Exodus 24 (BOGWICC)
1 Ndipo Yehova anati kwa Mose, “Bwera ku phiri kuno kwa Yehova, iwe pamodzi ndi Aaroni, Nadabu, Abihu ndi akuluakulu a Israeli makumi asanu ndi awiri. Enanu mundipembedze muli chapatali. 2 Koma Mose yekha ayandikire Yehova, ndipo enawo asayandikire. Komanso anthu ena onse asakwere nawe ku phiri kuno.” 3 Tsono Mose anapita kukawuza anthu mawu onse a Yehova ndi malamulo onse, ndipo anthu onse anayankha mogwirizana kuti, “Tidzachita zonse zimene Yehova wanena.” 4 Ndipo Mose analemba zonse zimene Yehova ananena.Mmawa mwake Mose anadzuka nayamba kumanga guwa lansembe mʼmunsi mwa phirilo ndipo anayimika miyala khumi ndi iwiri ngati zipilala kuyimira mafuko khumi ndi awiri a Israeli. 5 Kenaka Mose anatuma Aisraeli achinyamata kuti aphe ndi kukapereka kwa Yehova nsembe zopsereza zachiyanjano. 6 Mose anatenga theka la magazi ndi kuyika mʼmbale, ndipo theka linalo analiwaza pa guwa lansembe. 7 Anatenganso Buku la Chipangano ndi kuwerengera anthu. Anthuwo anayankha kuti, “Zonse zimene Yehova wanena tamva, ndipo tidzazichita.” 8 Kenaka Mose anatenga magazi, nawaza anthuwo ndipo anati, “Awa ndi magazi a pangano limene Yehova wapanga ndi inu molingana ndi mawu ake onsewa.” 9 Kenaka Mose pamodzi ndi Aaroni, Nadabu, Abihu ndi akuluakulu makumi asanu ndi awiri a Israeli aja anakwera ku phiri, 10 ndipo anaona Mulungu wa Israeli. Pansi pa mapazi ake panali njira yoyendamo yopangidwa ndi mwala wa safiro woyalidwa bwino wa maonekedwe owala ngati thambo. 11 Ngakhale anaona Yehova koma sanafe, mʼmalo mwake anadya ndi kumwa. 12 Yehova anati kwa Mose, “Bwera kwa ine ku phiri kuno, ndipo udikire konkuno. Ndidzakupatsa miyala imene ndalembapo malemba kuti ndiwaphunzitse.” 13 Ndipo anayamba ulendo wopita ku phiri la Mulungu pamodzi ndi womuthandiza wake Yoswa. 14 Apa nʼkuti Mose atawawuza akuluakulu aja kuti, “Mudikire pano mpaka titabweranso. Aaroni ndi Huri ali nanu, aliyense amene ali ndi milandu apite kwa iwo.” 15 Mose atakwera ku phiri kuja mtambo unaphimba phirilo. 16 Ulemerero wa Yehova unakhala pa phiri la Sinai, ndipo mtambo unaphimba phirilo kwa masiku asanu ndi limodzi. Pa tsiku lachisanu ndi chiwiri Yehova anayitana Mose kuchokera mu mtambowo. 17 Ulemerero wa Yehova uja unkaoneka ngati malawi a moto pamwamba pa phirilo. 18 Ndipo Mose analowa mʼmitambo nakwera phiri. Iye anakhala ku phiriko 40 usana ndi usiku.
