2 Timothy 3 (BOGWICC)

1 Koma dziwa izi: Mʼmasiku otsiriza kudzafika nthawi zoopsa kwambiri. 2 Anthu adzakhala odzikonda, okonda ndalama, odzitama, onyada, achipongwe, osamvera makolo awo, osayamika, wopanda chiyero. 3 Adzakhala wopanda chikondi, osakhululuka, osinjirira, osadziletsa, ankhanza, osakonda zabwino, 4 opereka anzawo kwa adani awo, osaopa zoyipa, odzitukumula, okonda zowasangalatsa mʼmalo mokonda Mulungu. 5 Adzakhala ndi maonekedwe achipembedzo koma mphamvu yake ndi kumayikana. Anthu amenewa uziwapewa. 6 Iwowa ndi anthu aja amene amayendayenda mʼmakomo a anthu nʼkumanyenga akazi ofowoka mʼmaganizo, olemedwa ndi machimo ndiponso otengeka ndi zilakolako zoyipa zamitundumitundu, 7 amaphunzira nthawi zonse koma samatha kuzindikira choonadi. 8 Monga momwe Yanesi ndi Yambere anawukira Mose, momwemonso anthu amenewa amawukira choonadi. Nzeru zawo ndi zowonongeka ndipo pa za chikhulupiriro, ndi okanidwa. 9 Koma sadzapita nazo patali kwambiri zimenezi, pakuti anthu onse adzaona kupusa kwawo monga anachitira Yanesi ndi Yambere. 10 Tsono iwe, umadziwa zonse zimene ndimaphunzitsa, makhalidwe anga, cholinga changa, chikhulupiriro changa, kuleza mtima kwanga, chikondi changa, ndi kupirira kwanga, 11 mazunzo anga, masautso anga, monga zinandichitikira ku Antiokeya, ku Ikoniya ndi ku Lusitra. Ndinazunzika kwambiri. Koma Ambuye anandipulumutsa pa zonsezi. 12 Kunena zoona, munthu aliyense amene akufuna kukhala moyo wolemekeza Mulungu mwa Khristu Yesu, adzazunzikadi, 13 pomwe anthu oyipa ndi onyenga adzanka nayipirayipira, kunamiza ena, iwo nʼkumanamizidwanso. 14 Koma iwe pitiriza zimene waziphunzira ndi kuzivomereza, chifukwa ukudziwa amene anakuphunzitsa zimenezi. 15 Kuyambira uli wamngʼono wakhala ukudziwa Malemba Oyera, amene akhoza kukupatsa nzeru zokupulumutsa kudzera mʼchikhulupiriro cha mwa Yesu Khristu. 16 Malemba onse anawalembetsa ndi Mulungu, ndipo othandiza pophunzitsa, podzudzula, pokonza cholakwika ndi polangiza za chilungamo 17 kuti munthu wa Mulungu akonzekere bwino lomwe kugwira ntchito iliyonse yabwino.

