Ecclesiastes 3 (BOGWICC)
1 Chinthu chilichonse chili ndi nthawi yake,ndi nyengo yake yomwe anayika Mulungu: 2 Nthawi yobadwa ndi nthawi yomwalira,nthawi yodzala ndi nthawi yokolola. 3 Nthawi yakupha ndi nthawi yochiritsa,nthawi yogwetsa ndi nthawi yomanga. 4 Nthawi yomva chisoni ndi nthawi yosangalala,nthawi yolira maliro ndi nthawi yovina. 5 Nthawi yotaya miyala ndi nthawi yokundika miyala,nthawi yokumbatirana ndi nthawi yoleka kukumbatirana. 6 Nthawi yofunafuna ndi nthawi yoleka kufunafuna,nthawi yosunga ndi nthawi yotaya. 7 Nthawi yongʼamba ndi nthawi yosoka,nthawi yokhala chete ndi nthawi yoyankhula. 8 Nthawi yokondana ndi nthawi yodana,nthawi ya nkhondo ndi nthawi ya mtendere. 9 Kodi wantchito amapeza phindu lanji pa ntchito yake yolemetsa? 10 Ine ndinaona chipsinjo chimene Mulungu anayika pa anthu. 11 Iye anapanga chinthu chilichonse kuti chikhale chabwino pa nthawi yake. Anayika nzeru zamuyaya mʼmitima ya anthu; komabe anthuwo sangathe kuzindikira zomwe Mulungu wachita kuyambira pa chiyambi mpaka chimaliziro. 12 Ine ndikudziwa kuti palibenso kanthu kabwino kwa anthu kopambana kusangalala ndi kuchita zabwino pamene ali ndi moyo. 13 Ndi mphatso ya Mulungu kwa munthu kuti azidya, azimwa ndi kumakondwera ndi ntchito zake zolemetsa. 14 Ndikudziwa kuti chilichonse chimene Mulungu amachita chidzakhala mpaka muyaya; palibe zimene zingawonjezedwe kapena kuchotsedwa. Mulungu amazichita kuti anthu azimuopa. 15 Chilichonse chimene chilipo chinalipo kale,ndipo chimene chidzakhalapo chinalipo poyamba;Mulungu amabwezanso zakale zimene zinapita kuti zichitikenso. 16 Ndipo ndinaona chinthu chinanso pansi pano:ku malo achiweruzo, kuyipa mtima kuli komweko,ku malo achilungamo, kuyipa mtima kuli komweko. 17 Ndinalingalira mu mtima mwanga kuti;“Mulungu adzaweruzaolungama pamodzi ndi oyipa omwe,pakuti anayika nthawi yochitikira chinthu chilichonse,nthawi ya ntchito iliyonse.” 18 Ndinalingaliranso kuti, “Kunena za anthu, Mulungu amawayesa ndi cholinga choti awaonetse kuti iwo ali ngati nyama. 19 Zimene zimachitikira munthu, zomwezonso zimachitikira nyama; chinthu chimodzi chomwecho chimachitikira onse: Monga munthu amafa momwemonso nyama imafa. Zonsezi zimapuma mpweya umodzimodzi omwewo; munthu saposa nyama. Zonsezi ndi zopandapake. 20 Zonse zimapita kumodzimodzi; zonsezi zimachokera ku fumbi, ndipo zimabwereranso ku fumbi komweko. 21 Kodi ndani amene amadziwa ngati mzimu wa munthu umakwera kumwamba, ndipo mzimu wa nyama umatsikira kunsi kwa dziko?” 22 Kotero ndinaona kuti palibe chinthu chabwino kwa munthu kuposa kuti munthu azisangalala ndi ntchito yake, pakuti ichi ndiye chake chenicheni. Pakuti ndani amene angamubweretse kuti adzaone zimene zidzamuchitikira iye akadzamwalira?
In Other Versions
Ecclesiastes 3 in the ANGEFD
Ecclesiastes 3 in the ANTPNG2D
Ecclesiastes 3 in the AS21
Ecclesiastes 3 in the BAGH
Ecclesiastes 3 in the BBPNG
Ecclesiastes 3 in the BBT1E
Ecclesiastes 3 in the BDS
Ecclesiastes 3 in the BEV
Ecclesiastes 3 in the BHAD
Ecclesiastes 3 in the BIB
Ecclesiastes 3 in the BLPT
Ecclesiastes 3 in the BNT
Ecclesiastes 3 in the BNTABOOT
Ecclesiastes 3 in the BNTLV
Ecclesiastes 3 in the BOATCB
Ecclesiastes 3 in the BOATCB2
Ecclesiastes 3 in the BOBCV
Ecclesiastes 3 in the BOCNT
Ecclesiastes 3 in the BOECS
Ecclesiastes 3 in the BOHCB
Ecclesiastes 3 in the BOHCV
Ecclesiastes 3 in the BOHLNT
Ecclesiastes 3 in the BOHNTLTAL
Ecclesiastes 3 in the BOICB
Ecclesiastes 3 in the BOILNTAP
Ecclesiastes 3 in the BOITCV
Ecclesiastes 3 in the BOKCV
Ecclesiastes 3 in the BOKCV2
Ecclesiastes 3 in the BOKHWOG
Ecclesiastes 3 in the BOKSSV
Ecclesiastes 3 in the BOLCB
