Ephesians 3 (BOGWICC)

1 Nʼchifukwa chake ine Paulo, ndili wamʼndende wa Khristu Yesu chifukwa cha inu anthu a mitundu ina. 2 Ndithudi, inu munamva za ntchito yachisomo cha Mulungu imene anandipatsa chifukwa cha inu, 3 ndicho chinsinsi chimene chinawululidwa kwa ine mwa vumbulutso, monga ndinakulemberani kale mwachidule. 4 Pamene mukuwerenga izi, inu mudzazindikira za chidziwitso changa pa chinsinsi cha Khristu, 5 chimene sichinawululidwe kwa anthu amibado ina monga momwe tsopano chawululidwa ndi Mzimu wa Mulungu mwa atumwi oyera ndi aneneri. 6 Chinsinsicho nʼchakuti, kudzera mu Uthenga Wabwino anthu a mitundu ina ndi olowamʼmalo pamodzi ndi Aisraeli, ndi ziwalo za thupi limodzi, ndi olandira nawo pamodzi malonjezo a mwa Khristu Yesu. 7 Mwachisomo cha Mulungu ndi mphamvu zake, ine ndinasanduka mtumiki wa Uthenga Wabwinowu. 8 Ngakhale ndili wamngʼono kwambiri pakati pa anthu onse a Mulungu, anandipatsa chisomo chimenechi cholalikira kwa anthu a mitundu ina chuma chopanda malire cha Khristu. 9 Ndinasankhidwa kuti ndifotokoze momveka bwino kwa munthu aliyense za chinsinsi chimenechi, chinsinsi chimene kuyambira kale chinali chobisika mwa Mulungu amene analenga zinthu zonse. 10 Cholinga chake tsopano nʼchakuti, kudzera mwa mpingo, mafumu ndi a ulamuliro onse a kumwamba adziwe nzeru zochuluka za Mulungu. 11 Chimenechi chinali chikonzero chamuyaya cha Mulungu, chimene chinachitika kudzera mwa Khristu Yesu Ambuye athu. 12 Mwa Khristu ndi mwa chikhulupiriro chathu mwa Iye, timayandikira kwa Mulungu momasuka ndi molimbika mtima. 13 Choncho, ine ndikukupemphani kuti musakhumudwe popeza ndikusautsidwa chifukwa cha inu pakuti masautso angawa ndi ulemerero wanu. 14 Nʼchifukwa chake ine ndikugwada pamaso pa Atate, 15 amene banja lililonse kumwamba ndi pa dziko lapansi limatchulidwa ndi dzina lawo. 16 Ndikupemphera kuti kuchokera mʼchuma cha ulemerero wake alimbikitse moyo wanu wa mʼkati ndi mphamvu za Mzimu wake, 17 kuti Khristu akhazikike mʼmitima mwanu mwachikhulupiriro. Ndipo ndikukupemphererani kuti muzikike ndi kukhazikika mʼchikondi 18 kuti mukhale ndi mphamvu, kuti pamodzi ndi anthu oyera mtima onse muthe kuzindikira kupingasa, kutalika ndi kukwera komanso kuzama kwake kwa chikondi cha Khristu. 19 Ndikukupemphererani kuti mudziwe chikondi chija cha Khristu chopitirira nzeru za anthu, kuti mudzazidwe kwathunthu ndi moyo wa Mulungu mwini. 20 Tsopano kwa Iye amene angathe kuchita zochuluka kuposa zimene tingapemphe, kapena kuganiza molingana ndi mphamvu zake zimene zikugwira ntchito mwa ife, 21 Iyeyo akhale ndi ulemu mu mpingo ndi mwa Khristu Yesu pa mibado yonse mpaka muyaya. Ameni.

