2 Corinthians 7 (BOGWICC)

1 Abwenzi okondedwa, popeza tili ndi malonjezo amenewa, tiyeni tidziyeretse, kusiyana nazo zilizonse zimene zikhoza kudetsa thupi ndi mzimu, ndipo tiyesetse kukhala oyera mtima poopa Mulungu. 2 Mutipatse malo mʼmitima mwanu. Ife sitinalakwire munthu aliyense, kapena kuyipitsa munthu aliyense, kapena kumuchenjerera munthu aliyense. 3 Sindikunena izi kuti mupezeke olakwa. Ndinanena kale kuti ife timakuganizirani kwambiri kotero kuti tili pamodzi, ngakhale tikhale moyo kapena timwalire. 4 Ndimakukhulupirirani kwambiri ndipo ndimakunyadirani kwambiri. Ndikulimbikitsidwa kwambiri; mʼmasautso athu onse, chimwemwe changa chilibe malire. 5 Pakuti titafika ku Makedoniya, sitinapume nʼkomwe, koma tinavutitsidwa mbali zonse. Kunja kunali mikangano, ndipo mʼmitima mwathu munali mantha. 6 Koma Mulungu, amene amatonthoza mtima wopsinjika, anatitonthoza mtima ndi kufika kwa Tito, 7 sikubwera kwake kokhako, komanso mawu achilimbikitso amene analandira kuchokera kwa inu. Iye anatiwuza kuti mukufuna kundiona, zachisoni chanu chachikulu, ndi kudzipereka kwanu kwa ine, motero chimwemwe changa chinachuluka kuposa kale. 8 Ngakhale kalata yanga ija inakupwetekani mtima, sindikudandaula kuti ndinalemberanji. Ngakhale zinandikhudza, ndikudziwa kuti kalata yanga inakupwetekani, koma kwa kanthawi kochepa. 9 Koma tsopano ndine wokondwa, osati chifukwa chakuti kalatayo inakupwetekani, koma chifukwa chakuti chisoni chanu chinakuthandizani kutembenuka mtima. Pakuti munamva chisoni monga mmene Mulungu amafunira, choncho simunapwetekedwe mwanjira iliyonse. 10 Chisoni chimene Mulungu amafuna chimabweretsa kutembenuka mtima komwe kumabweretsa chipulumutso, ndipo sichikhumudwitsa. Koma chisoni cha dziko lapansi chimabweretsa imfa. 11 Taonani zimene chisoni chimene Mulungu amafuna chatulutsa mwa inu. Chatulutsa khama lalikulu, chakuthandizani kuti mudzikonze nokha, chakukwiyitsani kwambiri, komanso chakupatsani mantha aakulu. Chakuchititsani kuti mufune kundiona ine, mwakhudzidwa kwambiri ndipo mukufuna kuonetsetsa kuti chilungamo chachitikadi. Pa nkhani yonseyi, mwaonetsadi kuti ndinu osalakwa. 12 Choncho ngakhale ndinakulemberani kalata ija, sindinayilembe ndi chifukwa cha amene analakwayo kapena wolakwiridwa, koma ndinayilemba kuti inuyo muone kudzipereka kwanu kwa ife pamaso a Mulungu. 13 Zimenezi zatilimbikitsa kwambiri.Kuwonjezera pa zotilimbikitsazo, tinakondwa kwambiri poona chisangalalo cha Tito, chifukwa nonsenu munamuthandiza kukhazikitsa mtima wake pansi. 14 Ndinamuwuza kuti ndimakunyadirani, ndipo simunandichititse manyazi. Koma monga zonse zimene tinakuwuzani zinali zoona, tsono zomwe ndinawuza Tito zokunyadirani zinali zoona. 15 Ndipo chikondi chake pa inu nʼchachikulu kwambiri akakumbukira kuti nonse munali omvera, munamulandira ndi mantha ndi kunjenjemera. 16 Ndine wokondwa kuti ndingathe kukukhulupirirani pa zonse.

