2 Samuel 4 (BOGWICC)
1 Isiboseti mwana wa Sauli atamva kuti Abineri waphedwa ku Hebroni, anataya mtima ndipo Aisraeli onse anachita mantha kwambiri. 2 Koma Isiboseti anali ndi anthu akuluakulu awiri amene ankatsogolera magulu a ankhondo. Mmodzi mwa iwo dzina lake linali Baana ndipo mnzakeyo anali Rekabu. Iwo anali ana a Rimoni wa banja la Beeroti wa fuko la Benjamini Beeroti. Iwo ankatengedwa ngati mbali imodzi ya Benjamini, 3 chifukwa anthu a ku Beeroti anathawira ku Gitaimu ndipo akhala ali kumeneko ngati alendo mpaka lero lino. 4 (Yonatani mwana wa Sauli anali ndi mwana wamwamuna amene anali wolumala mapazi ake onse awiri. Iye anali ndi zaka zisanu pamene nkhani ya Sauli ndi Yonatani inamveka kuchokera ku Yezireeli. Amene amamulera anamunyamula ndi kuthawa naye, koma pamene amachita zinthu mofulumira mwanayo anagwa ndipo analumala. Dzina lake linali Mefiboseti). 5 Choncho Rekabu ndi Baana ana a Rimoni wa ku Beeroti ananyamuka kupita ku nyumba ya Isi-Boseti, ndipo anafika nthawi ya masana kukutentha pamene iye amapumula. 6 Iwo analowa mʼchipinda chamʼkati ngati kuti amakatenga tirigu, ndipo anamulasa mʼmimba. Kenaka Rekabu ndi mʼbale wake Baana anathawa. 7 Iwo analowa mʼnyumbamo iye akugona pa bedi mʼchipinda chake. Atamulasa ndi kumupha, anadula mutu wake nʼkuwutenga, nayenda usiku wonse mʼnjira yopita ku Araba. 8 Iwo anabweretsa mutu wa Isi-Boseti kwa Davide ku Hebroni ndipo anati kwa mfumu, “Nawu mutu wa Isiboseti mwana wa Sauli, mdani wanu, amene anafuna kukuphani. Lero lino Yehova wabwezera mbuye wanga mfumu adani anu, Sauli ndi ana ake.” 9 Davide anayankha Rekabu ndi mʼbale wake Baana, ana a Rimoni wa ku Beeroti kuti, “Pali Yehova wamoyo, amene wandipulumutsa ku mavuto anga onse, 10 pamene munthu wina anandiwuza kuti, ‘Sauli wafa’ ndipo ankaganiza kuti wabweretsa nkhani yabwino, ine ndinamugwira ndi kumupha ku Zikilagi. Iyi inali mphotho imene ndinapereka kwa iyeyo chifukwa cha uthenga wake! 11 Nanji pamene anthu oyipa apha munthu wosalakwa ali mʼnyumba mwake ndiponso pa bedi lake! Kodi ine ndingaleke kukulangani ndi kukuchotsani pa dziko lapansi pano?” 12 Kotero Davide analamulira ankhondo ake, ndipo anawapha. Iwo anawadula manja ndi mapazi ndi kupachika matupi awo pa dziwe la ku Hebroni. Koma anatenga mutu wa Isi-Boseti nawuyika mʼmanda a Abineri ku Hebroni.
In Other Versions
2 Samuel 4 in the ANGEFD
2 Samuel 4 in the ANTPNG2D
2 Samuel 4 in the AS21
2 Samuel 4 in the BAGH
2 Samuel 4 in the BBPNG
2 Samuel 4 in the BBT1E
2 Samuel 4 in the BDS
2 Samuel 4 in the BEV
2 Samuel 4 in the BHAD
2 Samuel 4 in the BIB
2 Samuel 4 in the BLPT
2 Samuel 4 in the BNT
2 Samuel 4 in the BNTABOOT
2 Samuel 4 in the BNTLV
2 Samuel 4 in the BOATCB
2 Samuel 4 in the BOATCB2
2 Samuel 4 in the BOBCV
2 Samuel 4 in the BOCNT
2 Samuel 4 in the BOECS
2 Samuel 4 in the BOHCB
2 Samuel 4 in the BOHCV
2 Samuel 4 in the BOHLNT
2 Samuel 4 in the BOHNTLTAL
2 Samuel 4 in the BOICB
2 Samuel 4 in the BOILNTAP
2 Samuel 4 in the BOITCV
2 Samuel 4 in the BOKCV
2 Samuel 4 in the BOKCV2
2 Samuel 4 in the BOKHWOG
2 Samuel 4 in the BOKSSV
2 Samuel 4 in the BOLCB
