2 Corinthians 3 (BOGWICC)

1 Kodi tayambanso kudzichitira umboni tokha? Kapena kodi ifenso tikufuna makalata otivomereza kwa inu, kapena ochokera kwa inu monga anthu ena? 2 Inu ndinu kalata yathu, yolembedwa pa mitima yathu, yodziwika ndi yowerengedwa ndi aliyense. 3 Inu mukuonetsa kuti ndinu kalata yochokera kwa Khristu, zotsatira za utumiki wathu, osati yolembedwa ndi inki koma ndi Mzimu wa Mulungu wamoyo, osati pa miyala yosemedwa koma mʼmitima ya anthu. 4 Kulimba mtima kumeneku tili nako pamaso pa Mulungu kudzera mwa Khristu. 5 Sikuti mwa ife muli kanthu kotiganizitsa kuti tingathe kugwira ntchitoyi patokha, koma kulimba mtima kwathu kumachokera kwa Mulungu. 6 Iye watipatsa kulimba mtima kuti tikhale atumiki a pangano latsopano, osati malamulo olembedwa koma a Mzimu; pakuti malamulo olembedwa amapha koma Mzimu amapereka moyo. 7 Koma ngati utumiki umene unabweretsa imfa uja, wolembedwa ndi malemba pa mwalawu, unabwera ndi ulemerero mwakuti Aisraeli sanathe kuyangʼanitsitsa nkhope ya Mose chifukwa cha ulemerero wa pa nkhopeyo, ngakhale kuti unali kunka nuzilala, 8 kodi nanga utumiki wa Mzimu sudzaposa apa? 9 Ngati utumiki umene umatsutsa anthu unali ndi ulemerero, nanga koposa kotani ulemerero wa utumiki wobweretsa chilungamo! 10 Pakuti zimene zinali ndi ulemerero, tsopano zilibenso ulemerero pofananitsa ndi ulemerero wopambanawo. 11 Ndipo ngati zosakhalitsa zinabwera ndi ulemerero, koposa kotani ulemerero wamuyayawo! 12 Choncho, popeza tili ndi chiyembekezo chotere, ndife olimba mtima kwambiri. 13 Ife sitili ngati Mose amene amaphimba nkhope yake kuopa kuti Aisraeli angaone kuti kunyezimira kwa nkhope yake kumazilala. 14 Koma nzeru zawo zinawumitsidwa, pakuti mpaka lero chophimbira chomwecho chikanalipo pamene akuwerenga Chipangano Chakale. Sichinachotsedwebe, chifukwa chimachotsedwa ngati munthuyo ali mwa Khristu yekha. 15 Ngakhale lero lomwe lino akuwerenga mabuku a Mose pali chophimbabe mitima yawo. 16 Koma pamene aliyense atembenukira kwa Ambuye, “chophimbacho chimachotsedwa.” 17 Tsono Ambuye ndi Mzimu, ndipo pamene pali Mzimu wa Ambuye, pali ufulu. 18 Ife tonse, amene ndi nkhope zosaphimba timaonetsera ulemerero wa Ambuye, tikusinthika kufanana ndi ulemerero wake, umene ukunka nuchulukirachulukira, wochokera kwa Ambuye, amene ndi Mzimu.