In Other Versions

2 Timothy 3 in the ANGEFD

2 Timothy 3 in the ANTPNG2D

2 Timothy 3 in the AS21

2 Timothy 3 in the BAGH

2 Timothy 3 in the BBPNG

2 Timothy 3 in the BBT1E

2 Timothy 3 in the BDS

2 Timothy 3 in the BEV

2 Timothy 3 in the BHAD

2 Timothy 3 in the BIB

2 Timothy 3 in the BLPT

2 Timothy 3 in the BNT

2 Timothy 3 in the BNTABOOT

2 Timothy 3 in the BNTLV

2 Timothy 3 in the BOATCB

2 Timothy 3 in the BOATCB2

2 Timothy 3 in the BOBCV

2 Timothy 3 in the BOCNT

2 Timothy 3 in the BOECS

2 Timothy 3 in the BOHCB

2 Timothy 3 in the BOHCV

2 Timothy 3 in the BOHLNT

2 Timothy 3 in the BOHNTLTAL

2 Timothy 3 in the BOICB

2 Timothy 3 in the BOILNTAP

2 Timothy 3 in the BOITCV

2 Timothy 3 in the BOKCV

2 Timothy 3 in the BOKCV2

2 Timothy 3 in the BOKHWOG

2 Timothy 3 in the BOKSSV

2 Timothy 3 in the BOLCB

2 Timothy 3 in the BOLCB2

2 Timothy 3 in the BOMCV

2 Timothy 3 in the BONAV

2 Timothy 3 in the BONCB

2 Timothy 3 in the BONLT

2 Timothy 3 in the BONUT2

2 Timothy 3 in the BOPLNT

2 Timothy 3 in the BOSCB

2 Timothy 3 in the BOSNC

2 Timothy 3 in the BOTLNT

2 Timothy 3 in the BOVCB

2 Timothy 3 in the BOYCB

2 Timothy 3 in the BPBB

2 Timothy 3 in the BPH

2 Timothy 3 in the BSB

2 Timothy 3 in the CCB

2 Timothy 3 in the CUV

2 Timothy 3 in the CUVS

2 Timothy 3 in the DBT

2 Timothy 3 in the DGDNT

2 Timothy 3 in the DHNT

2 Timothy 3 in the DNT

2 Timothy 3 in the ELBE

2 Timothy 3 in the EMTV

2 Timothy 3 in the ESV

2 Timothy 3 in the FBV

2 Timothy 3 in the FEB

2 Timothy 3 in the GGMNT

2 Timothy 3 in the GNT

2 Timothy 3 in the HARY

2 Timothy 3 in the HNT

2 Timothy 3 in the IRVA

2 Timothy 3 in the IRVB

2 Timothy 3 in the IRVG

2 Timothy 3 in the IRVH

2 Timothy 3 in the IRVK

2 Timothy 3 in the IRVM

2 Timothy 3 in the IRVM2

2 Timothy 3 in the IRVO

2 Timothy 3 in the IRVP

2 Timothy 3 in the IRVT

2 Timothy 3 in the IRVT2

2 Timothy 3 in the IRVU

2 Timothy 3 in the ISVN

2 Timothy 3 in the JSNT

2 Timothy 3 in the KAPI

2 Timothy 3 in the KBT1ETNIK

2 Timothy 3 in the KBV

2 Timothy 3 in the KJV

2 Timothy 3 in the KNFD

2 Timothy 3 in the LBA

2 Timothy 3 in the LBLA

2 Timothy 3 in the LNT

2 Timothy 3 in the LSV

2 Timothy 3 in the MAAL

2 Timothy 3 in the MBV

2 Timothy 3 in the MBV2

2 Timothy 3 in the MHNT

2 Timothy 3 in the MKNFD

2 Timothy 3 in the MNG

2 Timothy 3 in the MNT

2 Timothy 3 in the MNT2

2 Timothy 3 in the MRS1T

2 Timothy 3 in the NAA

2 Timothy 3 in the NASB

2 Timothy 3 in the NBLA

2 Timothy 3 in the NBS

2 Timothy 3 in the NBVTP

2 Timothy 3 in the NET2

2 Timothy 3 in the NIV11

2 Timothy 3 in the NNT

2 Timothy 3 in the NNT2

2 Timothy 3 in the NNT3

2 Timothy 3 in the PDDPT

2 Timothy 3 in the PFNT

2 Timothy 3 in the RMNT

2 Timothy 3 in the SBIAS

2 Timothy 3 in the SBIBS

2 Timothy 3 in the SBIBS2

2 Timothy 3 in the SBICS

2 Timothy 3 in the SBIDS

2 Timothy 3 in the SBIGS

2 Timothy 3 in the SBIHS

2 Timothy 3 in the SBIIS

2 Timothy 3 in the SBIIS2

2 Timothy 3 in the SBIIS3

2 Timothy 3 in the SBIKS

2 Timothy 3 in the SBIKS2

2 Timothy 3 in the SBIMS

2 Timothy 3 in the SBIOS

2 Timothy 3 in the SBIPS

2 Timothy 3 in the SBISS

2 Timothy 3 in the SBITS

2 Timothy 3 in the SBITS2

2 Timothy 3 in the SBITS3

2 Timothy 3 in the SBITS4

2 Timothy 3 in the SBIUS

2 Timothy 3 in the SBIVS

2 Timothy 3 in the SBT

2 Timothy 3 in the SBT1E

2 Timothy 3 in the SCHL

2 Timothy 3 in the SNT

2 Timothy 3 in the SUSU

2 Timothy 3 in the SUSU2

2 Timothy 3 in the SYNO

2 Timothy 3 in the TBIAOTANT

2 Timothy 3 in the TBT1E

2 Timothy 3 in the TBT1E2

2 Timothy 3 in the TFTIP

2 Timothy 3 in the TFTU

2 Timothy 3 in the TGNTATF3T

2 Timothy 3 in the THAI

2 Timothy 3 in the TNFD

2 Timothy 3 in the TNT

2 Timothy 3 in the TNTIK

2 Timothy 3 in the TNTIL

2 Timothy 3 in the TNTIN

2 Timothy 3 in the TNTIP

2 Timothy 3 in the TNTIZ

2 Timothy 3 in the TOMA

2 Timothy 3 in the TTENT

2 Timothy 3 in the UBG

2 Timothy 3 in the UGV

2 Timothy 3 in the UGV2

2 Timothy 3 in the UGV3

2 Timothy 3 in the VBL

2 Timothy 3 in the VDCC

2 Timothy 3 in the YALU

2 Timothy 3 in the YAPE

2 Timothy 3 in the YBVTP

2 Timothy 3 in the ZBP