In Other Versions

2 Corinthians 7 in the ANGEFD

2 Corinthians 7 in the ANTPNG2D

2 Corinthians 7 in the AS21

2 Corinthians 7 in the BAGH

2 Corinthians 7 in the BBPNG

2 Corinthians 7 in the BBT1E

2 Corinthians 7 in the BDS

2 Corinthians 7 in the BEV

2 Corinthians 7 in the BHAD

2 Corinthians 7 in the BIB

2 Corinthians 7 in the BLPT

2 Corinthians 7 in the BNT

2 Corinthians 7 in the BNTABOOT

2 Corinthians 7 in the BNTLV

2 Corinthians 7 in the BOATCB

2 Corinthians 7 in the BOATCB2

2 Corinthians 7 in the BOBCV

2 Corinthians 7 in the BOCNT

2 Corinthians 7 in the BOECS

2 Corinthians 7 in the BOHCB

2 Corinthians 7 in the BOHCV

2 Corinthians 7 in the BOHLNT

2 Corinthians 7 in the BOHNTLTAL

2 Corinthians 7 in the BOICB

2 Corinthians 7 in the BOILNTAP

2 Corinthians 7 in the BOITCV

2 Corinthians 7 in the BOKCV

2 Corinthians 7 in the BOKCV2

2 Corinthians 7 in the BOKHWOG

2 Corinthians 7 in the BOKSSV

2 Corinthians 7 in the BOLCB

2 Corinthians 7 in the BOLCB2

2 Corinthians 7 in the BOMCV

2 Corinthians 7 in the BONAV

2 Corinthians 7 in the BONCB

2 Corinthians 7 in the BONLT

2 Corinthians 7 in the BONUT2

2 Corinthians 7 in the BOPLNT

2 Corinthians 7 in the BOSCB

2 Corinthians 7 in the BOSNC

2 Corinthians 7 in the BOTLNT

2 Corinthians 7 in the BOVCB

2 Corinthians 7 in the BOYCB

2 Corinthians 7 in the BPBB

2 Corinthians 7 in the BPH

2 Corinthians 7 in the BSB

2 Corinthians 7 in the CCB

2 Corinthians 7 in the CUV

2 Corinthians 7 in the CUVS

2 Corinthians 7 in the DBT

2 Corinthians 7 in the DGDNT

2 Corinthians 7 in the DHNT

2 Corinthians 7 in the DNT

2 Corinthians 7 in the ELBE

2 Corinthians 7 in the EMTV

2 Corinthians 7 in the ESV

2 Corinthians 7 in the FBV

2 Corinthians 7 in the FEB

2 Corinthians 7 in the GGMNT

2 Corinthians 7 in the GNT

2 Corinthians 7 in the HARY

2 Corinthians 7 in the HNT

2 Corinthians 7 in the IRVA

2 Corinthians 7 in the IRVB

2 Corinthians 7 in the IRVG

2 Corinthians 7 in the IRVH

2 Corinthians 7 in the IRVK

2 Corinthians 7 in the IRVM

2 Corinthians 7 in the IRVM2

2 Corinthians 7 in the IRVO

2 Corinthians 7 in the IRVP

2 Corinthians 7 in the IRVT

2 Corinthians 7 in the IRVT2

2 Corinthians 7 in the IRVU

2 Corinthians 7 in the ISVN

2 Corinthians 7 in the JSNT

2 Corinthians 7 in the KAPI

2 Corinthians 7 in the KBT1ETNIK

2 Corinthians 7 in the KBV

2 Corinthians 7 in the KJV

2 Corinthians 7 in the KNFD

2 Corinthians 7 in the LBA

2 Corinthians 7 in the LBLA

2 Corinthians 7 in the LNT

2 Corinthians 7 in the LSV

2 Corinthians 7 in the MAAL

2 Corinthians 7 in the MBV

2 Corinthians 7 in the MBV2

2 Corinthians 7 in the MHNT

2 Corinthians 7 in the MKNFD

2 Corinthians 7 in the MNG

2 Corinthians 7 in the MNT

2 Corinthians 7 in the MNT2

2 Corinthians 7 in the MRS1T

2 Corinthians 7 in the NAA

2 Corinthians 7 in the NASB

2 Corinthians 7 in the NBLA

2 Corinthians 7 in the NBS

2 Corinthians 7 in the NBVTP

2 Corinthians 7 in the NET2

2 Corinthians 7 in the NIV11

2 Corinthians 7 in the NNT

2 Corinthians 7 in the NNT2

2 Corinthians 7 in the NNT3

2 Corinthians 7 in the PDDPT

2 Corinthians 7 in the PFNT

2 Corinthians 7 in the RMNT

2 Corinthians 7 in the SBIAS

2 Corinthians 7 in the SBIBS

2 Corinthians 7 in the SBIBS2

2 Corinthians 7 in the SBICS

2 Corinthians 7 in the SBIDS

2 Corinthians 7 in the SBIGS

2 Corinthians 7 in the SBIHS

2 Corinthians 7 in the SBIIS

2 Corinthians 7 in the SBIIS2

2 Corinthians 7 in the SBIIS3

2 Corinthians 7 in the SBIKS

2 Corinthians 7 in the SBIKS2

2 Corinthians 7 in the SBIMS

2 Corinthians 7 in the SBIOS

2 Corinthians 7 in the SBIPS

2 Corinthians 7 in the SBISS

2 Corinthians 7 in the SBITS

2 Corinthians 7 in the SBITS2

2 Corinthians 7 in the SBITS3

2 Corinthians 7 in the SBITS4

2 Corinthians 7 in the SBIUS

2 Corinthians 7 in the SBIVS

2 Corinthians 7 in the SBT

2 Corinthians 7 in the SBT1E

2 Corinthians 7 in the SCHL

2 Corinthians 7 in the SNT

2 Corinthians 7 in the SUSU

2 Corinthians 7 in the SUSU2

2 Corinthians 7 in the SYNO

2 Corinthians 7 in the TBIAOTANT

2 Corinthians 7 in the TBT1E

2 Corinthians 7 in the TBT1E2

2 Corinthians 7 in the TFTIP

2 Corinthians 7 in the TFTU

2 Corinthians 7 in the TGNTATF3T

2 Corinthians 7 in the THAI

2 Corinthians 7 in the TNFD

2 Corinthians 7 in the TNT

2 Corinthians 7 in the TNTIK

2 Corinthians 7 in the TNTIL

2 Corinthians 7 in the TNTIN

2 Corinthians 7 in the TNTIP

2 Corinthians 7 in the TNTIZ

2 Corinthians 7 in the TOMA

2 Corinthians 7 in the TTENT

2 Corinthians 7 in the UBG

2 Corinthians 7 in the UGV

2 Corinthians 7 in the UGV2

2 Corinthians 7 in the UGV3

2 Corinthians 7 in the VBL

2 Corinthians 7 in the VDCC

2 Corinthians 7 in the YALU

2 Corinthians 7 in the YAPE

2 Corinthians 7 in the YBVTP

2 Corinthians 7 in the ZBP