In Other Versions

Ephesians 3 in the ANGEFD

Ephesians 3 in the ANTPNG2D

Ephesians 3 in the AS21

Ephesians 3 in the BAGH

Ephesians 3 in the BBPNG

Ephesians 3 in the BBT1E

Ephesians 3 in the BDS

Ephesians 3 in the BEV

Ephesians 3 in the BHAD

Ephesians 3 in the BIB

Ephesians 3 in the BLPT

Ephesians 3 in the BNT

Ephesians 3 in the BNTABOOT

Ephesians 3 in the BNTLV

Ephesians 3 in the BOATCB

Ephesians 3 in the BOATCB2

Ephesians 3 in the BOBCV

Ephesians 3 in the BOCNT

Ephesians 3 in the BOECS

Ephesians 3 in the BOHCB

Ephesians 3 in the BOHCV

Ephesians 3 in the BOHLNT

Ephesians 3 in the BOHNTLTAL

Ephesians 3 in the BOICB

Ephesians 3 in the BOILNTAP

Ephesians 3 in the BOITCV

Ephesians 3 in the BOKCV

Ephesians 3 in the BOKCV2

Ephesians 3 in the BOKHWOG

Ephesians 3 in the BOKSSV

Ephesians 3 in the BOLCB

Ephesians 3 in the BOLCB2

Ephesians 3 in the BOMCV

Ephesians 3 in the BONAV

Ephesians 3 in the BONCB

Ephesians 3 in the BONLT

Ephesians 3 in the BONUT2

Ephesians 3 in the BOPLNT

Ephesians 3 in the BOSCB

Ephesians 3 in the BOSNC

Ephesians 3 in the BOTLNT

Ephesians 3 in the BOVCB

Ephesians 3 in the BOYCB

Ephesians 3 in the BPBB

Ephesians 3 in the BPH

Ephesians 3 in the BSB

Ephesians 3 in the CCB

Ephesians 3 in the CUV

Ephesians 3 in the CUVS

Ephesians 3 in the DBT

Ephesians 3 in the DGDNT

Ephesians 3 in the DHNT

Ephesians 3 in the DNT

Ephesians 3 in the ELBE

Ephesians 3 in the EMTV

Ephesians 3 in the ESV

Ephesians 3 in the FBV

Ephesians 3 in the FEB

Ephesians 3 in the GGMNT

Ephesians 3 in the GNT

Ephesians 3 in the HARY

Ephesians 3 in the HNT

Ephesians 3 in the IRVA

Ephesians 3 in the IRVB

Ephesians 3 in the IRVG

Ephesians 3 in the IRVH

Ephesians 3 in the IRVK

Ephesians 3 in the IRVM

Ephesians 3 in the IRVM2

Ephesians 3 in the IRVO

Ephesians 3 in the IRVP

Ephesians 3 in the IRVT

Ephesians 3 in the IRVT2

Ephesians 3 in the IRVU

Ephesians 3 in the ISVN

Ephesians 3 in the JSNT

Ephesians 3 in the KAPI

Ephesians 3 in the KBT1ETNIK

Ephesians 3 in the KBV

Ephesians 3 in the KJV

Ephesians 3 in the KNFD

Ephesians 3 in the LBA

Ephesians 3 in the LBLA

Ephesians 3 in the LNT

Ephesians 3 in the LSV

Ephesians 3 in the MAAL

Ephesians 3 in the MBV

Ephesians 3 in the MBV2

Ephesians 3 in the MHNT

Ephesians 3 in the MKNFD

Ephesians 3 in the MNG

Ephesians 3 in the MNT

Ephesians 3 in the MNT2

Ephesians 3 in the MRS1T

Ephesians 3 in the NAA

Ephesians 3 in the NASB

Ephesians 3 in the NBLA

Ephesians 3 in the NBS

Ephesians 3 in the NBVTP

Ephesians 3 in the NET2

Ephesians 3 in the NIV11

Ephesians 3 in the NNT

Ephesians 3 in the NNT2

Ephesians 3 in the NNT3

Ephesians 3 in the PDDPT

Ephesians 3 in the PFNT

Ephesians 3 in the RMNT

Ephesians 3 in the SBIAS

Ephesians 3 in the SBIBS

Ephesians 3 in the SBIBS2

Ephesians 3 in the SBICS

Ephesians 3 in the SBIDS

Ephesians 3 in the SBIGS

Ephesians 3 in the SBIHS

Ephesians 3 in the SBIIS

Ephesians 3 in the SBIIS2

Ephesians 3 in the SBIIS3

Ephesians 3 in the SBIKS

Ephesians 3 in the SBIKS2

Ephesians 3 in the SBIMS

Ephesians 3 in the SBIOS

Ephesians 3 in the SBIPS

Ephesians 3 in the SBISS

Ephesians 3 in the SBITS

Ephesians 3 in the SBITS2

Ephesians 3 in the SBITS3

Ephesians 3 in the SBITS4

Ephesians 3 in the SBIUS

Ephesians 3 in the SBIVS

Ephesians 3 in the SBT

Ephesians 3 in the SBT1E

Ephesians 3 in the SCHL

Ephesians 3 in the SNT

Ephesians 3 in the SUSU

Ephesians 3 in the SUSU2

Ephesians 3 in the SYNO

Ephesians 3 in the TBIAOTANT

Ephesians 3 in the TBT1E

Ephesians 3 in the TBT1E2

Ephesians 3 in the TFTIP

Ephesians 3 in the TFTU

Ephesians 3 in the TGNTATF3T

Ephesians 3 in the THAI

Ephesians 3 in the TNFD

Ephesians 3 in the TNT

Ephesians 3 in the TNTIK

Ephesians 3 in the TNTIL

Ephesians 3 in the TNTIN

Ephesians 3 in the TNTIP

Ephesians 3 in the TNTIZ

Ephesians 3 in the TOMA

Ephesians 3 in the TTENT

Ephesians 3 in the UBG

Ephesians 3 in the UGV

Ephesians 3 in the UGV2

Ephesians 3 in the UGV3

Ephesians 3 in the VBL

Ephesians 3 in the VDCC

Ephesians 3 in the YALU

Ephesians 3 in the YAPE

Ephesians 3 in the YBVTP

Ephesians 3 in the ZBP