Ecclesiastes 3 in the BOLCB2
Ecclesiastes 3 in the BOMCV
Ecclesiastes 3 in the BONAV
Ecclesiastes 3 in the BONCB
Ecclesiastes 3 in the BONLT
Ecclesiastes 3 in the BONUT2
Ecclesiastes 3 in the BOPLNT
Ecclesiastes 3 in the BOSCB
Ecclesiastes 3 in the BOSNC
Ecclesiastes 3 in the BOTLNT
Ecclesiastes 3 in the BOVCB
Ecclesiastes 3 in the BOYCB
Ecclesiastes 3 in the BPBB
Ecclesiastes 3 in the BPH
Ecclesiastes 3 in the BSB
Ecclesiastes 3 in the CCB
Ecclesiastes 3 in the CUV
Ecclesiastes 3 in the CUVS
Ecclesiastes 3 in the DBT
Ecclesiastes 3 in the DGDNT
Ecclesiastes 3 in the DHNT
Ecclesiastes 3 in the DNT
Ecclesiastes 3 in the ELBE
Ecclesiastes 3 in the EMTV
Ecclesiastes 3 in the ESV
Ecclesiastes 3 in the FBV
Ecclesiastes 3 in the FEB
Ecclesiastes 3 in the GGMNT
Ecclesiastes 3 in the GNT
Ecclesiastes 3 in the HARY
Ecclesiastes 3 in the HNT
Ecclesiastes 3 in the IRVA
Ecclesiastes 3 in the IRVB
Ecclesiastes 3 in the IRVG
Ecclesiastes 3 in the IRVH
Ecclesiastes 3 in the IRVK
Ecclesiastes 3 in the IRVM
Ecclesiastes 3 in the IRVM2
Ecclesiastes 3 in the IRVO
Ecclesiastes 3 in the IRVP
Ecclesiastes 3 in the IRVT
Ecclesiastes 3 in the IRVT2
Ecclesiastes 3 in the IRVU
Ecclesiastes 3 in the ISVN
Ecclesiastes 3 in the JSNT
Ecclesiastes 3 in the KAPI
Ecclesiastes 3 in the KBT1ETNIK
Ecclesiastes 3 in the KBV
Ecclesiastes 3 in the KJV
Ecclesiastes 3 in the KNFD
Ecclesiastes 3 in the LBA
Ecclesiastes 3 in the LBLA
Ecclesiastes 3 in the LNT
Ecclesiastes 3 in the LSV
Ecclesiastes 3 in the MAAL
Ecclesiastes 3 in the MBV
Ecclesiastes 3 in the MBV2
Ecclesiastes 3 in the MHNT
Ecclesiastes 3 in the MKNFD
Ecclesiastes 3 in the MNG
Ecclesiastes 3 in the MNT
Ecclesiastes 3 in the MNT2
Ecclesiastes 3 in the MRS1T
Ecclesiastes 3 in the NAA
Ecclesiastes 3 in the NASB
Ecclesiastes 3 in the NBLA
Ecclesiastes 3 in the NBS
Ecclesiastes 3 in the NBVTP
Ecclesiastes 3 in the NET2
Ecclesiastes 3 in the NIV11
Ecclesiastes 3 in the NNT
Ecclesiastes 3 in the NNT2
Ecclesiastes 3 in the NNT3
Ecclesiastes 3 in the PDDPT
Ecclesiastes 3 in the PFNT
Ecclesiastes 3 in the RMNT
Ecclesiastes 3 in the SBIAS
Ecclesiastes 3 in the SBIBS
Ecclesiastes 3 in the SBIBS2
Ecclesiastes 3 in the SBICS
Ecclesiastes 3 in the SBIDS
Ecclesiastes 3 in the SBIGS
Ecclesiastes 3 in the SBIHS
Ecclesiastes 3 in the SBIIS
Ecclesiastes 3 in the SBIIS2
Ecclesiastes 3 in the SBIIS3
Ecclesiastes 3 in the SBIKS
Ecclesiastes 3 in the SBIKS2
Ecclesiastes 3 in the SBIMS
Ecclesiastes 3 in the SBIOS
Ecclesiastes 3 in the SBIPS
Ecclesiastes 3 in the SBISS
Ecclesiastes 3 in the SBITS
Ecclesiastes 3 in the SBITS2
Ecclesiastes 3 in the SBITS3
Ecclesiastes 3 in the SBITS4
Ecclesiastes 3 in the SBIUS
Ecclesiastes 3 in the SBIVS
Ecclesiastes 3 in the SBT
Ecclesiastes 3 in the SBT1E
Ecclesiastes 3 in the SCHL
Ecclesiastes 3 in the SNT
Ecclesiastes 3 in the SUSU
Ecclesiastes 3 in the SUSU2
Ecclesiastes 3 in the SYNO
Ecclesiastes 3 in the TBIAOTANT
Ecclesiastes 3 in the TBT1E
Ecclesiastes 3 in the TBT1E2
Ecclesiastes 3 in the TFTIP
Ecclesiastes 3 in the TFTU
Ecclesiastes 3 in the TGNTATF3T
Ecclesiastes 3 in the THAI
Ecclesiastes 3 in the TNFD
Ecclesiastes 3 in the TNT
Ecclesiastes 3 in the TNTIK
Ecclesiastes 3 in the TNTIL
Ecclesiastes 3 in the TNTIN
Ecclesiastes 3 in the TNTIP
Ecclesiastes 3 in the TNTIZ
Ecclesiastes 3 in the TOMA
Ecclesiastes 3 in the TTENT
Ecclesiastes 3 in the UBG
Ecclesiastes 3 in the UGV
Ecclesiastes 3 in the UGV2
Ecclesiastes 3 in the UGV3
Ecclesiastes 3 in the VBL
Ecclesiastes 3 in the VDCC
Ecclesiastes 3 in the YALU
Ecclesiastes 3 in the YAPE
Ecclesiastes 3 in the YBVTP
Ecclesiastes 3 in the ZBP