2 Samuel 4 in the BOLCB2
2 Samuel 4 in the BOMCV
2 Samuel 4 in the BONAV
2 Samuel 4 in the BONCB
2 Samuel 4 in the BONLT
2 Samuel 4 in the BONUT2
2 Samuel 4 in the BOPLNT
2 Samuel 4 in the BOSCB
2 Samuel 4 in the BOSNC
2 Samuel 4 in the BOTLNT
2 Samuel 4 in the BOVCB
2 Samuel 4 in the BOYCB
2 Samuel 4 in the BPBB
2 Samuel 4 in the BPH
2 Samuel 4 in the BSB
2 Samuel 4 in the CCB
2 Samuel 4 in the CUV
2 Samuel 4 in the CUVS
2 Samuel 4 in the DBT
2 Samuel 4 in the DGDNT
2 Samuel 4 in the DHNT
2 Samuel 4 in the DNT
2 Samuel 4 in the ELBE
2 Samuel 4 in the EMTV
2 Samuel 4 in the ESV
2 Samuel 4 in the FBV
2 Samuel 4 in the FEB
2 Samuel 4 in the GGMNT
2 Samuel 4 in the GNT
2 Samuel 4 in the HARY
2 Samuel 4 in the HNT
2 Samuel 4 in the IRVA
2 Samuel 4 in the IRVB
2 Samuel 4 in the IRVG
2 Samuel 4 in the IRVH
2 Samuel 4 in the IRVK
2 Samuel 4 in the IRVM
2 Samuel 4 in the IRVM2
2 Samuel 4 in the IRVO
2 Samuel 4 in the IRVP
2 Samuel 4 in the IRVT
2 Samuel 4 in the IRVT2
2 Samuel 4 in the IRVU
2 Samuel 4 in the ISVN
2 Samuel 4 in the JSNT
2 Samuel 4 in the KAPI
2 Samuel 4 in the KBT1ETNIK
2 Samuel 4 in the KBV
2 Samuel 4 in the KJV
2 Samuel 4 in the KNFD
2 Samuel 4 in the LBA
2 Samuel 4 in the LBLA
2 Samuel 4 in the LNT
2 Samuel 4 in the LSV
2 Samuel 4 in the MAAL
2 Samuel 4 in the MBV
2 Samuel 4 in the MBV2
2 Samuel 4 in the MHNT
2 Samuel 4 in the MKNFD
2 Samuel 4 in the MNG
2 Samuel 4 in the MNT
2 Samuel 4 in the MNT2
2 Samuel 4 in the MRS1T
2 Samuel 4 in the NAA
2 Samuel 4 in the NASB
2 Samuel 4 in the NBLA
2 Samuel 4 in the NBS
2 Samuel 4 in the NBVTP
2 Samuel 4 in the NET2
2 Samuel 4 in the NIV11
2 Samuel 4 in the NNT
2 Samuel 4 in the NNT2
2 Samuel 4 in the NNT3
2 Samuel 4 in the PDDPT
2 Samuel 4 in the PFNT
2 Samuel 4 in the RMNT
2 Samuel 4 in the SBIAS
2 Samuel 4 in the SBIBS
2 Samuel 4 in the SBIBS2
2 Samuel 4 in the SBICS
2 Samuel 4 in the SBIDS
2 Samuel 4 in the SBIGS
2 Samuel 4 in the SBIHS
2 Samuel 4 in the SBIIS
2 Samuel 4 in the SBIIS2
2 Samuel 4 in the SBIIS3
2 Samuel 4 in the SBIKS
2 Samuel 4 in the SBIKS2
2 Samuel 4 in the SBIMS
2 Samuel 4 in the SBIOS
2 Samuel 4 in the SBIPS
2 Samuel 4 in the SBISS
2 Samuel 4 in the SBITS
2 Samuel 4 in the SBITS2
2 Samuel 4 in the SBITS3
2 Samuel 4 in the SBITS4
2 Samuel 4 in the SBIUS
2 Samuel 4 in the SBIVS
2 Samuel 4 in the SBT
2 Samuel 4 in the SBT1E
2 Samuel 4 in the SCHL
2 Samuel 4 in the SNT
2 Samuel 4 in the SUSU
2 Samuel 4 in the SUSU2
2 Samuel 4 in the SYNO
2 Samuel 4 in the TBIAOTANT
2 Samuel 4 in the TBT1E
2 Samuel 4 in the TBT1E2
2 Samuel 4 in the TFTIP
2 Samuel 4 in the TFTU
2 Samuel 4 in the TGNTATF3T
2 Samuel 4 in the THAI
2 Samuel 4 in the TNFD
2 Samuel 4 in the TNT
2 Samuel 4 in the TNTIK
2 Samuel 4 in the TNTIL
2 Samuel 4 in the TNTIN
2 Samuel 4 in the TNTIP
2 Samuel 4 in the TNTIZ
2 Samuel 4 in the TOMA
2 Samuel 4 in the TTENT
2 Samuel 4 in the UBG
2 Samuel 4 in the UGV
2 Samuel 4 in the UGV2
2 Samuel 4 in the UGV3
2 Samuel 4 in the VBL
2 Samuel 4 in the VDCC
2 Samuel 4 in the YALU
2 Samuel 4 in the YAPE
2 Samuel 4 in the YBVTP
2 Samuel 4 in the ZBP