In Other Versions
Exodus 24 in the ANGEFD
Exodus 24 in the ANTPNG2D
Exodus 24 in the AS21
Exodus 24 in the BAGH
Exodus 24 in the BBPNG
Exodus 24 in the BBT1E
Exodus 24 in the BDS
Exodus 24 in the BEV
Exodus 24 in the BHAD
Exodus 24 in the BIB
Exodus 24 in the BLPT
Exodus 24 in the BNT
Exodus 24 in the BNTABOOT
Exodus 24 in the BNTLV
Exodus 24 in the BOATCB
Exodus 24 in the BOATCB2
Exodus 24 in the BOBCV
Exodus 24 in the BOCNT
Exodus 24 in the BOECS
Exodus 24 in the BOHCB
Exodus 24 in the BOHCV
Exodus 24 in the BOHLNT
Exodus 24 in the BOHNTLTAL
Exodus 24 in the BOICB
Exodus 24 in the BOILNTAP
Exodus 24 in the BOITCV
Exodus 24 in the BOKCV
Exodus 24 in the BOKCV2
Exodus 24 in the BOKHWOG
Exodus 24 in the BOKSSV
Exodus 24 in the BOLCB
Exodus 24 in the BOLCB2
Exodus 24 in the BOMCV
Exodus 24 in the BONAV
Exodus 24 in the BONCB
Exodus 24 in the BONLT
Exodus 24 in the BONUT2
Exodus 24 in the BOPLNT
Exodus 24 in the BOSCB
Exodus 24 in the BOSNC
Exodus 24 in the BOTLNT
Exodus 24 in the BOVCB
Exodus 24 in the BOYCB
Exodus 24 in the BPBB
Exodus 24 in the BPH
Exodus 24 in the BSB
Exodus 24 in the CCB
Exodus 24 in the CUV
Exodus 24 in the CUVS
Exodus 24 in the DBT
Exodus 24 in the DGDNT
Exodus 24 in the DHNT
Exodus 24 in the DNT
Exodus 24 in the ELBE
Exodus 24 in the EMTV
Exodus 24 in the ESV
Exodus 24 in the FBV
Exodus 24 in the FEB
Exodus 24 in the GGMNT
Exodus 24 in the GNT
Exodus 24 in the HARY
Exodus 24 in the HNT
Exodus 24 in the IRVA
Exodus 24 in the IRVB
Exodus 24 in the IRVG
Exodus 24 in the IRVH
Exodus 24 in the IRVK
Exodus 24 in the IRVM
Exodus 24 in the IRVM2
Exodus 24 in the IRVO
Exodus 24 in the IRVP
Exodus 24 in the IRVT
Exodus 24 in the IRVT2
Exodus 24 in the IRVU
Exodus 24 in the ISVN
Exodus 24 in the JSNT
Exodus 24 in the KAPI
Exodus 24 in the KBT1ETNIK
Exodus 24 in the KBV
Exodus 24 in the KJV
Exodus 24 in the KNFD
Exodus 24 in the LBA
Exodus 24 in the LBLA
Exodus 24 in the LNT
Exodus 24 in the LSV
Exodus 24 in the MAAL
Exodus 24 in the MBV
Exodus 24 in the MBV2
Exodus 24 in the MHNT
Exodus 24 in the MKNFD
Exodus 24 in the MNG
Exodus 24 in the MNT
Exodus 24 in the MNT2
Exodus 24 in the MRS1T
Exodus 24 in the NAA
Exodus 24 in the NASB
Exodus 24 in the NBLA
Exodus 24 in the NBS
Exodus 24 in the NBVTP
Exodus 24 in the NET2
Exodus 24 in the NIV11
Exodus 24 in the NNT
Exodus 24 in the NNT2
Exodus 24 in the NNT3
Exodus 24 in the PDDPT
Exodus 24 in the PFNT
Exodus 24 in the RMNT
Exodus 24 in the SBIAS
Exodus 24 in the SBIBS
Exodus 24 in the SBIBS2
Exodus 24 in the SBICS
Exodus 24 in the SBIDS
Exodus 24 in the SBIGS
Exodus 24 in the SBIHS
Exodus 24 in the SBIIS
Exodus 24 in the SBIIS2
Exodus 24 in the SBIIS3
Exodus 24 in the SBIKS
Exodus 24 in the SBIKS2
Exodus 24 in the SBIMS
Exodus 24 in the SBIOS
Exodus 24 in the SBIPS
Exodus 24 in the SBISS
Exodus 24 in the SBITS
Exodus 24 in the SBITS2
Exodus 24 in the SBITS3
Exodus 24 in the SBITS4
Exodus 24 in the SBIUS
Exodus 24 in the SBIVS
Exodus 24 in the SBT
Exodus 24 in the SBT1E
Exodus 24 in the SCHL
Exodus 24 in the SNT
Exodus 24 in the SUSU
Exodus 24 in the SUSU2
Exodus 24 in the SYNO
Exodus 24 in the TBIAOTANT
Exodus 24 in the TBT1E
Exodus 24 in the TBT1E2
Exodus 24 in the TFTIP
Exodus 24 in the TFTU
Exodus 24 in the TGNTATF3T
Exodus 24 in the THAI
Exodus 24 in the TNFD
Exodus 24 in the TNT
Exodus 24 in the TNTIK
Exodus 24 in the TNTIL
Exodus 24 in the TNTIN
Exodus 24 in the TNTIP
Exodus 24 in the TNTIZ
Exodus 24 in the TOMA
Exodus 24 in the TTENT
Exodus 24 in the UBG
Exodus 24 in the UGV
Exodus 24 in the UGV2
Exodus 24 in the UGV3
Exodus 24 in the VBL
Exodus 24 in the VDCC
Exodus 24 in the YALU
Exodus 24 in the YAPE
Exodus 24 in the YBVTP
Exodus 24 in the ZBP