronicles 22 in the PFNT
2 Chronicles 22 in the RMNT
2 Chronicles 22 in the SBIAS
2 Chronicles 22 in the SBIBS
2 Chronicles 22 in the SBIBS2
2 Chronicles 22 in the SBICS
2 Chronicles 22 in the SBIDS
2 Chronicles 22 in the SBIGS
2 Chronicles 22 in the SBIHS
2 Chronicles 22 in the SBIIS
2 Chronicles 22 in the SBIIS2
2 Chronicles 22 in the SBIIS3
2 Chronicles 22 in the SBIKS
2 Chronicles 22 in the SBIKS2
2 Chronicles 22 in the SBIMS
2 Chronicles 22 in the SBIOS
2 Chronicles 22 in the SBIPS
2 Chronicles 22 in the SBISS
2 Chronicles 22 in the SBITS
2 Chronicles 22 in the SBITS2
2 Chronicles 22 in the SBITS3
2 Chronicles 22 in the SBITS4
2 Chronicles 22 in the SBIUS
2 Chronicles 22 in the SBIVS
2 Chronicles 22 in the SBT
2 Chronicles 22 in the SBT1E
2 Chronicles 22 in the SCHL
2 Chronicles 22 in the SNT
2 Chronicles 22 in the SUSU
2 Chronicles 22 in the SUSU2
2 Chronicles 22 in the SYNO
2 Chronicles 22 in the TBIAOTANT
2 Chronicles 22 in the TBT1E
2 Chronicles 22 in the TBT1E2
2 Chronicles 22 in the TFTIP
2 Chronicles 22 in the TFTU
2 Chronicles 22 in the TGNTATF3T
2 Chronicles 22 in the THAI
2 Chronicles 22 in the TNFD
2 Chronicles 22 in the TNT
2 Chronicles 22 in the TNTIK
2 Chronicles 22 in the TNTIL
2 Chronicles 22 in the TNTIN
2 Chronicles 22 in the TNTIP
2 Chronicles 22 in the TNTIZ
2 Chronicles 22 in the TOMA
2 Chronicles 22 in the TTENT
2 Chronicles 22 in the UBG
2 Chronicles 22 in the UGV
2 Chronicles 22 in the UGV2
2 Chronicles 22 in the UGV3
2 Chronicles 22 in the VBL
2 Chronicles 22 in the VDCC
2 Chronicles 22 in the YALU
2 Chronicles 22 in the YAPE
2 Chronicles 22 in the YBVTP
2 Chronicles 22 in the ZBP