In Other Versions

2 Corinthians 3 in the ANGEFD

2 Corinthians 3 in the ANTPNG2D

2 Corinthians 3 in the AS21

2 Corinthians 3 in the BAGH

2 Corinthians 3 in the BBPNG

2 Corinthians 3 in the BBT1E

2 Corinthians 3 in the BDS

2 Corinthians 3 in the BEV

2 Corinthians 3 in the BHAD

2 Corinthians 3 in the BIB

2 Corinthians 3 in the BLPT

2 Corinthians 3 in the BNT

2 Corinthians 3 in the BNTABOOT

2 Corinthians 3 in the BNTLV

2 Corinthians 3 in the BOATCB

2 Corinthians 3 in the BOATCB2

2 Corinthians 3 in the BOBCV

2 Corinthians 3 in the BOCNT

2 Corinthians 3 in the BOECS

2 Corinthians 3 in the BOHCB

2 Corinthians 3 in the BOHCV

2 Corinthians 3 in the BOHLNT

2 Corinthians 3 in the BOHNTLTAL

2 Corinthians 3 in the BOICB

2 Corinthians 3 in the BOILNTAP

2 Corinthians 3 in the BOITCV

2 Corinthians 3 in the BOKCV

2 Corinthians 3 in the BOKCV2

2 Corinthians 3 in the BOKHWOG

2 Corinthians 3 in the BOKSSV

2 Corinthians 3 in the BOLCB

2 Corinthians 3 in the BOLCB2

2 Corinthians 3 in the BOMCV

2 Corinthians 3 in the BONAV

2 Corinthians 3 in the BONCB

2 Corinthians 3 in the BONLT

2 Corinthians 3 in the BONUT2

2 Corinthians 3 in the BOPLNT

2 Corinthians 3 in the BOSCB

2 Corinthians 3 in the BOSNC

2 Corinthians 3 in the BOTLNT

2 Corinthians 3 in the BOVCB

2 Corinthians 3 in the BOYCB

2 Corinthians 3 in the BPBB

2 Corinthians 3 in the BPH

2 Corinthians 3 in the BSB

2 Corinthians 3 in the CCB

2 Corinthians 3 in the CUV

2 Corinthians 3 in the CUVS

2 Corinthians 3 in the DBT

2 Corinthians 3 in the DGDNT

2 Corinthians 3 in the DHNT

2 Corinthians 3 in the DNT

2 Corinthians 3 in the ELBE

2 Corinthians 3 in the EMTV

2 Corinthians 3 in the ESV

2 Corinthians 3 in the FBV

2 Corinthians 3 in the FEB

2 Corinthians 3 in the GGMNT

2 Corinthians 3 in the GNT

2 Corinthians 3 in the HARY

2 Corinthians 3 in the HNT

2 Corinthians 3 in the IRVA

2 Corinthians 3 in the IRVB

2 Corinthians 3 in the IRVG

2 Corinthians 3 in the IRVH

2 Corinthians 3 in the IRVK

2 Corinthians 3 in the IRVM

2 Corinthians 3 in the IRVM2

2 Corinthians 3 in the IRVO

2 Corinthians 3 in the IRVP

2 Corinthians 3 in the IRVT

2 Corinthians 3 in the IRVT2

2 Corinthians 3 in the IRVU

2 Corinthians 3 in the ISVN

2 Corinthians 3 in the JSNT

2 Corinthians 3 in the KAPI

2 Corinthians 3 in the KBT1ETNIK

2 Corinthians 3 in the KBV

2 Corinthians 3 in the KJV

2 Corinthians 3 in the KNFD

2 Corinthians 3 in the LBA

2 Corinthians 3 in the LBLA

2 Corinthians 3 in the LNT

2 Corinthians 3 in the LSV

2 Corinthians 3 in the MAAL

2 Corinthians 3 in the MBV

2 Corinthians 3 in the MBV2

2 Corinthians 3 in the MHNT

2 Corinthians 3 in the MKNFD

2 Corinthians 3 in the MNG

2 Corinthians 3 in the MNT

2 Corinthians 3 in the MNT2

2 Corinthians 3 in the MRS1T

2 Corinthians 3 in the NAA

2 Corinthians 3 in the NASB

2 Corinthians 3 in the NBLA

2 Corinthians 3 in the NBS

2 Corinthians 3 in the NBVTP

2 Corinthians 3 in the NET2

2 Corinthians 3 in the NIV11

2 Corinthians 3 in the NNT

2 Corinthians 3 in the NNT2

2 Corinthians 3 in the NNT3

2 Corinthians 3 in the PDDPT

2 Corinthians 3 in the PFNT

2 Corinthians 3 in the RMNT

2 Corinthians 3 in the SBIAS

2 Corinthians 3 in the SBIBS

2 Corinthians 3 in the SBIBS2

2 Corinthians 3 in the SBICS

2 Corinthians 3 in the SBIDS

2 Corinthians 3 in the SBIGS

2 Corinthians 3 in the SBIHS

2 Corinthians 3 in the SBIIS

2 Corinthians 3 in the SBIIS2

2 Corinthians 3 in the SBIIS3

2 Corinthians 3 in the SBIKS

2 Corinthians 3 in the SBIKS2

2 Corinthians 3 in the SBIMS

2 Corinthians 3 in the SBIOS

2 Corinthians 3 in the SBIPS

2 Corinthians 3 in the SBISS

2 Corinthians 3 in the SBITS

2 Corinthians 3 in the SBITS2

2 Corinthians 3 in the SBITS3

2 Corinthians 3 in the SBITS4

2 Corinthians 3 in the SBIUS

2 Corinthians 3 in the SBIVS

2 Corinthians 3 in the SBT

2 Corinthians 3 in the SBT1E

2 Corinthians 3 in the SCHL

2 Corinthians 3 in the SNT

2 Corinthians 3 in the SUSU

2 Corinthians 3 in the SUSU2

2 Corinthians 3 in the SYNO

2 Corinthians 3 in the TBIAOTANT

2 Corinthians 3 in the TBT1E

2 Corinthians 3 in the TBT1E2

2 Corinthians 3 in the TFTIP

2 Corinthians 3 in the TFTU

2 Corinthians 3 in the TGNTATF3T

2 Corinthians 3 in the THAI

2 Corinthians 3 in the TNFD

2 Corinthians 3 in the TNT

2 Corinthians 3 in the TNTIK

2 Corinthians 3 in the TNTIL

2 Corinthians 3 in the TNTIN

2 Corinthians 3 in the TNTIP

2 Corinthians 3 in the TNTIZ

2 Corinthians 3 in the TOMA

2 Corinthians 3 in the TTENT

2 Corinthians 3 in the UBG

2 Corinthians 3 in the UGV

2 Corinthians 3 in the UGV2

2 Corinthians 3 in the UGV3

2 Corinthians 3 in the VBL

2 Corinthians 3 in the VDCC

2 Corinthians 3 in the YALU

2 Corinthians 3 in the YAPE

2 Corinthians 3 in the YBVTP

2 Corinthians 3 in the ZBP